KODI IYI NDI INTERVIEW KAPENA NKHONDO? EEH BRIAN BANDA ANAMUKHAULISA MOSES KUNKUYU NDI MAFUNSO

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 14 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 68

  • @lastonkadula5022
    @lastonkadula5022 51 хвилина тому

    Brian Banda you're a great intelligent adalipo unice chipangula zaka zina zake zakale great works

  • @MfipaKapwera
    @MfipaKapwera 2 години тому

    Bro Brian Banda God bless you, you are intelligent.

  • @MaggieCement
    @MaggieCement 3 години тому +2

    Kkkkkkk ine nde olo ndili ntulo koma mcp sindingachite kuibvotera mpaka mayanga atadzuka kumanda ndithu

  • @TambuliAbubaka-g3u
    @TambuliAbubaka-g3u 2 години тому +1

    Amakadya ziboda za ngamira ku Abidabi basi 😂😂😂😂

  • @blessingschinyamu4634
    @blessingschinyamu4634 2 години тому +1

    Minister of information opanda data

  • @ApostleZulu
    @ApostleZulu Годину тому

    Brian Banda, m'tola nkhani.

  • @VincentKalata
    @VincentKalata 5 годин тому +1

    Kkkkk at kuyankhula zopanda Pake including anuwa? KomabBrian

  • @JosephyTembwe
    @JosephyTembwe Годину тому

    Km Brian umatha kucheza osamunyengelela ameneyo akuyakha bodzaso km

  • @watsonmhango8794
    @watsonmhango8794 Годину тому

    Kunena zoona Brian Banda ndi Katundu, Chakwera walephera apa kuyendesa dziko ,folex kulibe ,petrol and deasel kulibe,njala boma akuti lapanga lokha create chifukwa ndalama anakasiya ku butchery, komaso this country is worse today kusiyana ndi mene dziko analipezela😂😂😂😂😂

  • @NoelKhwimba-bh3ts
    @NoelKhwimba-bh3ts Годину тому

    Kuyakhula Kwa pa mwamba kumkuyu

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani Годину тому

    Guyz Kumkuyu akukhal ngt oyamba ndye kuyendesa dziko nyimbo yake ikhal BRANDON LAKE praise the Lord all my souls koz Kunkuyu ndiotaisa nthawi

  • @user-ux3ed3ni1p
    @user-ux3ed3ni1p 5 годин тому +1

    So why is the President using up all the forex to go and celebrate Idi.

  • @JustinChimera
    @JustinChimera Годину тому

    ghana
    united states of america
    Namibia
    Botswana
    momwemoso zikhalelire next year😢

  • @RodgersMtonga
    @RodgersMtonga 5 годин тому +1

    Koma kukuuyu ndiwe dolo especially kuyankha mafuso moveka bwino

  • @IdrissahHassan-vi9lx
    @IdrissahHassan-vi9lx Годину тому

    Ziboda zangamila zinamuzunguza mutu chikangawa mpakana kuiwala mafuta kkkkk😅😅😅😅 koma wabakili muluzi iwe akazangoti akupeza azakusenda wamoyo kkkkkk

  • @SOLDIERLOVE-e1q
    @SOLDIERLOVE-e1q 12 хвилин тому

    Moses kunkuyu, ndimbuzi yothelatu apapa zikuchita kuwoneka kuti a MCP chitseko chawapana nose a MCP machende anu

  • @bisweckchimphamba8497
    @bisweckchimphamba8497 5 годин тому +1

    Kumkuyu let me correct you, misewu ndi aid ya China yomwe inapemphedwa ndi Peter Muntharika mu term yake,stop fooling Malawians

  • @CharlieChirwa
    @CharlieChirwa 48 хвилин тому

    Chiboma chokanika kuyendetsa dziko

  • @HenryMero-nf4vh
    @HenryMero-nf4vh 6 годин тому

    Minister wamisala ngati ameneyi sinnamuonepo amalawi akt aip siikuafika iye akt akupeleka kuposa ma boma akele is that making sense

  • @JosephThengeza-x9r
    @JosephThengeza-x9r 6 годин тому

    My vote ikupita ku dpp agalu a MCP ozikonda awa

  • @VictorPhiri-c6l
    @VictorPhiri-c6l 6 годин тому

    Ngati president wapitila zina mu nthawi yoikika ndipo uko nkukawonjezera zina zochita it means security protocol yake silibwino. What if president akanaphedwa because of Eid? 😢

  • @HenryMero-nf4vh
    @HenryMero-nf4vh 6 годин тому

    President amanena without action wanena azikwanje amangidwe omwe tinawaona sanavale mask koma kulibe chochitika bwanji osachosa minister of security komanso inspector general aaa

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc 6 годин тому

    Koma kuyuyu akut thawi ya DPP anthu timagula bread wontchipa Koma timafa tikadya😢

  • @VincentDonald-ho6hq
    @VincentDonald-ho6hq 6 годин тому

    Mayakhowo Ali mayetso a MCE ndi zero 😢😢😢😢

  • @MosesDicostar
    @MosesDicostar 5 годин тому

    Viva Brian banda

  • @RenardPhiri
    @RenardPhiri 3 години тому

    Mfiti imeneyo anthu oponda chifundo ndi amalawi anthu amene amasunga nthayo m'manyumba mwawo amenewo zitsiru za Mcp

  • @AlihIbrahim-s7v
    @AlihIbrahim-s7v 4 години тому

    Kodi kugula zinthu kunja zayamba ndi boma lanuli😂😂😂koma a Kumkuyu mbwelela zake,,,,kuyambila nthawi ya mulu timagula zinthu kunja mukufuna munamepotu

  • @DanielZunguza
    @DanielZunguza 4 години тому

    Kape uyu amadziwona ngati odziwa kuyakhula.

  • @HenryMalisen
    @HenryMalisen 5 годин тому

    Uyu ndi dolo kuyanka moveka

  • @JohnMacneall
    @JohnMacneall 5 годин тому

    Km uy eish pasana pake ndthu

  • @EndkenChisuse
    @EndkenChisuse 5 годин тому

    MCP singawine kunkuyu kunkuyu midzimu anthu akwiyananu osati zibwana

  • @RaheemNgoma-pk1ev
    @RaheemNgoma-pk1ev 4 години тому

    Witika akukudikira Nakadazi

  • @AlihIbrahim-s7v
    @AlihIbrahim-s7v 4 години тому

    Koditu mukanakwanilitsa zomwe mumkanama zija kuti feteleza azakhala pa K4,500 poyambila bwezi anthutu akulima mpsavuta

  • @DorotyMussah
    @DorotyMussah 5 годин тому

    Mzimu WA Allan witika upitilize kuwusa mu mtendere

  • @lewisdicksonmlozi130
    @lewisdicksonmlozi130 4 години тому

    Iwe mbuzi kwabasi kumalawi magalimoto achuluka ndichifukwa chake Forex ikusowa

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 3 години тому

    Mbava kuchinjiriza mbava yaikulu mwa ukadaulo .

  • @HenryMero-nf4vh
    @HenryMero-nf4vh 6 годин тому

    aaa kugawa chimanga 50kg for 5yrs uzadabwa iwe

  • @LomezyWhite-vq9bv
    @LomezyWhite-vq9bv 7 годин тому

    Ndrama zakuyanja ukuoneka mwa munthu.

  • @PatsonmahoweNyirongo
    @PatsonmahoweNyirongo 5 годин тому

    Za covid 19 inu a mcp zisiyeni, chifukwa panthawi ya campain mumati covid kulibe ndiye lero mukutenga covid kukhala chobitsalako pankhani ya chuma cha dziko

  • @AnusaChiwale
    @AnusaChiwale 3 години тому

    Mwachidule mwalephera bs

  • @SolomonMumba-i5n
    @SolomonMumba-i5n 3 години тому

    Ku ndirande kuli kwawo, malowo amene amakamba anthuwo sakwaziwa? Bridge limene limafuna kuduka, sakulidziwa? Come on kunkuyu!! You can do better but unfortunately you won't next time.

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 3 години тому

    Akunkuyu , inu ndi boma lanu lakongresi siinu ozinfikira Koma amwano , odzimva , odziona kuti anthu ndi chipani choyenera kuyendetsa dziko ndi inu nokha .

  • @LucksonChipofya
    @LucksonChipofya 6 годин тому

    Kulibe wanzeru ku mcp

  • @EddiePhiri-w2d
    @EddiePhiri-w2d 5 годин тому

    Chisilu uyu Paribe chomwe apanga

  • @LoyceshadShad
    @LoyceshadShad 5 годин тому

    Acoke chakwera tatopa naye ticita kuona kuchedwa 2025 akapitize zaubusa zero pa ten

  • @BlessingsLuclus
    @BlessingsLuclus 5 годин тому

    Anthu awa mvuto ndiloti magopakila ndalama mmutumba mwawo

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 3 години тому

    Dziko ili lilibe mtsogoleri

  • @Yohane-bg8bn
    @Yohane-bg8bn Годину тому

    Koma mulila

  • @JustinChimera
    @JustinChimera Годину тому

    mwatikanika

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g 6 годин тому

    Ndi ntchito ya boma kulimbikitsa anthu adziwe chomwe angalime chomwe chingawapindulile

  • @RudoChirambo-hy2jz
    @RudoChirambo-hy2jz 3 години тому

    Helicopter phephelephephele😂😂😂😂

  • @MarthaBango-s3y
    @MarthaBango-s3y 5 годин тому

    Kkkkkk koma Brian 😂😂😂😂😂

  • @AlexMzati
    @AlexMzati 5 годин тому

    Kkkk km brian😂😂😂

  • @FellenMwale
    @FellenMwale 5 годин тому

    Gayz kukuyu ndi doro ndale tiziyke apo kkkk ngakhaleso Brian banda a kudziwa

    • @mishecksipolo7153
      @mishecksipolo7153 3 години тому

      Ngati pali nduna yonne Imadziwa ntchito yake nddameneyu ,kungoti bwana wakeyo amantumayo ndiye manyi eni eni ,

    • @geoffreymsampha4679
      @geoffreymsampha4679 3 години тому

      Brian has a grudge t against this government you remember he sued for what he called illegal dismissal. Even if it was me I would do the same He is a bitter person

  • @HamzahTwaib
    @HamzahTwaib 5 годин тому

    Iwe Moses mutu wako simagwila ungayankhe kut AIP kugwila ntchito chotan osangovomela kt mwalephela bwanji kt lamulila ngt ikugwila ntchito bwino bwanji paka lelo anthu akugula fertilizer,, ndiwe galu bwanji,, zamafuta zomwe ukuyankhazo ukuyankhazo zosamveka apita kukakambilana zokhuza mafuta lelo kakubwela kumatiuza zosagwila mutu,, kt atiuza bwino bwino mwezi wa kucha chotan osangolankhula kt zaka ika bwanji ife tikufunana kulandila panopa chithandizo azitiuza zolanda zelu zoona iwe...
    . Iwe.... Undisamale,, km bwanji abwele pulezidet wina tiyeseso

    • @DanielZunguza
      @DanielZunguza 3 години тому

      Koma mcp ichoke guyz,apo bii dziko lidzapoyililatu.

  • @liz9425
    @liz9425 3 години тому

    Brian is with us and is our guy! Clearly showing Chakwera is not his president

  • @ChikondiChingana
    @ChikondiChingana 3 години тому

    This government is not serious.
    Mbewù kut itheke it's just three or four months. But they talk like mbewu imatenga so many years kut munthu akolole.

  • @GraceChenda-q2g
    @GraceChenda-q2g 6 годин тому

    Chizaone nchipande powomola

  • @johnjoachim3820
    @johnjoachim3820 3 години тому

    Kumamvomeleza kuti zithu zakuvutani basi

  • @SekelaniTembo
    @SekelaniTembo Годину тому

    Hon kumkuyu the great❤

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 3 години тому

    Mbava kuchinjiriza mbava yaikulu mwa ukadaulo .