History is a best teacher mzimu wa bingu uwuse mumtendere ndinadziwa ndale chifukwa cha iye, munthu amene anaphuzitsa a malawi kudzidyetsa okha osati manyaka a lerowa ❤❤❤❤u bingu, 💙💙💙💙💙caka cinonso boma!
He will forever be in our hearts not only as our president but as a father figure He was ..U touched many Souls until now we wished if U were still with us...Rest well Bingu
May his soul continue to R I P, the first investigation about this death was supposed to start with his doctor ,because its shows the president was poisoned, why his doctor left all the tools he use to help the president was inside the amburance while it was not inside the amburance but at his home,showing that he new something thats why he put everything away. Very bad ,sorry to our country. The time they where going to hospital they didn't even call the doctors to be ready everything was scuttled , That's why now we are getting punishment in our country .
Eti? Mmalo mongothamanga naye kuchipatala ndi galimoto yomwe idalipo. He was mismanaged. Kukhala ngati zokonza ngati zaku chikangawa. Doctor wa president osadziwa first aid, opanda zipangizo, osadziwa kuti ambulance ya president iri kuti?
Ku state house nkoyenera kukhala special medical immergency aid, MONGANSO ku office yake ,Malawi is a joke always,but I blv he was killed mostly by the west ,Bingu had a pan Africanism mindset like Gadaffi Malema ,sankala
History is a best teacher mzimu wa bingu uwuse mumtendere ndinadziwa ndale chifukwa cha iye, munthu amene anaphuzitsa a malawi kudzidyetsa okha osati manyaka a lerowa ❤❤❤❤u bingu, 💙💙💙💙💙caka cinonso boma!
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤1
😂😂😂❤❤❤
Dzikomo gyz chifukwa cha makomenti anu dzkoli ndilathu osati la mcp.
Bingu was and is my inspire and hero of my Life appointed by Almighty God of Israel the Lion of judah I ❤ Bing and I'll ❤ Him forevermore ‼️‼️‼️
Abwino sakhalitsa history is the best teacher
Bakili Muluzi TV fan😂
Mzimu wanu Bingu upitilire kuusa mu mtendere
Anatiphera hero wathu because he wasn’t a puppet of western world wabwino sakhalitsa RIP mr Bingu wamuthalika
Muthuwakulu sitizakuyiwalani😢😢😢😢
History is the best teacher 🎉🎉
History is the best ause ndimtendere ngwazi Bingu
History is a best teacher ,rest in peace Bingu Muthalika 😭😭😭😭😭😭
He was great thinker❤❤❤😢
Continue resting well 🙏🙏Ngwaziiii.
History is the best kwathu thanks ❤❤❤❤ l love
Will not forget him for wat u did to my father pointing him as ur guard commander, we miss u our legend
Ai zikomo 😭😭
Keep resting well Your Excellency 😢
Rest in peace father, takusowani dada
May his soul rest in peace 😭😭😭
Za ziiii ma Prophet okubawa
😢ndiye mwati Zikhale Ng'oma nso?
Our dear Lord please hear our prayers on late Bingu's innocent soul,, Rest in peace
Mzimu wa Dr Bingu wamuthalika uwuse mumtendere
He will forever be in our hearts not only as our president but as a father figure He was ..U touched many Souls until now we wished if U were still with us...Rest well Bingu
Big man rest in peace
Mudzapitiliza liti😢😊
Dr.. Namalika
😭😭😭😭😭😭sitizakhalaso ndi president ngati bingu
Such a Great President we lost
I remember the song tiyende pamodzi ndi mutima omodzi
Akudziwapo kanthu maikaliyati ndi peter munthalika anamupha bingu akuziwapo kanthu
Abwino sakharisa rest in peace Machine Mutharikka❤❤❤❤
The great loss of Malawi, bwana continue resting in peace 😭😭
Peter ndi oyipa anamupha bingu kufuna uprisedant
big up
Imis U Mr President machine that can manufacture another machine wabwino sakhalitsa mzimu wanu ukapule kumpumulo wa bata🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Aja adali akatundu.... Aziusa mu mtendere bwanawa😢😢😢
Why today?
May the soul of Bingu continue to rest in peace 😭
Zowona (?
Bingu munachita Kuti wachita bwino kumwalira lero mukuti anali wabwino muzikhala ndimanyazi
May his soul continue to R I P, the first investigation about this death was supposed to start with his doctor ,because its shows the president was poisoned, why his doctor left all the tools he use to help the president was inside the amburance while it was not inside the amburance but at his home,showing that he new something thats why he put everything away.
Very bad ,sorry to our country.
The time they where going to hospital they didn't even call the doctors to be ready everything was scuttled ,
That's why now we are getting punishment in our country .
Ntchito za kaliati izi zopha ma president
😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭 abwino sakhalisadi ndipo Tikanakhara tili ndi president uyu mbwezi Malawi sitiri apa lero 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭 a mbuye tikhulumireni
I miss our hero
Rest in peace bungu
Mbiri ndi mphunzitsi wabwino, koma sitiphunzirapo kanthu. Phunziro labwino la momwe Amalawi akuyenera kuika patsogolo zinthu zotiteteza.
We don't have emergency policies in place kuboma for these type of situations. Mpaka the doctor had to leave just to get items for treatment.
Koma agaluwa since anaba utsogoleri kumangobulema zambirimbiri?
Big up brother mumatiyimilila. Please patapezeka ya Samola manchero Please tiponyereninso
Pa nthawi imeneyo panalibe ma galimoto ina imene akada user pamene ambulance panalibe???
Eti? Mmalo mongothamanga naye kuchipatala ndi galimoto yomwe idalipo.
He was mismanaged. Kukhala ngati zokonza ngati zaku chikangawa. Doctor wa president osadziwa first aid, opanda zipangizo, osadziwa kuti ambulance ya president iri kuti?
Apa palidi nkhani ndithu
Every process was happening slow, due to lack of resources
Mzimu wa Bingu uwuse
😢😢
Bwanji Peter sizimukhudza Zaida ya bungu koma lero
Background sound mmh
Recklessness of state house stuff,,munthu sungatenge ambulance ya president mkumakasewelesa komaso sungatenge first aid kukasiya kunyumba..
Banja lodala la amutharika rest in peace bingu chisulo cha njanji
Poor communication...Bingu anali machine, rest well
Kod sizingatheke kungoyila popanda background sound
Uyu akuona kuti mafuta avuta agone pasewu. Awa adali akatundu amademo amaombera amakana chibwana pano bwezi zachibeana kulibe r.i.p.
Apa ifa inatidula nthenje ndipo inatilakwira but anyway MHSRIP gone but not forgotten
Zina kumatsutsako bingu tinayambaso kumamudaso kwambili ndie poti adamwalila aoneke wabwino pano???
Kutengera ndi nyengo zomwe Malawi wadusamo kuchula dzina la Bingu zikugoyenela kutelo 🎉
Timakunyadirani mukamatikumbutsa nkhani zimenezi
Aaaaaa 😢😢😢
Anali osayamika uyu anamuchita chipongwe bakili muluzi
Nzeru zako naweso zili ngati Bakili Muluziyo 😢 ukudziwa zomwe Bakili ankafuna ,, ankafuna aziyendera nzeru zake ndizomwe Bingu ankakana
Mbiri yomvetsa chisoni, dokotala wake anali osadziwa emergency management. Sadathandizidwe moyenerera.
Adali osadziwa kuthokoza kwa omwe adampsngira zabwino uyu
Zimu wamalemu bingu ikause mutendele
zitathauza,chiyani,zimenezo,kd,masautso,ambuye,yesuyu,,mumamutengela,kuntoso,bwanji,bingu,mungamuyelakeze,ambuye,yesu,chibwanaichi,
Ku state house nkoyenera kukhala special medical immergency aid, MONGANSO ku office yake ,Malawi is a joke always,but I blv he was killed mostly by the west ,Bingu had a pan Africanism mindset like Gadaffi Malema ,sankala
Anachepesa njala pamalawi pophuzitsa ulimi wothirira pano ku malawi kuli ngati Egypt awuse ndi mtendere
Continue R I P
uyu anali president okonda ziko lake
Inu background sound muzichosa
Sindikudziw kt nchifukw chiyan Anthu timamuchemerer munthu akaf kod maesa malir A bing ndiaj anthj adachezer kusangalal kt wachit bwino kuf
Lelo tikut adal wabwino
Chilim ndiujanso amangidya nao misonkh osadzudzul kt sizikuend lelo waf tikunso taluzmtsogoler wabwino
Zona
Anamumpha apm naye amayenela kut afufuze, chinampha bingu, ndichani
The sound is so boring
He's was great leader in Malawi
bingu,anali,osadziwa,kuthokoza,pazomwe,wapadzibwa,,,,,anapatsidwa,udindo,waukulu,wautsogoleli,wadziki,km,akadadziwa,bakili,sakadamupatsa,adayaba,kumutola,zifukwa,,npaka,bingu,kum,mangita,,,,,bakili,muluzi,zaka,,17,osakumbukila,zaudindo,omwe,anapatsidwa,,moti,atupele,asapuse,ndi,dpp,idzanpanga,ziwawaso
Olo kulembaso kukuvutani
Imfa sithawika nthawi ikakwana imankhara yakwana chilichonse simakhara chochedwachedwa munthakuona kt mafoni akuchipatala osagwira doctor mkono siunali bwino zinthu zake zimankhara zoti bc nthawi yafka
Koma pena zinthuzi Amalawi timazilekelela. Maphone kusagwila kuchipatala😢, no emergency protocols. Tizingoti ndi ntawiyake zoona.
Utter nonsense, all this to divert attention from the fuel crisis
Eish Bingu was the best president 😊
May his soul rest in peace😭😭😭
😢😢😢