A Chakwera Opanda Anthu Mukhala Mfumu? - Pastor G Tembo

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 15 вер 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Pastor G. Tembo reminds His Excellency the President that his presidency is based on trust. Without the people of Malawi, he cannot be President. Therefore, it is imperative that he condemns the violence being perpetuated by the MCP Youth.
    Pa Nyasa VoiceBox, Pastor G. Tembo akukumbutsa a President kuti udindo wawo wa utsogoleri ndi kukhulupirirana. Popanda anthu aku Malawi sangakhale Purezidenti. Choncho, mpofunika kuti adzudzule ziwawa zomwe zikuchititsidwa ndi Achinyamata a MCP.
    #malawi

КОМЕНТАРІ • 22

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza 12 днів тому +2

    Zonsezo chikangawa. yo akupangisa mesa iyetu akufuna nkhondo, ku Malawiko munthu woyipa uwu, kodi mukumusiya
    be kuti azipitiza kula mula dziko la lathu la 🇲🇼 Ambuye chonde, tichoseleni chakwera chonde Ambuye munati tipempha ife, tikupempha inu. Mulungu wathu,

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os 12 днів тому +3

    Anthu adzuke koma amuchotse uyu akumuti President yu.

  • @phindiswatshibo7101
    @phindiswatshibo7101 12 днів тому +1

    Auze ankhutukuvewa

  • @user-eo8dw8ss3j
    @user-eo8dw8ss3j 12 днів тому +1

    Tikayamba kubwezera police isazagwile munthu chifukwa tizawotcha ma offence awo

  • @chanzibadic
    @chanzibadic 12 днів тому +1

    Amcp tiwabwesela ndipo Monga ine nditanawo ngakale yamifuti

  • @user-jb5hr4rz2s
    @user-jb5hr4rz2s 12 днів тому

    Apresdent ndi munthu woyipa ,anthu akuphana iyeyo osayakhulapo osawonesa usogoreli

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 12 днів тому

    Zikomo abusa MCP ndi chakwela wawoyi anthu amagadzi tsadzasintha paka ndi akawina 2025 mobelamu amalawi OCHULUKA AKUFA 2025

  • @DamianoYohane
    @DamianoYohane 12 днів тому

    Jezebel ndi mchewa waku mchinji

  • @JohnMota-o2u
    @JohnMota-o2u 12 днів тому

    Tamufufuzeni chakwelayo kuomwe adabadwira kapena komwe kunachokela makolo ake. Nkutheka kuti simMalawi ai. Monga manganya kwa.mayake nku Zimbabwe nkuona akusineza Amalawi

  • @lyiemax
    @lyiemax 12 днів тому

    Things are not going on well, sizikukhala bwino

  • @WandileTradding-ph6fb
    @WandileTradding-ph6fb 12 днів тому

    Anthu inu please mulungu osamasewela naye please mukamapanga za ndale zanuzo wosamayikapo dzina la mulungu

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 12 днів тому

    Amaudindo wonse anagulidwa, palibe chimene apolis angachite, akuwopa kuchotsedwa ntchito, boma la mcp likufuna nkhondo zikuoneka ngati choncho

  • @malvinhusted6245
    @malvinhusted6245 12 днів тому

    Kwa iwowo ndizabwino mesa akufuna anthu azimenyana aziphana iwo azitolera magazi

  • @Kabwilachikangawa
    @Kabwilachikangawa 12 днів тому

    Wadzetsa kale chisokonezo inu simukuona??

  • @johnkambala692
    @johnkambala692 12 днів тому

    Alomwe kulilila ulamuliro

    • @jacquelinChitsulo
      @jacquelinChitsulo 12 днів тому

      this is racism

    • @UseniMailosi
      @UseniMailosi 12 днів тому

      Koma alomwe ndiye munatolatu

    • @lyiemax
      @lyiemax 12 днів тому +1

      Kulankhula kopusa

    • @tasmania527
      @tasmania527 8 днів тому

      Ukunena zoona..anthu awa akulira ngati achule a mu White Nile River.

    • @tasmania527
      @tasmania527 8 днів тому

      Kodi ukamati Chakwera akutuma anyamata ukutanthauza chani? Iwe mbuzi kwabasi