Koma eish mcp zoona osayamika ntchito zonse zimene Chirima anagwira. Kupha Great and Model leader skc . Mcp inaphanso Mr Aaron Sangala- Dick Matenje - Atate Mpakati- Kanyama Chume - Muwalo plus Henry Chipembere - Sidik Mia - Ralph Kasambara and many others. We hope kuti Mulungu ationetsa ukulu wake poononga ndi kulanga mcp ndi Chakwera..... Pa maso pathu ndipo maso athu akuonelera.. monga mmene anamuchitira faraoh ndi asilikali ake.
Tikimva kuwawa kutisiya kwanu a chilima yee!! Koma inuyo munatipitsa ku phatikana ndi chipani ca kuphachi cha mcp .pano mwatosiya pa mabvuto oopsya .kumeneko mzimu want utichotse mmanja mwa ng'onazi.zakuohazi zi manja a chakwera and mcp party .members
😭😭😭😭😭😭😭 don't Skype my tears crying for president wathu wachinyamata🎉
Munthu uyuyu anachita kukonzeredwa chipongwe chophedwa
Chakwera, unatilakwiraa
Koma eish mcp zoona osayamika ntchito zonse zimene Chirima anagwira. Kupha Great and Model leader skc . Mcp inaphanso Mr Aaron Sangala- Dick Matenje - Atate Mpakati- Kanyama Chume - Muwalo plus Henry Chipembere - Sidik Mia - Ralph Kasambara and many others. We hope kuti Mulungu ationetsa ukulu wake poononga ndi kulanga mcp ndi Chakwera..... Pa maso pathu ndipo maso athu akuonelera.. monga mmene anamuchitira faraoh ndi asilikali ake.
Wakuba mkulu uyu ndikusokoneza mulungu alemekeze
Chikhala plugs amadzuka,,tikanati adzuke Kwa chaka chimodzi chabe..Rest in peace SKC
Bola ndilomweli sitikusintha mulungu amachotsa dzosokoneza
Ngati ndikulota ineeee😢😢😢😭
SKC legacy may his soul rest in peace
Mmmmm akuluawawa amatha ndithu komanso sitizapeza munthu ngati amenei
Ngati ndilire aaaa Koma
Munthu uyu uyu mhuuu mcp zowona pakana kumupha nyamatayu mhuu
Masomphenya anapitaa
Abwino sakhalitsadi, zoona
Misozi yokha yokha mmaso mwathu 😭
Anali Ndi ziwindi ameneyu Anali bo kwambiri
May his Soul continue resting in peace . SKC legacy DK
Chilima Anali ngwazi
Only God knows
So sad tizakusowa heavy Mr man
Dziko lidataya munthu amene adali ndi masophenya otukula dziko lathu
Akanangotchoka mwendo koma kupitilatu 😢
Chakwera unatirakwira zedi
Sitizampedzanso ngat uyu😢😢😢😢
Mwatisiya osati mwatosiya
😭😭😭😭 mmmmhhh
We missed you sir😢😢
Vuto losewelesa nkango nchila ndilimenelo
Forever In Our Hearts SKC,,, Rest Well Comrade
Mmmmm,makwana
Naah anapha uyuyu Or kutengapo gawo mulungu achita naye
Ndipo sindinavomele mpaka lelo.... 2025. Ok
2025 mulungu ayankha
Tikimva kuwawa kutisiya kwanu a chilima yee!! Koma inuyo munatipitsa ku phatikana ndi chipani ca kuphachi cha mcp .pano mwatosiya pa mabvuto oopsya .kumeneko mzimu want utichotse mmanja mwa ng'onazi.zakuohazi zi manja a chakwera and mcp party .members
Dziko ili adzalana
Ngat boza skc mmmmm😢😢😢😢😢😢
May your soul RIP 😢😢
Mmmmm😢😢😢😢😢
May his soul rest in peace
Masomphenya aja anapita
😢😢😢
😭😭😭😭💔💔💔💔
Km ifa ifa ifa bwanj km
Tikumva not tikimva
We lost a patriotic citizen
Indeed
He was a different gem😢