I am disappointed with what my Lord Bishop has said. The report is very clear. Let us all pray for our Bishop so that he may not be led into temptation. We need each other's prayers.
ndie mwati chani pamenepa. Disappointed chifukwa walankhula maganizo ake za report? Tsono dziwani kuti zomwe walankhula Msusa zikuimira maganizo a aMalawi about 95% ya population. 5% yo ndianthu adyera ngati a Mvula, a Msonda, Dan Lu..... just to mention the least.
which temptation akulu. Because he is saying the truth!? Do you trust that trash and compromised report!? Inu ndiye mugwadadi. Pempherani koma chilungamo chidziwika. Wakubayani basi
Ndikovuta kuti a Malawi tivomeleze lipoti limeneli la Ndege yomwe idapha anthu 9. The same way zidachitikila za imfa ya Gadama Matenje, chiwanga komanso Sangala tinkauzidwa kuti tisalankhule koma zoonadi zenizeni zinali zoti anthuwo adachita kuphedwa ndi MCP....leronso akuti tisiye kulankhula chipani chake ndi chomwechinso funso mkumati Kodi adafawo ndi abale awo? Ife tilankhula mosawopa ayi mudatinaniza kuti ndege idagwera ku kuphedi kunkhalango yokhwitima, ndege idafika ku mzuzu kenako siyidafikeko timve zitizo? Mwatenga nyau kumazunza ife a Malawi ngati dzikoli ndi anthu Ali chigawo chapakati lokha.....2025 mukalowa ku ndende monga majaji opuma ajaaaaa alankhulira. We are not stupid Malawian like before....we are in a democratic county....no smartmatic kuno ku Malawi ayi....Mau a mphamvu a Bishop athu omwe mwalankhula ndipo sinthawi yomuopa munthu ngati iyeyo ndi Mulungu
Am amuslim but am solely behind on u Bishop but what iwant zomwe munamupanga Peter pliz panganis panop munkakhal ndi misa mwina pasiku 6 kuti Peter achoke munthu opanda bekoz ngt uja lerol mukungoyankhul no action mmmm ayi
Kodi 17 million munatenga ndi yomwe ikukulakhulitsani izi.last time ku nsipe munayankhulatu za mzeru kwambiri.lero nde mwapala tu ambuye.paja amafuna anthu apeleke umboni inu simumaoneke,nde mau anuwo ndiomasula osati kumanga.
A bishop a dyera awa awoneseratu ankamudyera chilima uja nde uku ndikulilira chabe zomwe ankapasidwa ndi bwana chilima, kulankhula mopanda nzeru ngati bishop and he don't even deserve to be a bishop, bwanji simunapite inu a msusa kukapereka zomwe mukuziwa ku commission of inquiry. Awa a bishop akuyenera kupempheleredwa ndi ma bishop anzawo plz.
I understand your pain. I am also disturbed by what my Lord has said. He is definitely on the wrong. But please, address him respectfully. You are not alone, but some of us he is our leader. That way, we will be on the same page, else we might reluctantly change sides if you disrespect him.
Aaah inu a fidex kumwenda mutu wanu sugwila inuo ndi amene mukufunika dilivalasi mukulankhula mopusa kwambiri.Bishop akuyima pachilungamo a bambo ako a chikangawa awononga chinachilichonse mmalawi muno. I think iweo ndi wa mcp chifukwa ukulankhula mopusa. Lipoti la ndege palibe ca mzeru ciliconse cilimo bodza lokha lokha basi ife si ana, A malawi a lero si a 1930 inu a manyaka congress party mudziwe zimenezo tionana 2025 nyau zonse wa ku kasiya.
Inu nonse a manyaka congres party tionana 2025.Palibe ca mzeru chilichonse chili mu lipoti lija mbwelela dzokhadzokha cikangawa akuona ngati a malawi a lero ndi a 1930 mbuzi za anthu.
That's why Kuli mipingo yambiri yomwe inatuluka mu katolika, kuzimva kuti ndi olungama, chonsecho amfiti ndi iwowo. Oweluza ndi Mulungu. I hate ur comment bishop. Preach abouy hope to the hopeless. Paja timakudziwani kuti mumapita kugome mutamwa mowa no wonder why Pena u behave like this

Siife ana iwe we all know imene ijayi si NGOZI ndiife akulu akulu sitinganamizidwe anthu ndmantha chabe koma Mulungu adzatithandiza
which temptation akulu. Because he is saying the truth!? Do you trust that trash and compromised report!? Inu ndiye mugwadadi. Pempherani koma chilungamo chidziwika. Wakubayani basi
Inu ndi Achitsiru ndithu ndipo Mulungu akukantheni, amalawife siopusa ugaru wanu mudziwanso ndithu mfiti zinyau zachachabe
Mfiti iwe kanyere kudabwe mfiti iwe
God bless you Bishop ......uku ndiye kulakhula.....kwà mzika ya Malawi 👏
I agree with you Bishop mwayankhula zomanga malaw osat kuononga God bless you
Fantastic Bishop God blessed🙏🙏
May ALLAH Bless You Bishop
True true our beloved Bishop for speaking the truth
@@CatherineMunthali-r1f reality
Chilungamo Chake my Lord Bishop,,, Amene zikuwawawa akudziwapo kanthu ,,,Zizaziwika zoona zake patsogolo
Mulungu apitilize kukudalisani a bishop Thomas Luku nsusa chifukwa chiyankhula mosawopa mosafooka koma mwayima pa Chilungamo ❤❤❤❤❤
Kwa Jehovah kulibe Mantha and Glory be to HIM
Chilungamo chimazaveka ngat bwano...God be with you man of God
God bless you our really Bishop
Reality talk be strong bishop
Big up❤❤❤❤❤❤
Thank you my Lordship. May the Lord bless you for taking the stand on these issues
Am with u bishop
Uku ndiye kuya khula chilungamo anthu awa osawaphwekesa
May the Good Lord protect you our beloved bishop
Ngati zakuwawa ndizako ndi ufiti wakowo kkkkk😅😅😅 A men and 🙏 God bless you Bishop, ngakhale ena zawawa chifukwa cha chilungamo chanu....
You stand for the truth bishop
You have spoken the very powerful message.you are the really choosen to demonstrate the truthful what Jesus shown while He was on earth.keep it up
may God always continue to guide and protect you bisho Msusa🙏
May God protect you ✊🙏osaopa, osatopa, osafooka!✊✊✊
may God continua to guide and protect you bishop Msusa
Ndikovuta kuti a Malawi tivomeleze lipoti limeneli la Ndege yomwe idapha anthu 9. The same way zidachitikila za imfa ya Gadama Matenje, chiwanga komanso Sangala tinkauzidwa kuti tisalankhule koma zoonadi zenizeni zinali zoti anthuwo adachita kuphedwa ndi MCP....leronso akuti tisiye kulankhula chipani chake ndi chomwechinso funso mkumati Kodi adafawo ndi abale awo? Ife tilankhula mosawopa ayi mudatinaniza kuti ndege idagwera ku kuphedi kunkhalango yokhwitima, ndege idafika ku mzuzu kenako siyidafikeko timve zitizo? Mwatenga nyau kumazunza ife a Malawi ngati dzikoli ndi anthu Ali chigawo chapakati lokha.....2025 mukalowa ku ndende monga majaji opuma ajaaaaa alankhulira. We are not stupid Malawian like before....we are in a democratic county....no smartmatic kuno ku Malawi ayi....Mau a mphamvu a Bishop athu omwe mwalankhula ndipo sinthawi yomuopa munthu ngati iyeyo ndi Mulungu
Amen Amen Bishop🙏🙏🙏
Tili pa mbuyo pa a Bishop
God bless our bishop timadalira asisongoleri monga Inu absp
Amen bishop
Speak reality
CATHOLICS hav spoken ikakubaya ndiye kuti ndiyako
Love AM TV channel
🥳💙
May God bless you our bishop
Am amuslim but am solely behind on u Bishop but what iwant zomwe munamupanga Peter pliz panganis panop munkakhal ndi misa mwina pasiku 6 kuti Peter achoke munthu opanda bekoz ngt uja lerol mukungoyankhul no action mmmm ayi
God bless you
Koma ndidzowona ambuye yesu anabadwa pa 25 December kodi bible likuti chani yelemiya 52:31
Kuyankhula mosapsatira , chilungamo chenicheni ichi. Kuyankhula kopanda chigamba. Where is black box
I agree 💯
Kulankhula mwanzeru a bishop chikangawa akuchoka 2025 ndipo ameneyu adapangadi
Mulungu akudaliseni bishop nsusa chilungamo chizaziwika pangachedwe mdima uzachoka kuwala kuzafika
Unenesko a bishop report la Chikangawa Ili better mphanyi wakaleka Waka ndaniche
Khokhokho a bishop
Wakwiya ndi mfiti , pakutiso chilungamo chimawawa, ngati kwanuko sikunafeko munthu udana ndi zomwe wanena Bishop m'susa....
Kuyankhula choonadi Bishop koma tipemphelereni mvula
Kugwa kwa Congress party
Ulemu wanu Bishop ifeso tili pambuyo panu chakwera anapha chilima ndipo choona chake
Azogoreli ose aa mcp ndiophusa palibe asogorelu ndimasataniki
Mufuna muononge ndale waziyamba litigation?
Mulungu mwini mayo ndeye mwini chilungamo, ziululika
Zoonadi chilipo chinachitka pokugwa kwa ndege imene ija ndipo ochitawo adali ACHAKWERA ndi CHIMWENDO adatuma zigawenga kukapha Chilima.
Point
siinu nokha bishop amalawi tonse
Ndiwe mbuli
Kodi 17 million munatenga ndi yomwe ikukulakhulitsani izi.last time ku nsipe munayankhulatu za mzeru kwambiri.lero nde mwapala tu ambuye.paja amafuna anthu apeleke umboni inu simumaoneke,nde mau anuwo ndiomasula osati kumanga.
I am also disappointed with the bishop. Why not to ask Monsior Thawani who was part of gulu lofufuza. A Thawaniwo akuwakayikira.
Biyeni anachita chobaya siyinu nokha Bishop tonse tili okumudwa ndikusagwitsana Kwa report limeneli
Amen
Awa amangidwa ndipo.mundikhulupilira pazomwe ndalosera ine coz wawolokera za eni aziwona crc
That's the end of Malawi Cain Party ( MCP)
Inenso sindingakhulupilire ndi anthu awa chifukwa black box sanatulutse akubisa chani
Tiri busy kusaka ndalama
Naye Bishop ndi munthu amasankha chomusangalatsa kusiya chomuipira.
A bishop a dyera awa awoneseratu ankamudyera chilima uja nde uku ndikulilira chabe zomwe ankapasidwa ndi bwana chilima, kulankhula mopanda nzeru ngati bishop and he don't even deserve to be a bishop, bwanji simunapite inu a msusa kukapereka zomwe mukuziwa ku commission of inquiry. Awa a bishop akuyenera kupempheleredwa ndi ma bishop anzawo plz.
Yatha game
Sono ngati muli nawo umboni mulekelanji kupeleka umboniwo chonde
Only God knows 😜
Let the bishop do his own enquiry. What a confusionist!!
Mad bishop
Munthu kufa or nkozo osaoneka nde ife tikakhulupirire zimenezo kkkkkkk tiye nazo a bishop
Ndiye iweyo osakafufunza zoti ukhutirezo bwanji
chisilu galu iwe
@@RhodrickBanda pa nyapako galu
I understand your pain. I am also disturbed by what my Lord has said. He is definitely on the wrong. But please, address him respectfully. You are not alone, but some of us he is our leader. That way, we will be on the same page, else we might reluctantly change sides if you disrespect him.
Ngt mumalandila ndalama ku MCP ife zisatikhudze AMBUYE anena anena osakwiya
Kugwa kwa Mcp @@DadTshepo
Azibusa amasikuano chinyengo
Busa walakhulatu uyu chakwera walakhula chochi dzulo hmmmm ndakayika Mau Mau
A bishop just do your own enquiry otherwise to us . Malawians the report is just ok
😮😮😮😮satanic.
Anapanga kale that's why akulakhula chotero
@@SliviaJosephyALITULUTSE TILIONE
Aaah inu a fidex kumwenda mutu wanu sugwila inuo ndi amene mukufunika dilivalasi mukulankhula mopusa kwambiri.Bishop akuyima pachilungamo a bambo ako a chikangawa awononga chinachilichonse mmalawi muno. I think iweo ndi wa mcp chifukwa ukulankhula mopusa. Lipoti la ndege palibe ca mzeru ciliconse cilimo bodza lokha lokha basi ife si ana, A malawi a lero si a 1930 inu a manyaka congress party mudziwe zimenezo tionana 2025 nyau zonse wa ku kasiya.
Bwanji munapita kukapereka umboni wanu ndiye anaukana kapena?
BISHOP tu simunthu wamba ayi ayenera kulemekezedwa.Monga ndanena kale kuti iwonso ndi munthu amadziwa choipa ndi chabwino ndiye tiyeni tiwapatse ulemu wawo monga mabukhu adzipembedzo amati AMVERENI OKUTSOGOLERANI. Koma funso nanga nali.Kodi a Bishop anapita kukapelekera umboni ku Inquiry? Chifukwatu mu Inquiry muja munalinso a mipingo ndiye panalibe chovuta kupita kukakumana ndi amipingo anzaowo ndikwanong'oneza zomwe akudziwa olemekeza a Bishop osati zomwe akungoganizira ayi.
Dzikomo a yasini cifukwa coyima pacilungamo MABISHOP ngati awa pofunikadi kuwalemekeza coz monga mwanena nawonso ndimunthu akutha kuona momwe dzinthu zilili dziko muno.
Ngati a Satana ndinu a Roman Catholic mbuzi Za anthu
Zikhuzana bwanji 😂
Satanic wankulu ndi mbuye wako chakwera yemwe adapha chilima osalakwa, machende ako mwana wahule iwe
Obisa machimo sadzaona mwayi
Very disappointed with my Bishop
I thought you will talk about unity .
Inu nonse a manyaka congres party tionana 2025.Palibe ca mzeru chilichonse chili mu lipoti lija mbwelela dzokhadzokha cikangawa akuona ngati a malawi a lero ndi a 1930 mbuzi za anthu.
Dziwanda idzi muwuzetu ana anjoka 666 anthu oyipa ingoyambitsani chipani aloma patey
Sukuziwa chomwe ukuyankhula ase
Ndi m'mene anagwela Ngwazi Dr H.Kamuzu Banda. Kusamva chidzudzulo.Anthu ake ndi omwewa.
Eeeeish koma
That's why Kuli mipingo yambiri yomwe inatuluka mu katolika, kuzimva kuti ndi olungama, chonsecho amfiti ndi iwowo. Oweluza ndi Mulungu.
I hate ur comment bishop.
Preach abouy hope to the hopeless.
Paja timakudziwani kuti mumapita kugome mutamwa mowa no wonder why Pena u behave like this
Tifufuza tokha ife a Catholic
You are speaking as a politician not as a Bishop
Ndale ndi zamulungu ndizimodzi iweyo ndamene uli wandale , bishop akukamba choona iwe uziti ndale ndale utathauza chani
A katolika ndiye satsekedwa pakamwa olo mamiliyoni atakhala apa
Zoona zake anaphedwa mtumiki wao
Akadachita bwanji nthumba muli 17 million kwacha yochokera kwa Kabambe
Lemba lako galu iwe report
Galu ndiwe
Ndiwe galu kwambiri ndi chipani chakocho
Malawi wathu
Nanga ngozi ya kuchikangangawa ya Bishop zuza munanena zimenezi
Bishop zuza anafa pa ngozi yodzidzimutsa
Ndiwamdale uyu pali za mau a mulungu apa? Bwanji sadakapereke umbon pakafukufuku satana akuchokeren a bishop
Muyalukabe akupha inu
@@Noelbanda-j1l Bwanji sanamuyikemo mu komishoni yo amawopa chitani???
Ayambure iweyo ku kuchokera Mw wa njoka iwe ukhaula
Akamba pati kuti sakukhuthila ndi report landege apa mwina sindinanve ndiyine
@@AlihIbrahim-s7v veraniso yonse kut munve anena choncho
Replay maybe u will hear pomwe akamba zoti sakukhutila ndi zofufuza za ngoziyi.
ngati simunamverebe a Ali, pangani FF>> to 2:53 mumva

Wanena zoona,