Kumangidwa Kwa Kaliati Kwachoka Kwa Anthu Amene Amadya Nawo Mbale Limodzi - Bon Kalindo

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 24 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 9

  • @BAULENIBAMUSI
    @BAULENIBAMUSI 2 години тому

    Shalom malawi

  • @YamzyNedson
    @YamzyNedson 3 години тому

    The DC🔥🔥🔥🔥💪💪💪

  • @BeatriceSaulosi
    @BeatriceSaulosi 3 години тому

    Malawi wanga😢😢

  • @JusticeMikondo-i9e
    @JusticeMikondo-i9e 52 хвилини тому

    Tiyeni tikumane this morning tiyeni tituluke mwa unjinji ndithu tithane nawo amenewa😢😮😮

  • @ChimwemweMathyola
    @ChimwemweMathyola Годину тому

    The DC Mwana opsa kwambiri

  • @BerthaMkwinika
    @BerthaMkwinika 31 хвилина тому

    Kumangidwa asamangomangidwa osauka okhaokha, myeyo ngati walakwila lamulo akuyenera amangidwe,kundendeko kuli azimayi ambiri, kodi iwowo ndiosafunika? aliyense azimanhidwa akalakwitsa
    Bon k muzinena zinthu moopa mulungutu

  • @JusticeMikondo-i9e
    @JusticeMikondo-i9e 53 хвилини тому

    Komatu ngakhale amumanga akunama amenewa akungofuna kutiwonjezela mikwiyo tikugonakale okufaifa ndiye asatimwaliritse mwachango

  • @InnocentKayaka
    @InnocentKayaka 2 години тому

    Koma malawi 🤭🤭🤭

  • @MatikiMatiki-r7c
    @MatikiMatiki-r7c 47 хвилин тому

    Munthu samathokoza