Apapa ndiri mbariyako or mntaniwa atanva audio yakoyi akunva kukoma mot utamatero anthu akukonda kwambiri the fact u hv say to day congrats Mr Layton big up tufuna chirungamo choncho
Iwe Lyton Mangochi apa wanena mfundo osati yamasewera. Ndamvera each and every sentence looking for a mistake koma mwalankhula zaufumu weniweni. I love you
Nkhani iyi ya Straight forward 🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌 ulemu wanu uku kulakhura mwabnzeru manganya or tsiku limodzi lopedzeka pa mwambo oyasa ma candle yoooo or tsiku loyakhulapo zokhudza imfa ya chilimba mmmmm Ambuye akukhululukireni iwe ndi mpeni othwa konse konse iiiih Chilima Rest well tidzakulirani mpaka kale 😭😭😭😭😭😭
Zanzeru ndizochepa umu kuti mumumvele bwinobwino statement yakeyi yachoka kwa iye manganya mwini kuti awuze mtundu wa anthu kuti akazamati ndine wa mcp anthu asazazizimuke kwambili, Ndipo chakwera ali mommu this is propaganda of mcp
Fundo zinazo za mangochi ndi zopoila, amalawi tikuyenera kudziwa kuti tonse ndi amalawi koma zinkhulupiro ndi zotsiyana,kutsapedzaeka a Micheal usi ku candle 🕯️ light sichifukwa choti anene kuti si wa utm koma anene zifukwa zina
Iwe mangochi umandibowa pazambiri koma leroli wakamba chilungamo ❤❤ the spirit
😂😂😂
This is straight forward talk and advice
Munthuyu nthawi zina amalankhula zoduka mutu koma lelo walankhula chilungamo ndakukonda Mr mango hi for this audio.
Galu ndi gula manganya siwa utm komaso anamupeleka chilima
Apapa ndiri mbariyako or mntaniwa atanva audio yakoyi akunva kukoma mot utamatero anthu akukonda kwambiri the fact u hv say to day congrats Mr Layton big up tufuna chirungamo choncho
Mwayankhula chilungamo malumee,May God bless you!!! Ameneyu adzazunzika nao mzimu wa Chilima
Iwe Lyton Mangochi apa wanena mfundo osati yamasewera. Ndamvera each and every sentence looking for a mistake koma mwalankhula zaufumu weniweni.
I love you
Nkhani iyi ya Straight forward 🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌🙌 ulemu wanu uku kulakhura mwabnzeru manganya or tsiku limodzi lopedzeka pa mwambo oyasa ma candle yoooo or tsiku loyakhulapo zokhudza imfa ya chilimba mmmmm Ambuye akukhululukireni iwe ndi mpeni othwa konse konse iiiih Chilima Rest well tidzakulirani mpaka kale 😭😭😭😭😭😭
I think you are coming back to your senses Mr Mangochi.... Keep it up.
Well composed speech keep it up Mr Mangochi. Teach him a lesson
Uthenga opanda chigamba, apa ndiye chilungamo.
Mr Lyton Mangochi ulemu wanu mwayankhula chilungamo God bless you Mr Mangochi
100%. Usi si wa UTM. Angofuna kusokoneza UTM yo.
Tilitonse mau olawura asiye.
Ngati zolankhura alibe angosiya. zamadirama ife sitikufuna.
Ine ndili wakwanu. Kumwitu koku Karonga. Komam'sasiye kudziwitsa anthu choonadi, monga m'nachitira pakatipa.
Tinali kuganiza kuti nanutso mwagudwa.
Ine umandinyasa heavy kma lero Mutu wako wayamba kugwila ntchito ❤zanzeru
Someone hit Like for me
Lero wayankhula mwanzelutu a bro, more fire 🔥
Mqngochi your right ukunena zenizeni congratulations bro
Bwana Lyton mangochi lero mwakambako mfundo zomveka bwino ulemu wanu
Madala madala tsopano, munasowatu😁💗💗
Today it's ur best audio mr mangoch best audio ever muuzenidi achose kachiwanda ka ma drama kkkk
Mwanena zoona Mr Mangochi. Manganya akufuna Kuba Chipani!
Anali ngati Petro yemwe amamuonera Yesu patali ali pakati pa adani kumfunsa uyunso anali waiwo amvereke akunama sindikumudziwa ine ameneyo.
Ndipo bwana Mangochi mwang'alula ulemu wanu akulu awa eeeish atipepelesa sure
mwayankhula bwino kwambili ngati zikadi wa Malawi❤❤❤❤
Well spoken.....
Apa pokha Usi avomereza chilungamo kuti anthu alindi maso ndipo amaona ndithu iiiii
Well said big man,thumb up🔥
Chilungamo chimawawa koma izizi ndi zoona..Malumewa SI a UTM
Mr Lyton excellent spoken keepitup
Mr mangochi took his time to recharge and came back stronger 💪
Apa nde wang'alula zeni zeni momveka bwino dziko akulitengela chibwana
Lerotu Mr Mangochi mwakambatu mfundo zomveka bwino. Ulemu wanu manganya komwe aliko amve. Chipan chathiko Ife ayi.
AMangochi,apatu mwaonesa umunthu.ndipo mukukhala ngati siinu a Mangochi,koma zikomo. coonadi ncofunika
Bravo, wayamba kuyankhula mfundo zenizeni, zamphamvu.
Well spoken 🔥🔥
Apa ndiye wayanbapo kumeneko zanzeru
Uku tu nde kuyankhula kopanda chigamba mau mau. pena nso atipeperetsa a Usi wa Aaaaa inu
Apa wayankhulatu za nzelu even BON Kalindo ajuyamikila
Very good Mr Mangochi good Message ❤
Mr. Mangochi awuxeni abambo amenewa chifukwa ndiye akupanga. Zinthu zobowa kwabasi.kasatana kachabe chabe kauzeni kamvetsese
@@TheresaNtodwa exactly
Powerful advice from Mr Mangochi.
Mwayakhura fundo ❤
Ndakuombela mmanja mangochi apa pokha chilungamo chimamasula usi ndi wa MCP
Powerful message
Lyton Mangochi apa walankhulatu ngati munthumuuzeni usi akutitenga ngati ife zitsilu hule wamunthu
Ife UTM sangatigulitse .... UTM yachilima ija ilipobe ija yachina Kaliati
Straight talk keep it up
Good speaking mr Lyton mangochi
Long live Impi Biyeni
Ay Mr mangochi apa pokha mwayesesa kulakhula kwa nzeru
Koma apapa zikumveka bwino kwabas Mangochi walankhula mwanzeru chifukwa Manganya samamukonda Chilima .
Listening Keenly .....kambani ndithu
Iweso ukuti musiyeni usi ndwe Galu team ya Mr chikangawa fiti agalu lnu
Good Message Mr mangochi
Welcome back Mr Mangochi
Michael Usi the big man
You. have said. the truth utsi. is not for utm
Respect
Let the Vice President be please !!!
Mangochi apa nde wandilankhulila ndithu angofusa kutisokoneza ife a UTM
Apa mwayankhula big.
Osaka asowa poyambira.
For the first time I am happy with you Mr Mangochi pa zanzeru zomwe mwalankhula apa.
I'm sure kuti we're expecting more from you
Amangochi mukafuna mudye za ausi .
very true mangochi
Zanzeru ndizochepa umu kuti mumumvele bwinobwino statement yakeyi yachoka kwa iye manganya mwini kuti awuze mtundu wa anthu kuti akazamati ndine wa mcp anthu asazazizimuke kwambili,
Ndipo chakwera ali mommu this is propaganda of mcp
Mangochi lero mwakambako zanzelu
True talking mangochi
More fire
Well spoken
Wakamba zazelu
Bwanji osakayendera ma office a NRB ku southern, eastern and northern regions kuti anthu alandire za unzika mu nthawi yabwino?
Akanangopanga za tikufzlanji asamasokoneze anthu
Apo Nde wanena zoona a usi Sia UTM
Chikangawa will never break the movement's resolve
Resign, Mr Usi too much drama,
Well said
Fundo zinazo za mangochi ndi zopoila, amalawi tikuyenera kudziwa kuti tonse ndi amalawi koma zinkhulupiro ndi zotsiyana,kutsapedzaeka a Micheal usi ku candle 🕯️ light sichifukwa choti anene kuti si wa utm koma anene zifukwa zina
Bwana mangochi kubwera kumeneko USI ndi wa mcp akungobisara
Mwayamkhula bwino sure
Amangochi lero mwayankhula chilungamo pitilizani
Manganya ndichisilu galu ndi mozi mwa anthu ogwesa ndege ameneyo😮😮
Ndwochenjela mopusa ameneyo
manganya watikwana kale.Mr Mangochi mwabwera
Apo wabaya
Good good lyton
Mangochi go deeper iweeeeeeee
Lyton. mwalankhula zan,zelu. Kwambiri kwambjri. takuyamikila kunokuchitipa
Apa nde mwayankhula zoonadi 100%ausi si a UTM zinayamba kuwoneka kale kale Chilima alipo
Mumafuna muzidya naye ngati achipani muziyenda naye mwauponda. Musiyeni zanu agwire ntchito ya boma mufune musafune president wa UTM ndi Usi
Mangochi lero apa nde waza mwakathithi
Zoona,kuyimba nyimbo zachinamwali pamsonkhano
aLyton APO mwalankhu zoona avaice si a UTM ayi
Zangongore zakezo tilibenazotchito koma asamatinamizekuti ndi wa UTM ai sitikumudziwaife
Manganya palibe akulakwitsa and zomamena kut sanali wa UTM kapena kut si wa UTM ndikulakwa chabe.Mvuto lomwe Malawi tili nalo ndi nsanje.Chilima anamutenga chifukwa chani Micheal usi ngat sanali ofunikila?.Amene akudzimva UTM kwambiriwo bwanj Chilima sanawaike pa vice president?.Nsanje kusavomeleza phunzirani makape inu
Mangochi wandigwira mtima koopsa
Mau a mphamvu(powerful voice)
Zoona zake
Mangochi go deeper iweeeeeeee 😂😂😂😂😂
🔥🔥🔥🔥♥️♥️♥️💪💪
Wayakhula ndithu za zeru
Leroditu alangula zaseru
Vice State President, Malawians expect change from rut to prosperity:Genuine philanthropy and patriotism.
Mau a chilungamo