- 270
- 943 750
Dreams Media MW
South Africa
Приєднався 7 лип 2023
Trending News Today 📰 Stay informed with our daily news updates, in-depth analysis, and expert commentary on:
🔥 Politics
🎬 Entertainment
📱 Tech
👥 Lifestyle
Subscribe now and stay ahead of the curve
🔥 Politics
🎬 Entertainment
📱 Tech
👥 Lifestyle
Subscribe now and stay ahead of the curve
KU MALAWI NDE KUKUCHITIKA ZAMBIRI , TAWONERANI MKHANI ZA LERO PA 30/11/24
KU MALAWI NDE KUKUCHITIKA ZAMBIRI , TAWONERANI MKHANI ZA LERO PA 30/11/24
Переглядів: 200
Відео
ANTHU AYAMIKIRA KULIMBA MTIMA KWA SAMEER SOLEMAN , IWO AMAYAMKHULA MOSAWOPA NDI MOPANDA MANTHA
Переглядів 2,1 тис.6 годин тому
ANTHU AYAMIKIRA KULIMBA MTIMA KWA SAMEER SOLEMAN , IWO AMAYAMKHULA MOSAWOPA NDI MOPANDA MANTHA
COMRADE MTANYIWA NDE WAULULA ZISISI ZIKULUZIKULU PA LIMPOMPO FM 📻
Переглядів 14 тис.8 годин тому
COMRADE MTANYIWA NDE WAULULA ZISISI ZIKULUZIKULU PA LIMPOMPO FM 📻
PAN’GONON’GONO KU PARLIAMENT KUKANAYAMBIKA NDEWU, SAMEER SOLEMAN ANAFUFUMA KOWOPSA
Переглядів 3 тис.2 години тому
PAN’GONON’GONO KU PARLIAMENT KUKANAYAMBIKA NDEWU, SAMEER SOLEMAN ANAFUFUMA KOWOPSA
ZODABWITSA NDE ZIKUPITILILA KUCHITIKA PA MALAWI PANO ,TAWONERANI MKHANI ZA LERO PA 29/11/24
Переглядів 1,7 тис.2 години тому
ZODABWITSA NDE ZIKUPITILILA KUCHITIKA PA MALAWI PANO ,TAWONERANI MKHANI ZA LERO PA 29/11/24
PASTOR SHUMBAH NAYE WALOWA YA BON KALINDO ! KUN’GALULA BASI ,
Переглядів 1,3 тис.2 години тому
PASTOR SHUMBAH NAYE WALOWA YA BON KALINDO ! KUN’GALULA BASI ,
KU PARLIAMENT NAKO NDE KWAYAKA MOTO LERO
Переглядів 1,5 тис.2 години тому
KU PARLIAMENT NAKO NDE KWAYAKA MOTO LERO
KOMATU MANGANYA SADZATHEKA ! UYUYU ALI NDI CHIKOKA NDITHUU
Переглядів 5972 години тому
KOMATU MANGANYA SADZATHEKA ! UYUYU ALI NDI CHIKOKA NDITHUU
KOMA LIMPOMPO FM NDI COMRADE MTANYIWA NDE YANG’ALULA MOSAWONA MKHOPE LERO
Переглядів 16 тис.2 години тому
KOMA LIMPOMPO FM NDI COMRADE MTANYIWA NDE YANG’ALULA MOSAWONA MKHOPE LERO
ANTHU ADABWA NDI ZOKAMBA ZA AKUKU AKULU A MBC TELEVISION KUTI KODI BASI NDEKUTI AMANGODANA NDI DPP?
Переглядів 7692 години тому
ANTHU ADABWA NDI ZOKAMBA ZA AKUKU AKULU A MBC TELEVISION KUTI KODI BASI NDEKUTI AMANGODANA NDI DPP?
ZOMWE WAYAMKHULA BOB KALINDO LERO PA 29/11/24
Переглядів 8462 години тому
ZOMWE WAYAMKHULA BOB KALINDO LERO PA 29/11/24
ZINA MWA ZOMWE APHUNGU ATHU AKUKAMBIRANA MU NYUMBA YA MALAMULO LERO PA 28/11/24
Переглядів 4454 години тому
ZINA MWA ZOMWE APHUNGU ATHU AKUKAMBIRANA MU NYUMBA YA MALAMULO LERO PA 28/11/24
ANTHU NDIWODABWA NDI M’MOMWE AKUMAMUGULILA BONYA A MICHAEL USI MISIKAMU.
Переглядів 2 тис.4 години тому
ANTHU NDIWODABWA NDI M’MOMWE AKUMAMUGULILA BONYA A MICHAEL USI MISIKAMU.
PAMALAWI PANO PAKUCHITIKA ZAMBIRI TAWONERANI MKHANI ZA LERO PA 28/11/24
Переглядів 6 тис.4 години тому
PAMALAWI PANO PAKUCHITIKA ZAMBIRI TAWONERANI MKHANI ZA LERO PA 28/11/24
ANTHU ADABWA NDI ZOMWE ANAYAMKHULA A BEN PHILI KU PARLIAMENT DZULO
Переглядів 9 тис.4 години тому
ANTHU ADABWA NDI ZOMWE ANAYAMKHULA A BEN PHILI KU PARLIAMENT DZULO
MIKHULA N’GONA IYIYI IPHWETEKANA CHAKA CHAKE NDI CHINO :SI MMENE KULILI
Переглядів 9674 години тому
MIKHULA N’GONA IYIYI IPHWETEKANA CHAKA CHAKE NDI CHINO :SI MMENE KULILI
PETER MUNTHALIKA APHWETEKA GULU! UYU NDI KA SONGO NDITHU!
Переглядів 10 тис.4 години тому
PETER MUNTHALIKA APHWETEKA GULU! UYU NDI KA SONGO NDITHU!
KUYANKHULA KWA BON KALINDO LERO PA 28/11/24
Переглядів 4044 години тому
KUYANKHULA KWA BON KALINDO LERO PA 28/11/24
PETER MUNTHALIKA SI MUNTHU WAMBA ! ANTHU ADABWA NDI ZOMWE WAYAMKHULA KU MWAMZA
Переглядів 3,1 тис.4 години тому
PETER MUNTHALIKA SI MUNTHU WAMBA ! ANTHU ADABWA NDI ZOMWE WAYAMKHULA KU MWAMZA
KOMATU DPP NDI SAMEER SOLEMAN APHWETEKA GULU , MPAKA PAMENEPO? TIDZITI SAMAWOPA?
Переглядів 8 тис.7 годин тому
KOMATU DPP NDI SAMEER SOLEMAN APHWETEKA GULU , MPAKA PAMENEPO? TIDZITI SAMAWOPA?
KWIMBI LA ANTHU KAYIMA MBALI MWASEWU KUDIKIRA PETER MUNTHALIKA , KWAVUTIRATU KUMWANZA
Переглядів 2,7 тис.7 годин тому
KWIMBI LA ANTHU KAYIMA MBALI MWASEWU KUDIKIRA PETER MUNTHALIKA , KWAVUTIRATU KUMWANZA
ANTHU ADABWA NDI ZOMWE ZACHITIKA KU MWANZA POMWE PETER MUNTHALIKA AMAFIKA KUMENEKU LERO
Переглядів 14 тис.7 годин тому
ANTHU ADABWA NDI ZOMWE ZACHITIKA KU MWANZA POMWE PETER MUNTHALIKA AMAFIKA KUMENEKU LERO
KU PARLIAMENT DZULO KUNAYAKA MOTO! BEN PHIRI NAYE ANATOKOTA
Переглядів 8 тис.7 годин тому
KU PARLIAMENT DZULO KUNAYAKA MOTO! BEN PHIRI NAYE ANATOKOTA
ZINA ZOMWE ZIDACHITIKA POKHAZIKITSA CHIPANI CHA UTM KU NJAMBA FREEDOM PARK CHAKA CHA 2018
Переглядів 5457 годин тому
ZINA ZOMWE ZIDACHITIKA POKHAZIKITSA CHIPANI CHA UTM KU NJAMBA FREEDOM PARK CHAKA CHA 2018
ZAMBILI ZIKUCHITIKA KU MALAWI KUNO ,ONERANI MU MKHANI ZA LERO PA 27 OCTOBER 2024
Переглядів 5967 годин тому
ZAMBILI ZIKUCHITIKA KU MALAWI KUNO ,ONERANI MU MKHANI ZA LERO PA 27 OCTOBER 2024
MPAKANA KUMUNENA CHAKWERA “ KUTI AMKANYAMULA MATUMBA KU CHIPIKU”? SOLEMAN ALIBE MANTHA ETI?
Переглядів 2,3 тис.7 годин тому
MPAKANA KUMUNENA CHAKWERA “ KUTI AMKANYAMULA MATUMBA KU CHIPIKU”? SOLEMAN ALIBE MANTHA ETI?
KUYAMKHULA KWA BON KALINDO LERO PA 27/11/24
Переглядів 1,9 тис.7 годин тому
KUYAMKHULA KWA BON KALINDO LERO PA 27/11/24
ZOKAMBIRANA ZA KUNYUMBA YA MALAMULO ZIKUPITILILABE LERO PA 26/11/24
Переглядів 6629 годин тому
ZOKAMBIRANA ZA KUNYUMBA YA MALAMULO ZIKUPITILILABE LERO PA 26/11/24
Uyu mulungu amudalitse sapanga nawo zachibwana Ulemu wake Ndithu
Sure mani ndikatundu
We need mps like Suleiman,osati ndwiiiii wina akufuna kuononga forex-opposition tulo too much eeeeish😢😢
Pangani muone, akuphwetekani boma sirimasewera ai, munapha anthu 21 ku mzuzu, anapindula nchiyani?
Osaopa sureiman
Iwe mbavanyai
Pauline ukunena chazeru Garu lwe
Ndipo ndiye tukusalilan kudya bwana osaopa osatopa osafooka
sanadye ko chibazi koma akadzangodya azacheteka awa........
Adad no one to compare with
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣NDE mphamvu yonyamula makatoniyo
Ku parliament timaudindo amatitenga ngati tapermanet kuti azizuza azawo tsiku lina timaudindo tizatha timaudindo ta 5years malawi ndiwa tonse
Awa chomwe anapitila Ku palayament amachidziwa osafoka osatopa
Kuda kuli ngati kokhalila kwa poto speaker uyu speaker amandinyasa komaso Chimwendo iweso ndi chisilu kwambili poti mukuchoka enanu or kwanu anthu sakakuvotelani sure
💪💪💪💪💪💪💪 Seleiman is big man more fire
Ameneyudi akuyenela kukhala laeda of opposition 100% percent
Timayamikila a big amenewa sanyengelela zopusa atapezeka mwa anthu 4 otelowa bwenzi parliament ikuyenda bwino
Adad omweo
Nonsense
Simbi ya moto
Suleiman amatha iwe chimwendo umatan kuyakha big man yo asanatuluke umawopa kut anakakupondatu kkkkk
Akatundu omanga ndimawaya ❤❤❤ we love you
Ndipo usafooke usatope our eyes are on you
Ine ku mtima kuti beeeeee bs
Mr ntanyiwa inuyo mulungu adzikudalitsan ndithu tikumva zambiri kamba kainuyo
Peoples radio 😅
.😅Blantyre rural west kumafunika ngat awa
Sameer 100%
mbambande big❤❤❤❤
Allah bless him sam
Ntanyiwa umakwana😂😂
Koma mcp kungokupeza iweyo eeeeeh akudya wamoyo 😂😂😂😂
Pakudzitenga nzelu adaputsa, idzi ndi MA qualified fool, anthu omadziwa choonadi koma kumachigulitsa, zitsiluuuu
Iwe chitsiluuuuu, during mutharikas tanure fuel adali PA 640, now chakwela 2530, and ukuti muthalika nzeru alibe?? Iwe chitsiluuuuu
Machine opangira machine anzake.
Apa ndiye wasonyeza umbuli wako iwe cadet wa malawi camera's pathako pamako refugee
Kabambe, Suleiman, Chisale,Ben phiri, komanso Mai kaliat, Mery Navicha
Big up 💪
Allah Subuhana Watala amusunge Sameer Suleiman
Uyu azimusungadi ndi moyo wa Heath kut next time azakhale read
M thubu Mgoroso,,,Big man wamkulu kwambiri Ben Phiri
Suleman ali ngati kabambe komaso chisale anthu amenewa be careful
ADA ASULEMAN NDI MKALADE KODI AMENE MWAKHARA NAWO MAKALADE AMAPANGA BWANJI AMAKHARA OLIMBA MTIMA SAOPA AYI ULEMU WAKE
Ameneyu ndiye ofuna kukhala leader of opposition kumalawiko
Uyuyu ndiujaotumizidwauja alibho kobas
Komaso muzinenaso anthu munampha kumzuzu kuja okwana 21 komaso kuno asazambwereso tizagenda ku mwanza
Ndipo mulungu amupatse moyo wautali ndikumutetezela mulungu atachotsela zigawenga zimenezi za MCP zi asatana zakupha kuba ndi kuononga
Iyu ndi pangolin weniweni
Suleman his heart akufunila amalawi sabwino Mulungu azikutetezani osati aphungu aboma angoti phwiii mu parlliament osayankhula ngati ali pa toilet kuvomereza chilichose choipa
Pangorine uyu
Big up