Aise, wayamba bwino… you have my support brother. I hate politicians cause they practice politics just to enrich themselves. But since governance can not stay away from politics, the only way is to change the face of politics in order to change the government systems that keep making citizens more poorer yet leaders become rich overnight after winning elections.
Asogo mulitu ndi nzeru koopsa and I Really appreciate you are such an interigent guy🙏 langizo langà don't change broh aliponso ena ofuna kukonza zinthu koma mwuna ali ndi mantha so keep going anthu akusatani broh ❤
ehhhhh ngamo in malawi we have brains koma mbuli zimakhala busy saying these are crazy people. anthu ngati alex kamangira, adha awawa and achina winiko these people have brains
Ine uzandisasakhe nduna ya za Ulimi ndizathesa njala Chaka choyamba chomwecho sitingama hokombirana za nsima every year chosecho tili ndi madzi nthaka Anthu ambiri amphavu opanda chomwe amachita kumangosewera Bawo and kuchulika kwa Anthu ongokhala ndi njira yoonekelatu kuti titha kuthana ndi mavuto pogwolitsa ntchito kuchulika kwathuko each and every Village komaso each and every region or district idzakhala ndi Munda wakewake omwe aliyese azizakakamizidwa kutenga nawo mbali andpaxakhala mpikisano wa midzi district region , Madzi tizizakumba zitsime komaso kukatunga madzi mmitsine Nyanja osadikilira mvula ai
azungu paja amadana ndi munthu ozindikila,
May God protect you.
😂😂😂😂😂 akunena zoonadi Munthu uyu ndipo ndizoonadi izi yehova wamoyo akhale Nanu brother 🙏🙏🙏🙏🙏🙏💯✔️
Congratulations brother mahata you have open us in so many categories and I hope as Malawians we can now look for change May God bless you
We need a leader like this person.....this guy is 100 times more than S K C
SKC was just another overrated elite
truly speaking
I see John Chilembwe in you my brother.God bless you
Am in love with this Guy Ali ndi mfundo zotukula dziko la Malawi
Aise, wayamba bwino… you have my support brother. I hate politicians cause they practice politics just to enrich themselves. But since governance can not stay away from politics, the only way is to change the face of politics in order to change the government systems that keep making citizens more poorer yet leaders become rich overnight after winning elections.
Uremu wanu ndipo mukulakhula moveka bwino....boss Ambuye akutetezeni paja timadana ndi anthu Achilugamo....oyakhula👏🙏
Indeed You're John chilembwe I'm with you
As a country we need this kind of sensitisation to the public.
Brave young boy.
Keep it up.
Mwina zinthu nkusitha
Our own Ibrahim traore 🔥🔥🔥🔥🔥
this guy ❤❤❤ is amazingly boy eeee akundidabwisa kwambili alindilutha
He is from the planet mars
God bless you comrade 💯 watching from Cape town.
GOD BLESS YOU DENIS MAHATA FOR OPENONG OUR EYES AND MINDS TO THE LIGHT.OF GOD.
This guy is very wise during kamuzu he couldn't survive and even now he must watch because his brother is present
Guys this man can make our children not to suffer anymore 🎉
Soon or later you will be our president. Its my prayer
Our own traore proud of you
Ukutisegula m'mutu athu akumuzi ife thanks brother
Aaaaaaa uyu mkatundu omanga ndi mawaya guys ❤❤❤
True definition of the leader..u have my vote son
John Chilembwe has risen, Mr Mahata lets go to Exparanza estate to give us John chilembwe Documents and the place that they buried John chilembwe.
Asogo mulitu ndi nzeru koopsa and I Really appreciate you are such an interigent guy🙏 langizo langà don't change broh aliponso ena ofuna kukonza zinthu koma mwuna ali ndi mantha so keep going anthu akusatani broh ❤
Komaditu zoona nkhani yachuma aliyese amaona ngati ndi vuto lake😂
Let joint together this country needs social power not political power coz political power has failed
You are so brave , will vote for you
As if you should be leading already....You are powerful,,,,I pray that The Lord God almighty should protect you. Psalms 125:2..
My vote tayimila pa u president tikuvoteta GOD BLESS YOU
Ali ndi zaka 29 sangamulole kuimila koma ndi pangolin mfanayu
I do love what this man said
Thanks potisegula ubongo 2030 vote yanga ndiyako
Vote for Mahata❤
You born to be a leader, Big up
Our own Ibrahim traore 💪💪
My brother muli ndizelu zodabwisa eeee ❤❤❤
Lord protect this young leader for us
Africa we need Anthu ngati Denesi we will pray you my brother this ideas is great future President of Malawi ❤
Following with great interest. Economic revolution is an emergency demand for Malawi ❤
Chikangawa uyerekeze.! Tikukuwona.!
May the almighty God keep you safe wherever you shall go our hope
Shaaaa! This guy reveals the secrets. We Malawian should organize the security to protect him otherwise he is in danger
Malawi is having educated people but I don't know how this country is poor that's a shameful
Best ever president Mahata
Genius very talented to be honest brother
💪💪💪Ine ndapezeka watchito wako,,,
Osati kungokuyamikila
Muli mzeru. Keep it up bro.. tidzagwira ntchito ku office kwanuko basi
May God protect you bro keep it up❤❤
You have hit the nail Comrade.
Much respect ❤❤❤❤❤
I salute you. Pitiliza Malawi azakhala pabwino.❤❤❤
❤from Cape Town mitchells plain town centre
Courageous Man Mr Denis Thanthwe Mahata
National anthem yovuka mwa njala i understand
We are not safe here
Get up guys
Uyu ndi munthu wanzelu kwambili akuyenera upresident
Mmmm iweo utha kuthandiza ziko lino kwambiri ndiwe dolo
Big kasongo there is wonderful mind ❤❤
We have more chilima here in Malawi, one of them Daniel Mahata my Good God bless you
Watching from Capetown DELFT
Ndimulungu yekhayo angakutetezere pakuti ukusewerensa mchira wang'onayo. Mulungu akhale nanu brother mwanthawi zonse
I agree with you. Brother
Mr Bon kalindo,ulemu wanu paja munanena kaletu kuti kudzuka zipani nde zina ndizimenezi😂😂😂😂😂
The best ❤
We Malawian we dont know what we want, 2020 we said Chakwela is good Peter Mtharika is bad.
For sure kkk
Come on buddy apule analowadi mu system yolakwika 😂😂😂
Munthu ngati uyu ndiye amene akufunika ndimunthu Amene atha kukonza dziko.
Munthu ameneyu apange ubale ndi President wa UTM Kabambe then dziko la Malawi litha kutukuka
Anthu azelu ndi abwino alipo ndinthu mdziko muno, ambue akuonjezelenii nzuluu!!
Uyu ndiye n kasongo weniweni pangolin wamalwi
You're so wonderful and am happy for you
You are a true leader
The DC bon kalindo, Anati A malawi siowafela timangoziwa kuyamikila bas Kom sitimatenga Gawo, mulungu adalise nd kumuteteza munthu uyu zikomo
😂😂😂
Eeeee wandimwaza broo...😮
Trauole wathu ameneyo tili pambuyo very proud you as amalawian
🎉All the best
Well explained
Bright future big up guys
Much respect 🙏 👏
The guy ndizoonatu zimene mukunenazi achoke ndithu chitani achoke mukatelo muthandiza amalawi mulungu akuonetselani ndiyemuyenela kuchita zimenezo
Uphawi wa ife wunachokera pa division ya midzi by politicians
I think you have my vote
ehhhhh ngamo
in malawi we have brains koma mbuli zimakhala busy saying these are crazy people. anthu ngati alex kamangira, adha awawa and achina winiko these people have brains
This mindset is useful
That's very good example pictures
My favorite 🎉
Politicians hate people like this one for obvious reasons.
Uthengawu upite kutali makamaka kwa anthu a m’midzi yathu. Zabwino kwambiri kwa Mr Mahata. Zipani za ndale zimenezi zikugwirizana ndi mavuto athu. Tiyenera kukumana pamodzi ndikusankha anthu omwe ali ndi ndondomeko zabwino kuti akonze dziko lathu.
Long live ase iwe ndi katundu muzinthu
You deserve to be president but malawi mmm
You are the best bwana
Chilungamo chiyende ngat mazi osafooka brother
mfana atha. kukhala. good leader
Machine 🎉❤
Following Mr Mahata
I stand together with Denis mahata..
Uyu akufunika chitetezo.
Ayi zkm tiona zithu 2025 bola moyo😊❤
Ineyo ndiimila u MP kuli nzelu uku
Denis ngati zitheka kuzaimila ifeyo tizamuvotera
Iweyo ase number 1
Ine uzandisasakhe nduna ya za Ulimi ndizathesa njala Chaka choyamba chomwecho sitingama hokombirana za nsima every year chosecho tili ndi madzi nthaka Anthu ambiri amphavu opanda chomwe amachita kumangosewera Bawo and kuchulika kwa Anthu ongokhala ndi njira yoonekelatu kuti titha kuthana ndi mavuto pogwolitsa ntchito kuchulika kwathuko each and every Village komaso each and every region or district idzakhala ndi Munda wakewake omwe aliyese azizakakamizidwa kutenga nawo mbali andpaxakhala mpikisano wa midzi district region ,
Madzi tizizakumba zitsime komaso kukatunga madzi mmitsine Nyanja osadikilira mvula ai
All the best my brother