KUNO NDE KWACHEMA |

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 6 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 37

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Місяць тому +2

    Zikuonetsa kut a usi akuwatenga amalawi ngat opusa mokut akhale buys kumayendera mumaofesi akulu akulu

  • @pauljosephmakaula6835
    @pauljosephmakaula6835 Місяць тому +3

    Kikkkk mwayambapo ma REFORMS Kikkkk....sitidzidzimutsa zimenezi timakhala pansi nkukambilana nkuyamba mentorship process through QIP.....Otherwise sizithandiza

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Місяць тому +1

    Usi machende ake anagulisa chilima 😢😢

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 Місяць тому

    Nthawi zambiri ukakhala kuti zeru ulibe kupupuluma ndi ntchito no1 umasiya kumene kuli vuto umapita kumene kulibe vuto manganya akupanga campaign sakuyendera ntchito manganya akufuna anthu ayiwale ifa yachilima koma sizingatheke .

  • @UlemuKamanga-yn4jk
    @UlemuKamanga-yn4jk Місяць тому

    We already knew that KABAMBE will go to this side ,we have been monitoring him all along though candlelight memorial for DR LATE CHILIMA,mind you there was MGODE from faction AFORD,NDA from UDF,DPP from UDF ,PDP from DPP ,what to expect now is another faction from UTM

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 Місяць тому

    Singapore ku immigration chifukwa choti wauzidwa kale chochita. Iyi ndi office ya chakwera ndi mwana wake.

  • @Ghama-k4i
    @Ghama-k4i Місяць тому +1

    No passport
    Expensive fertilizer
    No medicine
    Political crimes
    Loss of VP
    Corruption
    Choose Usi as VP
    These are major problem in Malawi

  • @FloraBanda-w7t
    @FloraBanda-w7t Місяць тому

    A usi akupanga zapatikuferanji😂😂😂pakusowekera nanyoni ndi make sikono😂😂😂😂😂😂

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz Місяць тому

    Angofuna attention uyoooo oyendele ku NRB akaone mavuto ali kumeneko ife tinadziona za ziiiiiii

  • @ISMAILJula
    @ISMAILJula Місяць тому

    😂😂😂😂😂😂

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma Місяць тому

    Usi apange za ku MCP komko amationa ngati anthu sakuona

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh Місяць тому

    Akabwandira mukuthandawuza kuti kumisika akuyenda a usi kulibe athu ovutika

  • @UlemuKamanga-yn4jk
    @UlemuKamanga-yn4jk Місяць тому

    A kambwandira alibe mfundo awa

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r Місяць тому

    Kumalawi muli ndivuto munthu akati atele basi wachimwa .kufuna bwanji

    • @user-rf4br1fv2z
      @user-rf4br1fv2z Місяць тому

      Koma kodi munthu angatani uanga izi walakwa mmmmm

  • @MulowokaBlessings
    @MulowokaBlessings Місяць тому

    A Malawi a Malawi munthu kugwira ntchito molikira alkwitsa kodi mukufuna chani?

  • @YaqoobStandwell
    @YaqoobStandwell Місяць тому

    Amalawi ma vote awo akupita ku dpp or mutamuipisa mbir yake

  • @ShabaniKuswere
    @ShabaniKuswere Місяць тому

    Koma Kabambeyu asatiyankhulitse pambali, wadziwa Liti zoti UTM ndichipani chamfundo zabwino? Asapusitse anthu uyu akufuna mpando a UTM chenjerani,ndukuuzani kungopanda kumupatsa mpando ameneyu muona akuchoka, Ngati simukukhulupirira tayesani

    • @FrancisNyayi
      @FrancisNyayi Місяць тому

      Zisiyen akulu chilima anapita ku mcp kuchoka ku dpp

  • @user-xg5dg7jj4d
    @user-xg5dg7jj4d Місяць тому

    Penanso amalawi tilibe pabwino ayendela bwanji usi Malo onse munthawi imodzi

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi Місяць тому

    😢

  • @JackMvura-ik2td
    @JackMvura-ik2td Місяць тому +2

    DPP ndiye kudya kwao kupha malubino maka a look alomwe ena chakwera asalore anthu athu awonongeke ndi dpp amalawi osaivotera titha muno ndukuuzani

    • @Lee-lee-w1r
      @Lee-lee-w1r Місяць тому

      Mungoti andale onse ndi anthu oipa. Mmalawi muno Palibe wandale yemwe azatukule dziko lathu lino

    • @BLESSINGSSTOLO-lt9di
      @BLESSINGSSTOLO-lt9di Місяць тому

      Machedeako ndithu nkhumba iwe, amako ndi agalu eeet???

    • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
      @HappyAbyssinianCat-xt2bm Місяць тому

      Naweso ukulankhura kut chan chakwera ndindaniso uja ndye waononga anthu ambiri kumalawi chakwera manja mwake mwadzadza ndi magazi kagwere uko ndi wa satanic nzakoyo

    • @uzaleuzale8603
      @uzaleuzale8603 Місяць тому

      Kuthako kukapose momwe tikutheramu kapena ndiwe wankhungu osaona

    • @JackMvura-ik2td
      @JackMvura-ik2td Місяць тому

      @@uzaleuzale8603 iweyo ndiye wakhungu usiya tatewakoyo chakuphazedi malubino sungandiuze zautsiru iwe kagwere DPP Ife ayi Maka Lilongwe kapena central ifeyo ayi DPP komweko kwaoko mudza sendeso malubino forget not this country no

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz Місяць тому

    Usi tampaseni makofi

  • @clivemhango6183
    @clivemhango6183 Місяць тому

    Nonse mukuti a usi akulakwisa mulibe kuyamika. Munthu angoyamba kumene kiyendela moti inu mukanati muyendelenso kwakuti. Kodi program yawo mukuyidziwa?
    Kwali inu mukutukwana, sorry, mwachitapo chani inuyo?

    • @isaihmagani5697
      @isaihmagani5697 Місяць тому

      Sakunena zoti kulakwisa akuti aziyendera momwe muli mavuto

  • @NelsonMarley-m6p
    @NelsonMarley-m6p Місяць тому

    Usi mulibe ilionse,,, what he's doing is nothing

  • @billymhoni9527
    @billymhoni9527 Місяць тому

    Attention searcher.

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 Місяць тому

    Singapore ku immigration chifukwa choti wauzidwa kale chochita. Iyi ndi office ya chakwera ndi mwana wake.