The DC, Kuno ku South Africa kunonso asilikali 9 afa ku Drc komatu kwavutatu kuno, anthu ndi zipani zotsutsa zikupempha kuti Defence minister and Army commander atule pansi maudindo awo ,
Nanunso tun a Bon Kalindo muyamba misala.... Inu asilikali athu ku DRC anayamba kupita mu ulamuliro uwu wokha?. Izizi mukukamba just cuz ena amwalirako, akanakhala kuti sikunafe munthu simukanalankhula ayi.... Kupita kwa a Silikali ku Peace keeping mmayesa ndi Mgwilizano wa SADC. Inu mumati msilikali ntchito yake ndi chani Mdziko?. Mmayesa nkutetedza dziko,,nzika ndi chuma Cha dziko lo.... If u see our Soldiers driving nice vehicles today it's because of ku field amapitako. May the souls of our Soldiers rest in peace. Tiyeni tizikamba nkhani zomanga osati zanu mukukambazi... Pa za asilikali po zitayeni... We benefit security for Africa ,,,, we benefit funding imene imabwera from UN,,,,, we benefit experience ..... Tiyeni tizikamba za Ndale osati izizi.
Vuto loti zida akugwilitsa ntchito a m23 zaphamvu kwambli Pamene asilikalo athu ndi south Africa atenga zida zakale kale komaso zochepa phavu kungoganiza kulibe amene akumenyela sniper a new pamene m23 ikugwilitsa ntchito ma sniper achabe aphaso general waku drc dzana i think komaso amapititsa asilikali oti alibe luso len len pa ntchito kuja sikopitila ngt mwa training ayi kuja kuli nkhondo kuyenela mikangala asilikali osati anawa ai
Perfectly said, may God bless you bwana wathu.
Nthawi zonse Ichichi chimakonda kuyima pachilungamo long live Hon Comrade Kalindo 💪
The DC,
Kuno ku South Africa kunonso asilikali 9 afa ku Drc komatu kwavutatu kuno, anthu ndi zipani zotsutsa zikupempha kuti Defence minister and Army commander atule pansi maudindo awo ,
Akufuna kut asilikali ao axibwera boss... Cz angoononga ma billion ama rand kom sapindula kwambli
The DC'S perfect said......
Chifukwa chiani kulondela zithu za ziko lina mmalo molondera nyanja yathu
Nanunso tun a Bon Kalindo muyamba misala.... Inu asilikali athu ku DRC anayamba kupita mu ulamuliro uwu wokha?. Izizi mukukamba just cuz ena amwalirako, akanakhala kuti sikunafe munthu simukanalankhula ayi.... Kupita kwa a Silikali ku Peace keeping mmayesa ndi Mgwilizano wa SADC. Inu mumati msilikali ntchito yake ndi chani Mdziko?. Mmayesa nkutetedza dziko,,nzika ndi chuma Cha dziko lo.... If u see our Soldiers driving nice vehicles today it's because of ku field amapitako. May the souls of our Soldiers rest in peace. Tiyeni tizikamba nkhani zomanga osati zanu mukukambazi... Pa za asilikali po zitayeni... We benefit security for Africa ,,,, we benefit funding imene imabwera from UN,,,,, we benefit experience ..... Tiyeni tizikamba za Ndale osati izizi.
uyinvereso bwino vn galu iwe ukudana ndi chilungamo nkhumba iwe eti
Vuto loti zida akugwilitsa ntchito a m23 zaphamvu kwambli Pamene asilikalo athu ndi south Africa atenga zida zakale kale komaso zochepa phavu kungoganiza kulibe amene akumenyela sniper a new pamene m23 ikugwilitsa ntchito ma sniper achabe aphaso general waku drc dzana i think komaso amapititsa asilikali oti alibe luso len len pa ntchito kuja sikopitila ngt mwa training ayi kuja kuli nkhondo kuyenela mikangala asilikali osati anawa ai
Kulibe kupuma
The D.C.
Kodi anthu azipita kunkhondo koma asamakawaombeledwe poti ndamalawi but iwowo azikapha anthu? Akalindo uku ndikuganiza mwaumbuli Chitsiru iwe ndimaona ngati wanzelu. Nde ngati zili choncho MDF ithe Pamalawitu anthu poti anthu akuopa kufa . Chitsiru iwe eti.
Chitsiru ndiwe
Chitsiru ndiwe omwe kwanu sikudapatikaneko msilikali,
Mwana owopsya kwambiri 10:53