ZILI LERO KU BLANTYRE NDILANDE _KUYANKHULA KWA MICHAEL USI 🙌🙌

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 8 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 242

  • @user-ss2rk9up5r
    @user-ss2rk9up5r Місяць тому +1

    I have liked the speech of the VP. Whoever is against him has his own challenges but I stand to watch his speech. God is our true judge.

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole Місяць тому +10

    Uyu sanachenjere bwino wafa chilima iye anali phee mbuyomu chadza ndiyani a usi tsopano .

  • @godrickmapepu2754
    @godrickmapepu2754 Місяць тому +5

    Michael usi Muthu oipa kwambiri. Ukanaziwa kuti maloto anga sanaphelezele sibwenzi ukupanga zimenezi. Koma Mulungu akulanga pa zomwe ukuchitazi

  • @JofariLameck
    @JofariLameck Місяць тому +5

    Ndalama yavuta odi ndilandile ngongole yosabweza ine komaso kulavotera chipani chakumtima kwanga😂😂😂

  • @EmmanuelMoyo-hy5ni
    @EmmanuelMoyo-hy5ni Місяць тому +8

    Ngongole yopelekedwa last time koma yudasi

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 Місяць тому +6

    Convention ija ikufunika ndipo ichitike mwachangu😂😂 awawa apite ku MCP 😂😂

    • @user-zv3cy2xj5p
      @user-zv3cy2xj5p Місяць тому

      Usachita sanje musiyen agwire ntchito ya dziko jealous down please

    • @AchinaKellz
      @AchinaKellz Місяць тому

      Changu changu kaya akalowera pati

  • @TopoTopo-bm4vw
    @TopoTopo-bm4vw Місяць тому +9

    Chofunika kulandila ndalamazo koma osavotela

  • @user-zv3cy2xj5p
    @user-zv3cy2xj5p Місяць тому +3

    Upresident ukukuyenera bwana usi

  • @user-xb6em7nj3r
    @user-xb6em7nj3r Місяць тому +13

    Yudas Iscaritots cannot be taken seriously. I am waiting for the convention. If this guy will be endorsed that will be my last day as a UTM member and am going back to DPP.

  • @MustaphaCassim
    @MustaphaCassim Місяць тому +3

    Manganya ndi kapolo wachakwera

  • @ayaanchaudhry9370
    @ayaanchaudhry9370 Місяць тому +2

    This mn will bring change in this world , reason he knows how to deal with poor people , belive me , lets just give him chance

    • @omarshaffi447
      @omarshaffi447 Місяць тому

      😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Are you sure 😂😂😂😂😂?

    • @BornwellChipango-s9m
      @BornwellChipango-s9m Місяць тому

      U don't think in your mind

  • @CharlesPhiri-ds1rk
    @CharlesPhiri-ds1rk Місяць тому +1

    Ine munthu uyu ndinkonda kwambiri... osamalankhula ngat kulibe mawa...usi ndi munthu amene amalankhula akudziwa kt kuli mawa....❤❤❤❤❤❤ Powerful vp....more ❤❤❤❤❤❤

  • @KingfrahMachado
    @KingfrahMachado Місяць тому +1

    Choka apa ndiwe galu 🐕🐕🐕kwabasi tamuoneleni ndevu zake bodza ukunenali Zachison Kupemtaso ndevu ngt malemu Chilima mmm zachison 😂😂😂😂😂

  • @user-mm3wq8qp2q
    @user-mm3wq8qp2q Місяць тому +7

    awa tawathamangiseni achisiru

  • @CharlesPhiri-ds1rk
    @CharlesPhiri-ds1rk Місяць тому +1

    Km usi nkanakudziwa komwe ukhra nkanabwera kudzakithokoza pokhapa ......nzakutha izi....aliyese adzafika pando wakuweluza...powerful

  • @kevinchipembere1137
    @kevinchipembere1137 Місяць тому +3

    Madhala Usi 😂🔥🔥🔥 inu ndi one bwana

    • @AchinaKellz
      @AchinaKellz Місяць тому

      Pola pola ngati ukujabura

  • @wonganimtabayiranyondo9880
    @wonganimtabayiranyondo9880 Місяць тому

    So interesting. Why kuyitanira ngongole lero? Kudya katatu lero after 4 years? Ayi sankiyu

  • @FOSTERLUPIYA-zc1xv
    @FOSTERLUPIYA-zc1xv Місяць тому +1

    Mulungu alemekeze potipatsa S VP Dr Usi.wodzichepetsa

    • @JohnfosterNkusengwa
      @JohnfosterNkusengwa Місяць тому

      Koma iwe manganya ambuye akuone zedi ufiti ulipo MO ndithu

  • @ganizanimanyamba
    @ganizanimanyamba Місяць тому

    Koma musamayiwale Mr Don't trust Malawian alingat mbuzi sachedwakuiwala manganya wagundika kuwabwatika muzamukumbukila ntanyiwa ndi Mr Don't trust pa Limpopo FM

  • @frankandson9900
    @frankandson9900 Місяць тому +1

    Idont blame this guy I blame pple who crap fr him shame

  • @jedoforsure2842
    @jedoforsure2842 Місяць тому +2

    Mumakwana big Mr vp

  • @phwanyamusiq
    @phwanyamusiq Місяць тому +3

    Anthu mukuputsitsidwa heavy😂😂

  • @pauljofilisi
    @pauljofilisi Місяць тому

    Ngongole akatenga kodi awagule ndani umphawi ngati umenewo anthu akufuna ndi njala bwerani ku Nsanje mudzawone mene akuvutika minda yawo madzi okha okha

  • @BMDMasulani
    @BMDMasulani Місяць тому

    Uyuyu ndi wanzeru koma wafika nthawi yovuta koma mwa iyeyu muli utsogoleli kuposa enawa

  • @mkhulukinyata5198
    @mkhulukinyata5198 Місяць тому

    Michael Usi pamodzi ndi agalu amzako a MCP Tamvani idzi" . Inuyo pakadali panopa palibe chomwe mungatichitire a MALAWI ife kuti Tiyiware dza momwe munamuphera CHILIMA Pamodzi ndi An'thu 8 womwe munawapha ngati Njoka aja, . Anthu woyipa wopanda manyazi, Wopanda chisoni , Wopanda umun'thu ..

  • @BensonChilundu
    @BensonChilundu Місяць тому +1

    Mutu ngati ngwime (bwampini)Mcheal usi umandinyansa heavy

  • @RejoiceKaliya-i9t
    @RejoiceKaliya-i9t Місяць тому +1

    Bwanaaa tabwerani kuno ku immigration mudzamuone uyuuuu! Akupanga mwanotu uyuuuu kuno. Tabwerani muli mu Blantyre mommuno.

  • @ishmaelashleyrobin4195
    @ishmaelashleyrobin4195 Місяць тому +2

    Zoona kumaombera m'manji zimenezi koma abale munthu zatheka ndithu

  • @user-bf1sz6pu1n
    @user-bf1sz6pu1n Місяць тому

    Munthu sungamazichemelele kuti ine ndimaziwa kupempha, umenewo ndiye uchitsiru.

    • @gracioussinoya2850
      @gracioussinoya2850 Місяць тому

      Inenso I'm feeling uncomfortable with that words ,mpakana kumadzichemelera ndikupepha

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q Місяць тому

    😂😂😂😂😂 zaziii ndiye chikukukochanu chonamiza anthu kuti muwapasandarama zangongore zaziii zenizeni kupotoife sikufuna ayi iwe usi kagaru iwe

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 Місяць тому +3

    Chikangawa iwe munthu oyipa iwe

  • @dorcasmwale6328
    @dorcasmwale6328 Місяць тому

    anati saziyankha ngati KSC koma akupanga zotsutsana ndizomwe ananena, munthu oipa

  • @Michael1989Nqube
    @Michael1989Nqube Місяць тому

    Dr Usi must be aware of what he is doing, ili ndi Dziko. Akapanga masewela awa ndi mathero ake.
    Ayenela kudzukuta Mmene. Chililima ankamusankhila U VP. Uyu thembelero limupeza Akapanga masewela.

  • @Chikumbuso-l5m
    @Chikumbuso-l5m Місяць тому

    Ndipu ameneyo ngati Akutuluka muchipani cha UTM mlungu amulange

  • @ChrissySalimu
    @ChrissySalimu Місяць тому +1

    Kampeniyoooo munali kt nthawi Yoseyi osatipatsa ngongoleyo munyaaa

  • @mkhokholasamuzonda5094
    @mkhokholasamuzonda5094 Місяць тому

    NGONGOLE YA FERTILIZEEEEEEEEEEEEER MWABWEZAAAA

  • @JimmyIsaac-xd4ef
    @JimmyIsaac-xd4ef Місяць тому +1

    Gwape oipa chikangawa party

  • @user-nt9go2fz3k
    @user-nt9go2fz3k Місяць тому +1

    Mache... Ake tikumufuna ndichakwelayo tizamugendeee

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d Місяць тому

    Madzi achita katondo, manganya ukudziwapo kathu za ifa ya Chilima

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Місяць тому +1

    Ngongole ndi imeneyo koma anthu wo business yake iti ndi m'mene ndlama ya Malawi iliri panomu nde adziwinapo chani

  • @MaliyaMalamusi
    @MaliyaMalamusi Місяць тому

    Palibe chomwe anganene chifukwa mwini wake panalibe zomwe ankanena, ndiye apapa Dr Usi walakwa chiyani,Ndipo akunena zoona kuti pakhale kugwilizana onse azipsni zimenezo ndiye zofunika

  • @MangaDamiano
    @MangaDamiano Місяць тому +1

    Kazitape Ngati iwe

  • @stevemtambalika
    @stevemtambalika Місяць тому

    Munthu oipa iwe usi ngati chikangawa choka.rip my president skc

  • @BlueTicksound-ow4fq
    @BlueTicksound-ow4fq Місяць тому

    😮😊 ndipo mu ofesi anthu akuwonjeza zoona tizivutika ngati misokho simaperekedwa... Tamayendaniso ma company muziwona momwe maliporo akukharira.

  • @ErnestChansa
    @ErnestChansa Місяць тому

    Munthu amene angachenje ziko lino ndi mozi yekha basi bhon kalindo president wa anthu awuphawi..manganya alibe phavu becoz Ali pasi pachakwela ...

  • @andychingwalu
    @andychingwalu Місяць тому

    everyday basi nkhani izikhala yokuti "ndinkavala makabudula awiri, thako nkumaonekela" basi? awa ndiye phala lenileni. AChilima mudatisiyilanji?

  • @SteviePatrick-g2p
    @SteviePatrick-g2p Місяць тому +1

    Uyu akupanga Za chipani chake cha odya zake

  • @user-nf5go5ic9x
    @user-nf5go5ic9x Місяць тому +1

    Akut abwana ngt wina anapereka abwana ake inu sazakuperekan???wina akuziona ngt dolo km dkila tsku lako likubwera 😂😂❤

  • @SifatiMoses
    @SifatiMoses Місяць тому

    Koma Fada katundu wakwiratu kongolero mukunama kwambiri musuzitsa anthu.

  • @Chikumbuso-l5m
    @Chikumbuso-l5m Місяць тому

    Mndiyakhe ndani president wa UTM now

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj Місяць тому +3

    Zikutathauzanji zimenezo abale

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Місяць тому

    Koma amalawi sitizaphunzila munthu uyu mkamwa mwake palibe fundo

  • @WillyZuze
    @WillyZuze Місяць тому

    You have too late,usi unali kuti nthawi yonseyi and I have no time to give u my vote Mr chikangawa

  • @BenadettaThom-n8n
    @BenadettaThom-n8n Місяць тому

    Galu iwe tizingokhalira kumva za matako akowo, pereka ndalamayo koma vote yako kulibe

  • @BestMtawali
    @BestMtawali Місяць тому

    Et chilima pot wandiuza zonse mowe tingapangile campain then ndimuphe ine ndzapanga zimene wandiuzazo😆😆😆galu kwabas 😂ndevu szinali choncho🤣🤣

  • @CharlesPhiri-ds1rk
    @CharlesPhiri-ds1rk Місяць тому

    Zooona usi. Auzeeee kt mau alionse ankamwa mwawo amene Ali olipa Mulungu adzawerengera mulandu....tsiku Lina adzaweluzidwa.

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire Місяць тому

    Mbuzi yaimuna phongo usi

  • @CHIMWEMWECHILUNGA
    @CHIMWEMWECHILUNGA Місяць тому

    Kkkkkkkkk koma ati ali ndi ukadaulo opempha maiko akuja (masikini wamkulu)😂😂😂😂

  • @WallyMsiska
    @WallyMsiska Місяць тому

    MCP yabisala mwamanganya kt atonthoze anthu akhale bata pa zokwiya za SKC

  • @user-pn1yo3ll9e
    @user-pn1yo3ll9e Місяць тому

    Fundo imodzi imodzi kulionse angapite mmmmmmm😢😢😢😢

  • @user-dl1dg4yz1j
    @user-dl1dg4yz1j Місяць тому +2

    Usi ndichitsiru cha MCP. Wapanga chani iweyo gwape? Tikaonana ku convention

  • @TonyMhone
    @TonyMhone Місяць тому

    Chadza ndi yani a Usi. SKC wamwalira lero busy. Mmmmmmmmh. Njawala sakunama" mkango ukafa fisi sangalere ana"

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r Місяць тому

    Yunda sikalioti chikangawa party

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 Місяць тому

    Akubw inu mukugura mavote panyopanu

  • @EstherNamasala
    @EstherNamasala Місяць тому

    Eya tipaseni ngongoleyo kkk

  • @kangungufoundation2020
    @kangungufoundation2020 Місяць тому

    Anthu amene akumunena Michael usi alibe nzeru ndichifukwa chake tizivutika nthawi zonse, tili busy kuyankhula za imfa ya chilima kumutenga chilima innocent pamene chilima anali gulu la chakwera remember the birds of same feathers flock together, chilima was not innocent, the president that was innocent and was killed by the citizens of Malawi was bingu wamutharika, alipo mwa inu amene akumukumbuka bingu pa zabwino zonse zimene anachita??? After that inu amalawi munapanga chani bingu wa mtharika?? Lero muli busy kutukwana chakwera amene munamulowesa nokha kumuchosa Peter mwa chipongwe do you think malawians will go unpublished, mzimu omwe wakwiya ndi wa bingu not chilima and if you are not careful chakwera akhala mpaka 2030 just for your punishment chifukwa sindikuwona wanzeru mwa onse omwe akuzitcha omenyera ufulu. Truth is bitter koma ndakuuzani chilungamo sinthani khalidwe amalawi, dziko lathu tikuliwononga tokha chifuwa cha dyera ndi kusaganiza

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz Місяць тому

    Tachokani apa kodi iwe uyimira pati dikira tione convention ukagwa ngati atakulabade tiona uzasowa mtendere my friend Chima chopanda Zimu woyera sichikoma olo aturo oil kutota njeeee

  • @PreciousBanda-mq3kf
    @PreciousBanda-mq3kf Місяць тому +1

    Tambwali weni weni manganya

  • @Nefitalamoises
    @Nefitalamoises Місяць тому

    Pitizani masewero osati vp simukukwana

  • @Jessica-pg6ep
    @Jessica-pg6ep Місяць тому

    Uku mwangogwelako koma siphatso yanu, inu koma ma drama mumatha. Munalemela kale koma kusakhutisidwa. Zinazi umangoona wadziputa😮

  • @evancenasoro922
    @evancenasoro922 Місяць тому +1

    Malawian are malawian indeed😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @YusufChipojola
    @YusufChipojola Місяць тому

    Manganya mwanama zaka 4 ambuyanuwo apangachani

  • @fatsosmart4295
    @fatsosmart4295 Місяць тому

    A president akowo ngongole yo nthawi yonseyi saamapeleka bwanj?
    Nde mwakambilana lelo fukwa iweyo wabwela pampandopo?
    Is tht what u want to tell us? Hmmmmmm ayi ndthu may SKC’s soul keep resting in peace😢

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire Місяць тому

    Mugendeni ndi miyala

  • @innocentpalapasa5059
    @innocentpalapasa5059 Місяць тому

    Anamizana ndi chakwera wakeyo,Need siyochiitira Campaign

  • @RodgersMhango-ff2nu
    @RodgersMhango-ff2nu Місяць тому

    Zikakhala ndalamazo tilandila nawoo koma Micheal usi ndi Chakwela mukagwere tsitikumvotelani malawi wake sii waleroyi ayi, wagwa nayo iwe galu wamuthu iwe

  • @user-pv2xx3lu8b
    @user-pv2xx3lu8b Місяць тому +1

    Aaah koma umphawi sizithu mmmm 😢

  • @JaneMoyo-ws2di
    @JaneMoyo-ws2di Місяць тому

    Mu misonkhanoyi ndikuona kuti anthu angopemyesesa chetee okuwa ndi ochepa zeedi. Cheteyu kaya anthuwa akuganiza chani?

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz Місяць тому

    Watha ameneyo mphamvu zake zatha pamene skc adalowa manda,chilegwalegwa kapeta ngongole last minute,njara chani? Mfiti chedza ndizitsiru zizako koma for ma y nod z not bc,udampeleka dzako iwe woyipa kobasi ine nditenga nawo koma vote yanga nyooo

  • @Gmtmphats124gy
    @Gmtmphats124gy Місяць тому

    Kodi gogile zopanda chikole anthu azipasindwa thawi yakampen yokha ?

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 Місяць тому

    Mfiti yaikulu iwe garu

  • @HaliJana
    @HaliJana Місяць тому

    KOMA USI PAMATAKO PAKO WAVA ,KODI ANTHU ALI APA NDI A UTM UKUFUNA UTANI NAO KOD ,PALIBEPO WA MCP APA AI KODI USI ULI KU UTM MWINA KU MCP UFATU IWEYO NDI NDALE ZAKO ZOPUSAZO

  • @RemitterFlik1130
    @RemitterFlik1130 Місяць тому +1

    anakakhala wa UTM original bwezi pamenepo Pali kaliyati achina njawala koma apo Ali ndi chakwela awiri

    • @Slyvia-uu3wc
      @Slyvia-uu3wc Місяць тому

      100%

    • @omarlux3434
      @omarlux3434 Місяць тому

      Ife sitifuna chipani simaphika ayi koma.chitukuko

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 Місяць тому

    Anthu landilani ngongole koma vote ku mtima

  • @SteveSamson-t9d
    @SteveSamson-t9d Місяць тому

    Mugenden ameneyo mbuzii yamuthu

  • @user-tb6yh1kx3o
    @user-tb6yh1kx3o Місяць тому

    Palibe kubweza ndalama Zimenezo, Inu zomwe mukupakulazo muzabweza?

  • @FainesMasina
    @FainesMasina Місяць тому

    Kudya katatu ko nde munene lero mmmmm kale lonseli munali kuti? Kufuna kuononga utm uku 😊

  • @FulindaMuhamad
    @FulindaMuhamad Місяць тому

    Nthawi yatha kale dzisintha liti iwe galu khobasi

  • @user-lr5bz7qk2d
    @user-lr5bz7qk2d Місяць тому

    Yudasi mfiti unathandizila chakwela kumapha chilima

  • @user-qq3ln3qr6x
    @user-qq3ln3qr6x Місяць тому

    Ngongole mpakana liti chitsiru iwe usatinyatsepo eti tibwezera nchani ngongolezo ngat tili ndi business yolongosoka galu iwe

  • @EthelKubalasa
    @EthelKubalasa Місяць тому

    uyu ndimpera kuwiri. Tisamale naye amalawi satigulitsa ku MCP.

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire Місяць тому

    Usi nda chakwera ndapao midzu yakachere akumana pasi
    Asaaah mbuzi eti umphawi ndi njala ya mmalawi mwauona lero?👹👿😈👽💀

  • @LawrenceBelson
    @LawrenceBelson Місяць тому

    Hmmmm usamachule dzina la mulungu pachabe ndiwe yudasidi a2 sakukunamizira

  • @ClementMinyanga
    @ClementMinyanga Місяць тому

    Uphawi kachitsiludi et🤣🤣🤣

  • @SamuelMthengo
    @SamuelMthengo Місяць тому

    Kodi mwayamba kugwila ntchito ku neef?

  • @vincentsitolo1224
    @vincentsitolo1224 Місяць тому

    Aaaaaa koma ndale eeee dziko ili ngongole ndikupempha kwa azungu basi.

  • @osmanwanja3733
    @osmanwanja3733 Місяць тому +1

    Malawian don't trust this man he is not capable of changing Malawi their is no readership in him

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 Місяць тому

    Ine kuno ku Ntcheu ndinalandira kale 1M yangongole koma sindibweza chifukwa ndadya Misonkho yanga iyaaa!! ndipo ndapangitsa kale passport Next month ulendo wa ku Capetown Ukandipezera kuti Manganya

    • @wisdom20mkango49
      @wisdom20mkango49 Місяць тому +1

      Kavutikeni adhara ....kukhale kunyadira kumeneko south to.....pitani UK or tipezeni Ku USA kuno 😂😂😂😂😂😂 anthu koma ...you are pathetic my guy better ukanayamba business ndikubweza you could get opportunity yoti uzatenge ndalama yambili

  • @BptomanPhiri
    @BptomanPhiri Місяць тому

    A usi si wandale koma akutsiluza nthawi ya chilima mudzamuona akupita ku tikufelanji uyu

  • @LinesiKanzota-fw7sj
    @LinesiKanzota-fw7sj Місяць тому

    Ndipo anthu Ife tichejere ndithu asatinamize thawi yotha yithayi NDI ngongole Kuti tazavoter ayi ndarama Zo tilandire Koma osayiwala m,fiti NDI m,fiti sangasithe kukhala wabwino