New song from Lawrence Mbenjere kung'alula Mcp akuti yayaluka akufuna kubera mavoti.

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 27 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 91

  • @JuvenileDebwe-bv8ow
    @JuvenileDebwe-bv8ow Місяць тому

    Big up Lawrence you are an artist indeed kkkjj

  • @RaphaelWinford-t7u
    @RaphaelWinford-t7u Місяць тому +1

    Chikangawa music 🎶😊😊😊 chakwela wakoyo, busa wachinyengo wakuba 😂😂😂😂 kusiya kutumikila MULUNGU kuthamangila zakudziko....Yudasi😊😊😊😊

  • @GraceChikosa
    @GraceChikosa Місяць тому +2

    Nice song Mbenjere ,,yaphedukad tere ndipo saberaso coz ayaluka tsonooooooo😂😂😂😂😂

  • @AmandaConstance-fx8cr
    @AmandaConstance-fx8cr Місяць тому +2

    Nice nice song 🎵 ❤❤❤❤

  • @MadalitsowiquessoneWiquessone
    @MadalitsowiquessoneWiquessone Місяць тому +3

    Ambejeli inu ndinu mamuna weniweni ndichebwa kuvelela pano❤😂

  • @FortyoneHarwa
    @FortyoneHarwa 3 години тому

    Mmatiimilila Mr mbenjere tikunyadilani boma ilili tithapo tonse

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 27 днів тому

    Vivaaaaa. DPP

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka 2 місяці тому +4

    Mulungu salakwitsa kalikose akuwoneni pokuyikani nose wokhudxidwa pa ifa ya chilima Ilove this song

    • @user-mw-tv
      @user-mw-tv  2 місяці тому

      Mulungu akuona chilichonse

  • @Maxielyies
    @Maxielyies Місяць тому +2

    Nyimboyi siyakale waimbila ulamuliro oyipawu wa MCP

  • @LawrenceDickens-jk3zx
    @LawrenceDickens-jk3zx Місяць тому +2

    Mwemo Komatu kuli mwazi 2025 😢😢

  • @andrewmaluwa2713
    @andrewmaluwa2713 2 місяці тому +2

    Nyimboyi ndiyapakanthawi koma yangongwilizana ndi zomwe zuchitika panopa, ndidayimvelapo ku TikTok 2019

    • @LastonMmanga-r2u
      @LastonMmanga-r2u Місяць тому

      Ndiyakale koma wayiwonjezera Zina ndi Zina, mumve nkhani ya ndege ndi nkhani ya ziphaso ziwiri...

    • @MaxwellChiwaya-i8q
      @MaxwellChiwaya-i8q Місяць тому

      Nanga nkhani ya ndege akuinenayo

    • @WallyMsiska
      @WallyMsiska Місяць тому +1

      Ndege imene anagulisa Joyce banda

  • @kassimwalusa
    @kassimwalusa 26 днів тому

    Nice tune

  • @BhekiLithuli
    @BhekiLithuli Місяць тому +1

    Kavala nkuzi mbenjere amuna Bambo esh waitha mbenjere

  • @MadalitsowiquessoneWiquessone
    @MadalitsowiquessoneWiquessone Місяць тому +1

    ❤❤❤❤❤❤

  • @WilliamTycoonKalua
    @WilliamTycoonKalua 25 днів тому

    Shhhh😊

  • @AllanGonthi
    @AllanGonthi Місяць тому +1

    Katundu waboma Mbenjere

  • @EscoChingaipe99
    @EscoChingaipe99 Місяць тому +1

    God is love if you don't know love you don't know god

  • @McjoeJamu
    @McjoeJamu 15 днів тому

    Mr Nthothah kumaChinjiriko

  • @johnkatapeh7182
    @johnkatapeh7182 Місяць тому +1

    Fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @isaackinod1256
    @isaackinod1256 Місяць тому +1

    Kuswa kuswa mbenjere😊

  • @musawadal
    @musawadal Місяць тому

    🎉

  • @SelinaMasangwi
    @SelinaMasangwi Місяць тому +1

    More fire

  • @LafickDickson
    @LafickDickson Місяць тому

    Mwaita bmana

  • @FrancisChimbewa-vu1ys
    @FrancisChimbewa-vu1ys Місяць тому +1

    Musam'bere ine mkomweka ka chiphaso 😢😢

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi Місяць тому +2

    MCP time to pack and go , see what happens in Botswana and America

  • @McjoeJamu
    @McjoeJamu 15 днів тому

    Fakamphweya Mbenjere

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift Місяць тому +1

    Ndipo ndipo ndiyapopan iyi

  • @ChirwaElita
    @ChirwaElita Місяць тому +1

    Umatha mbenjere

  • @FracksonMadani
    @FracksonMadani Місяць тому +1

    Poti ijaso ya ndege yaphedukaaa tere😂😂😂😂

  • @papelariareis.e.
    @papelariareis.e. Місяць тому +1

    Komatu mbenjere akuimba bwino kuposa kale

  • @OwenTembo-xq6ug
    @OwenTembo-xq6ug Місяць тому +1

    Nyimbo imeneyo ndiyakale muwulamulo wa Joyce Banda osati chwakwela ndiya 2013❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @NumeriGomangoBanda
    @NumeriGomangoBanda Місяць тому

    Nyimbo yakalekale iyi mu ulamuliro wa Joice Banda

  • @MaxwellChaminju
    @MaxwellChaminju Місяць тому +1

    😂😂😂😂😂ADolo anga azimwale awa. Kkkk mwaiswatu😅😅

  • @AchumileRadebe-c2x
    @AchumileRadebe-c2x Місяць тому +1

    Nyimbo ndiyapopano siyakal

  • @AllanGonthi
    @AllanGonthi 28 днів тому

    Ndizoonadii anthu awa atha kukutukwanitsadi 😂😂😂😂

  • @KelvinMahiyu
    @KelvinMahiyu Місяць тому +1

    Mmmm ndi mbenjele yemweyo uyu koma wabwela ngat coming 😅😅😅😅

  • @HenryMziwanizga-p1d
    @HenryMziwanizga-p1d 21 день тому

    Nyimbo yapompano iyi

  • @williamsalexmbonga
    @williamsalexmbonga Місяць тому

    Ndakatulo kapena nyimbo

  • @GeorgeWalani
    @GeorgeWalani Місяць тому +1

    amene akuti nyimboyi ndiakale ndi Cadet wa MCP mwana wa chimwendo😂😂😂

  • @Innocentkafa-dq9gf
    @Innocentkafa-dq9gf Місяць тому +1

    Iwe ndi yakale iyi sungatinamize

  • @MUSSAHKASTOMZ
    @MUSSAHKASTOMZ Місяць тому +1

    True story

  • @shongafilms3925
    @shongafilms3925 Місяць тому +1

    Amanena dpp

  • @McjoeJamu
    @McjoeJamu 15 днів тому

    Ayalutsono achina Goerge kanyenda

  • @ChrispinKashosha
    @ChrispinKashosha Місяць тому +1

    Ndiyakale kalele iyi nthawi ya amayi joice banda

    • @EdwinThawani
      @EdwinThawani Місяць тому

      Apapa ndipamene umadziwa kuti nyau mutu sukugwira.
      Nanga nthawi ya JB ukunenayo kudagwa ndege?
      Anabel Ntalimanja yo adaliko nthawi ya amayi?😊😅😮

    • @IBRAHIMJULIUS-bq6iu
      @IBRAHIMJULIUS-bq6iu Місяць тому

      Muzerezeka2 yakale kut imvesesen

  • @jacobsaikolo4320
    @jacobsaikolo4320 23 дні тому

    This is nthawi ya Peoples Party. Za ndege amanena denge yomwe JB adagulitsa.

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick Місяць тому +1

    Nyimboyi. Adayambila chipani cha dpp nachoso chinkapanga zopusa nachoso

  • @ChipiriroDumba-q2e
    @ChipiriroDumba-q2e 15 днів тому

    athu mudziwa kusaka nyimbo zakale kkk

  • @LawrenceDickens-jk3zx
    @LawrenceDickens-jk3zx Місяць тому +2

    Mwati uyuyu ndi busadi?

  • @ThomasDziko
    @ThomasDziko 18 днів тому

    Nyimboyi ndi yakalekale koma yangopherezera

  • @AbdullahSaeed-tg1cm
    @AbdullahSaeed-tg1cm Місяць тому +2

    Kod mu nthawi ya pp ndi DPP mudagwanso ndege iti....nkumbutsen ndaiwala

  • @thomluciouss7360
    @thomluciouss7360 Місяць тому +1

    Nyimbo yakale nanga ngozi ya ndege ya Chilima inagwa liti muisovatu mbenjele namba wani kkkk

    • @MarkoGenifala
      @MarkoGenifala Місяць тому

      Joice Banda paja amkati anagulitsa ndege

  • @HarrisonMganga
    @HarrisonMganga Місяць тому +1

    😂😂😂😂

  • @stevezulu2108
    @stevezulu2108 Місяць тому

    Chalira chinyimbochi zoona😂

  • @WilliamMlongoti
    @WilliamMlongoti 10 днів тому

    Nyimbo yakalekale akulamulira Joyce Banda ndiye Chakwera chikumukhudza nchani,Boma sitikusintha

  • @NdaonaSandifolo
    @NdaonaSandifolo Місяць тому +1

    Nyimboyi ndayivetsetsa ndiyakale ankadzudzula dpp koma inuyo mwangoyiponya pompano

  • @JohnYoweli
    @JohnYoweli Місяць тому +1

    Nyinbo ya kale thai ya dpp kadeti ukanalira

    • @StevoZimba
      @StevoZimba Місяць тому +1

      Nanga ndege yapezeka bwanji mu nyimbo umu chikala chobe kolokombwa pushiiwe imbwawe

  • @PeterJames-h3h
    @PeterJames-h3h Місяць тому +2

    Ngati nyimboyi iliyakale kale nanga zangozi ya dege akuzitenga kuti? Maboza basi, ayalukabe basi

  • @MusaLion-os1lx
    @MusaLion-os1lx Місяць тому +1

    Koma anakwapula bwino kwambiri kwake ndipo zooonad

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs Місяць тому +2

    Inu amene mukut amaimbira dpp eya ndizoona koma nanga za ndegezi zabweramo bwanji?

    • @MoosaBanda-su3zp
      @MoosaBanda-su3zp Місяць тому +1

      Tafusen athu amenewa kkkk muthawi ya dpp kunagwa ndege kkkkk chikangawa party aziwona this is not 1984 this is 2024 we are week up apm my vote

    • @StevoZimba
      @StevoZimba Місяць тому

      Apm boma​@@MoosaBanda-su3zp

    • @MarkYohane-m2n
      @MarkYohane-m2n Місяць тому

      Ndiyatsopano nyimboyi

  • @MarkoMayuni
    @MarkoMayuni Місяць тому +1

    Koma cadet uli ndi ntchito pezani china timve zakale zakale izi

  • @StaphelMvula
    @StaphelMvula Місяць тому +1

    Nyimbo yatha zaka zodutsa 6 iyi

    • @LastonMmanga-r2u
      @LastonMmanga-r2u Місяць тому +1

      Nanga nkhani ya ndege ili mkati yi ndi ya zaka 4, kapena wangoyipenta??? 😂

    • @PrinceBlessings-bv5bs
      @PrinceBlessings-bv5bs Місяць тому

    • @MangaDamiano
      @MangaDamiano Місяць тому +1

      ​@@LastonMmanga-r2unaneso kudabwa ATI nyimbo ndiyakale Koma nanga nkhani yandege ilimoyo ndiyakaleso

    • @LastonMmanga-r2u
      @LastonMmanga-r2u Місяць тому +1

      @@MangaDamiano nthawi Zina ndimawona ngati amalawife tili ndi vuto lothamangira kulankhula zinthu tisadamvetse kochola nkhani ndi komwe ikupita, kungotengera kuti ena alankhula basi tisadamve... 😜😂🤣

    • @LastonMmanga-r2u
      @LastonMmanga-r2u Місяць тому +1

      @@StaphelMvula paja a MCP simufuna kuwonekera kulakwitsa kapena kuti simufuna kudzudzulidwa ndichifukwa chake mu kungoti boma ndilomweri pomwe zinthu sizilibwino🤔🤔🤔🤔🤔🤔

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili Місяць тому +1

    Uyuyu ndi mchewa ozindikira