ANTHU ADABWA NDI MBIRI YA BOSHOP THOMAS LUKE MSUSA( ZOTI ANACHOKERA KU BANJA LA CHISILAMU NDI ZINA)

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 15 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 135

  • @ClaraNdovi
    @ClaraNdovi 16 днів тому +2

    Àmen.Indeed our be loved BiSHOP Luck MSUSA, ndipo sitikuphyatilaso nkhani yo ndi yoona, akuyankhula chilungamo, ndi ndi Mulungu u amene akuyankhula chilungamo kudzela mwa our LORD Luke MSUSA. Ambuye atihandize abale akudandaulawo. Mizimu yawo Ambuye ailandile ku mwamba. Amen.

  • @SandraIssa-lo8il
    @SandraIssa-lo8il 18 днів тому +3

    Bravo Archbishop Thomas Luke Msusa for speaking on behalf of poor Malawians. Through the intercession of Mother Mary, our heavenly Queen, we ask the Lord to protect him from the evil eyes. Put them to shame , their evil intentions should be exposed.
    Let Malawians get the truth of what happened during the brutal demise of our beloved vice president of the Republic of Malawi and 8 others .
    God Almighty, hear our cries❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @spargomw
    @spargomw 18 днів тому +5

    Bishop Msusa andifanananira nd Rv Yasin Gama wa mpingo wa Mvama CCAP, Azibusa opanda dyera ololera kut ndibwino aphedwe koma ataima pa Chilungamo, Ambuye akuthangatiren ndikutetezani ku Nkhandwezi mu dzina la Yesu khristu Ambuye wathu

  • @AllaniAufi
    @AllaniAufi 18 днів тому +5

    Amen! Munthu wamulungu Bishop msusa

  • @lungisanishezi1023
    @lungisanishezi1023 18 днів тому +1

    Ambuye adzikutsogolerani archbishop, ndipo Mulungu alange azibusa onse otsutsana nanu ameen

  • @JosephLupenga
    @JosephLupenga 18 днів тому +9

    Zangoonetseratu kuti president wa mpingo wa Catholic kuno kumalawi ndiwanzeru kwambiri than president wa chipani cha MCP,,,, period!!!

  • @ChristinahNkwanda
    @ChristinahNkwanda 18 днів тому +1

    Mulungu wanu alinanu phaka muyaya sakusiyani panjira ai tipemphere molimbika nthawi zonse AMEN AMEN AMEN AMEN ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @BeataChome
    @BeataChome 18 днів тому +3

    Bravo our bishop. Blessed are the peacemakers

  • @MarySinjirani
    @MarySinjirani 18 днів тому +2

    Ambuye Mulungu wathu tikupemphani kuti muwateteze Arc bishop Msusa, azibusa ndi anthu ena onse amene akufunila dziko la Malawi Zabwino komanso chilungamo 🙏🙏🙏

  • @JosphineJoshua-gq1rp
    @JosphineJoshua-gq1rp 18 днів тому +1

    Leading without fear Long live Our Bishops

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 13 днів тому

    Mr Msusa amaima achilungamo ndipo apitilize kuopa Mulungu ndikulemekeza Mulungu chitetezo pakati pawo mr NSusa

  • @PatriciaMtwana
    @PatriciaMtwana 17 днів тому

    Bravo my Lord Bishop.

  • @noahkalima5294
    @noahkalima5294 17 днів тому

    Asilam ambili ndmbuli ,,amaona ngat Muhammad chigawenga alindmalo,pomwe Allah fano lakufa lilibe moyo,,komaso Muhammad chigawenga alikudima wandiwe Yani,,

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 17 днів тому

    Ndi mulungu amene wamuuza zimenezo ❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @MathewsMandutu-q9l
    @MathewsMandutu-q9l 18 днів тому

    Thanks alot arch bishop Luke nsusa,

  • @AndreaBotoman
    @AndreaBotoman 18 днів тому +4

    Munthu website weni weni wa mulungu uyu ❤❤❤

  • @ClaraNdovi
    @ClaraNdovi 16 днів тому

    Yes .and Amen. Ife abale athu tawasowa. Tithandizeni ndipo mumve kulira kwa ana anu

  • @JoshuaNyirongo
    @JoshuaNyirongo 18 днів тому +2

    Game over....Truth is coming tommorow.

  • @PatsonJacksonfundi
    @PatsonJacksonfundi 18 днів тому +1

    Bravo more fire bishop

  • @ShareefKalima
    @ShareefKalima 15 днів тому

    Aaaaa chakwela pa ulendo wapanidwa pa mpan ngat mbewa iffa wachilima yizaziwika bwino Ansilam Musawadyoze komanso Mr nsusa Mulungu akudalisen chilungamo chionekabe

  • @ChimtamboWiliam
    @ChimtamboWiliam 18 днів тому +2

    Man of god bishop msusa

  • @EdithKawanga-m7j
    @EdithKawanga-m7j 16 днів тому

    Ambuye mulungu adzikudalitsa Ambuye msusa, life it's a journey in the life of a person

  • @DynaDemba
    @DynaDemba 18 днів тому +1

    Man of God❤❤

  • @WatsonMalanga
    @WatsonMalanga 18 днів тому +4

    Mcp nkhondo mwayambayi simuyimaliza ndithu

  • @EuniceKapepeka
    @EuniceKapepeka 18 днів тому +1

    God is good all the time ❤

  • @AndreaBotoman
    @AndreaBotoman 18 днів тому +3

    Katundu wa boma uyu ❤❤❤

  • @catherinekadwala3839
    @catherinekadwala3839 18 днів тому

    God bless you Bishop

  • @DaudgiftChimaliro
    @DaudgiftChimaliro 18 днів тому +1

    Great history

  • @ChimuzyNgolanga
    @ChimuzyNgolanga 18 днів тому +3

    Archbishop Luke Thomas Msusa anakula kwambiri ndi amalume awo a Luka omwe anali achikatolika. Ambuye wa aleledwanso mu chikhristu chao ndi malemu bambo Emelio Nozza amene anali Bambo mfumu a Namwera Parish. Zosangalatsa ndikuti bambo awo omwe anali a chisilamu pambuyo pake analowa mpingo wa katolika.

  • @lucyphiri-b5y
    @lucyphiri-b5y 18 днів тому

    Continue fighting for the truth Archbishop

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam 18 днів тому +3

    Mwana. wakulu wina aliyese akuziwa kuti ndichakwela anapha chilima ndipo ndikangova kut mcp ndiyakhaza kwambili koma ndakhulupilira. Ndipo chakwela, chimwendo banda ndi moses mkukuyu ndi msilikali wakulu ndiyama new Ali zigawenga zazikulu chiwembu chachilima

  • @BenardBenjaminNjanji-x9y
    @BenardBenjaminNjanji-x9y 18 днів тому +5

    Khani iyi siitha pokhapokha black box itapezeka ndiye kuti zonse zatha

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 18 днів тому +1

    More fire comrade bishop anachita bwino kwambili ndipo asasiye

  • @FrancisBanda-c4g
    @FrancisBanda-c4g 18 днів тому +1

    Man of God

  • @manuelsamuel293
    @manuelsamuel293 15 днів тому

    Bishop Luke Nsusa savomera dzombwambwana nkona onse okonda kuvumatitsidwa ndikukonda dzoyipa amadana naye

  • @MaceddingsMoyo
    @MaceddingsMoyo 18 днів тому +1

    Zimene Bishop Thomas LukeMsusa did not make any mistake. Instead he only preached the truth about what the Bible is saying.

  • @SandraIssa-lo8il
    @SandraIssa-lo8il 18 днів тому +1

    Heavenly Father,
    Through the intercession of Our Blessed Mother Mary, the Queen of Heaven, we come before You with humble hearts.
    We ask for Your divine protection over Your servant, Archbishop Thomas Luke Msusa, and the entire Blantyre Cathedral. Shield them from all harm and evil intentions. We pray for the nuns who were targeted, that You may guard them with Your heavenly angels.
    Lord, we lift up to You the guard who was injured in the attack. May Your healing hand be upon him as he recovers in the hospital. Comfort him and grant him a swift and complete recovery.
    Expose the evil doers, O Lord, and let their hearts be turned toward repentance. May they come to know Your boundless mercy and grace. We pray that they will seek forgiveness and turn away from their wicked ways, so that Your name may be honored and praised.
    We entrust all our fears and anxieties to You, confident in Your love and protection.
    In Your holy name, we humbly ..Ameen...🙏

  • @KennedyOManda
    @KennedyOManda 18 днів тому

    ❤❤❤❤❤ msusa god bless,

  • @IsaacNkhoma-b2g
    @IsaacNkhoma-b2g 18 днів тому +1

    Ambuye thomars msusa. Mulungu akudalitseni pitilizani kudzudzula choyipa mulungu akutetezani osawopa

  • @EdinaMzati
    @EdinaMzati 18 днів тому +1

    Ambuye pitilidzani ntchito younikila ntundu wa a Malawi pa chilungamo cheni cheni pa ifa ya VICE president Soulos chilima

  • @MadaMw-f1k
    @MadaMw-f1k 18 днів тому +1

    Dziko likufunika anthu achilungamo ngati awa osaopa komachilungamo chikhale pasogolo

  • @StalnLossan
    @StalnLossan 18 днів тому +5

    Azibusa akanakhara ngati uyu zikorathu lilibwino

  • @MUHAMMADABUBAKAR-e2n9j
    @MUHAMMADABUBAKAR-e2n9j 15 днів тому

    zoti bambo ake adali shehe ndizabodza, ndipo mukamakamba nkhani muzipita kaye kumudzi wamunthuyo ndikumakafufuza bwinobwino kaye

  • @Gift-g1x
    @Gift-g1x 17 днів тому

    more fire❤

  • @BornrichRich
    @BornrichRich 18 днів тому +1

    Chisilamu nfi chikhulupiriro.
    Mulungu mmofzi sadabdwe ndipo sabereka.

  • @MaryManonga
    @MaryManonga 18 днів тому

    Ambuye akuze malile awo.amen

  • @TakalaniGlenda
    @TakalaniGlenda 18 днів тому +6

    2025 chofunikira nkuzangochotsa chakwera basi

  • @MemoryMteketi
    @MemoryMteketi 18 днів тому +3

    Chakwera kunkuyu chimwendo zikhare ng'oma brack box yituluke Changu zisilu inu

  • @DicksonMbwana-j1x
    @DicksonMbwana-j1x 15 днів тому

    Bishop wadzelu zakuya ambuye mulungu akhale naye amusunge amuteteze

  • @AustinAmini
    @AustinAmini 18 днів тому

    Thanks

  • @PatrickBiswick-x4v
    @PatrickBiswick-x4v 16 днів тому

    Chilungamo sichiopsa, tilikumbuyo kwao

  • @LINNLYMBETA
    @LINNLYMBETA 18 днів тому

    🙏🙏🙏

  • @AliBlack-k6m
    @AliBlack-k6m 18 днів тому +1

    Adali muyaawo osati mslaa.

  • @ActionLMbewe
    @ActionLMbewe 18 днів тому

    Choonadi chimawawa. Mulungu ateteze ndi kitsogolera Bishop Msusa

  • @MariaDandazaraJSDmoio2024e
    @MariaDandazaraJSDmoio2024e 18 днів тому +1

    Ambuye tikuwaikiza abishop awa manja mwanu kuti muwatete ku adani onse amene akufuna kuwachita chipongwe mbuku muli mau awa diso kwa diso itani chithu kuti iwo adziwe kuti kunja kuno kli mulungu. palibe munthu amene angakhale achite choipa koma. La 40limakwana iwowatu akusowa mtengo ogwila ndipame akungoti munthu aliyese walakwa ndikuwaikidza mumapephelo a mususa

  • @FaithJonathan-u8t
    @FaithJonathan-u8t 17 днів тому

    Akutetezeni chifukwa choima pa chilungamo

  • @CliffordMtuwa-u8z
    @CliffordMtuwa-u8z 18 днів тому

    Bishop Mulungu azikudalitsani chifukwa choima pa chilungamo

  • @MphatsoChilangiza
    @MphatsoChilangiza 18 днів тому +1

    A catholic tisaope njoka zimenezi ndipo a bishop a nsusa sangagwede zeke akumana ndi zambili iyi mcp ndi misala mumadziwa galu akapanga misala amapanga chiwewe awaso ayamba chiwewe ineso ndi nkatolika sindi ngasekelere zopusa iwe chakwera uganize bwino bwino kodi moyo wonyasa uja sunasiye kuzikuza kuzikonda mabodza ayi zikomo Tionana 2025 wayiyambayo

  • @LimzeySande-b9n
    @LimzeySande-b9n 18 днів тому

    A Bishop thomas msusa tilipambuyo panu Bambo mulungu azikudalitsani

  • @AliNtolera
    @AliNtolera 16 днів тому

    Don't judge iwe ndi ndani leka mulungu akhale judge chomwe ndawona bishop msusa Ali ndi mdaliso wautsogoleri komanso alibe Dyera ngati azisogoleri enawa palibe mulungu wakufa kapena wamoyo msusa akhale chisanzo kwa iwe onyoza kuti aliyense ndiofunika. Posatengela mphamvu kutchuka kupha kapena ndalama koma kuyima pachilungamo ngati nsogoleri

  • @andrewchirwa2193
    @andrewchirwa2193 16 днів тому

    Abusa ose akumalawi akanakhala ngati inu bwezi Malawi akanakhala wabwino pachilungamo

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri 18 днів тому

    Msusa Ambuye akhale nanu

  • @GeorgeYohanePaul
    @GeorgeYohanePaul 18 днів тому

  • @sheedampama1462
    @sheedampama1462 18 днів тому

    Mulungu akalemba walemba.

  • @MichaelChikhazu
    @MichaelChikhazu 18 днів тому

    Inuyo a bishop mupitize kalakilila nchoncho

  • @SimonGumulira
    @SimonGumulira 7 днів тому

    Zoona zake

  • @JosephykSolomon
    @JosephykSolomon 18 днів тому

    Ife a Katolika ameneyu ndi m'busa wathu wamkulu

  • @minguchitulutseni579
    @minguchitulutseni579 16 днів тому

    Chilungamo ndi chofunika

    • @AnthonyMulenga-g6j
      @AnthonyMulenga-g6j 15 днів тому

      God will those against Bishop Msusa man of living God.

  • @KondwaniNgambi-yl3te
    @KondwaniNgambi-yl3te 18 днів тому +1

    Amemeneo siomuseweletsa ayii ngakhare achipani Cha mcp chikuwasewetsa

  • @JohnmjigoMalinda
    @JohnmjigoMalinda 17 днів тому

    Osaopa osafooka mcp ikufuna khondo basi koma ikunama kwambiri iyi ya Bishop yokhayi chakwera with ur guys unya manyi ndithu agulu inu okupha.

  • @ShareefKalima
    @ShareefKalima 15 днів тому

    Bwezan mawu nkhan yilipo ndiyot Chilima ndi anthu 8 anafa pa ngozid ya ndege kapena anachita kuphedwa? Osat zonyoza Ansilam kapena achristu.

  • @rodricklupiya
    @rodricklupiya 18 днів тому

    Mantha satukula dziko100% tata tikufinilani moyo wautali

  • @JamesSuman-if2xo
    @JamesSuman-if2xo 18 днів тому

    Mu video yi Mukulimbikira zopanda ntchito, zoti kaya bambo ake anali ndani tilibe nazo attend. Nkhani ndiyoti Boshop yi ndikatundu ndipo ndi wanzeru.

  • @RomulusPhiri
    @RomulusPhiri 18 днів тому

    Olo Tive za Musussa tilibe nazo ntchito koma tili ndi ntchito ndi chilungamo chomwe akunena amusaswo

  • @Dinalamakanjira
    @Dinalamakanjira 18 днів тому

    ❤❤

  • @JosephMillion-i6v
    @JosephMillion-i6v 18 днів тому

    Zafikano pomakhapa alonda aku limbe cathedral kunena nkumati achiwembu. koma akulu akulu zikoli tizingokhapana zoona ?

  • @FulumensioTembo
    @FulumensioTembo 18 днів тому +1

    Munthu wamulungu ameni

  • @InnocentKavalo
    @InnocentKavalo 18 днів тому

    Amen

  • @PriscaMussah
    @PriscaMussah 18 днів тому

    Mvula ikagwa,nthawi yoseyi aimumatipatsa mbiriyqke ,kma chifukw akanq ziphuphu nde munsakatulepo,amalawi sazatheka antaa

  • @KweseLubonga
    @KweseLubonga 18 днів тому

    Awawa nde akatundu

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 18 днів тому

    Yasini sangalalinge zimenezo ai

  • @PrinceChiwaya-q6s
    @PrinceChiwaya-q6s 17 днів тому

    Ine ndikuthokoza kwambiri chifukwa cha zolankhulidwa pa nkhani yokhudza report la ndege, andale akamadzudzula Boma amabweretsa njira zawo zomwe amati zidzathandiza kusintha zinthu iwo akadzatenga Boma kodi olemekezeka a Bishop Thomas Msusa popeza sanakhutire ndi report lija iwowo ngati munthu amene akudziwa bwino chomwe chinachititsa kuti ngozi ija ichitike bwanji osabweretsa poyera umboni kapena report lachilungamoro? Chifukwatu munthu wamkulu mchipembedzo asamachite zinthu mozembera ai ngati palibe kuzembera apa a Bishop bweretsani report lanu ife tikuliyembekezera koma chenjezo ndi ili mu chipembedzo cha katolika muli otsatilanso zipani zosiyanasiyana bwino kusoneza akristu anu musayiware mau aMulungu amati musakonde dziko lapasi ndi za mdziko lapasi za uzimu ndi za thupi nzosiyana

  • @patrickmatabwa5828
    @patrickmatabwa5828 18 днів тому

    Ofunikanso kuyamba kupanga regulate mipingoyi chifukwa oyipanso akugwilitsa ntchito mipingo eg thandizo la azibusa opanda mpingo linachokera kuti mpakana kupanga hire malo mkupangisa press briefing and kulipilanso pa wailesi...who sponsored them?? Mu church ndimomwenso mwabisala anthu oyipa kwambiri kuposa ku tarven....

  • @BiliatiJoâo
    @BiliatiJoâo 18 днів тому +1

    Zilibwino asosa sanalakwe ponena chulungamo

  • @LuluKansonde-e6c
    @LuluKansonde-e6c 18 днів тому

    Ndipo ifeyo sitikulora zopusa zomwe akuchita achakwere ndi azawo ndi galo kwabassi

  • @zayedmitawa8345
    @zayedmitawa8345 18 днів тому

    Che Msusa wakuche Iba,ku Katuli

  • @KingstoneManyanda
    @KingstoneManyanda 18 днів тому

    Munthu wamulungu amen❤❤

  • @CharlesKangulu-l2b
    @CharlesKangulu-l2b 18 днів тому

    Timenyeleni nkhondo a bishop athu

  • @GraceMwase
    @GraceMwase 18 днів тому

    Odala iwo okumva njala ndi ludzu lochita chilungamo

  • @MphatsoChilangiza
    @MphatsoChilangiza 18 днів тому

    Inu akunena za ansusawo akusowa chonena akufuna kusokoneza chikatolika amaona ngati mphavu zose zili mmanja mwao moti simaona kuli kose angakhale ansusa chilimaso amakhala komweko ana achepa inu a chakwera number yanu nda deleter mu 4n yanga mwandinyasa kwambili ndi ulamuliro wanu

  • @JamesKPhiri
    @JamesKPhiri 18 днів тому

    Umakwana iweyo umatha kumasuka

  • @HashimuMaximbo-g4c
    @HashimuMaximbo-g4c 14 днів тому

    Eee komatu ndikumwamba zonsezi

  • @MatlidaMsisya
    @MatlidaMsisya 18 днів тому

    Munthu wa Mulungu ameneyu

  • @MarthaMindiyera
    @MarthaMindiyera 18 днів тому

    ambiye salakwitsa

  • @InnocentHassan-m3r
    @InnocentHassan-m3r 18 днів тому +1

    Kuima pachilungamo

  • @Mirriumkamwendo
    @Mirriumkamwendo 18 днів тому

    Ife tikufuna black box basi

  • @ElvisMSESichali
    @ElvisMSESichali 18 днів тому

    Speak louder

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn 18 днів тому

    MA MEMBERS A MCP AKUNDIFUNSA NGATI KU DPP KULI MALO . KODI NDIWAYANKHE KUTI CHANI MR NAMALOMBA???

  • @BlessingsHarneck-p3y
    @BlessingsHarneck-p3y 15 днів тому

    Sindingamvele olo patavuta

  • @AliBlack-k6m
    @AliBlack-k6m 18 днів тому

    Zoonama uyu an alien muyaawo