MWANVA ZOMWE WALANKHULA KEN NSONDA LERO? WAULURA KUTI ADACHITA KUMUITANA KUTI ALOWE MCP - TINVENI

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 21 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 53

  • @DanMpinganjira-u8r
    @DanMpinganjira-u8r 15 днів тому +4

    Munthu onama kwambiri uyuuu 😂😂😂😂😂😂

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 12 днів тому

    Boza awa 😢

  • @Aliko-vb9zm
    @Aliko-vb9zm 12 днів тому

    Uyu akufunika Brian Banda..bodza lake lizaonekele poyera

  • @GwachaTembo-e7l
    @GwachaTembo-e7l 16 днів тому

    Matenda aja osazawaphweketsa anthu mutu umatha kujama kuno ken nsonda mankhwala anamupweteka akut nanuso happy new year yasopano

  • @JoeMchombo
    @JoeMchombo 16 днів тому

    Aaaaaah akuba awa

  • @ajasikalonga3210
    @ajasikalonga3210 16 днів тому +2

    Please munthuyu akumvetsa chisoni kwambiri.Chitsiru chamunthu ichi

  • @chauncychauncy1683
    @chauncychauncy1683 14 днів тому

    Awawa pantumbo pao sure

  • @GeorgeKambwiri-xr9ri
    @GeorgeKambwiri-xr9ri 13 днів тому

    Oyipa uyu ndiwe unapha bingu eti

  • @GraceMasiye
    @GraceMasiye 14 днів тому

    Koma wowonda uyu,aaayaa

  • @TimothyvascoVasco-j6d
    @TimothyvascoVasco-j6d 15 днів тому +1

    Apanga ifa ndi ken nsonda kumalawi za anthu andale

  • @ajasikalonga3210
    @ajasikalonga3210 16 днів тому

    Kodi asangompatsa udindo ku nyawu bwanji😂😂😂😂

  • @MaryTchapo
    @MaryTchapo 16 днів тому

    Kape

  • @AlihIbrahim-s7v
    @AlihIbrahim-s7v 16 днів тому

    Kwawonela Aken msonda,,,it's just westing time,,,komaso kutha Bundle pa chabe

  • @MeruMitha
    @MeruMitha 15 днів тому

    kufunsa buluzi ati amafuna kukula ngati ng'ona 😅😅😅

  • @ChipokaChirwa
    @ChipokaChirwa 14 днів тому

    Uyuyu ndi chifukwa chake Brian Banda anamkhamisa ndimafunso samatha kulankhula alibe nzeru

  • @ObinKayinga
    @ObinKayinga 14 днів тому

    I thought johaz Mumba is over 40years

  • @JoshuaNyirongo
    @JoshuaNyirongo 15 днів тому

    Matenda awa ndioopsya eish!.

  • @mayesodickbottoman9861
    @mayesodickbottoman9861 14 днів тому

    Population ya SA you cannot compare with MA .
    I mean ministry of education

  • @EliasKhofi
    @EliasKhofi 3 дні тому

    😂😂😂😂 chisilu ichi nzeru chilibe. ndipo chatha zipani ichi.and Is the waste listening to this guy.

  • @PrinceThom-pe6ie
    @PrinceThom-pe6ie 16 днів тому

    Kodi Garu iwe ndimayesa umanena chaka chatha KUTI Peter muthalika apita Ku America November chaka chatha

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri 15 днів тому

    Msonda anakumasura APM iwe kkkkkk

  • @StevenMsusa-h2l
    @StevenMsusa-h2l 15 днів тому

    Kkkkkkkk anthu osatila ndalama awa chikawina chipani china azathawa

  • @ChapwetekaChauluka
    @ChapwetekaChauluka 16 днів тому

    Kkkkkk ati New Year yatsopano what does it mean?

  • @BlessingSikefa
    @BlessingSikefa 16 днів тому +1

    Kd awa or udindo afelamo

  • @ScaverManjedza
    @ScaverManjedza 15 днів тому

    Limenero thupi lamunthu? Jeket ngati ayika pakantengoo

  • @OwenMunde-d8i
    @OwenMunde-d8i 14 днів тому

    Kukalambako kwakubela zelu keni kkkkk uyaluka pompano mcp ikachoka

  • @Eqrah-hj2nu
    @Eqrah-hj2nu 16 днів тому

    A tidye nawo😂😅😂😅😂

  • @AHAMADUJRAminie-c6q
    @AHAMADUJRAminie-c6q 15 днів тому

    Kkk uyu matenda amamubalalitsa

  • @JohnSoweso
    @JohnSoweso 14 днів тому

    Chibwatiko weneweni
    Chule wa padziwe uyu

  • @AlexsKazembe
    @AlexsKazembe 14 днів тому +1

    Wakalamba uyu mut suyenda bwino

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 12 днів тому

      Indeeeee mutu suyenda ngati amenenso anamusankhayo nayenso mutu suyenda

  • @TimothyvascoVasco-j6d
    @TimothyvascoVasco-j6d 15 днів тому

    Msonda adzazuzika ana ako

  • @PrinceThom-pe6ie
    @PrinceThom-pe6ie 16 днів тому

    Machende ako iwe kunoko Ku south Africa ungayelekeze NDI dziko losauka ngati Malawi

  • @AmosScott-z9x
    @AmosScott-z9x 16 днів тому

    Mwamangacho ndi chani amsonda tie kapena chingwe

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 16 днів тому

    Koma uyu mcp ukumukhala osati zopembelazo

  • @Johnybegood260
    @Johnybegood260 16 днів тому

    Mbuzi ya munthu

  • @UmaliDaili
    @UmaliDaili 16 днів тому

    Machena ako iwe keni sonda ukazitape ukupwetekesa tikumana kuzisakho

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo 16 днів тому

    Komatu a msonda mukavula ndiye tsatsa lenileni lokwapulira ana a standard 1 kkkkkk

  • @NiccoGama
    @NiccoGama 16 днів тому

    Chisilu ichi dyera lamuchurukir

  • @GwachaTembo-e7l
    @GwachaTembo-e7l 16 днів тому

    Ichi chipalamula kuno ati malemu peter mthalika ichi chimangidwe chaka chamawa

  • @AlexanderTraffick
    @AlexanderTraffick 16 днів тому

    Uyuyu aziyenda pa wheelchair.chifukwa azatha kugwa ndimphepo

  • @francissumbulero2291
    @francissumbulero2291 16 днів тому

    Mapwala ako galu iwe

  • @GiftThamangira
    @GiftThamangira 16 днів тому

    Sakupeza bwino uyu

  • @PhilemonLloydGalawanda-tz2zb
    @PhilemonLloydGalawanda-tz2zb 16 днів тому

    Kape uyu muli mthenda mmutu mwakemu ndipo anachita bwino kumuchotsa mu DPP... Ngati APM siwabwino anapita kukapepesa bwanji Page House? Ngati uli ndi mzeru bwanji sadakusankhe kukhala nduna ya Boma?

  • @ThivadoartistDyson
    @ThivadoartistDyson 14 днів тому

    Kkkķkkk awa nachitsilu sadziwa zomwe amachita