Let's bond together and develop this MALAWI . The time for planting a tree 🌴 was twenty years ago but still now we can plant it and it can grow 🪴. Let's build new Malawi 🇲🇼🇲🇼.
Hon.plz learn to tell the nation of Malawi 🇲🇼 the truth. Never joke on the nation of the Republic of Malawi 🇲🇼. But technically telling them the truth.
vuto ndi lakuti onsewo they are power hungries. Amtambo ndi oti Ali ndi mkwiyo owachosa unduna, Akaliyati ndiye tisanene a dpp ndiye kaya nkhani ndi jealous,munthu asagwile ntchito becouse bambo ake anali wandale, za mantha basi.
Atolankhani ndinu ana chonde mukamafunsa mafunso funsani Ngati mwapita Ku school chifukwa amene mukuwafunsawo Ali ndi nzeru Za chibadwidwe Za umunthu Ngati mumafunsa mafunso oimira chipani funani ntchito ina chifukwa inuyo a lasta zautolankhani pitaniso Ku school chomaliza ulemu wanu azipani zonse ife achinyamata tikutseguka nzeru mwayankha bwino kwambiri
Not usually, a company with integrity can build nsewu from Lilongwe to Mzuzu; good example. Since it's a construction company, then boom, the engineers will do the inspections. He was ridiculous, but though brutal honest soothes much better.
A Dipwipwi akuti akufuna MEC chair and officers who are neutral like the case of Jane Ansah and Jean Namathanga😂😂😂😂 Bwana Timothy Mambo what is your take?
Boma lathuli siliganiza bwino popanga zinthu zake, company yomwe atengayi ilibe mbiri yabwino pa kayendetsedwe ka zisango. Ndizomwenso zinachitika ndi nkhani ya fetlizer kukabetsa ndalama ku Butchary zija.
Iwe nde chisulu sungayakhe udindo umamyekeza ndi mmene ndi maphuzilo a munthu sunganene kuti poti ndi mubale msamupase udindo wawukulu nde mzapasa ndani mwina ukufuna kuti akupase iwe mokhito?
Good answer akwene
Well done ✅
G to h guy gyyuhuh u unuh it iiino😢🎉 be t to rt to hh to yhg uh hukuhu
Let's bond together and develop this MALAWI . The time for planting a tree 🌴 was twenty years ago but still now we can plant it and it can grow 🪴. Let's build new Malawi 🇲🇼🇲🇼.
Very wise question John Paul awawa ina ndi nsanje munthu asalephere kupeza ntchito chifukwa cha andale
Ndinu mbuli
Respect big up aganiza motchedwa chonsecho anthuwa amasakhidwa iwo akuona mantha basiii ndi chakwera sindikuziwa akuopa chani😂😂😂😂
Nkhan siimeneyo bwana... Nkhan ndimmene mkulu wa Mec amasankhidwira. Sipakhala transparent and accountability
Eti
Nzimayi wanzelù amaganiza fuso asanayakhe mayiwanga❤❤❤❤
Mama Patricia kalita.your the Best mama
Hon.plz learn to tell the nation of Malawi 🇲🇼 the truth.
Never joke on the nation of the Republic of Malawi 🇲🇼.
But technically telling them the truth.
We need more women like Kaliyati in politics❤ God bless
That's good comfence to show the reality of story👂👂👂🙏🙏🙏🙏
Kweni ndi one more 🔥🔥🔥🔥
Well done 👍 kaliyat kuyakha Kwa lero Ndi mmawa omwe😂😂
😂😂😂😂😂😂😂
A name
Well done our leaders , Malawi hope is in you please make citizens happy 🤝
Kholo kuyakha mwazeru plz plz mama kaliyat otsarora kuti mcp ikugureni ndindalama mukatero ndiye kuti tunduwamalawi ukha save
Yes yes awatu ndimakna amawa 🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏
She is very powerful woman
You are the best.good bless you and protect you
ZODIAK Jounerist 🔥🔥🔥
KWADHUMA tikuti KWADHUMA inu 😅😂😂😂😂kaliyat is very wise
We're most powerful , Iron lady
We lv you mama
Wel done madam Kaliati💪
vuto ndi lakuti onsewo they are power hungries.
Amtambo ndi oti Ali ndi mkwiyo owachosa unduna,
Akaliyati ndiye tisanene a dpp ndiye kaya nkhani ndi jealous,munthu asagwile ntchito becouse bambo ake anali wandale, za mantha basi.
Exactly ndipo simukunama
Koma akupanga bwino kumene sibwino ayi
Ngati mcp ilibe mantha osangowachotsa anthu akunenedwawo bwanji ??chikangawa party ikupakila
Nthawi yolira komaso nthawi yosangalala.where are we?
Atolankhani ndinu ana chonde mukamafunsa mafunso funsani Ngati mwapita Ku school chifukwa amene mukuwafunsawo Ali ndi nzeru Za chibadwidwe Za umunthu Ngati mumafunsa mafunso oimira chipani funani ntchito ina chifukwa inuyo a lasta zautolankhani pitaniso Ku school chomaliza ulemu wanu azipani zonse ife achinyamata tikutseguka nzeru mwayankha bwino kwambiri
Not usually, a company with integrity can build nsewu from Lilongwe to Mzuzu; good example. Since it's a construction company, then boom, the engineers will do the inspections.
He was ridiculous, but though brutal honest soothes much better.
She is very powerful mrs Kaliyati❤
A Dipwipwi akuti akufuna MEC chair and officers who are neutral like the case of Jane Ansah and Jean Namathanga😂😂😂😂 Bwana Timothy Mambo what is your take?
Akwenii nd akatundu 💪💪💪😂😂😂😂
Opposition ndio putsa kwambiri nanga kuli muntu amene sakhala ndi chipani kuputsa kumeneko
Where are the ID printed ? Is it Lilongwe or India ? Why printing the ID in India
Mumakwana mama❤
Good question akweni enawo ndi otumidwa
Akweni nthawi zose kuyankha mokhadzula 🤣🤣🤣 sangakhale president uyu
😂😂😂😂😂😂😂
kamtolankhani kayankhidwa nd akweniko kakundimvesa chisoni🙃
😂😂😂😂😂 bwanji
😂😂😂😂😂😂😂😂😂Kachepa nazo Kaliat ndimwana ovuta kulera Zedi 😂😂😂😂
@@MaryBanda-n3h mmene akuyang'anira mwamuona she recieved embarrassment of her life😄she was like ndinkafunsiranji ine
@@lovemorenaluso8965 kkkkkkkkkk koma
Kkkkk live
Amai anga 💪💪💪
Akweni my vote 🙏😅❤❤😂
Kuyakha mwa nzeru🔥🔥🔥
Mayi kaliyati ni one❤
😂😂😂😂😂kwatentha ku Malawi guys😂😂😂❤❤❤❤❤
Guyz we need to join dpp& utm Kt tichose bomali
Well done mabig nose for good
Again thank
Kaliyati ana anakodza
koma amayiwa mmmm ndimawagimera ine
😂😂😂😂😂Kweni ndimunthu owopsa zedi mwana wanzeru mmmmmmmmm😂😂
No sense palibe chikumveka apa kodi nthawi yomwe amalumbilitsidwa anthu amenewa iwowo anali kutiko mesa ivili olo paliament inachita kuvomeleza penanso andalewa mzeru alibe kuganiza mopepera bwanji sichinatu ayi ukakhala okuba nawenso umaopa kubeledwa palibe chamuyaya padziko lampasi🎉
Kutiwa wa wa!
Nyatwa akweni❤❤❤
Kkk😂😂😂 kma mayi awa
Kaliat motoo❤
Palije UDF mziti UTM afod ndi DPP
😂😂😂😂😂😂😂 madam kaliat more fire
Kweni🔥🔥
Akwene Ndikatundu💪
Mai P Kaliat ulemu wanu mmatiyimilira
Alomwe nzelu kkkk💪💪💪💪💪💪💪💪💪
Good guys ❤❤
😮😮god to zodiac
Zithu Ngati zimenezi amakhala Ngati sakuva Koma akava Kuti president. Kukhala Ngati akudwala amayakha nsanga
Kaliyati muli 1000GB osati masewela😅
Koma a Timothy mtambowo mesa ankapanga ma demo kut lituluke boma lomwel
Fuso lakolo lalowana ndi fuso la akwenilotu achemwa 😂😂😂😂
Boma lathuli siliganiza bwino popanga zinthu zake, company yomwe atengayi ilibe mbiri yabwino pa kayendetsedwe ka zisango. Ndizomwenso zinachitika ndi nkhani ya fetlizer kukabetsa ndalama ku Butchary zija.
Dolo 🔥🔥🔥🔥
Momie❤❤❤
Chonde a opposition mulowe parliament zisanayambe😊
Zikomo Hon.Kaliati, thank you aol participants,may God answer to have fair elections.
Kaliati 🔥😊
Mukamati akweni ndi machine zinawavuta bwanji ku conversation yawo pano awachotsa mphamvu at mulangizi kkkk pa timati zathapo
Ameneyo ndi kweni kkkkkkkk
Komat akwen😘
Osamayamikila anthu awa ndi anthu oyipa andale
Akweni anabwera eee😂😂
Mumakwana mama
Brian banda ameneyoo
Good job akulu akulu
Salute u mama
Akweni amayakha mothamangira tym tu 😂😂😂
mumakwana mayi kaliyati mwalakhulatu bwino
Kaliate hates the northern too much iheard. her speaking agaist them years ago
Poor alliance without knowledge
Think before you answer asa!!!!
Sanje bas!!
Kodi audio yako imamveka ngati wagwera mu cup bwanji?
Talongosokani man
Jane ansha anali neutral pakubera chisanko?
Kuyankha kwa Mtudzu. Kuyankha kopusa. Kuteroko kuti Kumkuyu ayankhe chonch uwona opposition inulankhula kuti ndiwamwano😂
Kodi nkunkuyunso ndindani
Amalawi tisamapuse ndi mawu okuti ntendere . Mawu amenewa ndemene akupangitsa kuti tizitoledwa. Tiyeni tilole kuti kwawo maliro kwathu maliro . Apa ndipo kutsintha mudziko mwathu Muno kuzaonekere poyela ndithu
sizitheka or pang'ono ndie chilima mwamuyendesa bwanji mukalankhula zoona.zokhuza chilima ndie kt patricia mumu imba mlandu
Awa ndiy madan aku utm
Kkkmkmmm you guys option tizaziwona tikamavota
Ntolankhani amalemba zomwe ofonsidwa wayankhula journalist sayankhula za maganizo ake,Smartmatic ichotsedwe kukomera a malawi monga ntundu
Chibaba cha utsogoleli chavuta chavuta apa dyera dyera dyera
😂😂😂😂 Akweni inu ndi one
Kachale abwerenso kapena anastasia nsosa abwere
Viva utm, viva dpp, viva aford
Kaliat ndidolo kkkk
azambili sidziwawa azikapanga kunyumba kwawo muthu mukuziwa kale kuti zambili sadziwa nde angaike odziwa zose zikuchitikaso mumbuli
Malawi walero yesu tamutaya tayanja zadziko tiyeni tisakhe yesu akhale msogoleli basi
Kodi Kayuniyu simumuyankha ?
Zayambikaso za alliance
Iwe nde chisulu sungayakhe udindo umamyekeza ndi mmene ndi maphuzilo a munthu sunganene kuti poti ndi mubale msamupase udindo wawukulu nde mzapasa ndani mwina ukufuna kuti akupase iwe mokhito?
What about an utmatum
Wafusa mafuso atatuwe ndi was mcp koma chomwe ukuchita sukuchiziwa
Nonse ndi azodiack?
Jane answer anali wa dpp ndipo ndiwa dpp pano zakuwawani
I like Akweni cz she z very strong in Mind komaso ndiopanda Mantha
😂😂😂😂 koma kaliat amwene