Amene muli ndikuthheketa chonde perekani chitetezo kwa Mr Namiwa chifukwa galu chakwera sakupuma naye bwino afuna amuphe chifukwa kupha to Mr chakwera it has become his habit,Yehova mtetezeni mkuluyu
Koma namiwa si munthu wamasewela ayi ndipo amaziwa milandu ......munthuyi ndi mwana wa amfumu a namiwa .......munthu ameneyi zina ili la namiwa kwawo ku thyolo ndi amfumu .....ineyo ndiye namiwa amandisangalasa kwambili chifukwa Ali ndi mfundo zogwilika ......chakwara akuyenela kuchoka ....mbuzi ya munthu iyi
Tell us what really happened during the plane crash at chikangawa forest. You are the voice of the voiceless in Malawi.on top of that you are not afraid to climb on top of the mountain fighting for our freedom.
Namiwa brilliant, u took time to read this report and replied this nosense old people call themselves advocates and lawyers. Ndege yogwa 4.5m singaoneke chonchija. The wreakage was worse
Namiwa must protect this is light person who help Malawian to now the truth about the plane crushes which take place on 10June 2024 who killed our Late Vice president Dr Souls Chilima ♥️♥️♥️
kumbali yandale Malawi ndiziko limene Lilibe Luntha pandale Anthu ake Ndi Amzeru Za sukulu koma Alibe kulimba mtima Mbuli ngakhale itakhala yosaphumzira koma ili yolimba mtima imaposa Gulu Lama Degree omwe angozimva sukulu ndi ndalama koma ali ogonaa😢
Ife tikuti Namiwa akunena zoona pakuyenera ena amangidwe monga Collin Mzamba,Valitino Phiri,Chimwendo,Londa wa pa Tawa kuti akanene bwino,amene adayimisa kafukufuku ku Chikangawa,ogwira ntchito ku Mzuzu airport ndi a Kunkuyu kuti chilungamo chiziwike osati kuti basi tikhare chete zatha ayi.
Akuluwa ali ndinzeru koma nzeru zawo akuzigwiritsa ntchito pachabe why, coz if anthu adakana the investigation not to be public akadadekha kukhala momo bwezi atadziwa zambiri kuposa pano and mwinanso ngodya zofunikirazi bwezi mafunso ambiri ataysnkhidwa .koma apapa aaaaaaaa ndikuona ngati mission yachilungamoyi ivuta plus kumathawa anthu azikwanje atatu okha basi aaaaaaa mbola iyi.
Amene muli ndikuthheketa chonde perekani chitetezo kwa Mr Namiwa chifukwa galu chakwera sakupuma naye bwino afuna amuphe chifukwa kupha to Mr chakwera it has become his habit,Yehova mtetezeni mkuluyu
Anali ku state house Namiwa. Chitetezo si vuto ayiii ndiodzidalira
Mulungu pasogolo
Anamiwa anthu awa osawasiya tiye nawo always ndimakupanga support course mumatiyakhulira
May the almighty God protect u Mr Namiwa
Amen
Namiwa couldn't fight from within coz he is intelligent. He knew that the report was already drafted
You are giving out the real facts, your explanation tells the right evidence
iweyo namiwa number one ❤❤❤❤
I didn't know kuti ku 🇲🇼 we have people like you more fire brother man
Keep it up mr Namiwa..
Tili pambuyo pano..tikufuna chilungamo basi😭😭
Yabaya .....Viva Namiwa ......Anthu oipa ompha Azawo......Azionatu. Ine ndimava kuwawa .....frola......selemani...chemwali wanga kufa....nkhondo ya Abare....😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢zimatiwawa munatenga mzati....Angalu A mcp inu munya 2025
We need.pple like u
Inu a opposition,you need to support Namiwa and his team .This is a team with 100% integrity. Thandizo lathu lili m'manja mwa anthu amenewa
More fire comrade osaopa osatopa osafooka Mr namiwa
inu ndi mkango wa a Malawi ambuye apitilize kukutetezerani Mr Namiwa
Ndipo imfa iyiyi mmmh Ambuye onetselani ukulu wanu onse atidye nawo azachite manyazi
God pls protect Mr Namiwa
Katundu Mr Namiwa osati mbuzi zonama zoyikidwa ma banzi pakamwa misalole mpaka the truth being reviewed iam following you my dear Brother
Basi skc wangolowa mitima yanthu ochuluka 😂😂😂asowa omuphatu sinanga anthu akuchuluka owapweteketsa mitu
😂😂😂😂😂
Namiwa needs support
Komatu wamisala anaonadi nkhondo.This is real facts
Anva kuwawa agalu amene anatengapo gawo lokupha anthu omwe anakwera ndege😅😅😅
Kma Namiwa ndi zii. I loved chilima , chilungamo chioneke ndithu.
Go ahead namiwa.... i love it
More 🔥 🔥 🔥🔥 🔥 🔥 🔥 🔥 Zikomo Mr Namiwa.
sure Namiwa ❤❤❤❤❤
A Namiwa ❤❤❤❤❤
Koma namiwa si munthu wamasewela ayi ndipo amaziwa milandu ......munthuyi ndi mwana wa amfumu a namiwa .......munthu ameneyi zina ili la namiwa kwawo ku thyolo ndi amfumu .....ineyo ndiye namiwa amandisangalasa kwambili chifukwa Ali ndi mfundo zogwilika ......chakwara akuyenela kuchoka ....mbuzi ya munthu iyi
Oo yes❤ Namimwa yemweyi
long live Mr Namiwa
Namiwa needs people to support and stand with him in public,osati support yobisalira yosabwera ku gulu
Koma namiwa 😂😂😂🎉🎉🎉respect
Kuli moto kuti buuuuu❤❤❤❤.
Good my brother ❤
Namiwa anakupanga ayise supanga ma ziyen kuchipinda 😂😂😂😂
Salute and Stay Safe Namiwa❤
Mr namiwa mulungu akudaliseni,,,ifa ya chilima imandiwawa paka pano
We need people like you namiwa in malawi
Big up namiwa💪💪💪
Eeeeee namiwa anapasa pakamwa😅 umakwana iweyo
We are behind you Mr namiwa osawasiya achikangawa awa
Hero!!!
Koma funso la Winston kalimira ndy ndilopeperatu😂😂😂
Eti eti 😂😂😂 ndimaona ngati ineyo ndamene ndikupepera koma atolankhani ena😂😂
Atola nkhani akuchikangawa awa
I salute you Namiwa, i loved chilima more
Good of you namiwa tifuna anthu ngati inuyo
Tell us what really happened during the plane crash at chikangawa forest. You are the voice of the voiceless in Malawi.on top of that you are not afraid to climb on top of the mountain fighting for our freedom.
Pafera mwazi ana Mulungu mosamvetsetseka mizimuyi imavuta kwambiri, 😮
🎉🎉🎉
The truth will prevail no matter how long
maulemu anu anamiwa ALLH azikudalisani
Inu atolankhani mmene akuyankhila namiwayo mukadali nchibaba chomafunsabe mafunso
We are listening and regurgitating
General Namiwa kkkkkk
Woooooo Mai Malawi wanga
Bravo namiwa❤❤❤
Good 👍
Koma Namiwa, ayayaya, ulemu wako aise
Atolankhani mpaka kugoja kufunsa mafunso?😂😂😂
U president uja ukufunika munthu wake ameneyu Mr Namiwa osati zinazi kungoziwa kupha anzawo basi mxieww!!!
ALLAH is your side Mr Namiwa
Chilichonse Mulungu amapanga ndi cholinga.
Ntambo uja anamusiira mpando munthu oyenera, wanzeru ndi othandiza kuposa m'mene akanayendetsera zinthu Ntambo.
Namiwa uja ndi boma payekha😂
Mtolankhani mene akufunsa kuti bwanji a cidec akugwiritsa report loti apanga condemn akuoneka kuti nzeru zake zili ndi malire
Fireeeeeee❤❤❤❤❤❤
No fear namiwa continue to equerry is guys
Namiwa brilliant, u took time to read this report and replied this nosense old people call themselves advocates and lawyers. Ndege yogwa 4.5m singaoneke chonchija. The wreakage was worse
Indeed these two deaths have a lot of questions than answers
Chomene ineyo ndimadziwa ndichakuti pa nkhani iyiyi aliyense amene maganizo ndioti anachita kukonza ngozi yija sangakhulupirire ganizolililonse losagwirizana ndi maganizo ake
Kusowa zochita awaa😂😂😂😂
You are a big fool. Nonsense
Iwe ndi kape
Athu opanda uzimu inu, ambuye achite nanu
Moti zonse zayakhulidwa pamenepo mwasakha kulemba zimenezi?😢
Namiwa must protect this is light person who help Malawian to now the truth about the plane crushes which take place on 10June 2024 who killed our Late Vice president Dr Souls Chilima ♥️♥️♥️
Zimangovuta koma umayesesa Namix 😅
Osawanyengelera Afiti amenewa
kumbali yandale Malawi ndiziko limene Lilibe Luntha pandale Anthu ake Ndi Amzeru Za sukulu koma Alibe kulimba mtima Mbuli ngakhale itakhala yosaphumzira koma ili yolimba mtima imaposa Gulu Lama Degree omwe angozimva sukulu ndi ndalama koma ali ogonaa😢
Straight
❤❤❤❤ namiwa
Zoona chirungamochizaziwika bola kusintha.vote yanga sogoro langa
Ife tikuti Namiwa akunena zoona pakuyenera ena amangidwe monga Collin Mzamba,Valitino Phiri,Chimwendo,Londa wa pa Tawa kuti akanene bwino,amene adayimisa kafukufuku ku Chikangawa,ogwira ntchito ku Mzuzu airport ndi a Kunkuyu kuti chilungamo chiziwike osati kuti basi tikhare chete zatha ayi.
Ngati iwowo ali ndi umboni wogwirika osapita nawo ku bwalo la milandu bwanji
Mwano kkkkkkkkk usazafe ngt eliya
Kung'alura osaopa osayisiyadi chifukwa ikangotha mosavuta ndale zatsogolo muna anthu azizangophana
Namiwa ndiwe mwamuna phwa!
Ndiye pali sisilu zina zikuyankhila zsusilu apa ...akudana ndi namiwa popangisa press briefing .....mbuzi za anthu zomwe zimalandila ndalama zokuba kwa chakwera
Afiti okhaokha
Kd makanilanja km awa😂😂😂😂😂😂
Akupatseni ndalama inuyo mufufuze
Osusa awa
Koma a Namiwa muli ndizochita???? Nthawi ndiyolima iyi, dziko lingatukuke chonchi
km,,zoti,,mungawine,mukunama,mcp,ikupitiliza,
NAMIWA ,ulibooh
Atolankhani akumalawi mumakanikatu kufunsa mafunso ongwirikatu
Osaopa uchitsiru ukuchitikawu ndithu atinyasapo makape awawa.
Joseph mazizi iweyo ndi ndikatundu chifukwa takhala maulamuriro ose palibe amene anachotsa ntchito 😂😂😂😂
bwana namiwa musasiye kuyankhula mopanda mantha chilungamo chidziwike panopa dziko lanthu lanunkha kwambiri
Inuyo mukanakhalabe mu Commission of inquiry muzikafusa zimenezo kaya
Tiyeni nawo akuphawa adzayamba kunjaira ngati dziko analikenga ndi Iwo!
Zitsiru nthawi zon se siziganiza .Amene anytime lipotili Lili bwino ndiye chitsirucho.Apresident anytime lipotili liwafikire onse amabanja omwe able awo anamwalira PA ngoziyo kuti alone ndi kuliwelenga bwino.Funso mkumati owerengawo sanakhutile ndi lipotili apanganso komishoni of enquiry Ina?kapena ayenere Kopitar ku ma khoti?
💪💪💪
namiwa,ngakhaale,ataphedwa
Boma limeneli musalisiye siye ayi linene bwino asatizolowele ayi ife si ana anu
😂😂😂kumangoloza kuti iphani uyu uyo ndi uja ,constituinal right ya Chakwera imeneyo?😅
😂😂😂😂😂
Brave Namiwa
Tikufuna anthu ngati inu ifetimasowa poyambira koma nafe sitikukhutira naxo mulungu akusungeni
mulungu oweludza ndiulula dzinsinsi zobitsika patalike pafupike dzizaululika ndithu tikulila ife chilima mmmmmmmm anatilakwila beavy anapangayo mulungu amuke naye ndithu poti kuweleza nkwake yaweh
Akuluwa ali ndinzeru koma nzeru zawo akuzigwiritsa ntchito pachabe why, coz if anthu adakana the investigation not to be public akadadekha kukhala momo bwezi atadziwa zambiri kuposa pano and mwinanso ngodya zofunikirazi bwezi mafunso ambiri ataysnkhidwa .koma apapa aaaaaaaa ndikuona ngati mission yachilungamoyi ivuta plus kumathawa anthu azikwanje atatu okha basi aaaaaaa mbola iyi.
Fana uyu Namiwa ndi wamtima eeeeeeee