Awawa chonde makolo awo afufuzidwe ndipo should be accountable for this. Report them to social services awasake azayankhe izizi. This is child abuse! Why have children when they can't take care of them?
Thank God, they are looking very strong. May God locate their destiney. Thank you Mr Rodwell for sharing a heart breaking story for the little ones. I know our good Lord will do something for them to live a beter life.
This is sad eeeee gayezi ndalila nsambi kwa ana mwati amakhara kt kweni kweni pls nane ndine osowa kma l just want to help pls lf you see my comment ndyankheni pls
Vutotoso masiku ano azibambo ena opanga umunthu akumangoti banja likatha osamawathandiza ana komaso ma single mothers amzanga please osalola kuthawa ana chonchi olo nyengo zitathina bwanji tsiku Lina ana omwewa ndi amene adzatigwile pankono please ambuye awatsogolele anawa mpaka apeze thandizo mabwana amawa ndi omwewa ndithu
Comment reserved 😭😭God please remember your children mudziko lomwe ena akusangalala ena akuvutikitsitsa ,may you please touch their parents to come back please ,we all need parents and live happily life 😭😭
Terrible situation.... 😢 Where is government mukungodya ndalam MMA office without assisting pple... Ana simplexs chithyola mukungogula magalimoto for nonsense kukanika kuthandiza anthu... Look at this... Be shame guys please
I agree with you wamkulu ,koma kuona kwanga anthu amudzimo ngoputsa bwedzi akabwela mayi wawo anawa ,asanachoke atha kuwafutsa then ,let's her no going otherwise kuwauza apolice ,sad news, tiyeni tithandizepo apa
No doubt amayi atha kukhala kuti akupanga uhule kwinakwake koma sizikuyendako. Gwero lalikulu ndi abambo amene anathawa udindo wawo. Such men need to be arrested.
Owooo my goodness ndakhuzika ndinkhani imeneyi, ambuye akumbukireni ana awa
Tiyeni tithandizeni osati kumangoyakhula chifukwa mwa ife muli kuthekera
She's too smart,,, ambuye agwetse mvula ya madalitso pa ana inu,,, muzachita bwino khulupilirani there's God and his name is Adonai
Awawa chonde makolo awo afufuzidwe ndipo should be accountable for this. Report them to social services awasake azayankhe izizi. This is child abuse! Why have children when they can't take care of them?
Exactly this is very bad that's why dziko lathu mavuto Ali osayamba how can you leave them like this mmm ayi ndithu
😢😢😢😢😢😢😢😢😢@@victorkapesi1014
Ndipo inu 😢kaya aliko akumva bwanji kaya eish!
Why Government is not funding Lodwell?
Ku ngotenga ufa kwapasa anawo ayi koma mwagwirise ganyu koma anthu .ndioipa.
She has a heart of a mother❤
This is so touching
This is so crazy, How can the parents left the kids like that?
Zomvetsa chisoni kwambiri,makolo ena ndiwoganiza mophoyira kwambiri kuzunza ana osalakwa chonchi.
Anakakhala kut atsogoleri anthu akupanga ngat Rodwell bwenz dziko lath atasintha. Kungoyambira mafumu kumakwera kuntundaku
Thank God, they are looking very strong. May God locate their destiney. Thank you Mr Rodwell for sharing a heart breaking story for the little ones. I know our good Lord will do something for them to live a beter life.
Omwe mukubanu ndalama zamisonkho Allah akukantheni ndithu ana akuvutika awa
Live Live bro
This is heartbreaking 💔 God save their souls.my humble prayer
Do we even have those instructions here?
This is sad eeeee gayezi ndalila nsambi kwa ana mwati amakhara kt kweni kweni pls nane ndine osowa kma l just want to help pls lf you see my comment ndyankheni pls
Ndipo zokhudzatu, some parents are just impossible 😔😔😔
Inenso mmoyo mwanga ndazinvera chisoni kwambiri Eish moyowu Sarah😭😤
You are an angel Rudwell may God continue blessing you..makolo a anawa onsewa afufuzidwe ndipo amangidwe for good
Eeeeeeh koma dziko ili 😢😢 Ambuye forgive us for being selfish 😢😢 kuzikundikila zochuluka ndi ana athu koma ena akuvutika , ana akuvutika awa mayooo😭
Ndipo atikhululukildi
Kodi aziphunzitsi mma school umu, sawona ana ngati awa kut ali munyengo zowawa ofunika kupanga follow komwe amakhala ndi zomwe amadya kukhala kugona,, nanga 13 yrs kukhala pa udindo wolera anthu awiri plus iye mwini 3? Amfumu mmadera momwe mumachoka ana oterewa sawona izi?? Tikuziwa mafumu, andale, amipingo, aziphunzitsi sangakwanitse koma apapa its too much ntchito yanu ndimeneyo yopanga allocate anthu ngat awa, ndipo amipingo, andale ndi awa mafumu anthu ngati awa ndiomwe amafunikira thandizo mwachangu..koma izi sizona guys and all children are traumatized they are releasing tears..they are concerned.....lets halp guys than spending 60,000-10,000, 3,800 betting chonsecho kumangobetsa ndalama pomwe mwai ulipo oti utha kuthandiza
Ndipo or mafumu kodi ntchito yawo ndichani abale? Moti samaona kuti pali ana mmudzi mwanga muno omwe akuvutika? What's wrong with amaudindowa abale mmm
I support your decision my friend, let's help these young ones instead of having regrets on betting
Vuto ndikukondera basi #sakho
Amayi awawa Aaah a Woman suffers for her kids
Why am I shedding tears please ana Ali pamavuto awa
Yesu abwere mnsanga koma dziko latopesa 😭😢
Mukugawa ndalama kwazigawenga nkumazikhululukila mmalo mothandiza Ana osowa ngati awa yehova Ali nayo nthawi yake salakwitsa
Osalaza zaka anthu nanuso tenganipo gawo
Chison chandigwira kwambiri. Ambuye chitanipo kanthu pa Ana awa. Makolo awo komwe aliko chikumbumtimba chiwapeze.
Eeeh,,,ana amavutuka awa. I can't even begin to understand what their pain has been like🤦. We thank God for the intervention
President amaona Kom zimenezo 😢😢
President ndikutali amfumu alikuti?
Koma amayiwo mutu wawo umagwila koma ??Anthu ana nkumabelekeranji??
Ineso ndikulila moyowu koma mmmmm
😭These children are suffering for sure God have mercy on them
Vutotoso masiku ano azibambo ena opanga umunthu akumangoti banja likatha osamawathandiza ana komaso ma single mothers amzanga please osalola kuthawa ana chonchi olo nyengo zitathina bwanji tsiku Lina ana omwewa ndi amene adzatigwile pankono please ambuye awatsogolele anawa mpaka apeze thandizo mabwana amawa ndi omwewa ndithu
My Allah for give us boma mkumaba ma billion anganingani mundu modzi mumafa bwanji mutima moyowo ndi wakandawi kochepa
Zugwirizana pati president ndi amene anati makolowo asiye ana azivutika
Mayi wabwino bwino kusiya ana okhala ake wina akusowa ana koma dzikoli😢
Too bad may they see the good hands of God and reach their destiny,,,, let's hold hands for the sake of lives of these innocent young ones
Ambuye akundalitseni ana inu ngakhale mukundutsa mu nyengo zovuta
abale inu zinthu zinazi ukati umve ndimakutuwa ngati sukumva ndinthu tiana ngati timeneti ndikumadutsa munyengo yowawitsa ngati imeneyi💔 it really break's my haert
Kodi nkhani ya anawa ilipati chonde tandidziwitsani.ndimakhala kudwangwa khotakota.chonde tandiuzani
Ana awa anathandizika Kodi?
😭😭😭😭😭 eeish i cant understand ena alindi chuma koma chosafuna kuthandizira anzawo😭😭😭
God I am sorry ineyo sindikuvutika💔💔💔💔💔💔💔💔💔
Comment reserved 😭😭God please remember your children mudziko lomwe ena akusangalala ena akuvutikitsitsa ,may you please touch their parents to come back please ,we all need parents and live happily life 😭😭
Amayiwo ndimunthu opanda zelu enafeso takwanisa kulera ana opanda bambo awo osati mpaka kuwathawa ana chonchi
Jesus Christ! Mkanakhala Kut ndili Ku Malawi mkanawatenga ndinthu😢 Koma Mulungu awakumbukire ana awa
Mbuzi yabambo imeneyo mulungu amukathe komwe aliko akumbukile ana ake😢😢
Ndikumva kuwawa mmoyo mwanga for sure maiwo adapita ku uhule
Tiwapeze bwanji anawa bwana Rodwell?
Mwana clean ngati uyu. God bless them
Moyowu pena pake eeeee 🙌🙌🙌🙌
Failed to control my tears 😭😭😭. Ambuye ayang'anireni ana anu
Mr R this is very hard situation for this beautiful souls.
Ndalira God have mercy
5:36 ngati muli ndikuthekera kundilumikizisa ndi lodwell plz this is my number send to him I'm from area 49 Dubai plz
Zinazi ukamaziva wekha kumangolila😢😢😢😢😢
Kom kuja ku kuli mavuto nag ana amenewa kumasamarana zandikhuza 😢
Tiyeni abale ndi alongo tiwathandize anawa kwasala tchile ndikomwe kupota moto komabe Ambuye akudaliseni nonse amene mukulingalira zotengapo mbali
Std 3 mwana koma kuvala udindo waukulu ngay uwu?? Aaaaa shhhhhh 😢😢😢😢😢😢😢ndalira nsaname
😢😢😢mmm ambuye atinthandize ndithu
So sad, God's grace up on them
😭😭😭😭😭😭😭😭 dziko ndilokondela ena akusala kudya kufuna ana...ena mpomwe akuwathawa, Tsapa boma lanji limenero
nkhaza kwaana ngati ariku hure azithandaixa ana ake
My heart bleeds 💔😭
Chibelekero changa kusuntha suntha ine nkhani yomvesa chidoni kwambili ngat dzimayi sikoonera kusiya anawa okha mavuto sathawika
Mulungu akumbukire Ana awa
😢😢 Anawa alipamoto ndithu anawa akufunika athandizidww
Terrible situation.... 😢 Where is government mukungodya ndalam MMA office without assisting pple... Ana simplexs chithyola mukungogula magalimoto for nonsense kukanika kuthandiza anthu... Look at this... Be shame guys please
So touching 💔
Kutundu kwa makolo awo ndikoyenera afufuzidwe chifukwa mudziwo okuoneka kuti paliso anthu othekera kuwathandiza komwe kuli makolo awo
I agree with you wamkulu ,koma kuona kwanga anthu amudzimo ngoputsa bwedzi akabwela mayi wawo anawa ,asanachoke atha kuwafutsa then ,let's her no going otherwise kuwauza apolice ,sad news, tiyeni tithandizepo apa
Sambitu izi, chochi makolo mungadalisike?mukusiya ana akuvutika.ganizani bwino onse amene akupanga makhalidwe amenewa
Koma zovetsa chisoni bwanji zimenezi mmmmm anthu ndalama zonse akuonongazi ayi zikomo kumalawi kulimavuto
Failed to control my tears 😭😭😭😭😭
No doubt amayi atha kukhala kuti akupanga uhule kwinakwake koma sizikuyendako. Gwero lalikulu ndi abambo amene anathawa udindo wawo. Such men need to be arrested.
Ntchito yayikulu mumaigwira a Rodwell mulungu azikudalitsani🙏
Ali boma liti tipatseni ADRESS ana athandizidwe
😢😢😢this is sad & heart breaking mmm.
Koma mafumu chito yanu ndi chan sangasonkhese Vandalia kocrpa mkuthandizra osowa mpka znthu kufika apa mmmm😭😭😭
Ena ndikumakhala ndimanyumba 10 kulephera kugaira nyumba imodzi kwa anthu osowa ngat awaaaa
Mwatani Kodi kunthandiza sikunkhala ndi zinthu
Ambuye bweran
😭😭😢😢 ambuye tag wire tagwireni dzanja anawa chonde
eishhh
Mulungu awakanthe makolo onse komwe aliko
Ndipo ine ndimachita kunena sindingathawe ana anga bola tivutikile limodzi
Ooh this is too much for sure💔
Makolo afufuzidwe ndipo anawa akuenela kulandila nthandizo
😢😢😢Lord please have mercy
Ambuye atithandize ndithu
Belita is in so much pain. 😫 mwana mpka kulira mmmhhh
God have mercy 🙏
Anthu ena mumabanjamu akhala zaka zambili akusowa mphatso ya Wana,, ena mulungu ndikuwadalitsa ndi kumawazuza chomchi . Ndakhumudwa nazo kwambili.
Anthu amene alandira ma 6mita a ziiii anthu amene akusowa nthandizo akuwaona
Ine chonena ndlibe kwanga ndkulira bas monga nanenso kholo 😢😢😢
Makolo a ana awa amangidwe. Aaaa😢😢 sizoona izizi
😢😢😢What a sad story
Ambuye achitileni chifundo anawa😭
so bad 😢 😢 😢 😢 i failed to control my tears 😭 😭 😭 but why some parents do this
Nde mwati mulungu alikod? And tose anthu tinalengedwa muchifanizo chake? Yesu anafad pantanda kutiombola ife kumachimo? Nde analengeranj anthu ambrimbri oti sangakwanise kusamala ose?
Mulungu alipo wankulukulu ndipo Yesu adafera aliyense. Vuto lomwe tilinalo ndilomwe adadzafera Yesuyo CHIKONDI. Anthu tidasowa chikondi ndikuumitsa mtima.
Funso lopusa ili nanu
Anthu Ena tikamati tuvutika tisiye mmmmm this is worse kunja kuno kuli mavuto 😭😭😭😭😭😓😓😓
😢😢😢😢😢😢😢😢😢
Mmmmmmmm walira mwana 😢😢 koma awo komwe aliko Mulungu awalange ndithu
Koma ndalila ambuye muwakumbukile ana anu mmmmm
Too bad may lord God change their life style.
Ine misozi mx kanyimboka eeeee mlungu atithandize ndithu
Eish. God have mercy