KOMA AMAYI A DPP AWA ANACHITA KUWALANDA MICROPHONE KU KASUNGU DZULO CHIFUKWA ANAYANKHURA MOKHADZULA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 24 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 109

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 2 місяці тому +15

    ❤❤❤❤ ngati Ku Malawi kuli chipani chomwe chingatukule Malawi ndi DPP basi 🤞💙

    • @LinlyMathewe
      @LinlyMathewe 16 днів тому +2

      😂😂😂Aaaaa anali kuti zaka 6 zija hu Dr Kabambe 2025 boma UTM my vote ❤❤❤❤

    • @samsonhavenoyayshonga2609
      @samsonhavenoyayshonga2609 12 днів тому

      Ineso ndikuona motero DPP ndiyokhayo chifukwa zitukuko timazionapo kale mu nthawi yawo

  • @LinlyMathewe
    @LinlyMathewe 16 днів тому +2

    UTM my vote ❤❤❤

  • @DominiqueChitimbe
    @DominiqueChitimbe 13 днів тому +2

    DPP vote

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 2 місяці тому +22

    Kumalawi kuli zipani koma chipani cha dpp amalawi mukachivesera bwino ziko litha kuyenda bwino kusiyana ndi ng'ona zilipozi mcp bambo wawo kamuzu oipa ana ake Chakwera chimwemdo kabwira gotani kumkuyu ndi ena ose oipa. Mcp or mwambi uja woti sayenda anabala mwana nayenda ku mcp kulibe wose akubereka ana osayenda.

  • @blairkaovwire-dc5zf
    @blairkaovwire-dc5zf 12 днів тому

    Facts cry mama,, APM my vote,,

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 15 днів тому +1

    Keept up mama ❤ mcp out 2025

  • @AntonyNgoma-p9h
    @AntonyNgoma-p9h 16 годин тому

    Dpp oyeeeee🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @RamseyYunusu-ls6mg
    @RamseyYunusu-ls6mg 2 місяці тому +12

    😂😂😂😂Exactly uyunde ndagwilizana naye uyu ndipo chakwera mphwala lake lothawila mbali imolizo losadulaso

    • @wisdomblack-u8n
      @wisdomblack-u8n 2 місяці тому +3

      Chakwela pa nsana paked man

    • @RamseyYunusu-ls6mg
      @RamseyYunusu-ls6mg 2 місяці тому

      @@wisdomblack-u8n man akulu awawa mutu mwawo munangozazamo manyi ngat chiwala palibe chomwe akuziwaso mkomwey

    • @bridgetmajor3646
      @bridgetmajor3646 15 днів тому

      😂😂😂😂😂😂

  • @AdamAhamad-k2i
    @AdamAhamad-k2i 2 місяці тому

    Mau akulu akoma akagonera DDP my vote ❤❤❤❤❤

  • @JamesALLi-m8i
    @JamesALLi-m8i 2 місяці тому +2

    Yes Apm is coming soon to be president of this country 😀 👏 🙌 😄 💙 😍 😀 dpp is my vote 🗳 boma 2025

  • @KondwaniMuonjeza
    @KondwaniMuonjeza 4 дні тому

    😂😂😂😂😂😂🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣Kulira kwa abwana

  • @MlambeLodge
    @MlambeLodge 2 місяці тому

    Sindikusintha my opinion apm❤❤❤❤❤boma

  • @ChapwetekaChauluka
    @ChapwetekaChauluka 16 днів тому +1

    Ati ku Chikangawa tinkapanga business yocheka matabwa lero MCP ikupangako business yocheka anthu kkkkk

  • @RosinaWakuthera
    @RosinaWakuthera 2 місяці тому +1

    Itchoke itchoke pakwawo😂😂😂😂😂

  • @ElnessMziya
    @ElnessMziya 7 днів тому

    Nsalu adyako chan

  • @JamiluSunday
    @JamiluSunday 2 місяці тому

    ❤❤❤ mumatiimilira azimayi

  • @MillicaBanda
    @MillicaBanda 2 місяці тому +1

    😂😂😂😂 wati kucheka anthu aaaaa zimayi uyu saopa chikagawa eeee kulinjaladi nkhotakota chimanga chinapita ndimadzi

    • @HannahTulizoh
      @HannahTulizoh 2 місяці тому

      Nde amene anachipititsa chimangacho ndi madzi unanva kuti ndi Chakwera?

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 2 місяці тому +3

    Kuchikangawa kale timapangako besnes yamatabwa pano a mcp ndi achakwera akupangako bessnes yocheka anthu .kukhesa mwadzi

  • @SibekoYusuf-m3f
    @SibekoYusuf-m3f 14 днів тому

    Makwana

  • @PeterLusewa-lk1bi
    @PeterLusewa-lk1bi 12 днів тому

    Koma 43 % ija ndiyoonadi apapa ndayamba kukhulupiliradi

  • @ShillaShamil-v2y
    @ShillaShamil-v2y 2 місяці тому

    My vote ❤❤❤❤❤

  • @Victoriabwaira
    @Victoriabwaira 2 місяці тому

    My vote uncle p

  • @MascotAnderson
    @MascotAnderson 2 місяці тому

    Koma muli chi vibe cha nyoooo apweteka ma team

  • @BerthaMkwinika
    @BerthaMkwinika 14 днів тому

    Zoopsa masiku otsiliza, zoona DPP ingamata pa home kunena ku KASUNGU???mwazolowera adpp inu etiiiii?? Chakwera mpaka 2090

  • @FulaKampoza
    @FulaKampoza 2 місяці тому

    Mumutiyimilira mayi osawopa ngati bakili mulizi tv

  • @wisdomblack-u8n
    @wisdomblack-u8n 2 місяці тому

    APM woooooo yeee eee eee eee we🕺🏻

  • @EmmanuelNasolo-o4c
    @EmmanuelNasolo-o4c 14 днів тому

    Fire 🔥 I can

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 місяці тому +1

    😂😂😂😂😂 Awuzeni anyapapiwo

  • @EmmanuelJester-q8x
    @EmmanuelJester-q8x 2 місяці тому

    please ladies and gentlemen don’t forget DPP 2025 comand am from mangochi but am stay South Africa

  • @EmertonNsato
    @EmertonNsato 2 місяці тому +2

    Chilungamo ndichomwecho awuzeni mcp ndiya kupha

  • @Andrewmwamadi
    @Andrewmwamadi 2 місяці тому +1

    Utm 4ever in my veins

  • @alexjeremanuel2541
    @alexjeremanuel2541 17 днів тому

    Mai ali bo uyu

  • @MaliyaMwantan
    @MaliyaMwantan 2 місяці тому

    Amen 🤝🤝🤝🤝

  • @MrJosephNkhata
    @MrJosephNkhata 2 місяці тому +3

    Tell us manifeso osati chiteze or chikangawa ndale zopoila

    • @YusufuYunusuSavielMakey
      @YusufuYunusuSavielMakey 2 місяці тому +1

      Nthawi inuo bwana cya manifestal

    • @LinlyMathewe
      @LinlyMathewe 16 днів тому +1

      Amene akudana ndi nkhani ya Chikangawa ongoziwiratu kuti ndi mwana wa njoka

  • @MaxwellChapulumuka
    @MaxwellChapulumuka 9 днів тому

    😊😊😊😊

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc 2 місяці тому

    Boma ilo 🔥🔥💪💪

  • @RudigerElectronics
    @RudigerElectronics 2 місяці тому

    Nice

  • @AlickKapapa
    @AlickKapapa 2 місяці тому

    Osati a dad koma a Gogo

  • @KhumboNyerenda
    @KhumboNyerenda 2 місяці тому

    Pa home 😂😂

  • @AshersSikanadze
    @AshersSikanadze 15 днів тому

    Kkkkk Mbuli zaanthu

  • @BlessingsMtalama-g4p
    @BlessingsMtalama-g4p 2 місяці тому

    Yomweyo yomweyo ife timafuna adad

  • @RaphaelKatimba
    @RaphaelKatimba 2 місяці тому +1

    A mai inunso ndi opusa kwambili mukuti azimai akufuna nsalu. bwanji osawapemphela chakudya inuyo mukuganiza kuli azimaiwo angadye nsalu? kulankhula kopusa kwambili. iweyo wakhuta ndiye anthu ena adzikadya nsalu .mai iweyo wayankhula mopusa kwambili. sindine wa MCP ai koma ndine wa DPP. Koma mai iweyo ndi galu chifukwa ukuwatenga ngati a zimai a ku Malawi 🇲🇼 amadya nsalu za chipani. anthu akufuna chimanga kapena ufa pa ground osati kumakamba za nsalu pamene anthu a kudya chitedze and that is nonsense.

    • @BrightZionga
      @BrightZionga 15 днів тому

      Mmmmm bodza mwana wa chikangawa

  • @MateyoSambir
    @MateyoSambir 2 місяці тому +1

    Kuankhula zoonad kumenelo ndiko kuankhula kumeneko

  • @ElnessMziya
    @ElnessMziya 7 днів тому

    Busy kupanga za azanu bwanj kukamba zot anthu amve

  • @EnnockChisanga-h6u
    @EnnockChisanga-h6u 2 місяці тому +1

    Adadi mumakwana

  • @AbuZunairaHanafie
    @AbuZunairaHanafie 2 місяці тому

    Masten ndiolusa olimba ntima

  • @RudigerElectronics
    @RudigerElectronics 2 місяці тому

    Dpp woyeeee

  • @DavieMwanza-m1s
    @DavieMwanza-m1s 2 місяці тому

    Sindingamalizitse zimandinyasa lne DPP simbaliyanga

  • @ChristopherJere-h5m
    @ChristopherJere-h5m 2 місяці тому

    My vote dpp

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 місяці тому +1

    Chakwera mapwala ake azimayi ake osadulidwa satana

    • @FrancisNyayi
      @FrancisNyayi 2 місяці тому

      Tikonza tanva we learn though mistake 2030 boma

  • @KingsleyLuka-f7b
    @KingsleyLuka-f7b 2 місяці тому

    Kuli ganyu bola Mulungu aweluze tikaone pamkwatulo

  • @Moyoyohane-i9h
    @Moyoyohane-i9h 14 днів тому

    Ooooo yes

  • @KalimuGerald
    @KalimuGerald 2 місяці тому

    Maiyu anena chilungamo palibeso kuopa atizunza chakwela kwakwana

  • @CharityMkandawire-t8u
    @CharityMkandawire-t8u 2 місяці тому

    💙💙💙💙💙💙💙💥💥💥💥💥💥

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 2 місяці тому +1

    Koma mcp yaonjeza guys kukweza ndi ufrash yomwe anthu akununkha kulephera kusamba kuchapa kkkk.koma mcp ndi afiti ndithu

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 2 місяці тому +3

    Zoona amalawi avutika mokwanira chikangawa achoke sitikumufuna

    • @ChimwemweZuze
      @ChimwemweZuze 2 місяці тому

      Kaya amkaziyanbira chani eishhhh mdikhale mbili ine😢😢😢

  • @EnetChiomba
    @EnetChiomba 2 місяці тому

    ❤❤❤

  • @EvahMaulid
    @EvahMaulid 16 днів тому

    😂😂😂😂❤❤❤

  • @YusufucaKasamilu
    @YusufucaKasamilu 16 днів тому

    Osatopa osafowoka

  • @TamalaKambanje
    @TamalaKambanje 2 місяці тому

    Machine achipani

  • @Dorah-zl9uf
    @Dorah-zl9uf 2 місяці тому

    Komana podya chiteze mmm

  • @ChipiliroLungu
    @ChipiliroLungu 2 місяці тому

    Nose adpp miti yanu sigwila ,kasungu sibweza kapena kugenda chipani chilichose koma iwo amadziwa kt MCP ndiye vote yawo

  • @JohnNyowani
    @JohnNyowani 2 місяці тому

    DPP ndi Boma

  • @DavieNoxxy
    @DavieNoxxy 2 місяці тому

    Kma dpp iwina guys

  • @FrancisNjabili
    @FrancisNjabili 2 місяці тому

    😮

  • @JudithNthini
    @JudithNthini 2 місяці тому

    kuno kumachinga daud chikwanje wa dpp wamangidwa chifukwa choti anachititsa sonkhano ati amayoza mcp boma lanji....boma lanji lomangomanga anthu 8:46

  • @LevisonFriday
    @LevisonFriday 2 місяці тому

    Mot bas muzikamb za salu Malo mwa zomw mudzacit

  • @JessyMagombo
    @JessyMagombo 2 місяці тому

    DPP chipan changa

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 2 місяці тому +1

    Dpp yakupha albino woyeeeeeee

  • @McfordKaunda
    @McfordKaunda 2 місяці тому

    Kkkk APM boma

  • @JACKSONHULUWA-j2n
    @JACKSONHULUWA-j2n 2 місяці тому

    Wabaya 4:18

  • @PreciousMatola-t9b
    @PreciousMatola-t9b 2 місяці тому

    Dpp kulibe ku centre

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 2 місяці тому

    Chikangawa akagwere uko kupha chilima unyera

  • @AlickKapapa
    @AlickKapapa 2 місяці тому

    Ine ndikufuana kuziwa izi Kodi DPP izilamulira ndi family ya mtharika okha okha kodi or Malawi izilamulira ndi family ya mtharika okha okha kodi or hlomwe belt kulibe oti akhale president of opposition or bwanji tivotele mlonda uyu chisale uyu panu ndi wa youth
    Tiyeni tizifuse zenizeni mawa tizalira mawa si ufumu uwu

  • @rabsonmanda-i6j
    @rabsonmanda-i6j 2 місяці тому

    No no

  • @AlickKapapa
    @AlickKapapa 2 місяці тому

    Dpp yinapha anthu 19 ku mzuzu,njauju, albino's,kukhapa anthu osalakwa kungosapota chipani china kumenyadwa ndi kuba ndi boza pano zosi zija zinatha

    • @Janekapats
      @Janekapats 2 місяці тому

      Ma trillion akubedwa aja ndi DPP eti??????

    • @beinhardkausiwa7107
      @beinhardkausiwa7107 2 місяці тому

      Wakwanitsa kukumbukira zinthu zochitika 5years ago koma ukuiwala zomwe zinachitika pa 10 June,2024 chikangawa....ubulutu eti

    • @ShamilahSaizi
      @ShamilahSaizi 2 місяці тому

      Ndiponso chikangawa son mpaka 3 comment wekha???? Osachita manyazi mukamayakhula zinazi bwanji

    • @PeterMsukwa-i1n
      @PeterMsukwa-i1n 2 місяці тому

      Mesa amapanga phulupulu akadakhara mmakhomo mwawo akadafa

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 2 місяці тому

    Muli kutondeka kale 15 years, mu boma

    • @nicolamarr7420
      @nicolamarr7420 2 місяці тому

      Iwe wakhumbanga kt apiter wakuzengele nyumba.undele pela

    • @FrancisNyayi
      @FrancisNyayi 2 місяці тому

      ​@@nicolamarr7420iwe nkhara chete dpp ijayo imaba koma anthuwa amadya

  • @MaxwellChapulumuka
    @MaxwellChapulumuka 9 днів тому

    😊😊😊😊