Malo moti ma foreigner ngati ali andalama azigulitsidwa Malo abisness okha kuti nyumba azipanga rent Malawi kuwapasa pokhala azitasa ngati alikwao maiko otizungulira rent yeniywniyi foreigner amafuna akhale ndi residence permit koma Malawi tulo
Koma inu a Chakwera choti mudziwe ndi ichi,dziko ili ndi dziko la democracy,si dziko la chipani chimodzi.Ndinenenso kunena kuti dziko ili ndi dziko la ulamulilo wosiyilana koma chenjezo ndilakuti tsiku ndi limodzi lomwe muzaone ngati kuti dziko lino lakhala ngati dziko la South Africa munyengo ya xenophobia.Dziwani kuti simuzathawa ndipo muzasanza magazi
We love you Bon kalindo ..Olimba mtima chonchi ndi osowa keep fighting for us poor people
Dziko la south africa ingakhale eni ake(mzika)alibe malo
Malo onse ndi aboma 🙌🙌
Ambuye zitidalitsirani presint wathu ndikumupasa moyo wawutali, the DC long life chief
Bon kalindo ...... speaking without no fear...❤❤❤we love you keep fighting for us
Bon kalind God bless you congratulations
You are strong MAN big up bro!!!
More fire Boni we're behind you
More love to you Mr Kalindo
Bigup Mr kalindo
DC ndidolo ndthu fire 🔥 🔥 🔥 🔥 🔥
He is crying for the country and fighting for poor people, may God protect you bro
Dzoona zimenezo awozeni Kuti panga talike bwanji lamulo lizawapedza kufuna osafuna
Mwana Wakwathu Ku Mulanje watulukilaso ndi chilungamoooo mulungu azikutetezani Kwa adani Boooooooon Kalindoooóoooo
Mwadzuka bwanji
Winiko mulungu akudaliseni chifukwa chomenyela anthu ufulu, kulankhula mosaopa
Power speech
Our president of poor pple speaking the truth without fear
Ukamuzonda Bon Kalindo , yembekezera kt atamwalire nda abambo ako akuba ndalama za misonkho m' bomamo. We love the DC😅😅😅😅😅 moto kuti buuuuu🔥🔥🔥🔥🔥🔥
❤❤❤❤❤❤karido Dc
Powerful speech fadah
Kaswili, born kalindo.
Powerful 💪💪💪💪
Best tv
Watulukiranso Mr DC president wa ife wosauka,Bonnnnn Kalindooooo The DC mwana oopsya kwambiri😅😅😅😅
Koma nde tisanduka North Korea via Zimbabwe tu...😢😢😢😢
Malo moti ma foreigner ngati ali andalama azigulitsidwa Malo abisness okha kuti nyumba azipanga rent Malawi kuwapasa pokhala azitasa ngati alikwao maiko otizungulira rent yeniywniyi foreigner amafuna akhale ndi residence permit koma Malawi tulo
Munsatope kutiyimirira bwana DC
Ndipo chilungamo ma foreigner kumakhala motakasuka kugula Malo motchipa opanda or ndondomeko ndipo dziko lophweka sinaonenso
Power speach mr kalindo
Tell them bro were together 💪
Bwana DC😢😢
Zona bwana Dc
Bwana wanthu ndinu
Koma inu a Chakwera choti mudziwe ndi ichi,dziko ili ndi dziko la democracy,si dziko la chipani chimodzi.Ndinenenso kunena kuti dziko ili ndi dziko la ulamulilo wosiyilana koma chenjezo ndilakuti tsiku ndi limodzi lomwe muzaone ngati kuti dziko lino lakhala ngati dziko la South Africa munyengo ya xenophobia.Dziwani kuti simuzathawa ndipo muzasanza magazi
Ulemu wanu bwana bon kalindo
Dc
The DC Tell them 😅😅😅 liyaliya
Big man timakunyadiran
You are very correct. Kukuoneka ngati tilibe unduna wazamalo and as if we don't have land policy.
Tsiku lomwe chakwera analengezedwa kuti wawina anthu anagona kunja kusangalala kuti tione zina zinthu zisintha osadziwa kuti akukondwera fisi weniweni aaa wakupha
Dats true
The DC❤
Mulungu akhale mbali yanu
😢we follow u brz
chilungamo bomalasonekela
Tembelero likakulitsa nkhutu ni mtima sidzitseguka. Too cursed to pick advice.
Osaonetsa kutopa Dc tinenereni
Kwanthele mboli yake
The DC
Kuli zinthu
😢😢😢😢
Kuyankhula mosaopa
You deserve thanks