Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Eeeeh ndadalitsika nayo nyimboyi..... Worship at it's best Mukule Baba
Amen... Proud of you my team.... I love your songs keep it up
I never knew Anglican can sing worship songs like these. Nyimbo zodalitsa. Am inspired. Pitirizani!!!!
Nyimbo zanu ,ndimadalitsika nazo guys,ndipo kavalidweso mmavala mozilemekeza ,keep it up ,
Amen mlungu apitilize kukudalitsa ndimphavu
Amen Amen God bless u all guys, mkule mbuye Ife tichepe
Amen choir yodzichepetsa koma yoimba bwino ,Anglican mpingo wapamalo ponse ,ambuye akuze malile anu
Amen
amen , mwatiphuzitsa kumuuza mulungu chomene alii,, zibwele zambiri nyimboo
Kulambira ndi moyo ose❤ mukure ife tidzichepa🙌👏
Powerful massage God bless you all today, tomorrow and forever
Amen lne yanditengera kutari nyimbo lyi ❤❤❤❤❤❤ mavalidwe wolemezeka Yawe u have nice vn
Mukutiimilira kwakauma kuno.keep it up
Maimbidwe abwino kwambiri ndipo mwatsitsimula moyo wanga, keep it up!🎉
Mumatilimbikitsa mulungu azikutsogolerani amen 🙏🙏
Amen you remind us of what is on Rev chapter 4 v11
Yehova mlipo nokha pachilichose pa moyo wanga
Ulemu wanu ambuye akhale nanu nthawi zonse
AMEN pitirizani kulalikila uthenga wabwino
Nyimbo zanu zimandisuntha daily Mulungu azikudalitsani
Kuyimba kwa pamwamba... Ambuye apitilize kukuvumbulutsilani ndikukuvumbulutsilani nyimbo zochuluka
Oh yes hallelujah amen 🙏
Zikomo nyimbo ndiyabwino iyi
Mwayimba nyimbo yabwino
Amen and Amen 🙏🙏🙏🙏
Powerful
Mumantha kuimba
nyimbo yabwino kwambili
Amen 🙏
To GOD be glory
Amen and amen
Zaphanvu ambuye apitilize kupatsani Zelu ndi kukuza malire amoyo wanu
Always God be exalted
Amen I love songs
Song inspirated on Sfiso
Amen and Amen
Eeeeh ndadalitsika nayo nyimboyi..... Worship at it's best
Mukule Baba