Honestly speaking amaiwa anamusekerera mamuna pachiyambi There's no way munthu wa mai ungamakasake mpaka ya rent mamuna Ali pompo nkumaberekabe ana chonchi Ngati alibe vuto la mmutu amayiwa ndekuti anasekerera zopepera kwambiri Ndawamvera chisoni anawa
Memory please do the needful. Call Rodwell. Mukantenge mwana wa Nzeru uyu. Kuisaka xul pomwe mmakomomu ana apatsidwa chilichonse koma akanika kulimbikira xul.
It's a welcome development only if mwanayu simukamusandutsa wantchito wanu. Ndaonapo ana akuzunzika manja mwa anthu amene ankadziti ndachifundo akamusamale.
Kumangoti ambuye ambuye muwoneni mphatsa sizithandiza at the end of the day tonse tingoyika ma comment onena kut ambuye alowelerepo .. koma nzofuna kut tonse tawonera titenge nawo mbali even 200 njambiri than ndalama zambiri mbiri zomwe timawononga podyetsa ku bet..tiye nazoni tiyambe..ine ndikuyamba apa
Truly wants to meet Mphatso please Rodwell make it possible
May God opens more doors of your blessings..
Just get that line for the help then it gonna take you to mphatso dear Eruby.
Mavuto ake amenewa mwanayi kusukuluko zinganayendeko??? Please Lord Jesus help our country Malawi. This is too much and we can't take it God help us.
I'm really need to help Mphatso please
Eruby tiye timuthandize Mphatsoyu Ngati ndili Kunoko Ku Capetown Ngati uli Ku Malawi ukalumikizana ndikukumana ndi mphatsoyo undiuze ndikufuna ndilumikizane naye mphatsoyo ndekha ineyo pa phone pa
Amayi akwanthu ku thete kwa Malirana..amayi inu nyamukani pitani ku mudzi dzikaliman ..Mukutani town mukuzuzitsa ana ...pitani ku mudzi 😢😢😢
Ndipo ma mphatso anayamba kalekale kuvutika or alibe mwana paokha amavitikaso koopsa moti iwo kumudzi kwawo kulibe achibale.ndamva chisoni kwambiri .
Please ngati ndikotheka mphasoyo ndimulele chifukwa kumuthandizila pakwawo abambo amanja lendewo azolowela
Zoona asis
And then I'm here, buying monthly bundles wina akusowa chakudya, We always need to thank God in everything
Mavuto osayamba mkumangoberekabe 😊
Komatu even Mphatso ndokongola hvy.....😢😢😢😢😢
Mphatsoyo ndingomutenga ine bwanji?
Azibambo ambiri ku Malawi analowa ulesi akusiyila azimai kuti azidyesa pakhomo zimene zikupangisa kuti azimai ambiri apabanja azipanga uhule
But the woman seemed strong enough, The best wishers just help her with capital for buziness.
Honestly speaking amaiwa anamusekerera mamuna pachiyambi
There's no way munthu wa mai ungamakasake mpaka ya rent mamuna Ali pompo nkumaberekabe ana chonchi
Ngati alibe vuto la mmutu amayiwa ndekuti anasekerera zopepera kwambiri
Ndawamvera chisoni anawa
Iwe amayi wo anayiwala zako zowo which means something is wrong with her, mavuto amatha kubarakitsa tu munthu, this is so sad btw 🥺😢
Ameneyonso ndi wakuba I think
Munthu sangayambe kuitanira or ma minibus Inu?
Mupitilize ntchito yotamandika bwana Rodwell , May God bless you.
athamangiseni amunawo bas mwamuna kuchipinda atayeni musikanayo tandipasen ine ndimusamale
Ine angondipatsa mphatsoyo azikakhala kwathu cz kumamuthandizila kwaoku nduonangat sizigwila aaaaah zundiwawa
Memory please do the needful. Call Rodwell. Mukantenge mwana wa Nzeru uyu. Kuisaka xul pomwe mmakomomu ana apatsidwa chilichonse koma akanika kulimbikira xul.
Pangani choncho
@@alexmajanja3179can you say that again 😢😢ndilinaye wanga akukana school ine 😢😢😢eish zandikhuzatu ine
It's a welcome development only if mwanayu simukamusandutsa wantchito wanu. Ndaonapo ana akuzunzika manja mwa anthu amene ankadziti ndachifundo akamusamale.
Koma moyo wu mh zomvetsa chisoni.Lord have mercy
Abale anga pale anzathu ena akuvutika pansipano tiyeni tiziwapempelela ndikadya mukadya sionse adya ayi mulungu awchitile chifundo❤😂😂
Zamveka bwana @rodwell
Mphatso afikilidwa ndithu, ndiwanzeru kwambiri
Ine mamuna ameneyo banja litha serious, ndizisunga chinthu chopanda ntchitocho aaaaa, I'm feeling sorry for mphatso 😢😢😢
This is so heartbreaking
Ambuye alowerepo nkhani yovetsa chisoni 😢😢😢😢
😢😢😢 mulungu yendelani banjali
Ebenezer kunenepa zot sadya ngat bodza 😂😂😂
Mayiwa ndiamene ali ndi vuto pachiyambi ubale ndi ofunikila
Komanso amayiwa akuoneka ngati mutu sugwira bhobho
Ine ndikuwadziwa kuyambira alibe mwana vuto ndi amayiwadi
Ndalama tikupangila bet zija it's better kumathandizila anthu ngat awa eeeee zikoli
Koma ndiyedit aaaah
Koma kuliso ntchito yoweleng ma bus town kani😂😂😂😂😂 ndaseka ngat zabwino
Tough,, God have mercy on her
Good job bro
Mwanayu akufunika thandizo nanga akufuna kwabwino tinga thandize bwanji?
😢zandikhuza kma mphasoyo akazapeza bwino ndiye azati ndakulela abambowo kma Mulungu simuthu
Oh!No😢zoliza izi m'bambo wabwanji ameneyu?Sanawakonde mayiwa akanawakonda akanakonda ndi ana owapeza😢..eish!Moyo penapake
Ndimfiti osati bambo
The way she explained that the late husband was a thief though 🤔🤔🤔
Mulungu sataya wake, and amaona paliponse, Mulungu asamalira. Amen.
Rodwell ife been calling you koma simmatiyankha l only want to ask for the way to Gangala village@Rodwell Lumbe
Bwana Rodwell , ntchito mukuigwira kwambiri. Pitilizani ndithu
Azimayi ofera dzina kt bola ndili pabanja aja ndi awa eeeeish Mulungu atithandize akuzuzitsa mwana 😥😥
Banja kkkkkkk
Anthu amene Mphatso amawagwilira ganyu onsewo chikondi.
Hw can i hv her pliz
Antuni tiyeni tizithandizana ndithu atsikanawa tandimilani kuno ku mzuzu azizikala ndi ine ndithu
She is strong woman indeed akuseka bwino bwino
God bless u Rodwell uyigwila tchito
Amayi kupempha kwamulungu muwapatse anawa ludzu osati njala ayi 😂😂😂 God have mercy on that family
Amaiwa ndiokoma kukhosi mmakwanitsa bwanji kumakhala ndi mamuna wamtundu ngati umenu? Bola banja eti?
Aaaa vuto ndi amayiwa,Kodi munthu ukuwona kuti mamunayu sakundisamala ndiye basi ungamangokhalila kubereka? Izizi ndizongofuna kuyankhulitsana molakwika,uchitsilu wamakolo umazuzitsa ana, azimayi kaziganiza sinthawi yongobereka ana phwii inoyi
Kumulakwira mwanayu
Amai mkusamala mwamuna wosathandiza musiyeni samalani anawa
Umphawi uli apo koma amayiwa amadzisamala
Kumangoti ambuye ambuye muwoneni mphatsa sizithandiza at the end of the day tonse tingoyika ma comment onena kut ambuye alowelerepo .. koma nzofuna kut tonse tawonera titenge nawo mbali even 200 njambiri than ndalama zambiri mbiri zomwe timawononga podyetsa ku bet..tiye nazoni tiyambe..ine ndikuyamba apa
Ambuye amuchitile chifundo Mphatso
Koma amayi awawa anawalekelera amunawo hiyaaa
Aaaaa chimzake cha banja ichi asaaaa,ana mkumabadwabe?
Timafera dzina ot amrs bas 😢😢😢
Very touching story
Zomvetsa chisoni kwabansi😢😢😢
Zosayenda Allah amufewesele
Ameen
Koma kumuona mamuna kuti ndi oshota waulesi osaziwa kusaka kumabelekabe ana ambuye atithandize
Eish mwana akufunika thandizo eish
Koma mkumangobelekabe. God help this kid
Amai wa ngoseka kwabasi 😂😂😂 komano abambowa ati mchani iwowa koma
Mulungu azimudalitsa lodiwelo nchito akuyigwila anthu ambili akuthandizika osanama.
Zokhudza kwambili 😓😓😓😓😓
Ambuye odziwa kudalitsa Dalitsan amayiwa ndi ana onsewo
Life😢
Zomvetsa chisoni kwambiri 😢
Men let's be responsible
Mhm the woman akuseka ngat zabwino🥺anthu akuvutika kunja kuno zandikhudza
Mmmm koma amayiwa mkumat Ali pa banja mm
Koma. Inuyo. Mulungu. Azikudalitsani. Pazotse. Mukumapanga.
God have mercy
Umphawi sizithi😢
Eishiiii koma zovetsa chison😢
Sad story
Pomwe a boma alipo ndithu koma kumangoba ndalama malo mothandizila anthu ngati amenewo zoona aboma tachitani manyazi inu a mcp mulikuti
koma eee ayi ndithu kunja kuno mavuto alipo komanso azibambo ali ndi khanza
Komatu kuli zinthu mmmmmm ambuye atithandize
Eish life 🤦♀️
Mlungu alowererepo
😱😱😱
Pitani kumuzi amayi mukusuzisa ana
Koma ine amunao amai wa iii ai too much yooo
Koma sukulu imeneyo ilibe school comitee yoti ikhoza kukambilana zavuto lamwayu kuti aziphuzila ulele
Zokhudza kwabasi
Jesus why am shocked
Eeee mwana wazunzika uyu,ambuye ndi nthawi yanu tsekulani makomo amphatso
Zomvetsa chisoni ndithu
Zosakhala bwino
mulungu atithandizw
Mr hit my inbox nambala yo pawap siyikupezeka
Eeee🥹🙌
eish too bad
Landroid yoo mgalu
Zovuta
Ummm guys kuMalawi tikudzudzika
Yawhatsapp bwanji number Mr Rodwel
Ngati mkotheka pls zandikhunza zamphatso
Mwanayu akufunika thandizo nanga akufuna kwabwino tinga thandize bwanji?