Nkasa is an artist, he can be hired to go and entertain people at any function. Musamunyoze chifukwa choti wayimba nyimbo ku msonkhano wa chipani chomwe mwina simugwirizana nacho. Next time he can be called to entertain people ku Convention ya UTM, DPP, UDF, AFORD or any other party. So izi nzabhobhoo. 🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Tisazabwereleso kuchipani cha family. Amalemela ndi ochepa mudziko...2025 muvutika.koooopa nose achipani cha ma family ichi...dziko linabwerera kwawo. Mistake yamakolo.athu inakozedwa 2019😅😅😅
Nkasatu ndi oyimba ali ndi ufulu opanga kuti zake zimuthekele nane kwathu ndi ku alomweko koma ndikugwilizana ndi mfundo za chakwela tonse ndife amalawi osayang'anila mitunndu
A Mkasa a Mkasa, munkati Chiyani inu zotamanda a tsogoleri a ndale? Pano mwayambilaso? Aaaaaaa, APA mumuuza chiyani mwini WA luso lanu Mulungu? Mukupitilizabe kumukhumudwitsa ifeso mwatikhumudwitsa. Mwaphwanya lonjezo lanu Mkasa. God for give you. Come back to him my brother Mkasa
Since this song doesn't concern me. Let me take this opportunity to ask all car manufacturers to include a horn a brake pedal on the passenger side. We also want to be greeting our friends.. Thanks in advance
Or atapeza oimba onse Kuti aimbe nyimbo zowachemera Koma kumwamba kukati ndi ai basi adziwe kuopa mulungu anthu a MCP onse omwe akujoya kuba misonkho yawanthu osauka.
Guys ngati boma ili tikufuna kuti titengeso otsutsafe tilimbe chifukwa Mmmm pa social media pano pasatipusitse anthu MCP Mmmm akuyikondabe pa ground pa ndiye pano tisamanamizane ifeso tipite pa groundipo tikathamangethamange mwina zitiyendera and even mutati muwonetsetse ma comments amene amapanga ndi amodzimodzi, tisapuditsidwe pano tiyeni tikakoze ma area, ma zone muthu wa kumudzi timupange convince
Ndikumummvetsetsa nkasa akupanga mchere basi ❤️
Mkasa amadziwa kutembenuza chikwangwani! Change goal! Beautiful song, beautiful composition, wise timing!
Wapanga zimenezo poyang'ana thumbs la ndalama lomwe labooka ku MCP
Miyoyo ikuvina kuyiwala ogogo anga akufa ndi njala
The song deserves a video, nice one in that matter, with all the infrastructures included.
APM 2025 MY VOTE💙💙✅
Komatu Amkasa zandale zizakuphani
Chipolopolo kumalawi pamaimbidwe mcp wooooyeeee 🔥🔥🔥🔥🔥🔥 big up
He is brilliant. He supports the President of the day.
❤❤❤ amukasa mamveka tili namwe
Nyimbo ikukoma iyi,, Ife tikunva kukoma Enawo akunva kuwawa eish 🎉🎉🎉🎉
@@mphatsochitimbe2205 🥰🥰🥰🥰💯
Tikumvadi kukoma mcp yomweyo
Wakwiya ndi mfiti 😂😂😂 opha malubino iyaaa
@@mphatsochitimbe2205 kukoma osati maseweraa ,, tiye tithamange pa ground basi
Nkasa is an artist, he can be hired to go and entertain people at any function.
Musamunyoze chifukwa choti wayimba nyimbo ku msonkhano wa chipani chomwe mwina simugwirizana nacho.
Next time he can be called to entertain people ku Convention ya UTM, DPP, UDF, AFORD or any other party.
So izi nzabhobhoo. 🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@@martinndawala8125 iwe nde chimunthu choganiza boooo 💯🥰🥰
Nkasa yemweyo 🎉🎉🎉
Chikachepa ponya nkamwa akakhala galu kuyan'gana ndikwake 😂😂😂😂😂 nkasa ndikatundu
@@GeraldChisamba😂😂😂😂
Koma ndalama anakonza ndithu zomwe akuchemererazo za ziiii aaaaah
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 mkasa yemweyo
yomweyoo ,,, wawulesi asadyee ,,, amene salimbikira pa yekha nde zimuwawa ,, dikira chakwera azakulimira ku Munda kwako
Akufuna ndirama ameneyo umphawi wamukwana
Ku MCP zaphweka bola plan ,salute Nkasa panga mchere
APM my vote
Ulova kupasa nzeru makemu Thomas chibade sananame
Nyimbo ya mbembatu moto kuti buuu🔥🔥🔥🔥bomalilo
Mukaona nyau zikuvina mudziwe kuti wina akutamba masana.
Tisazabwereleso kuchipani cha family. Amalemela ndi ochepa mudziko...2025 muvutika.koooopa nose achipani cha ma family ichi...dziko linabwerera kwawo. Mistake yamakolo.athu inakozedwa 2019😅😅😅
Chikachepa ikamkamwa 😅😅😅😅😢😢😢😂😂😂🎉 😊😊 akakhala galu kuyqng'ana kwache
Ine ndingowerenga ma comment basi 😝🤪🤪🤣🤣🤣🙌
Gule uja wayambapo tchito yake🙌😂
Nkasatu ndi oyimba ali ndi ufulu opanga kuti zake zimuthekele nane kwathu ndi ku alomweko koma ndikugwilizana ndi mfundo za chakwela tonse ndife amalawi osayang'anila mitunndu
Mkasa samakwera yakuphwa uyu amaonera patali mita akutanthauza china chake chachikulu mawu akulu akoma a kagonera.
Koma adha awawa sound amapha man
Mmmm kutaya a Malawi, kodi nyau imavita???
Ine ndezandisangalatsatu wakwiya ndimfiti😅😅
Mkasa afera ndalama
ndukuuzan adha uyu ndi galu kwambili
Nsip@@IzzyAsirndipo ndi mbuzi yayimuna ndithu😅😅😅😅😂😂😂
Mchape wachabe uyu
Ndani safuna ndalama, sanje ayi inu pangani zanu zochita zopezera ndalama
Anaimba Kale lasdema
Mbuzi nyimbo zako sizipita patali kamba ka ndale. Usayiwale amenewa apha Lucius Banda.
@@actuarialscience2283 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 inuso mwabwera ndi itiso
Pena umbuli siwabwino zokut Lucius amadwala sumaziwa???? Before you talk you need to think
@@VelessCBandah Lucious anatukwana MCPigs kwambiri koposa Chilima. Ralph Kasambala; Chilima; Orton Chirwa; Shanil Dzimbiri; Sidik Mia; Lucius Banda, onsewa munapha apusi inu. Afiti anyau inu.
@@VelessCBandah Onse amene afa ndi a UTM ndipo inali mthawi yoyandikizana. Mwazi wa iwowa uli pamutu panu.
Sikale panja amanyodza chakwera lero 😢akumuyimbila nyimbo nkasa sadzatheka
Nkasa sadzamva ndithu😂😂😂😂😂 mmene anamukhomera nthawi ya Amayi😂😂😂😂
A Mkasa a Mkasa, munkati Chiyani inu zotamanda a tsogoleri a ndale? Pano mwayambilaso? Aaaaaaa, APA mumuuza chiyani mwini WA luso lanu Mulungu? Mukupitilizabe kumukhumudwitsa ifeso mwatikhumudwitsa. Mwaphwanya lonjezo lanu Mkasa. God for give you. Come back to him my brother Mkasa
Since this song doesn't concern me.
Let me take this opportunity to ask all car manufacturers to include a horn a brake pedal on the passenger side.
We also want to be greeting our friends..
Thanks in advance
Chakwera my vote
😂for the sake of his survival Nyimbo yabwno 😍🥺😅udyapo zambiri aise
It's hot out there! he's doing it for survival
Live
But here is hot less
Exactly 💯
Pamalawi ndalama zilibe ntchito ndithu xikuchita kundindozana ngati akukapereka kuguwa la tcharitchi munthu ndi phuji zoonadi
Nkasa same same Brown Mpinganjira kumangopanga zokuthandiza that time basi😂😂😂😂
Kupanga khobili pa town Mkasa 😂😂😂
I like it 👌
We all need money to survive ,,and he is doing this for survival
😂😂😂😂 koma Nkasa ndi dolo
MCP 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Chamoyo chimasitha nkasa naye ndi munthu wayimbilaso kuimba zandale nde mutani? 😂😂
Nkasa doesn't know his Password 😅😅osamamutengera.
Nkasa is a legend indeed amatha kuzisaka
😂😂😂 kudzaaapopa apule
Ine uyuy aaaaaaaaa😂😂😂😂😂
Munthu ukakhala wosawuka umayamika zopusa cholinga akayivera nyimboyi ampatse ndalama 😂😂😂😂
Big up mkasa
Zinazo pambali koma sound iyi nkasa wapha eeee
Akasa nayenso kukadyanawo 😂😂😂😂
Siuja umati waisiya km akufafanthanso wayiwala kusalima🤛🤛👊👃🤛☹️🥳🤛
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Awa nde azafela zayen srs
Mose wa lero munakunga bwana 😂😂
Kodi mesa ankati sazaimbanso za ndale pa interview ya Brayani Banda
😂😂😂ankasa kumeneku mwatola chikwama kkkkkk umphawi sikanthu
Kapena kuopa kupotokoledwa khosi
Amakaka kkkkkk kwao gule
Eya akugwiradi nthito zabwino zokupha, kuononga,kugwesa ndalama komanso kugwesa ndenge
Nice song
Nyimbo yo it doesn't matter,what matters ndi thumba walandira kuti apezeke pa stage.
Ife mcp ndi boma lathu 2025 motoo❤
Ndinamumva Nkasa pa Cruise 5 ndi Joab akunena kuti anawononga tsogolo lake ndi ndale ndipo sazapangaso..Nde pano 🤷♂️
Akapusa adyele aise ndi nthawi yako naweerr😂😂😂😂😂😂😂, ndalama zaphweka uku
Mmene kulili kumudzi panopa bola kulimbikila ku pephela basi no voti is coming from my familly
Chanal chanu ndi mbola
Zaziiiii nyimbo mumati yabwinoyo ndiimeneyiyi aaaa kupusa ubwino wake chilichonseso chakwera
Amene akulowa chaka chammawa sitidzalola kuti udzamuimbile nyimbo chifukwa mbali yomwe uli sitikuiziwa
That's the only way to make money in Malawi.....😅😅😂😂😂put a smile on chakwela's face or you get locked up🤐🤐
Mkanandipasako number ya kasa chisilu cho
Mcp my vote
Pure Madness
He is a good composer ofcourse nothing he can do it's apart of surviving
He loves our president musically
Or atapeza oimba onse Kuti aimbe nyimbo zowachemera Koma kumwamba kukati ndi ai basi adziwe kuopa mulungu anthu a MCP onse omwe akujoya kuba misonkho yawanthu osauka.
Aaaah koma 😂😂
MG2 kumanja (Mkazi wa mwini=Vera Kamtukule) and MG1=Monica kumanzere. Ayi tiziona
Ku Malawi ulonva wafika pachimake.. nthawi zonse muzimuona mkasa Mutu wake sumagwira NDI bilimankhwe azake NDI alongwe
Kkkkkk kumeneko ndikumalawi kuona mfundo zimene akunenazo nyumba za police kkkķkkk
Padzana zinali bwino popeza anayimba yotamanda Mfumu yanu. Lero wayipa popeza wachemerera mdani wanu?
Pa interview munati chani ndalama koma
all the best mr president God help you
Akutitu omwe sitidalowe tilowe 😂 eti njara yatha, zinthu zili bwino palipose
NYC one Mkasa
Makosana mutakonza ma camera anuwo, or pezani ma engineers odziwa ntchito osamangotolapo
Brain is the measure of the mind
Atsogoleri kumalawi alibe vuto koma alivuto ndi iwo amavota
Ndikukaika ngati amadziwa chimene akusankha
Kodi DJ ukupanga zingati? 🙄🙄🙄🙄
Bola alandilepo bx ❤❤❤
Chineke 🙌🙌🙌🙌🙌🤣🤣🤣🤣
Tengani ankasa ndalamazo koma muzaziwa povota ,chinsinsi chili mu mtima mwanu.
Ndalama zikaphweka ngati tomato nawenso ndi sitayilo yako bwerapo utapepo nupitiliza ndawala zako 😅😂😅😅😅😂😢
Kuyankhula kwa Anthu ANDALEE amati “there’s no permanent enemy in politics “.
Nde J. Mkasa adzituwa milomo pomwe ku MCP vinyo alipo.
Zachisoni 😮 koma awa
Ndizimenezo amalawi mukuononga dziko chifukwa chokonda ndalama maso timva Kuti mkasa ndi vice President. Note that mukuononga dziko koma
Akulu awa dyela lidawakulira
Zinazi sizifunika ma Cadet pafupi iyai chifukwa atsegula nazo mumimba
Malawi Congress Party ndima Vampire
Fungo losamva perfume lija latha 😂😂😂 zipange ndalamazo but chakwera alibe mbili yabhoo
Fungo lija lathadi mwinu
Mmmm 😂😂😂😂😂 kunyoza kwabwanj uku mukatero zakunyasan bola akanayimba zochemelera ena aja 😂😂😂😂
Uyutu alibe 2 koloko iyi kwayimbirani poti mwafuna zikatha ndalama mwamupatsazo atulutsa ya kufuna kwake muone akunyozeniso 😅😅😅😅
Kasa kidzisaka😢😢
Ine ndinakakonda kuti 2025 MCP izatuluke m'boma sure
Guys ngati boma ili tikufuna kuti titengeso otsutsafe tilimbe chifukwa Mmmm pa social media pano pasatipusitse anthu MCP Mmmm akuyikondabe pa ground pa ndiye pano tisamanamizane ifeso tipite pa groundipo tikathamangethamange mwina zitiyendera and even mutati muwonetsetse ma comments amene amapanga ndi amodzimodzi, tisapuditsidwe pano tiyeni tikakoze ma area, ma zone muthu wa kumudzi timupange convince
Nkasa amalemba kusokerela nyimbo with catchy hooks Talented guy, 🎉