Malawi News Xtra
Malawi News Xtra
  • 6
  • 74 574

Відео

MCP YALAVULA MOTO PA LIPOTI LA AFROBAROMETER LOKUTI DPP IWINA 2025MCP YALAVULA MOTO PA LIPOTI LA AFROBAROMETER LOKUTI DPP IWINA 2025
MCP YALAVULA MOTO PA LIPOTI LA AFROBAROMETER LOKUTI DPP IWINA 2025
Переглядів 7 тис.5 днів тому
AZIMAYI A DPP NDI A MCP APWETEKANA NDI NYIMBO 2025 YI EEEEEEAZIMAYI A DPP NDI A MCP APWETEKANA NDI NYIMBO 2025 YI EEEEEE
AZIMAYI A DPP NDI A MCP APWETEKANA NDI NYIMBO 2025 YI EEEEEE
Переглядів 52 тис.10 днів тому
KWAVUTA KUMWANZA, TAONANI MMENE AMULANDILIRA PETER MUTHARIKA, EEEEKWAVUTA KUMWANZA, TAONANI MMENE AMULANDILIRA PETER MUTHARIKA, EEEE
KWAVUTA KUMWANZA, TAONANI MMENE AMULANDILIRA PETER MUTHARIKA, EEEE
Переглядів 3,3 тис.15 днів тому
Democratic Progressive Party president Peter Muthatika in Mwanza on 27 November 2024
TOP 5 YA NYIMBO ZODZUDZULA ANDALE KU MALAWITOP 5 YA NYIMBO ZODZUDZULA ANDALE KU MALAWI
TOP 5 YA NYIMBO ZODZUDZULA ANDALE KU MALAWI
Переглядів 14 тис.17 днів тому
MA DEMO A LERO MU ZITHUNZIMA DEMO A LERO MU ZITHUNZI
MA DEMO A LERO MU ZITHUNZI
Переглядів 7417 днів тому
This video is showing what happened during demonstrations in Lilongwe Malawi on 25 November 2024

КОМЕНТАРІ

  • @FrancisChikapa-o6l
    @FrancisChikapa-o6l 52 хвилини тому

    Ipeleka chikoka ndi ya DPP

  • @ChipiliroNason
    @ChipiliroNason Годину тому

    MCP 🎉❤ mesa

  • @ChipiliroNason
    @ChipiliroNason Годину тому

    Zosasangarasa

  • @MagiretChigaga
    @MagiretChigaga Годину тому

    DPP MBAMBANDE

  • @FelixScot
    @FelixScot 2 години тому

    Zakudambwe ndi ye kayatu

  • @BlessingsCyprianMondwe
    @BlessingsCyprianMondwe 3 години тому

    More fire Dpp🎉🎉🎉.❤❤.enawo angoyimba ngati Mano alibe kamwamo kkkkkkkkk

  • @EnesonWatheya
    @EnesonWatheya 5 годин тому

    Trump wathu back in office❤❤

  • @PixyBinoxy
    @PixyBinoxy 6 годин тому

    Azimayit abwera awa

  • @ElanioAlexandre
    @ElanioAlexandre 6 годин тому

    Yooo DPP Osanama umati munthu ukamavera nyimbo zake nthupi limachita kugwidwa Dzazi kuti ndinyimbo za chitimu chachikuru Koma zaenawo mmmm zauhule basi mavinidwe ake amenewo DPP mofaya basi📖🙏🏿

  • @RichardChagogo
    @RichardChagogo 8 годин тому

    MCP women no one 😂

  • @DeborahChapweteka-z9l
    @DeborahChapweteka-z9l 9 годин тому

    Yatsa moto ndi a DPP

  • @AlexPhili-e6c
    @AlexPhili-e6c 9 годин тому

    Mbambande dpp woye woye

  • @MayesoBikefa
    @MayesoBikefa 18 годин тому

    Kabwila sasamba iwe bwanji osavomeleza mukuwazuza amalawi

  • @KamuzuBanda-t2y
    @KamuzuBanda-t2y 18 годин тому

    🎉So lovely

  • @emilidarichardtembo
    @emilidarichardtembo 21 годину тому

    Abetcha loya APM boma

  • @rashidsabwe1616
    @rashidsabwe1616 23 години тому

    DPP nde kawawa❤

  • @ChametaJames
    @ChametaJames День тому

    Nice song from DPP woman

  • @FlorenceDouglas-x5c
    @FlorenceDouglas-x5c День тому

    Ine ndine ndani kusayamikila DPP my vote 👌

  • @SamuelNhlane-u3r
    @SamuelNhlane-u3r День тому

    Azimayi apeter amatha

  • @MikeyasiSalima-v1j
    @MikeyasiSalima-v1j День тому

    Bola dpp.moto kut buu

  • @MateyoMwale-u2n
    @MateyoMwale-u2n День тому

    Dpp,2025 boma zinthu zikwela boma lankhaza i

  • @MateyoMwale-u2n
    @MateyoMwale-u2n День тому

    Dpp,2025 boma zinthu zikwela boma lankhaza i

  • @CharlesAlindamao
    @CharlesAlindamao День тому

    Dpp ili bho bho

  • @holycity2017
    @holycity2017 День тому

    Palibe chazeru apa wose akumfunika ayambe dziwa Kaye Yesu

  • @WisdomMwale-j9h
    @WisdomMwale-j9h День тому

    Abetcha Loya Siyachibwana 🔥🙌

  • @WisdomMwale-j9h
    @WisdomMwale-j9h День тому

    Abetcha Loya Siyachibwana 🔥🙌

  • @YamikanBanda-z7z
    @YamikanBanda-z7z День тому

    Nanga bwanji osawamanga adpp wo,ndimayesa akuwaziwa awasiilanji?

  • @paulmartin8165
    @paulmartin8165 День тому

    Palibe chomwe dpp angabweletse cha nzeru mcp idalowa chifukwa chakulephela kwa Peter lero tivotelens Peter, tipite chitsogolo munthu uja wakula

  • @EdisonSipiri
    @EdisonSipiri День тому

    Dpp woyeeeeeeeee. Boma km ili osangozuka mkumati mulamulire manthongo ali mmaso mwatilephera basi vomerezan

  • @StainKambona
    @StainKambona День тому

    Dpp azimayiwa amatha kucheza

  • @MadalitsomanuelchiphakaMadalit

    A PM my vote

  • @MadaMachika
    @MadaMachika День тому

    Dpp yo kaa ine ai

  • @GasonBanda-i2f
    @GasonBanda-i2f 2 дні тому

    Km MCP BOMA chipani mchamoyo live tiyen amalawi tiziyamika osakonda ndale

  • @PatrickChikhwaza
    @PatrickChikhwaza 2 дні тому

    Abetcha lawyer yemweyo

  • @MarkMwale-x5p
    @MarkMwale-x5p 2 дні тому

    Kodi a congress akuyimba zichani nyasi zenzeni abetcha lyer nomber one❤❤

  • @GloriaSiyame
    @GloriaSiyame 2 дні тому

    Dpp

  • @JohnKanthiti-i1n
    @JohnKanthiti-i1n 2 дні тому

    Dpp WOYEEEEEEEEEE

  • @FredrickMunthali
    @FredrickMunthali 2 дні тому

    Apm my vote

  • @EnocWyton
    @EnocWyton 2 дні тому

    Mcp muloza zitukuko zaulele za ku china mulibe manyadzi

  • @EnocWyton
    @EnocWyton 2 дні тому

    Odi nane ndibetche loya ndizidikila chani

  • @Josephychithope-k2n
    @Josephychithope-k2n 2 дні тому

    Don't force matter

  • @ChipililoMaganga
    @ChipililoMaganga 2 дні тому

    Dpp ya Ana aosambatu

  • @ShabaniBashir-o8g
    @ShabaniBashir-o8g 2 дні тому

    Eya chilungamo tikuchiziwa kuti mwalephela Ife akumudzi tikuva kuwawa

  • @LenadiLenadikaziputa-r2s
    @LenadiLenadikaziputa-r2s 2 дні тому

    Mcp ikumwenya zitukuko posepose osati DPP imangoronjeza koma osapanga wamaso akuona boma ndiromweri

  • @CassimMeleka
    @CassimMeleka 2 дні тому

    Galu ameneyu wabwezelesa chiyani chiyambireni

  • @RaladyeTambala
    @RaladyeTambala 2 дні тому

    Panyapako wava mayi wopanda zelu akulemba ganyu chitsilu unapitako kulemba iwe panyini posatulutsa mwanapo ndipo usazalakhuleso sitikufunaso mbuzi yakoyo

  • @GabbinaTengen
    @GabbinaTengen 3 дні тому

    Ubwino wake tikavote ndife kusiyana ndinu muli thebanu

  • @ElliabWackson
    @ElliabWackson 3 дні тому

    Amene ayatsa moto mosapsatira kukamba koma azimai amcp chifukwa akukamba ndikuonetsa zitukuko zomwe president Lazarus chakwera wachita ndipo akadachita

    • @IjilanMwalija
      @IjilanMwalija 14 годин тому

      Kusonyeza asendela anakaonetsa zitukuko MCP bwenzi itawonesa chani😁😁😁😁😁😁😁

  • @HopeKatole
    @HopeKatole 3 дні тому

    DPP 2025 boma,,,,, a mcp mukhaula mwatinvetsa kuwawa

  • @KassimWilson-o8h
    @KassimWilson-o8h 3 дні тому

    Number kapena Ben zanyau bs