Madhala Edo muli skill so calm ..... Amatha ngini am sure Dhidhi akumunenayo ndwapholisi.... Buh keep it up guys.. Timachita kuona Kuchedwa kut friday lifike
🤣🤣wabwera ndi business yakeyu atha kutigulitsila cast...Pakufunika "tidakumana bwanji" wa Ngozo ndi Patricia chifukwa banja ilili eh🤣🤣palibe za yaviyavi🤣🙌🙌
Izibwera twice a week bwanji... Cant wait for next Friday 🙌
Zinthu zabwino ngat izi once a week nkutilakwira hevy
Et
Nkhn yo ndyoona 😢
Like the looks❤
Tikuphunzirapo zambiri keep it up
If you love patricia gather here 😂❤️
nthawi ikuchepa😭
The only thing I love about Patricia always amanena chilungamo 🥰🥰🥰🥰🥰🥰🥰🥰
Sure😂😂
I think Patricia akhale mlangizi wazaumoyo😂😂😂
I like this edo guy he always knows what he's doing so cool and calm
This bar man guy very professional kkkkk
Ati ngati opepera choncho ndikangomuyang'ana zachanguchangu😂😂😂😂😂😂Patricia
😂😂😂😂Scandal ya Albert ikanakhala ya Ngozo, Patricia akanavuta ehhh
Edo akuti m'busa ameneuja amaponda paliponse😂😂😂
Koma ngati ndizingokomenta🎉🎉🎉
kam'busa kachinyengoo in patricias voice 🤣🤣🤣🤣
Ka m'busa kachinyengo ngati kaja,in Patricia's voice😂😂
🤣😂Achita kutsimikiza
Iyi ndi expendables🎉🎉
Ukuseka ndima type ako 😭😭 this got me 😂😂😂😂🙌🙌
Me to my future husband 🤣 mukandiona muzisekelela apo biii pachema 😂😂😂
20% commission yanu.... 😂😂😂😂😂 Koma business yogwira gwirayi yandiwaza😂😂😂😂😂😂😂😂 this episode on 🔥🔥🔥
Ine business imeneyi yandiopsa😂😂😂
Ndye Tricia akutitu ka full grown boy😂😂
Edoh kukonda ma business😂😂🙌🏾🙌🏾
Madhala Edo muli skill so calm ..... Amatha ngini am sure Dhidhi akumunenayo ndwapholisi.... Buh keep it up guys.. Timachita kuona Kuchedwa kut friday lifike
Impatiently waiting for the next episode😂😂😂😂😂😂
Birds of the same feathers
Kma Patricia ndi chivibe😂😂😂
Koma Patricia always make my days mweeeee😂😂😂
Akoma Patricia...akuti kazisekelera ....😂😂😂😂😂😂....abambo akuti ndikukusekelera koma sukundiyang'anaso ....😅😅😅😅
It's tamasekerera for me 😂😂😂
Patricia iweo 🙌🏾
Sazatheka😂😂😂
Angozo plz really life tangomukwatin Patricia mungasumganetu😂😂😂😂😂
Nde mwati tidzionera from how old😂😂😂😂 vuto ndiwe (Patricia the mashini❤❤
Ukandiyang'ana ineyo udzitsekelera ngat mmene umasekelera pa phone chfkwa pa vuta pano 😂😂😂😂😂😂 patricia
It’s always Patricia for me😂😂😂😂😂
l
ll
l
p
p
pp
l
l
l
p
l
lp
l
lpl
l
p
p
pp
l
l
l
p
l
lp
l
lpl
l
p
l
p
p
pp
l
l
l
p
l
lp
l
lpl
l
p
You guys makes me feel great
I just like the Song basi... Ichi ndikondiii... Big up guys
Me busy watching basi from nowhere my 6years girl comes akuti eeeeeh busy tu ndi vuto ndiweyo kenako umumu angozonso ndivuto
Komanso a Edo ukumandiwadza bwanj kkkkk
Koma angozo ndi nkazi wawoyu eeeeee adzaphana ndithu😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Kkkkkkkkk koma Sangie iweyo ndiwamaboza😂😂😂
😂😂😂😂 kabanja aka kama gist😂😂😂😂
Angauzo ali pa chibalo chosekelera 😂😂😂
I really like this episodes sangie yomweyo....🎉🎉🎉🎉😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Koma edo😂😂 mpaka kusabisila nkhani ya mijedu
Omg 😂😂😂😂😂😂 Patricia 🤣 zikomo azisekelela 😂😂
Koma Patricia 😂😂😂🙌🏾 usekelela chan pa phone pakopo
Ati ukangondiona ineyo uzingosekelera eeeee Patricia anakonza 😂😂😂😂😂🙌🙌
Wooow
Wooow
Woooooow u guys are improving every week. I can't wait for next episode ❤😊
Patricia's support for Belita is on point
Koma tsiku lina #Edo ndizamuoneko atakhala pasi 😂😂😂😂😂 daily kuima ,mganixuleni barman mpando nayeso ndi munthu
Tufuna album yanu ife mutichedwesa this collabo is on fire asaaa
Ofcoz Friday limafka koma lina likuchedwa iiii😫😫 and then Patricia my favourite😂
Koma Patricia😂😂😂 akuti uzindisekelela nane...ayayayaya
Patricia u r very good.❤
Eh Aunt Patricia😂😅munadza😂
Ati akuleratu 😂😂 Sangie kukonda gist 😅
Sangie ndi vibe😂😂😂😂😂😂she will make a good wife I swear 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂waphokoso koma ndipo ulimbe
Sangie Ndi ngozo Yu banja lawo Ndi lokoma kwambiri apeze ebube wawo bwanji😂😂😂
Ngozo mwatani kod 😂😂
Nice one.. l can't wait to next week 😍😍😍😍
Kkkkkk😂😂😂😂 Patricia nsanjetu ngati yochita kupita Ku xool
Banja la Ngozo ndi patricia limandisangalatsa 1 Ngozo ndi ofatsa koma patricia iiiiiiii ayi nyongolido ndithu
Patricia uli ndi pakamwa ndisaname
Kkkkkkk koma kumeneko sekereran bas 😂😂😂😂😂
Patricia malo ake palibenso😂😂😂😂
Waseka Ngozo
Nthawi zambili pat and ngoz mumatha 💯
Patricia is number one❤
Patricia kodi Ali mbali iti kwenikweni🤣🤣🤣🤣
Patricia anakoza uzindisekerela 😂😂😂
Mumativesa kukoma kwambiri ❤❤
Ngozo mkazi uyu akusaukitsa kkkk nanga uzingoseka anga wamisala😂😂😂
Sangie my favorite❤❤❤
Ganizan is underrated, alikut kod😂
Birds of the same feathers🤝
Musasinthetu nkhaniyi😂😂😂😂 kma Patricia
Nde Patricia wati Albert amaoneka opepera pena 🤣
Nde mwati Mr Pondani???🤣🤣🤣🤣 Amunanga amalakwa chani
Ndukhulupilila kuti a Edo ayimbila a Police nanga za Stop & Search tizisekelere!
Nduona kuchedwa coz mumabebetsatu💃💃💃
Kma Edo eish i love his acting amwene am atha koopsa
Yandiwaza ati uzindisekelela love you guys
shadow nd ntebe akuyenda limoz 😅😅😅😅azichenjeresa nzake ndan apa fukwa onsewo ndakatakwe
Episode iyi ikubala zipatso za episode yikubwerayo.
Malo awiri kuli nkhan Kwa berita ndkwa Edo.
Patricia 😂😂,naye Edo kukonda hustle
Kkkkkkk Edo akumvesera ati Business and search
Sangie mwati alibwinobwino anyway zikomo Robbin Ngalande
Patricia my favorite ❤
Edoh 😂😂😂 waikhola police
Usover ndimaikonda kwambili koma chonde tatopa nawoo ma 2 minutes tamaikani ma 30 minutes kkkkkkk Patricia ndakuwona
🤣🤣wabwera ndi business yakeyu atha kutigulitsila cast...Pakufunika "tidakumana bwanji" wa Ngozo ndi Patricia chifukwa banja ilili eh🤣🤣palibe za yaviyavi🤣🙌🙌
Koma edo is the best ....level ya Hollywood mmmm
Eeeeeeeeee simene kulili kwachema😂😂
Akuti akulu ndimangowaona, sagula mowa koma 😂😂
Anyamata a stop and search...kkkk...koma iiii....tikufa...
Usauver makes me happy😂
Akuti ngozo aphunzira zoipa kwa albert😅
Keep it up malawi got talent 🙌🙌🙌🔥🔥🔥🔥🔥
Banja la Patricia ndi ngozo ay ndithu limandiwaza hvy😊😊
😂😂😂😂😂 km patricia zinangovuta iwe uchikwatilana zenizeni ndi ngozo banjalanu likanakhala lokoma gyz
Eeee koma belita zitha bwanji😅😅
Koma sangie ndi piksy😅😅🙌
The bar man guy for me massive probing 🙌🏻
🎉🎉 so nice. Ma sound track ngat ali available, share link
Koma ngozo tikulela mulibe Olo m'modzi😂😂😂
Mumatha inuyo guys Always Patricia milandu😂😂😂
Ma type, full chicken. Kkkkkkkkk km2 wna anjatidwa nd2
😂😂😂 Anyamata a Stop and Search
Sangie et😂😂🔥🔥🔥
😂😂😂 apa ndiye mwalakwesi kutha kwake kuzikhala kumeneko