I do follow you brother. What you normally speak comes out to be true most of the time. Keep on advising our leaders for the betterment of our beloved country.
Respect mr DC ndine Samuel go ahead mr boooniii kalindo am here in malawi from all the way RSA ndili ndi week am following you osaopa osanjenjemela ndi agalu
More fireee you and Tamia ja we are behind you🔥🔥
ndina ku sowana the DC dzulo bando ndinalibeeeeee big up mwana bon kalindo muma tiyimilila bwana wanga
I do follow you brother. What you normally speak comes out to be true most of the time.
Keep on advising our leaders for the betterment of our beloved country.
Umakwana bass bg mn go ahead ❤❤❤❤❤ ndipo aziooona tiri pambuyopo
Mwamuna iwee palibe amene angakugwenyeze iwee ndi pulezidenti wathu ife osauka palibe angakuopseze bon kalindo the Dc🎉🎉
We support you, DC kalindo. More fire
Respect mr DC ndine Samuel go ahead mr boooniii kalindo am here in malawi from all the way RSA ndili ndi week am following you osaopa osanjenjemela ndi agalu
Mr DC your are voice of voiceless,am always with you Comrade
My boss always, we support you
You are loved the DiiiiiiiiCiiiiii🔥🔥🔥🔥🔥
Dzikoli likufunika anthu ngati kalindo amuna awa aching ntanyiwa wa bakili muluzi TV embekezelani nyimbo imeneyi very soon from me
The DC Boooon Kalindo president wa aphawi Malawi 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
The DC💯
Dc 💯🔥
Nobody has stopp you is only Allah umakwana DC Mwenene
Viva Malawi
Keep it up dc
The great Bon Kalindo
I always listen to ur audios,,,,,,,you didn't insult Dpp,,,,you advise them
Exactly
🗣🗣🗣🗣🗣🔥🔥🔥
The DC respect
Big up bwana DC🎉
Kusa ganiza ndi kumene kumapangisa kuti azipanga zopusa zawozo ndipo adakakhala ena akanazivela chisoni coz athu tikudya chiteze ku Malawi
Ndinu big ndimakusatirani kwa. Bili km timagidwa a mbili zikomuno
the DC akatundu kumenya kugwesa chesaopa
Kkkkkk
😅😅😅ziliko liko kumalawi 😂
Excellent!
❤️🔥❤️🔥❤️🔥❤️🔥❤️🔥
Uzingobadula bs
A dpp mukuyeneladi kuuniko komwe munagwera tinakutulusani muboma chifukwa Cha mumene mumayendesela dziko nde be careful akunena zoona kalindo chifukwa chake ife tikuona kulibwino tiwoneko utm
Bon kalindo
Big hands to you bon kalindo
ugaru bwako mwana wamasikini
More 🔥
Tamutchulen ameneo timenye
🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Boss inu ndikatundu ndipo palibetso Mulungu akupaseni moyo wautali boss ndimadalitso palipose mungakhal chitetezo chizikha nanu palipose
Osaonesa kutopa komanso osafooka The DC
Or atakhala ma vote bwana DC mwaiona nokhatu APA mwawina kaletu
We are together the dc
Munthu akukulangizan chomamuyankhila nkukhala chaaa Malawi kwaculuka zitsilu kwambili
Mumakwana abg
Osamuyankha county man bwana DC ..ndikape ameneo !!!
The DC ❤
Machine
Mwana ataye amenewo ndipo uthenga uwu uwafikile anthu amenewo machendi awo, munthu omenyera ufulu sayang'ana mbari pofuna kulankhula
Dpp kukula mtima kwambiri
The DC ndipo or even me ndudabwa kt chilungamo nso is a crime?? Eee
Kkkkkk
❤
Nsalu Ya UTM ndi Ya UTM Ya UTM ndiyongolo
Koditu mcp dzikoli alitenga ngati la mawo koma 16 September ifika ndithu
we are together mr Dc Born kalindoh
Umakwana dima umadana ndikuunika
Kukwapula mr Dc
Mumakwana bwana
More fine mawa tikakumane komweko
Chimangacho ingolima chako, mankhwala gula iweyo ugawe mzipatala.
Akazi atatu sizinthu,kalindo udazungulira mutu😂😂😂
Iweyo ndi Chiwanda cha chakwera garu mapwala akoso pati
I silute you the Dc
Mbambande DC
Chilungamo kuwawa bwana dc
Adzudzulen chifukwa timawakonda a Dad ndipo tiwavotera molimba ntima
That's true DC
mbambande Mnyatha wanga
DC big man
Komadi anthu osauka tikuyenda ndimantha kuti kodi sitinamizilidwa milandu chifukwa akukhala kuprison achuluka anthu osauka Malawi what happens please
Ndiwe wamisala
Bon usazafe
Country man ndi chiweto chanji kod
Ife tili pambuyo pa Tamia
Ndimakape amenewo osalimbana nawo
Kkkkkkk born kalindo suzatheka
Ife timakondwera Nanu bwana ddddddccccccc
Malawi fest the DC zinazo pambuyo
The DCCCC
Pstsogolo ndi kalindo
Ndiyadzulotu audio 🔉 iyi
A dpp asinthe oimila chipanichi pamasankho
Amalawi ake ati?
Amalawi ake ati omwe umawayamkhulirawo,amakutuma ndani?
Malawi wake ineyo siweyo iwe ndichiwanda. Garu mapwala akoso pati
Zako zimenezo,ife phee!!,kupha khasu,tikugulitsani K5000/kg chimanga tikakolola
Ndakunvetsetsa mutu wako sumagwira, iweyo ukufuna utiuze kuti amene umalimba komaso kugwira ntchito ndiwe wekha mdziko muno? Mbuzi yamunthu@@JosephEphraim-j9x
Mumatiimilila
Kma mcp msatitenge ngati ndife oputsa
Team Bon Kalindo
Mumatha bwana dc
Yaku immigration nde waithadi pano athu sakutenga ma passport mpaka pano athu mvuto lomwe sakutengela ma passport sakuliziwa
Ngati ulibe mbali apa ndiye yr welcome on my side i can even now start to make donations on u ,cz really both mcp en dpp are both nonses ,wowononga.
ua-cam.com/video/iNqku7ivwZs/v-deo.htmlsi=A-A5EBcTbTvFlgeS
Kod amagozuka ndiku g\alura
Munthu wamkulu kwambiri
NACA yachimizi kutenga kuziwana bas