Report mene latulukira ndizomwe anayakhula Achakwera pa 10 June zosiyana

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 15 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 11

  • @SabinaChimbalanga
    @SabinaChimbalanga 16 днів тому +2

    Zoipa, kuseweretsa moyo wanzake ngati wankhuku

  • @Vincent-k4y
    @Vincent-k4y 16 днів тому +1

    chikangwawa bodza galu iwe Busa onyenga iwe 😱😱😱

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 16 днів тому

    Chakwera wabodza kwambiri.ndege inachoka ku Mzuzu mmawa osakumana ndi chifunga.chifunga chanapezena akubwerera past 10.eish akuluwa mngabodza

  • @AgnessMkwanda-xi7wq
    @AgnessMkwanda-xi7wq 16 днів тому +1

    Moyo wanu ndioyipa inu kumaligalira muli inu moyo wanu anthuu kuphedwa ngt nkhuku zooona😭😭

  • @SkabhuKabhu
    @SkabhuKabhu 11 днів тому

    Mulungu achita nawe kanthu chakwela wokupha iwe kod wuzakhala wambewu

  • @ThomasChilongo-m6f
    @ThomasChilongo-m6f 16 днів тому

    Uyu andichimwitsa shupit😮

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 16 днів тому +1

    PANYAPAKO IWE NDIWE CHITSILU KWAMBILI

  • @HafsaAbwanali
    @HafsaAbwanali 16 днів тому

    Maso ngati kazizi amangoti tong'ooo nthawi zonse kusonyeza ufiti mxxxx😮

  • @OsmanChisi
    @OsmanChisi 16 днів тому

    Chikangawa ndi MCP yako osakhalaso mu malawi

  • @AhmedPhillip
    @AhmedPhillip 16 днів тому +1

    Lazoro bodza bwanji kodi

  • @yusufbreak905
    @yusufbreak905 16 днів тому

    Repot lakale