Lwachitk malodza kom momwe akuipondabe msima kkkkk😂😂😂
Mutidziwitsa mmene zithere mwake,,Keep it up Balanco selemanol
Koma kuli njara, Pali nkhani yodabwitsa chomcho koma azimai kudya osasiya😄😄
Eish koma zoopsa inna lillah waina illah llah rajuun
Azimai siyani kaye kudya inu mudziyankhula bwanji ndi nthongo kukamwa 🤔🤔
Ndipo inu Aaaaa akuona ngati zotsangalatsa inu Azimayi opanda manyazi awa😭😭😭
Lamentável. zovetsa chisoni ndizlodabwitso, ndiye chachitika ndi chani Gova pambuyo posamba manja
Gova masowatu Mozambique mulibwanji?
😭😭😭zoopsa
Rádio yakula iyi Mwchidule ndi Tv. koma pa nkhani ya chitikayi ndiyomvetsa chisoni kwambiri nkhani ya ufiti ndiyovuta kwambiri mulimonse mmene zinthu zingakhalire imakhala yovuta basi.
Koma kunjaku kuli zinthu, Lyford Vasco
Zabodza izi ahh,sanadzuke. Wakufa ngwakufa
Man GOVA timakukondani mumatithandiza kudziwa zochitika mmudzi mwathu
Apemphele kwakuya ambuye ndiwokhulupilika ifa nina sizikuchokela kwa mulungu
Mukatelo munankhimila mulungu akukana pemphelani adzuka ameneyo
A Gova mukuyesetsa kwambili
Bwana mukuyesetsa kufukula khan
Komabe tikanamdziwa Kaye yesu zamasiku otsiriza ndithudi tikupereka anthu amoyo kumanda
Malawi akadangomuononga athu ayiwala mulungu
Ngankhale chinachake chisachitike koma Bola agogo akewo asamba mmanja iwowo akanangovomeleza ndikusamba mmanja osati mpaka mphuma thikiti zomwezo ayi, chifukwa zikuoneka kut ndizamasenga zimenezo mensa azimayi amadya nsima aja avomeleza ndiye iwowo akukana chani?? Nkumat akunama muthuyo sakutuluka thukuta mmmmm madalawo a pole mot hetii
Ashley mustafa
Kmtu kumalawi
Abel zulanga wamibawa alondoloze nkhani imeneyi
koma azimaiwo nde akusema mbamu zachabe
Zovuta kwambiri mutiziwitsa mmene zithere mumatiimirira
Zodabwitsa ndipo
Koma zikoli silikuenda bwino
Kuma kumachitika zinthu zoopsa mmmmm
Tikutsatila mwachidwi mutiuza momwe zithele
Timakunyadilani A Gova
Zochititsa Martha
Denza ndi ziko lina
What happened next
Mmm zoopsya
Following
😭😭😭😭😭😭😭😢
Wina anangolota zimenezo zamabodza
Hummmm koma!
Zikusowekera kupemphera zedi
Tidziwitseni ndithu
Zinatha bwanji tiuzeni
Onse anawasambitsa manja koma mwanayo sanadzuke. Mwambo wa malilo unachitika
Mmm z00pya
Aaaaaaaa zinthu zake zovuta
DRiemo
Muito triste
Koma azimai inu khalani serious nanga kudya kwabwanji uku tadikilni kale mudyabe
😭😭😭😭😭
Not good
Koma mutiphunzitseko chilankhulocho chifukwa 1 day ndizapezeka kuti ndili komweko nde ndisazakhale mlendo
Zikuchitsa mantha omwarira kumankharabe ndimoyo eee koma ufiti wake ndiweniwen