If you see people stoning the tree, it means there are fruits in that tree.Miracle is supposed to be happy because of those persecutions. Her gift attract the enemies heavy. They are stoning her to bring her down. What God blesses no man can put it down. I love you miracle.
Miracle sakondedwa sadekha ndi wopupuluma ,ndi mwana wolimba mtima ,ineyo sindimukondanso ndi zochitika zake ,pa maliro amai ake anayimba nawo group ya anthu woyimba nyimbo mkukhalanso yoyambitsa nyimbo, ndinamuona kuti alibe umuthu sanawonetse kumva kuwawa ndi imfa ya mai ake ,palibeponso za umzimu ngakhale amayimba nyimbo za umzimu
Miracle amaimba bwino ndlipo nyimbo zake ndimazikonda, koma vuto amavala mabuluku zimene ndinyimbo zake sizigwilizana Komano Mai ake sitinawaonepo atavala choncho
Ameneyudi ndi zoba moti video inatchuka ija yowonetsa Miracle akuba juice nkumaika mchikwama cha nzake mu shop ija sanaiwone, she was in school uniform around 2016/17
Nice narration koma use or show more pictures or references when narrating. For example, when u say page ya Mikozi inalemba so, so... put that post in your video so that people know how credible u are
Continue mimi God is with you😍😍😍😍
Ntengo umene ulindizipatso zabwino umakumana ndi miyala yochuluka kwabas more love miracle ♥️
I second it
You are blessed Miracle that's why people are fighting you, continue doing the work of God, i love you
❤❤ I love ur song. Miracle
The more you fight with her the more God will fight for her that's how God is GOD Bless YOU MIRACLE CHINGA FROM ZAMBIA
If you see people stoning the tree, it means there are fruits in that tree.Miracle is supposed to be happy because of those persecutions. Her gift attract the enemies heavy. They are stoning her to bring her down.
What God blesses no man can put it down.
I love you miracle.
I love this gurl 💗💖
Nkhani imeneyi ambiliwa ndi nsanje chabe , Miracle imabe njiiii! Ndipo Mulungu amene untumikila sadzakhala chete adzakumenyela nkhondo iwe uli chete.
Mulungu samamtumikila maliseche abale
Mayi wa mulungu don't move side or take another way coz u lost live but u may continue to preach the word of God and pray in the of jesus amen
What ever koma ndi role model waine foleva😘😘😘😘😘😘 I love you miracle
I love this gal alot💓💓
The more people hates miracle,the more God blesses her I love you mimi
Amen
Go ahead mom
God loves you more❤
Mimi ali cha moyooo mwanayuuy eeee more blessings mimi
❤❤❤❤❤❤ love miracle
When you are good you are good . continue with your good works forget about the failures who are rumour mongers. 🎉
The Top becomes the topic, bravo Miracle
I love u ndipo sindizasiya mama,takusowa kwa mbiza ku,muzabweretso
We really love her....kip it up miracle
I love her
When people talk much of you it means you are alive... Keep up dear don't turn back ❤❤ you
Endabe usatope munthu wamoyo ayenera kukumana ndimikwingwirima koma ukhurupirire murungu azakuteteza 🎉🎉❤❤🎉
mtengo omwe ulibe zipatso siugendedwa ayi,,,,,Miracle is a blessed woman
AFuna amugwetse mmene anagwetsela amai ake koma uyo Mulungu azamusunga azamusogolela Santana niwaboza love you change from ZAMBIA
Beautiful girl ❤❤❤❤
Anthu mli nd nsanje 🎉ife timakukondabe❤❤❤
Miracle My Fav😢❤
I really love her the way she is
mimi you will stay my role model
Watching from Mozambique
We love your music and your representation if few hate you don't mind them just go forward
Nice🎉
Miracle you are loved ❤❤❤❤
Power mimi
I love her
Akufuna kumulanda chili mwayiyeyu Koma ndolephera ndi jelous lawo Mwanayu amalimbikira uku akuti Ambuye mundithandize❤
❤ambuye adzakhara nawebe muthaw zonse
Miracle ❤
I love you Mimi 💕
Miracle ndiwanzeru, osamamunena.
Miracle Chinga God is with u no matter what,thamanga mwana wankazi thamanga
Nice
The more they hate the more God bless ❤
Lots of lv baby girl be strong this world is 2 wicked
Miracle sakondedwa sadekha ndi wopupuluma ,ndi mwana wolimba mtima ,ineyo sindimukondanso ndi zochitika zake ,pa maliro amai ake anayimba nawo group ya anthu woyimba nyimbo mkukhalanso yoyambitsa nyimbo, ndinamuona kuti alibe umuthu sanawonetse kumva kuwawa ndi imfa ya mai ake ,palibeponso za umzimu ngakhale amayimba nyimbo za umzimu
Hmmmmm mudzamvetsa nthawi inayake mayi, kulira maliro mogudubuka sikukhudzika. Nanga bwanji mumadya nyama osakhala week osadya? Muziganiza chili kwainu
God is with you sis
My favorite
Miracle, we need you here in Chiradzulu.. love you ❤ mamaa
Indeee, ku Chiradzulu kuno timamukonda, no matter what, adani osadziwa kuti Mulungu amakonda aliyense Komanso aliyense padziko pano ali ndi machimo ake zimangotengera kuti enawo timawadziwa tokha kumbali
No comment
Ilove you mama ❤
Ndipo miracle amazondedwa ngati ine iiii iwe miracle tiye tidzikhala Bola pakati pathu Pali ubale wathu ndi mulungu basi zinazo zitichedwetsa
Mtengo wopanda zipatso sugendedwa miracle dont give up
go ahead miracle to gospel
Pakurisa beans 😂😂😂 koma ndika huredi
Hmmmmm
Zabodza ibe miracle wakula ndikumuona nsanje ku Malawi 😂😂😂😂
Amalawi plz tisiyile mulungu akaweluze ekha
People are jealousy,,, Miracle is beautiful
Mwana opanda mantha God bless her
We still love her no matter what ❤❤❤ so much love miracle
Ulesa
Mfana uja ndi walutso Komas ndi chi vibe that's why athu amamuda (ukakhala pa top umakhala topic)
Sam mavita good explanation
May the Almighty God fight for you Miracle
Nice one
I love you miracle
Mtengo wazipatso ndio ugendedwa go.a.head mama timakukonda.ndipo umatiimira kwachinyamata
Olo anthu amunene koma ine nde sindingasiye kumukonda❤
Te amo
Yes Miracle she is beautiful 😍 🤩 girl 👧 she have powerful message to Malawi 🇲🇼 people's be strong 💪 girl 👧 we love you so much 💗 💖 💓
Munthu ukakhala pa top ambiri amakuda, koma ineyo ndikuona kuti zilibwino azimuda choncho chifukwa amuchulukisa matsiku amoyo wake pamene kuti aliyense aziyamikira sachedwa kumu thyola ndichoncho et more fire miracle Ife mwaiwe timapezamo mayankho asiyeni enayo ndimanong,onongo awowo akuchedwa
I love you miracle even if some people hate you
Pa zosez mboni wake ndi mlungu miracle maso patsongolo thamanga ccter
Nice🔥
Mtengo opanda zipatso palibe angagendemo😮
True fact
Subscribe
Khawa njeee miracle aliyese amapaga zake
Mtengo opanda zipatso sugendedwa❤
Kuno Kupanje,...Bola bundle ❤❤
❤❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Ilove u mama takusowan ife
Miracle amaimba bwino ndlipo nyimbo zake ndimazikonda, koma vuto amavala mabuluku zimene ndinyimbo zake sizigwilizana Komano Mai ake sitinawaonepo atavala choncho
Mtengo umene uli ndi zipatso ndi umene umagendedwa osadanda akakhala Amalawi anazolowera kukhala pampando. Oweluza basi😮
kwa ine ndiwa sekular uyu
Be strong dear
Amalawi ndi choncho njiru basi muphulika amalawi thats why zimakhala zotivuta
Brother chilungamo choti miracle ndioslakwa khan anthufe ndi sanje lomwelo omwe amakamba zmenezow azibwera nd umbon please coz sibwino kuipisilana mbili
Miracle chinga amadedwa chifukwa chazochita zake uyo mwana utsilu ulimo angamukonde ndizitsilu zinzake
So tonse tikonda nyimbo zake ndife zintsilu? From Zambia
akanatchiza chimoz amaphatikiza zovula ni gospel pamene sziyendela limoz chifukwa chake amandinyasa
I love you miracle umatha iweyo
I pray for God's protection and blessings on her, may she be covered under His wings and abide safely.
Yes zilibho km kuphoda too much
U still loved darling ❤
Miracle you are loved❤❤❤
Anthu nsiyeni mwana wanzanu a Malawi tiyeni tisiye mabodza kuyipitsa ana azanga Mulungu akunkhululukireni
More love Mimi❤️❤️😍
Adha awa saziwa kufufuza khani.
Ameneyudi ndi zoba moti video inatchuka ija yowonetsa Miracle akuba juice nkumaika mchikwama cha nzake mu shop ija sanaiwone, she was in school uniform around 2016/17
Keep the fire burning love
Kodi anthu mumasiya zanu zonyasa zija bwanji? Musiyeni mwanayu za yahwe izi ikani zanu mwabisa zija musiyeni miracle please 🙏🙏
Forward never backwards
Iwe time radio inakhalako ufulu fm??
Nice narration koma use or show more pictures or references when narrating. For example, when u say page ya Mikozi inalemba so, so... put that post in your video so that people know how credible u are
Thanks brother,
Mavalidwe ake sabwino pogwilizana ndi za Mulungu, kudzipenta siza Mulungu
Zaziiiiii kusowa zochita basi, Even amene wabweretsa nkhaniyi apa, peza zochita zina
Ndipo amawaposa n keep fire burning Miracle
Uyuyu ndi definition yoti mulungu amatiteteza ...