Sulemani Kwa ine ali ndende ngatMalema wa SA. Kulan khula mosaopa. Sinamvepo zot akufuna kumuchita impeach. Amantulusa koma amalowanso. Kuno vuto ndi chani
We leaving in a crazy World whereby people are die like flies cos of hunger ,diseases due to lack medical equipment in hospitals, no fuel in fuel saver stations. With people like Suleman and other dpp members mcp will see what shaved Guinea fowl.
tikusowa ma fees sukulu ikukanika nkumene, may the Lord help kwa ena onse amene mumatenga dzanja lanu kuthandiza ana ovutika munjila zosiyana siyana, .. sorry ndangopezelapo mwai kuti l can speak on this thank you
Mukuthatu mau apa nde magesi tizizangounikila pokudya pokha paja ndi zomwe mmapanga, dpp inasinthapo kukhala (diesel petrol palibe) nde muzapangeso ma albino analibe chitetezo muzabwelezeso tizathamangisanapo
Ineyo, I admire Sameer Suleman, the courage he has APM my vote
Bwana Suleiman osawalekelere anawa Luka from India
Naye Chakwera wasunga voti yake kuti akavotere Professor Peter Munthalika
Akulu inu chidwi chanu ndi chani?
Anthu akunena zinthu zomwe zikuchitika
Nde kummangako azimmanga pa zifukwa ziti?
Okay inuyo mukufuna kuti anthu azibvutikabe?
Mesa muli mmalawi mommuno
Mukafuna kuti muonetse anthu zomwe anthu Ena akuchita osanena zambiri
Ingonenani kuti kwachitika Idzi nde tikuti mukanva
Mutiudze maganizo anu monga inu a Malawi Eni dziko
Ndizoona kuti boma la mcp mosogozedwa ndi achakwera laononga ziko la Malawi mu zinthu zonse koma ndimafuna ndipemphe nawo ngati mkotheka andale onse zipani zonse titati tisiye ntchitidwe olalatirana sizingatithandize sizingatisungire ulemuu
Chimwendo akut nayeso avotera Peter Mutharika 😂
😂😂
Eya or so kumkuyu amatelo kuti voti yake ndi ya peter basi waganiza mofasa 😅
Kkkkkkkkkkkkkkk aganizeditu amenewo ,asanabense mavoti
Km ofunika MCP kuibana isazapangeso ndale evils
@@AusteenSumael inesotu ndimaganiza chonchotu Kaya sizingatheke eshi MCP ndilibe nayo mawu
Brother, sangawamange, palibe chifukwa chowasakila a police, akinena Chilungamo chokha chokha. APM basi, dziko lawonongeka economy ndi boma lake la MCP.
Sulemani Kwa ine ali ndende ngatMalema wa SA. Kulan khula mosaopa. Sinamvepo zot akufuna kumuchita impeach. Amantulusa koma amalowanso. Kuno vuto ndi chani
Titani poti tatani kale,, piter wapita kale pampando
Adad omweo on point 💙💙💙💙💙💙💙💙💙💙💫🌈🌈🌈🌈🌈🌈
Great
Thank u lord
😂😂❤❤ Kma Yaaaaaaaaa
🎉🎉 woyeeee
More fire wolemekezeka a Samir suleman God bless you
Koma Suleman🙆🙆🙆😀😀😀😀
We leaving in a crazy World whereby people are die like flies cos of hunger ,diseases due to lack medical equipment in hospitals, no fuel in fuel saver stations. With people like Suleman and other dpp members mcp will see what shaved Guinea fowl.
Tikufuna Tikufuna Tikufun adadi
Suleman woyeeee 🎉🎉
Selemani ndiwe katundu serious ❤
Chilima uja asanamuphe 😅😅😅😅
tikusowa ma fees sukulu ikukanika nkumene, may the Lord help kwa ena onse amene mumatenga dzanja lanu kuthandiza ana ovutika munjila zosiyana siyana, .. sorry ndangopezelapo mwai kuti l can speak on this thank you
Aaah kumangidwa kwachani waba chandani kuti ammange.tsogoleri wadzikoyo simunthu?
ndipo ngati sakuchichita bwino anthu azingosekelera cz of ndi president?
MUSINTHE MITU YANKHANI YOMWE MUMALEMBA PAMWAMBAPO , MUMAKHALA NGATI MUKULIMBIKITSA KUTI MCP IDZIMANGA ANTHU , CHONDE MUSINTHE MAU.OMWE MUMALEMBA PAMUTUNWANLHANI TIRI MU DIMOKALASI ANTHU AKUYENERA KUYANKHULA NNDIYE MUSAMASOGOZE MAU OTI KAYA SAWAMANGA A MCP AKAMAONA MAU AMENEWO MUMAKHALANGATI MUKUWALIMBIKITSA ZOMANGA ANTHU
APM,vote yanga.
Nice
Ndikubwerezanso kuti,mlungu akutsogoleleni,zonsezi mlungu akuona
Dzikoli likufunika anthu olimba mtima chonchi
Tiona zonse end of September 2025, ngati ena sazazimangila ndi mwai kkkkk
Ana amunatu awa, 😂😂😂 oowooo!!!
Aaaa iyi mcp kuyitsekekela tibwelela ku CHIPANI CHIMODZI
❤dpp.akafuna kumanga munthu akamange chakwera .
DPP woyeeee
Mr suleman yooh😂❤❤❤ Dpp woyeeee ❤❤❤❤❤❤❤
Summies iwe ndi 1
Apm my only vote
Kodi munthu akamayakhula mutinso mwina amnanga mukufuna anthu adziopa nyasizi zikuchitikazi, ife zikutinyasa awa palibe zomanganso, chilungamo chidutse ngati madzi
DPP chipani cha ulemelelo ,chimanga chinali ponse ponse
Akanakhala kuti Suleiman yo ndi m'busa akadakapulumutsa anthu ambiri, anthu amene tikuwafuna ndi mm church ndioterewa osaopa pakutumikila
My vote Apm Boma. iLoooooo 💙💙
❤❤❤
Tichosana 😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Suleiman 🔥 🔥
Ife Ana adad tiliphee❤❤
Koma SULEMANI mmmmmm , wam'maliza chakwera,eish!
siwamavuvu koma ndi odziwa kumasula anthu osamabisa
Uyu ndimunthu wankulu palibeso ngakhale MCP komwe iliko ikudxiwa
Machine 🎉
Dpp my vote
Ndinavotela MCP koma to much magadzi kwambiri chili chonse zikwanje Boma lanji limenelo guys
Utsogoleri amapereka ndimulungu
KO ma yaaaa zilikotu
Ana achepa akangomva kt kuli DPP km aziona 2025 ine charles wachnyamata osaopa tiyeni tiipanse moto DPP DPP DPP moto kt buuuuuuuuuu!
boma koma lomweli la dpp
Samezy ndikatundu
Iweyo ndamene ukufina kt amumange
Mulungu akutetezeleni adadi mutiombore mumavuto asatana amene alipo chipani choyipa cha emusip Galu zokhazokha emusip ikungo gunda gunda azimayi
kkkkkkk emusip kenako kugunga gunda kkkkkk bravo
Kodi Mesa zidakukanikani kale? Or kutsutsa kwakukanikani wanu ndi mkwiyo, nsanje ndi kaduka. Okhulupirira inu ndani?
DPP akulu osanama DZIKO limayenda bwino kwambili Koma pano mcp Nyasi zachabechabe
Abwana ngati simulima ndiye kuti MCP yikulamuradi bwino Koma Ngati mumalima ndiye kuti bola DPP yidali bwino kwambiri kupotsa mukuti chakwera ndiye eeeesh olo geni pano anthu tavutika nayo zedi ndiye kunena za MCP mutimalidza tonse wosapota DPP olo UDF ndinthu izi zichoke ndinthu abwere adad basi mwene tizilima chimanga ngati nthawi yimeneyo
Mcp kwawo kwatha
Motor kuti buu!!
Lovely party DPP
Peter ndiboma ndipo olo asapange alliance mkatundu uyu
Suleiman akuyankhula...
Kkkkkk anthu sakuyankha akungoyang,ana
Uli chitesi iwe ukuwona yayi umo wanthu wakuwuskila Chara m'mwamba chasanje iwe umva m'bebe chaka chale ndi chinocho
Dpp boma 2025 iwe unya
@SalatiKiddie ku Thyolo komweko
Kuli ma Band uku?
Ayi😂😂😂
Azipanga misonkhano panopa bwana chakwera akayamba misonkhano mutsekula mmimba
Not Pule Mr Chikangawa
Dziribwino apeter alowe mubwalo
Apa nbiye zafikikapo muti sathawa anthuwa
A P M ndi moto kuti buuu❤
DPP boma ilooooooo 🎉🎉🎉
Man awa ndimachi
DPP YOMWEYO
dpp inawina kare kwasara ndikupita kukatilamulila bas
mballi jashi jangankwasaka adadi
APM BOMA
Boma🎉
Tsogoleri wokupha chikangawa palibe zomangana apa
Osaphethira !!!!!!
Mrs namakhwa from mj adad woyeeeeee
Mukuthatu mau apa nde magesi tizizangounikila pokudya pokha paja ndi zomwe mmapanga, dpp inasinthapo kukhala (diesel petrol palibe) nde muzapangeso ma albino analibe chitetezo muzabwelezeso tizathamangisanapo
MCP chitetezo chonwe anapreka kwa ma albino ndi chotani?musatinamize imene ija inali propaganda amaoha ndi a Mcp
Adadi oyeee
Adad woyeeeee
Zilibwino Dpp boma😅😅😅
Chipani chokoma ichi
Suleiman 🎉
Boma ndilomweli ,,,, tingosintha chipani cholamula
Zonazake zimenezo adad bwalo
Amangidwa chifukwa chani?
A Peter boma2025
Boma iloo
Pangolin wa msena + mulanje uyu. .
Mbamba APM
Moto kuti buuu
Dpp chipani changa
Chiuta atsogolele
Mbambande Dpp
Aliyense amalankhula
Amanyozana koma kuseliku amadyela limodzi
adadi woyyyyyy
Agogo kkkkkk boza mukuluwe
Umafune asamayankhule watumiza audio imeneyi panyeropako