Comrade Ntanyiwa Pa Limpopo Fm "Ndalama Zabedwa Ku MDF Ndi Wankulu Wa Asilikali"

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 28 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 30

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 12 днів тому +2

    Powerful 💙 iwe mtanyiwa ndi dolo kwambili 🎉

  • @GutuJemus
    @GutuJemus 11 днів тому

    Dziko lapasi kulibe chisisi😂😂😂

  • @GetrudeBanda-sd1yf
    @GetrudeBanda-sd1yf 12 днів тому +2

    Sitiopa mfuti, Yehova ndie mfuti yathu

  • @HassanBabujr
    @HassanBabujr 12 днів тому +1

    President atakhala The Dc.... Vice president Ntanyiwa... Nduna ya dziko Bakili TV wallah malawa akadakoma cz ma guys awawa umunthu alinawo kwambiri, poti munthu umachita kusintha koma dziko lathu likadakhala lokoma... Babu Jr from polokwane Jon's 🇿🇦🇿🇦🇿🇦🇿🇦🇿🇦

  • @JerieWytonTengani-h9q
    @JerieWytonTengani-h9q 11 днів тому

    A Ntanyiwa izi sitheka ife takonzeka kuwachosa pa mpandopo ndi voting yathu.Achepa amenewa.

  • @EmilyKanyika
    @EmilyKanyika 10 днів тому

    🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @HabiboZimba
    @HabiboZimba 11 днів тому

    ❤❤❤❤ boom

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 12 днів тому

    100% agreed comrade smart matic isagwilisidwe tchito mademo acitike apo biiii mavoti alepheleke.Dzikuonetsa kuti ngakhale bambo ake a chikangawa analinso akuba ndichifukwa chikangawa ndi mwanayi akungoba bambo mbuu! Ana mbuu.

  • @AmisiDytoni
    @AmisiDytoni 11 днів тому

    Tikazangosintha president ntanyiwa bm tv DC unduna muzalowa zizayenda bwino

  • @GiftBello-v1i
    @GiftBello-v1i 11 днів тому

    Tikangovota sazafa ndalama imeneyo adyeletu ma bed awo Ali ready Ku mikuyu

  • @JohnOnious
    @JohnOnious 11 днів тому

    Mr mtanyiwa aululeni afitiwo ayaluke basi

  • @AlicePondani
    @AlicePondani 11 днів тому

    Nanga akubawa awachita bwanji

  • @AbdulJohn-t7l
    @AbdulJohn-t7l 12 днів тому +1

    A police ambili ndi amowa akazapanga zawozo tizikapondela ku mawa komwe kumukoka kukamutaya kunja zikatelo thatana naye asiyeni ambili asiya Ana ndi mabanja awo pa umasiye 2025

  • @JosephyHarry
    @JosephyHarry 12 днів тому

    Chilungamo chimamasula😢 zinthunzi zimatengedwa ngati zocheza koma apapa zafikapo 😠😠😠😠

  • @MartinNice-z9n
    @MartinNice-z9n 11 днів тому

    Akunama kwambiri amagwidabwe

  • @FreddieKanyerere-u2z
    @FreddieKanyerere-u2z 12 днів тому +1

    Salute comrade

  • @LouisChabwera-y2w
    @LouisChabwera-y2w 12 днів тому

    Koma ntanyiwaaaa aaaaa umazitengakuyi zinsisi zimenezi

  • @HassanBabujr
    @HassanBabujr 12 днів тому

    ❤❤❤❤❤

  • @SamuelMoyenda-p6k
    @SamuelMoyenda-p6k 12 днів тому

    Chakwela wationjeza kwambiliiiiiiiiiiiiiii km guys mmmmmm palibe njila yachidule kd guys taonan talima opanda feteleza mmmm

  • @HADIJAZAMBIA
    @HADIJAZAMBIA 12 днів тому

    Mumatha mr

  • @BlessingsGama-j3r
    @BlessingsGama-j3r 12 днів тому

    Mungoti pheee muoneeeeee 😫💔⚰️

  • @ulemunkhoma2867
    @ulemunkhoma2867 12 днів тому

    Kodi kasinja mutengo wake ulibwanji? Mr

  • @Malume2024
    @Malume2024 12 днів тому

    Ngwirizano wa zipani 9 unaphetsa anthu 9 mcp chipani choipa kwambiri mizimu wa chilima usawasiye amenewa

  • @LoynerGama
    @LoynerGama 12 днів тому

    Chakwela akanagotulapasi udindo kiri zikhale ndi ulem

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 12 днів тому

    South africa wa police aliyese ali ndi mfiti koma ife sitingaope mfiti ife kumata wa police so kumafa

    • @WisikiBlack-gj4gu
      @WisikiBlack-gj4gu 12 днів тому

      Mifuti imeneyo sigwila tchito tiwanda ndikuphela omwewo

  • @TinoChipangura
    @TinoChipangura 12 днів тому

    😢😢😢😢😢

  • @MphatsoChintengo-f5b
    @MphatsoChintengo-f5b 12 днів тому

    😂😂😂😂😂 komatu ntanyiwa