KAUMA ANGLICAN CHOIR - NDIRI NDIYESU (Official Music Video)

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 24 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 8

  • @YamikaniSanjani
    @YamikaniSanjani 6 днів тому

    Nyimbo zanu zimatusutha amen amen

  • @denniskanzingeni6053
    @denniskanzingeni6053 10 днів тому +1

    The Best choir of our times

  • @mtenderechilombe8381
    @mtenderechilombe8381 10 днів тому

    Azimai mavalidwe oonetsa manja, pa mtima, miyendo ndimavalidwe odetsedwa. Inu kufa lelo simukalowa kumwamba chifukwa chamavalidwe awa ovula.

  • @mtenderechilombe8381
    @mtenderechilombe8381 10 днів тому

    Makwaya a kumalawi amavina zachikunja ndipo nosenu mukapanda kulapa nkusiya mavinidwe ACHIKUNJAWA plus mavalidwe achikunja simukalowa kumwamba. Yesetsani kupempha Ambuye akuyeletseni muntima mukatelo mavalidwe anuso adzasintha chifukwa Mzimu oyela udzalowa mkati mwanu nudzakuphunzitsani mavalidwe oyenelela achi Christu. Welengani Bible kuti mudziwe zambili za Yesu

  • @arnoldchikopa2611
    @arnoldchikopa2611 10 днів тому

    Beautiful

  • @margaretglem6933
    @margaretglem6933 10 днів тому

    nice song

  • @KaputeniMpinganjira
    @KaputeniMpinganjira 9 днів тому

    Nosenu mukamayimba mumandidalitsa kwambili

  • @EzaraJanuary
    @EzaraJanuary 3 дні тому

    Amen