SAMEER SULEMAN WAULULA ZINSINSI ZOMWE ZIGAWENGA ZIKUPANGA KUFUNA KUMUPHA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 5 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 28

  • @MustaphaCassim-t7g
    @MustaphaCassim-t7g 4 дні тому +2

    Sheikh I promise that Allah will never and never loose and guide u ameen.

  • @chikondiCharles-p7z
    @chikondiCharles-p7z День тому

    May God protect you all the time

  • @LenadiMthandi
    @LenadiMthandi 3 дні тому

    God bless you Mr. Suleiman.

  • @ibrahemmillz2651
    @ibrahemmillz2651 День тому

    May Allah protect you

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 3 дні тому

    Allah is with you and protecting you

  • @MapataMohammed
    @MapataMohammed 3 дні тому

    Allah protect you. Your are next president after APm

  • @MasudiMatenje-s3i
    @MasudiMatenje-s3i 4 дні тому

    May Allah will protect you you have to be honest all the time like the way you are and I hope you will be next president after APM

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 4 дні тому

    God bless u suleman

  • @KhanMuhammad-n2w
    @KhanMuhammad-n2w 3 дні тому

    Mulungu akusamalirani Mr sir

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 4 дні тому

    Allah akbar Allah akutetezeni thawi zonse, ndipo mumaoneka kuti malawi 🇲🇼 mumaikonda , ndipo allah imililani malawi ndipo landilani mapephelo athu allah alandileni chakwera achoke muboma olo kufa kumeneko afee

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 3 дні тому

    Ambuye alemekezeke komatu mulungu alipo umati ukumusaka m,zako kuti umuphe komatu mulungu si Lazaro wava chakwela chimwendo kukuyu ndi zikhale ng,oma mulungu akulangeni posachedwa 😢😢

  • @tungwaprecious
    @tungwaprecious 4 дні тому +1

    Not good may GOD keep on guiding you sir we believe in you sir 🙏🙏🙏

  • @kekeaufi9834
    @kekeaufi9834 4 дні тому

    *Ya dhal jalali wal-ikraam,,,,,Ya dhal jalali wal-ikraam*

  • @EvanceMaster-v5o
    @EvanceMaster-v5o 4 дні тому

    Mr suleman musaope chifukwa mulungu alinanu ndipo akutetezelani ndinu olimba mtima osaopa okonda malawi ngati mmene analili chilima, chakwela walinunkhitsa manyi dziko linali lankaka ndi uchi lija mpakana kufuna kupha munthu masana aliyense akuona, mmmmh koma ya umakwana

  • @arnoldnjirika6087
    @arnoldnjirika6087 2 дні тому

    Angamuphe ndani uyu

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 3 дні тому

    Zikhale ng'oma amuimitsa kaye ntchito zabomandicholinga choti athane ndi anthu angapo , ndicholinga choti akamapha anthu zizikhala ngati sizikumukhuza

  • @GracieRejoice
    @GracieRejoice 4 дні тому

    Ambuye akhale nawe Sulemani kod ndale zanj zomangopha ndpo Malawi siiingabwelere ku one party system ana anjoka inu kumwamba kulibe chanu ngt simulapa

  • @wizchisale1686
    @wizchisale1686 День тому

    Tithana. Nao agalu amenewa atikwana

  • @davienoah1022
    @davienoah1022 4 дні тому

    Koma ndi chan kwen kwen chifunika ku Malawi kuno abale 😢

  • @JamesLeonardhowa
    @JamesLeonardhowa 4 дні тому

    Ndiye amariza kupa amalawi ose😂😂😂 bichopu kufunaso kumupa

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg День тому

    Chimwendo Banda one day udzanyelera kukamwa

  • @BerthaKasambala-y5k
    @BerthaKasambala-y5k 4 дні тому

    Chakwera akutumbwa chifukwa cho kt ku marawi mafuti samapezeka chisawawa kukana khara kuno chakwera anapeza porekera sure

  • @MagieJames
    @MagieJames 3 дні тому

    Naweso mcp sinyoza DPP pa nsana pako chifukwa muli boma muzayaluka tsiku limakwana

  • @WeloNyondo-d4c
    @WeloNyondo-d4c 4 дні тому

    Ngati ziri nchoncho waziwa bwanji kuti anyamatawa atumidwa ndi a m.c.p Si ndale zaboza zimenezo ngati ineyo ulangizi wanga ndikuti ngati uli pasonkhano usiye kunyoza chipani cha m.c.p bas

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg День тому

    Chimwendo Banda one day udzanyelera kukamwa