She is a threat to Michael Usi at the UTM convention and is the fierce critic of the current regime and this arrest is aimed at silencing her and preventing her from challenging Usi at the convention.
Muthalika ndi mfumu ya ufulu wa dimokalase kumalawi siku Lina ndinava mau akaliyati ochemelela chikangawa muchaka Cha 2020 lelo kuli chiphopho chovuta kudupha
Amkulu amkulu zomwe akungapanga aboma ndi a police sizabwino ku Mozambique azawo aboma zavuta a police akumawocheledwa nyumba akungona ndi wosusa chifukwa chakhazawo aboma ndi a police kunoso ku Malawi ziyambika anthu akakwiya muzapwetesa ma banja an wosalakwa amalawi anasukusula
Walakwa chianii? Inu A M C P, bvuto lanu ndi chini, maonjeza, ziwani kuti. Mwamagayo muziwe kuti ndi mai wa nkulu kuno ku Malawi so sinthani ganizani bwio anthuwa akutuluksni.
Ubwino wake mcp munayika nokha pa mpando, muzimangidwa ndi kuphedwa chomcho....muthalika is master of democracy.
Zoona kufuna kwanu inu sinanga ukata mau kwa adadi pamosi nditupere
That is a plan of Usi
You are right
Yes thats true
Usi ndi pusi
Nanga apa ndi MCp kapena UTM yokhayokha osati MCp km zilipo wina arira walila wapalamula wapalamula chiteze chizakuyabwa Mcp patari izakuyabwa aaaaahaaaa
She is a threat to Michael Usi at the UTM convention and is the fierce critic of the current regime and this arrest is aimed at silencing her and preventing her from challenging Usi at the convention.
Koma zoona izi?? She is a woman can't you just be proud of her 😊
Andale mkukhala kwawo Kamuzu anamangidwa, Bakili anamangidwa ndiye tidikira tiva
Police is there to deal with people violeting laws regardless of political pressure.
Exactly, Kaliati wapalamula chachikulu.
Ufulu uzikhala ndmalile kma osaphelaso ufulu ena uyu amaonjeza
Kulakwa ndi kulakwa kaya ndi wandale.. MCP musawope kusavoteredwa Olakwa ndi basi
Muthalika ndi mfumu ya ufulu wa dimokalase kumalawi siku Lina ndinava mau akaliyati ochemelela chikangawa muchaka Cha 2020 lelo kuli chiphopho chovuta kudupha
Kaliat ndi pangolin akumuopa
Mukuwaopa akwen...inuso a police mboro zamanu kwambri
Ndale..mukumuopatu kweni
Mcp urendo umenewu musayiwere n'gona ndi n'gona ,tidzaonana tsongolomo , eshee Malawi warero ,
Kodi ku Amerika akagwa khunyu chakwerako kaliati analiko?apolisi musamale tiyamba kukumashani.
Ife nda UTM ❤or mumumange kaliati sitisiya kusapota UTM
Enough is enough come clear osayankhula zizingu zanuzo
So sad
My vote utm
Kaliati woohyee
A m c p amadana ndimunthu ozindikira tilipambuyo pa akweni
The story is that the vp knows that the story is conventional but it is not a good life
Mcp muzaziona
Amkulu amkulu zomwe akungapanga aboma ndi a police sizabwino ku Mozambique azawo aboma zavuta a police akumawocheledwa nyumba akungona ndi wosusa chifukwa chakhazawo aboma ndi a police kunoso ku Malawi ziyambika anthu akakwiya muzapwetesa ma banja an wosalakwa amalawi anasukusula
This is politic dirty game akweni be strong
Amafuna kupanga koma wina anapha witika kumwamba kulemekezeke
Ndipo inu mmmm
Kod kupha ndkuganizilidwa choopsa ndichit? Iwo anapha koma palibe chikuchitika nde asatinyase bola lilipoli Malawi tikutani aaaaa😢😢😢
Manganya salibwino amanga angt sanakwane muja mwayambila mukufunaso ziti kwa kaliyati
Ndi mwanganya ameneyo
Mmmm koma ndale ndale si za bho
Koma MCP mwanyanya kumanga anthu ndi chani
Ngati walakwitsa akuyenera kumangidwa basi
Aboma akufuna kunsonkoneza nsonkhano wawukulu wa UTM
Get ready for demonstration viVa Malawi viVaaaa
Mvuto amkaidziwa mcp amatenjae aganama. Achiwamgah anapita ana ajoka ndi anah ajoka bas
Utm my sound
Ameneyi ndikape whats felon iyeyi wapha chilima tikuona wamumanga ndindani chot aziwe thawi atha alimmadzi
Manganya mmmm kulakwatu uku
Ndi manganya ameneyo
Koma mmakonda kuyankhula kwambiri kuposa vdio
Tizakutulukani 1 day
Koma chomangilaanthu mcp ikuganizabwanji mudzikomuno tizikhalabwanji njilayofunakuphelawanthu mudzikomuno tikhalamotani ambuye tiwoneni titani
Wakasuma ndani
Ati felony kusonyeza Kt a utm akulowetsa ziphuphu dziko muno? Kmt a MCP muzitenge bwino chifukwa magazi akudza Kwa inu masiku akubwerawo
Manganya akuopa akweni ku convetion
Akweniwo alakwira felone wachani za usiru basi ammasule iyaa
Koma chikangawa ayi zicomo 😢😢😢
Skc, now kaliati, manganya tred carefully
Stupid government including president chatsika
Munthu akalakwitsa pazifukwa zoveka azimangidwa ndi Thu koma zikakhala zandale izo sizabwino koma ngati anali pachiwembu sibwino kusekelera chili Gamo chizitsogola
We know who is behind all this, kama drama akunama
Komatu idzi mmmm mavuto ndi2 😢😢😢😢
Iyo ndi game ya Manganya pofuna kuphelatu UTM.
Koma A1
Maganya game over to jump
Musiye mayi k zimenezo ndi kuopa vote
Mmmmmmhhhhhh
Mwayambazi chibwana
Walakwa chianii? Inu A M C P, bvuto lanu ndi chini, maonjeza, ziwani kuti. Mwamagayo muziwe kuti ndi mai wa nkulu kuno ku Malawi so sinthani ganizani bwio anthuwa akutuluksni.
Laine ya manganya imeneyo ndipo nkhaniyo ndiyowona kwambiri
Amalawi mwayamba zopusa Ngati ndiwe manganya umuleke mzakoyo ,akupusitsa a mcp
Tiwuzen zoona
Kod iwowa a mcp amanga anthu angati koma aziziwa kuti mawa ndi iwowa apalamula mkwiyo wa Malawi ndi za ndenge osayiwala ku mcp kwanuko
Mayiwa ninjoka
Malamulo mumayika nonkha aliyese asanalakwe, ngat alakwa amangigwe
Manganya izi zikumukhuza Khan ya convention Moyo oipa umeneyo
But God is not human body ok
Mumudziwe YESU koma kuchabe
Manganya timchotsa ku mpingo wathu wa SDA
Malawi it's too much now
Zinangowona kuvuta ku Garden City kuja
Aboma asafetu Mai kaliatio
Shame manganya
Ineyo choyankhulapo chundisowa mmm
Nde kuishoshatu kumeneko
atuluke afufudze ky kt murandu umukwera ndan???
Manganya ameneyo
Koma iweyo manganya ine sindimakuwopa oro pang,ono ukusiye manganya
Km tisawasiye okha ndipo mcp yazolowela 30 timashebasi chakwela achoke
Alinaye zifukwa za ndale asakaime Ku convention mwina sngawine ambuye achitepo kanthu
Manganya ndiwachabe kwambiri ndipo amasewera basi manganya amachita zachiwembu ngati siyiyo koma Ali iyeyo
Manganya ndiwe munthu oipa 😢
Ndisatana mwanawa hule
Ndimilandu ya mtunduwanji yongomanga apposition okha,pamene anthu ena alindimilandu mboma sakumangidwa
Mafuta okamangira ena akupezeka? Chilungamo chili mmanja mwa mulungu
Police ya Malawi ndiyopoila imayendetsedwa ndi makape andale koma munya muona ife sitiopa sitifoka sititopa
Kaliat wooooyeeee asawawopseze auze amalawi chomwe alakwa
Lamulo ligwire ntchito basi
Bwanji osamumanga Chakwera ndi timu yake yomwe anapha chilima
Kodi a pulezident a UTM akuti chiyani za member wawo
akufuna kuti kuzokambilana za nec ya UTM asakakhaleko
Akurakwisa kwambili sakukhoza
Amanganya akumuopa kaliat ku comvetion
Mmmmmm kma chikangawa,,mukuwonjezer mkwiyo Kwa amalawi😢😢
Ndipo inu...manganya's plan iyi ndi chikangawa party
Sopano akathamangila kumanga anthu than kuzafufuza kupeza Kuti munthu ndi osalakwa amuthandiza bwanji
Kamangira nkhuniyo please
Aboma afotokoze bwinbwino za mlanduwu osati tidikile ku court muyaluka
Akangotuka kuvuta
Akufuna di kupha chipani ngati mene anaphela chilima
Tikupita ku lingadzi konko
Ndi manganya akuchititsa izi koma aphwa pompano kunali nankhumwa osati khandali
Uku ndiye kuwakanda amalawi uku😮
Ngati akumuganizira zimenezo nanga iye chakwera anapha chilima osamumanga bwanji