Zina kambu zina leku mwanayu ali ndi luso loopsa mumayimbidwe.....kumayamikira munthu ngati akuyimba akuchita bwino mumayimbidwe cos mwanayu ndi wakhama ndipo she keeps the name of her mother alive....mulungu apitilize kumugwiritsa ntchito kuti akamakula tizipitiliza kuonanso creativity yake mmene ikukulira....we love keep the fire burning
Miracle iweyo ine ndimasowa pokuika❤❤❤❤❤ You are really a Miracle to our Nation, the way i loved your mother esh ambuye apitilize kukugwilitsa ntchito posintha miyoyo ya anthu ndi utumiki wako mimi. Receive your flowers 🌹🌹🌹🌹🌹
Misozi maso mwanga ya zisomo eti😭🙏Imfa ya Amama inaziwisa mwanayu kuti mwaiye mulinso Madalitso 🫂chikhala kuti mayako alipo ife kuno bwezi tikungoti nyimbo nda mayako iwe angokuyika pa tsongolo😭koma ai ndinthu......
Asisi anga mwaimba ndipo iwe ndi One serious ukutivinitsa Mulungu apitilize luso lako ndipo Amai ako atamwalira nnalira cos ndinkazifunsa kuti tizapezanso mzimai ngati amene uja koma Mulungu sanatitaye apa anatininkhadi Miracle ❤❤❤❤❤

Obwera kuchoka ku mikozi let's gather here
👍
We here
Grace Chinga weniweni zuchita kusangalatsa well done miracle qeen of Gospel iweyo 🔥🔥
Grace chinga uja sanafe alipo, ndiye mwana wakeyi love this song 🎉🎉🎉🎉
Apapa ndie ndamuona Grace Chinga weniweni ndendende mwa iwe for the first time.Iyiyi wapha♥️♥️♥️🔥
What a young talented lady like my comment I will come back to watch this video ❤❤
Miracle iweyo ine ndimasowa pokuika❤❤❤❤❤ You are really a Miracle to our Nation, the way i loved your mother esh ambuye apitilize kukugwilitsa ntchito posintha miyoyo ya anthu ndi utumiki wako mimi. Receive your flowers 🌹🌹🌹🌹🌹
What a talented young woman is kusungabe mbendera ya mama like my comment
Misozi maso mwanga ya zisomo eti😭🙏Imfa ya Amama inaziwisa mwanayu kuti mwaiye mulinso Madalitso 🫂chikhala kuti mayako alipo ife kuno bwezi tikungoti nyimbo nda mayako iwe angokuyika pa tsongolo😭koma ai ndinthu......
Sending flowers miracle ❤❤❤❤❤❤this is great
Aaa Miracle receive my flowers❤️❤️❤️❤️umandiyimbira bwino
Wow...this is nice....Grace chinga weniweni
Awwww am happy you trusted us to Dress your team 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Umatha Mimi
Excellent a Miracle mungotikumbutsa Masten,big up.
Like mother like daughter, powerful song 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Fire mabomba miracle nyimbo ili bwino kwambiri keep it up
I don't understand anything but I like the song and dance too...
Lots of love from Kenya❤
Keep soaring 🦅
December nde tailowa bwino tu miracle moto 🔥🔥🔥🥳🥳🥳
Mbambande. Cheers to the gentle voice ❤
Keep the fire burning🔥🔥🔥ur on the map
Nice dear mwaiwe muli zazikuku aaaa nice
Miracle you are a miracle indeed ❤ this
Miracle always deliver 🔥🔥🔥Five minutes straight of vibing, lyrics, costume and the dance all top notch amwene! Talent yosakamiza iyi
Jealous down, the song is vibrant 🎉
Zilibwino kwambili...umatha iweyo love u mimi
Great song keep on fire burning 🔥
Wapeza book la Nyimbo la masten etiii....it's giving gra🔥
Nice song miracle moto kuti buuu,, may God continue to bless you ❤❤
Grace is not gone coz we are still blessed with her daughter's songs 😊❤️God bless you Miracle
Nice miracle ❤❤ keep it up
Nice miracle chinga ❤❤
Wow🎉🎉🎉 true definition of zoyamwira😊😊😊
Chi hit chili bho 🔥🔥🔥🔥🔥
Ambuye apitilize kukudza malile anu sister good song ❤❤
Grace chinga ndendende🔥🔥🔥🔥🔥🔥
To say truth, you're blessed with talent
Luso lipose apa..Keep it up ..May God bless you Miracle
Asisi anga mwaimba ndipo iwe ndi One serious ukutivinitsa Mulungu apitilize luso lako ndipo Amai ako atamwalira nnalira cos ndinkazifunsa kuti tizapezanso mzimai ngati amene uja koma Mulungu sanatitaye apa anatininkhadi Miracle ❤❤❤❤❤
Eeeeeeh Aunt Mimi iyiyi mwapha mmm Ambuye azilemekeza okha apa🔥🔥🔥🔥
miracle umativetsa kukoma kwambiri.. keep it up pitiliza kuimba kwabwino
Unabwera mimi🔥🔥🔥🔥❤️
🎉🎉🎉Nyimbo ndiyomweyi sitikusitha❤❤❤
Ooh yes powerful song 🔥 🔥🔥🔥🔥🔥❤❤❤❤❤❤
Chinyimbotu mbambande 🔥🔥🔥🔥💥💥💥💥
Ayi zkomo thats awesome🔥
Those follow Real Future Malawi let's all gather here 🔥 to support our sister's video 🔥 nice video ❤❤
Keep it up miracle your such a blessings to the world received your 🎉🎉🎉🎉🎉❤
🔥🔥🔥🔥🔥 tapeza nyimbo yapa Christmas tiyeni tiyipase moto wambiri
Ndadzikonda kwambili luv this song 🥰 Great osa4ka mwainu tikondwera❤
Ili bwino shaaaa❤❤
Well done May God bless you
This is a hit song demn😭😭♥️am just smiling inu eeeh Miracle ndiwe dolo kwambiri ❤
Ine pheeee pano kuseka ngati ndapengatu nice song CC 💯
Indeed, Grace Chinga is a legend.
Amen umatha iweyo like mother like daughter ❤❤
Like mother like son ,, perfect madam🎉🎉🎉🎉 mwayiyakisa hvy💥💥
Iyi indithera ndalama sure🎉❤💥
Mbambande kuimba kwa mphamvu 👏👏👏👏👏
🎉🎉🎉🎉wabwela ngati coming ❤❤❤❤
Mbambande tikuzomuka ndthuu 🎉❤❤
Good song keep it up iweyo umatha🙏🙏🙏🙏🙏
Bombatuuuuu. Iweyo umatha Ambuye azikudalisa tivine basiii🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Mbambande miracle chinga
Moto kuti buuu 🔥🔥🔥🔥🔥
Nice tune, keep it up mama
💪💪💪💪💪💪💪💪
Ooooh my God continue to bless this young lady
Ehee kom chi mwana ichii😂😂😂🙌🙌🙌
❤❤😅 this is great so unique 🔥🥰
Well done Mimi ur great in gospel music ❤❤❤
Iweo umantha 💞💓🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Nice Song ❤ Miracle 😍
Nyimbo ya bwino,well crafted ,well composed and well sang ,,video on point
Miracle iweyo ndi mbambande umandivetsa kukoma
This is powerful song ❤❤❤
Good job Mamie, the osaopa Maria part is giving 🔥 your mama is proud in heaven 🥰
Beautiful song ❤❤❤❤❤ 🎉🎉🎉
Wow umatha miracle
Kuyinvera kuchokera ku Mozambique ♥️♥️♥️♥️♥️♥️♥️ usabwerere
Hallelujah 🙏🏾🙏🏾🙏🏾
Love from Zambia 🇿🇲
Wabaya miracle uli ndi luso 🙏
Chi Hit chabwera kuzakhala
Miracle chinga you're talented , continue to bring nice songs to us we're like gospel music
Love the natural look🔥🔥
Ambuye alemekeze ndithu timely message in the song
Ya December nd yomwey🔥🔥🔥
Miracle chinga iweo ndi one..... keep the fire burning mamie 🔥
Powerful mimi ambuye akuze tsogolo ndi masomphenya ako love you mamie 🎉
Chimbinacho ukamafutuka umandinyamula nayo mtima... You are a gee
Mayi mumatha kuyimba❤
Keep the fire burning Mimi💝💝🎉🎉🎉
Great song... 🔥 🔥
❤❤❤ km iweyo ndi one
Well done miracle❤
Ya December ija ndi iyi🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳💃💃🕺🕺🕺
Chinyimbo iwe🥳❤️❤️
umakwanisa make🔥🔥🔥🔥
It's giving 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Powerful song,mwana uyuyu amantha🔥🔥🔥
This is fire 🔥🔥🔥🔥🔥
Glory to God pakuti sitikumusowa grace chinga mulungu anatidzitsila miracle 🎉🎉❤❤
Apa nde wabwela 🎉🎉🎉