Ineyo kuyambira kale ndinaziwa kuti pali kugwilizana pakati pa imfa ya Ralph Kasambala ndi Chilima chifukwa amaziwa bwino kuti Chilima sangalephere kupita chifukwa anali ma friends
Wamtumbo dazinlako this this new generation 2025 nose adpp mumagidwa bas ife tatopa ndikuva zadege madzi akatayika sawoleka ukafa wafa kulibeso kubwelele or utalila chotani sadzikaso wapita bas ndiye usatuzuguze dazi lako
Munthu opusa iwe chifukwa chiyani umathawa thawi yofunika kwambiri. Zimenezo uzikauza ma bwana ako ku dpp. Iwe timayembekeza kuti uzikanena zodabwitsa uli konko. Wina akanena zodabwitsa nthawi yomweyo iwe kutiuza koma iwe Kewee ngati those. Aaa a freedom fighter a fake inu.
Iyi zoona ndi mbuzi ...ukusowa choyankhula apa ...osamangodya ndalama zokubazo bwanji zochokera Kwa chakwera ......Malawi muno ndiye muli mbuzi zambili
Mr namiwa ndinudi munthu oopa mulungu pitilizan kufufuza paka okupha aziwe may God continue protecting you
God bless Mr Namiwa
Long live brother Namiwa, may God Almighty protects you? we need people like you in this country.
big up Mr namiwa we love u
Munthu okonda ziko muchoonadi long live Namiwa
I wish you the best
Mulungu akusogoren mr
Nkulu wankhondo kungofika polankhula chibwibwi chonchi umangodziwira2 kuti zokonza...bigup namiwa dziko likufunika anthu ngati inu mwina titha kuzasimba lokoma tsikulina
Ineyo kuyambira kale ndinaziwa kuti pali kugwilizana pakati pa imfa ya Ralph Kasambala ndi Chilima chifukwa amaziwa bwino kuti Chilima sangalephere kupita chifukwa anali ma friends
protect this man at all cost
Namiwa ur the best
❤❤❤❤❤❤❤❤
Zeluxanu anamiwa ndizonthandiza mulungu akusungeni
One day is one day
Iwe nde muthu
God bless you
Koditu Chakwera akuganiza ngati ino ndi 1801, akuganiza ngati tidakalibe ombwambwana. Koma zoona SKC anapita zoona 😭😭😭😭
Mr namiwa ❤❤ lumikizani madal khaniyi pak okuphay
Aziwik
Katundu namiwa
Keep it up Mr Namiwa
Olo ine pano mtima mmene ukundipwetekelamo 😭😭. Zoona SKC anapita?😢💔💔
Wakwiya ndithakati
Namiwa,,Be strong and energetic
Malume pitilizani tchito yabwino osaopa osafooka mulungu atimenyela nkhondo ife tili chete ambuye akuonjedzeleni dzelu zochuluka
Nàmiwa uli ndi nzeru
Iwey ndidor kwambir srs
Chofunsila mchizungu mchan pamene anzao akufunsa mchichewa
Ndinu munthu olimba mtima pitilizani
Sad😢😢😢😢😢😢
MCP ndimanyi komaso anthu akupha
Amalawi tiyeni tichose mawere makut tizankhare ngat nkhanga inu ahhhh😢 Rip charles kasambara and SkC😢 and namiwa plzz God bless you 🙏🙏
Chakwera is making a big mistake ...udzionera forensic file then you will understand...there was person amene amaona zonse
Kodi iwo amkaona ngat zatha basi mmene adapangira zimenezi
koma ndipo ukalozedwa sumanunkhatu
Bg mn good
Namiwa ndi akatundu
Kwayaka
😢
Wamtumbo dazinlako this this new generation 2025 nose adpp mumagidwa bas ife tatopa ndikuva zadege madzi akatayika sawoleka ukafa wafa kulibeso kubwelele or utalila chotani sadzikaso wapita bas ndiye usatuzuguze dazi lako
Chisilu iwe ukufuna chakwera apitilizebe kupha anthu ....kupusa sti
Mwaganiza bwanji kutukwa namiwa 😢
Mcp. Mumatha.
Munthu opusa iwe chifukwa chiyani umathawa thawi yofunika kwambiri. Zimenezo uzikauza ma bwana ako ku dpp. Iwe timayembekeza kuti uzikanena zodabwitsa uli konko. Wina akanena zodabwitsa nthawi yomweyo iwe kutiuza koma iwe Kewee ngati those. Aaa a freedom fighter a fake inu.
@@gersommalama iwe ngopusa kwambir fukwa suxiwa kalikose and u want to give us problems here get out
Iyi zoona ndi mbuzi
...ukusowa choyankhula apa ...osamangodya ndalama zokubazo bwanji zochokera Kwa chakwera ......Malawi muno ndiye muli mbuzi zambili
Iwe panyo... Siwunave zomwe anachokera? Akutuma eti galu
@akanamuphatuWilliamKawaza
Iwe nde ndi galu machende ako ndika chipani kako kakuphako nose machende amanu
Ine ndiye ayi ,bwanji munakama enquiry kuti muwauze anthu chilungamo,,,,mmafuna muziikamo mabodza anu,I don't trust you Namiwa,