Kaliati ndi Brian Banda for president, it’s about time she’s the only one who can lead this party to victory , kabambe akuoneka watulo opusa, Brian Banda is a true son of the country, it would be a good combination
Eeeeish that song "kusayamika" hit differently. The guy gave all of him kut tonse iwina Kom mphotho yake mkukhala imfa.... Continue resting in peace my President SKC... Till we meet again.
Aaa WHERE HAS BEEN THIS SPEAKER SINCE 1994 ::? POLITICS IS A DIRTY GAME... SINCE 1984 TILL TODAY HAS BEEN IN THE GOVERNMENT. THE CLAIM IS NOT UTM BUT HERS... THE PRESENT GOVERNMENT SHE HAS AMONGST MANY TOP PRACTITIONER IN THE 🇲🇼. I DOUBT SHE CAN NOT DELIVER... POLITICS IS NOT CHILIMA YET WE DID LOSS OUR VP... NOT A PERSONAL PRESIDENT 💺🙏 PRAYERS
Koma kuphuzira si school yokha guys, Moti kukwera njinga Kwa a Chakwera lero yasanduka political speech? Kaliati mpake DPP inakutaya umayankhula za manyi heavy I hate you.tachioneni eti
Kumangoyankhula basi ngati nzophweka, she has been there with DPP and Tonse. Constitution yathu sangasinthe uyu. aMalawi anvekere Bomaaaaaa! Kunvetsa chisoni
Yomweyo my kaliyati ndinu presednt
Kaliati ndi Brian Banda for president, it’s about time she’s the only one who can lead this party to victory , kabambe akuoneka watulo opusa, Brian Banda is a true son of the country, it would be a good combination
@@shotsfired588 nzeru zanu ndizochepa akulu
Where did you get this information?
Hmmm 🤔. Tisadzanvenso kulira atakupusitsanitu 😂. Kupepela amalawi nkani andalewa amangokuyuzani
Nkhani yabwino chonde ÙTM musagawanikane be united divided we fall
Mayi uyu pena amayankhula chomwe sakuchidziwa, ndipo pazonse wayankhulazi anthu achoka pa masintha osanvapo kanthu
@@BoscoMaluzi nanga hule pajatu makhalidwe ake ndi amaphokoso ningomuitanitsa ku room akamalize uhule kkkk
Let us try to find sponsors to empower women to be leaders
Eeeeish that song "kusayamika" hit differently. The guy gave all of him kut tonse iwina Kom mphotho yake mkukhala imfa.... Continue resting in peace my President SKC... Till we meet again.
mcp ndiyakupha aliyese auziwa tikumana pa voti ife tikungoyangana tizakumana
Aaa WHERE HAS BEEN THIS SPEAKER SINCE 1994 ::? POLITICS IS A DIRTY GAME... SINCE 1984 TILL TODAY HAS BEEN IN THE GOVERNMENT. THE CLAIM IS NOT UTM BUT HERS... THE PRESENT GOVERNMENT SHE HAS AMONGST MANY TOP PRACTITIONER IN THE 🇲🇼. I DOUBT SHE CAN NOT DELIVER... POLITICS IS NOT CHILIMA YET WE DID LOSS OUR VP... NOT A PERSONAL PRESIDENT 💺🙏 PRAYERS
Akaliyati mulindiboza mwakhala zaka zingati muboma inuyo or saulosi chilima ngati munali anthu anzeru bwanji pamene munali muboma osathandiza anzanu mibomamo kuti mutukule malawi inuyo ndinu simukuyikpnda malawi inuyo chifukwa ngati mumayikonda malawi bwezi mulindanzanu kupanga nawo nzeru zimenezo tikususa inu mayi ndinu aboza kpma simulowaso muboma ndikupusisa anthu zinthu zaboza chilima akhala kawiri pa u vice prensdent bwanji zinthu ngati zimenezo osaphunzisa anzanu zaboza zimenezo
Nyimbo ya Azimai A utm yandimaliza mbambande ❤️ song
Kaliti wakhala unduna maboma onse apitawa bwanji sumasintha dzikoli? Galu wabodza iwe.
@@mosesadam-sk2yb so nduna ndi president nanu inu inudi ndachitsilu a mcp
@@NathanMaunda-dz8gc osanyoza munthu akukamba chilungamo
Chipani chaanthu ozindikira komaso azelu,,,God bress you,
UTM more 🔥
Munagwesa dziko nokha awkweni tthawi onsei munali momwemo zaka 30 MCP inali pa opazishoni mwawuwala kale
Angoti mulungu akuona ngati khazeni wake akadakhumudwa uyu mkwiyo wa chitsilu supindulitsa
U T M ndichipan chomwe ndikupepherera kt chiwine bas
Kaliati sanakhalepo president mmaboma onse wakhalaye, ndie analephera pati? She is just the best because akapasidwa ntchito amagwira ndi mtima
Where is the party president? Dr Usi. Basi chipani chatha ichi, taonani anthu akewo ngati msonkhano wa Masintha CCAP . 😊😊😊😊😊
Go deeper akweni
Kaliati mashini as UTM continues....palibepo angamumake nzimayi ameneyu ❤
Akweni ndi katundu omanga ndi mawaya,wayiponyera kwa Ma Big boys
Amai ndiye number 1 muthu mmodzi okondela
Kodi mai kaliati anali nduna Boma lomweri tanenani za atupere
Akweni has changed her tone and approach, that's better!
Kod nduna ndi president amalamulila dziko ndindani popeza akweniwa samakhaleko prsdnt
ama Khalsa president , ndina alingati mwana otumidya kokatunga madzi
Popanda kutelo nduna alichabe
Nde ntchito ya nduna ndi chani?? Nduna zinzake zimanyozedwa uko, ndunazo ndi ma president amalawi mukamazinyoza??
Eish that speech is tough
Dzikomo kwambili may kariati cotienue
Inu muiuyenera kutenga chithuchi
Bakili uja wakoma lero? Koma anthu andale
utm foreverr❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Mayi Kalayati ndi more palibeso
Exactly
Akaliati, ife tidzifunsa Inu kunena kuti ndichifukwa chani tikadali pa number 5. Chifukwa Inu ndinu mwakhala nduna konseko uku mmatani muundunamo ziko tsilikutdintha, mmatanimo muundunamo Akaliati?
keep it up madam
Iwe ndye ulibe mfundo zimayi iwe
More fire akweni
Makwana mama awuzeni abwampiniwa
🔥🔥🔥
Mama you're carrying us. Osafooka
Mai kaliyat mulungu atalikise Moyo wako
chipani chatha basi ichi...aaaa bola SKC mweni wake...uja.anali machine
❤❤❤
Kunoso ku Mponela mudzachitseko msonkhano mutivetsa kukoma kwambr
Kodi mesa inu munali momwemo kod mwaziwa liti zimezi
❤
Nanga mungayerekeze Malawi ndi xambia
Moti dziko likhoza kumadzsti kariati ndi president wa marawi kkkkkkk koma ndale!!!
Koma kuphuzira si school yokha guys, Moti kukwera njinga Kwa a Chakwera lero yasanduka political speech? Kaliati mpake DPP inakutaya umayankhula za manyi heavy I hate you.tachioneni eti
Umafu akonze zonse in 3years? Openga iwe
Iweyo umatani osamutsata chilima chifunga chitavuta?
Kumangoyankhula basi ngati nzophweka, she has been there with DPP and Tonse. Constitution yathu sangasinthe uyu. aMalawi anvekere Bomaaaaaa! Kunvetsa chisoni
Amalawi ambiriwa ndi zitsiru ndinaona kale. Amapanga ziganizo ali ndi mkwiyo osadekha lero ndi izi
Chitsiru Cha mzimayi ichi chitsiru chenicheni
M'MAI IWE! MULUNGU ADZIKUDALITSA."MORE FIRE"ADONA!!!!!
Chihule ichi chimatitopesa ndipo muzifunse kut zonsezi zabwera chifukwa Cha iwe unali nduna nthawi yaitali unapangapo chani ndi zigogo zako zilomwe zako
Utagwanika mwanawe
Mwafuma pa unduna Tu agogo
Ngati iyeyo analephera kutukula dziko lino ali ku dpp kaliat pano angapange chani😂😂 BOMAA NDILOMWERI AMALAWI SITIKUSITHASO AYI❤❤❤ MCP WOYEEEE CHAKWERA 2025 BOMAAAAAAAA
Munawoononga ziko ndinuyo alomwe inu a kaliati ndi chipani chanu Cha dpp
😁😁😁😁😁Koma zoona
Mwakhala mumaboma ambiri mayi kukhala panumbara 4 or 5 you are part of this failure
Koma amai awa aludziwa izi alulankhula. njala ya utsogoleri sungauone
Zako izo..
utm
Don't do compaign under chilima's death
Kaliati zose akukamba ndi zauhule basi amalawi adapenyatu ndipo akadachita ngozi amako suchita manyazi ukatchula chilima?
Chitsilu cha Mayi Ichi,wakhala nduna Ku boma angapo ap uzilakhula zofoira zakozi aaah nyesi za munthu
Imfa ya chilima wayesa yomenyera campaign ulibe manyazi
Mayi inu ndi panja penipeni nzeru mulibe inu munagulitsa ma company a boma mbava inu
Let us try to find sponsors to empower women to be leaders