I love you Mr kalindo , mfundo Yako yandigwila mtima. Ine Galimoto yanga anandilanda paboda akut ndipeleke 1.6 MITA koma chosecho ili ndi mapepala okwanila from south Africa south
Always he stand with truth and mulungu iwe azikudalisa ndinthu ,amalawi let's wake up ,nde imeneyo ya MRA ayi akuba anthuwa ,ukapusa kwambili osowa ndi transport yopitila kwanu katundu yonsenso atagawana agalu awa mamba lendee anthu kuathamanga kut adyeste ma family awo inu nkumaba, ta police tanonda akut a traffic amangokhalila kuimika anthu museu nkuwaimba timilandu topanda page, nde ineyo ndikunenesa simuzaudyatu yanga ndalama anthu aphulupulu inu
I love you Mr kalindo , mfundo Yako yandigwila mtima. Ine Galimoto yanga anandilanda paboda akut ndipeleke 1.6 MITA koma chosecho ili ndi mapepala okwanila from south Africa south
❤❤❤❤❤❤❤
DC always giving us hope and confidence..... keep doing the needful.🔥🔥
May good Lord continue protecting our speaker DC
Congratulations Mr Dc mumatipasa chiyembekezo chifukwa mumayankhula mosawopa wina aliyense ulemu wanu ndithu😊
Ulemu wanu bigy tlinanu inuo osaopa🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Loud and very clear sir, the DCCCCCC! mwana owoooophsya kwambiriiii!!!!
THE DC mwana woopsya kwambili ❤❤❤❤❤❤
Everything what you said always comes true that's why the government always hunted on you😊😊😊😊😊😊
Ndipo PA border akutibera heavy ku Malawi one day kudzavuta, tatopa ndikubeledwa
Ndripamodzi ndinu bwana boni kalindo my president wa 2025 ❤🔥🔥🔥💯
Keep doing fitting us am proud of you the DCCCC!!
Uyu angokhala president wadxiko ❤❤❤
More fire we are together
Awuuzeni ❤
The DC my president ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤💪💪💪💪💪
Mumakwana mr born kalindo
Ifetu timawoma ngat tidziendera limodzi pamacuto ndipa mtendele koma aaaaaa bara yachabe chabe iiiii amalawi musaelekeze akukudyeran masuku pamutu utuuu!
Miti yawo sikuyenda bwino😢😢
Munthu opanda chikhalidwe yakobo wake wakwajendatu
Malilo ndieno simumaliranawo ADC?
Ulemu wanu big
Good
The Dc🎉🎉🎉
Bon to Lead
Wooo mmmm kumalawi shaaa
I love you so much my president
DC de genius
Your Excellency Mr President Bon Kalindo
Number one DC
Program yazisilu zopanga comment
Chekwela mbuzi yamuthu
A opposition akumalawi ndi makape kwambiri kuti osayankhulapo mene anthu akuzunzikilamu
Olo mmodzi et!!! Malo moti bwez akutiyakhulira kumaletsa zinazi ngat malemya ayi ndithu koma akufuna tidzawavotere eti iwo sakutithanduzapo aaaa
akudikira kut wina aziwalakhulira
😂😂😂😂😂 koma iwe president waife anthu osauka
Koma a DC sakuyamkhulapo kanthu za manganya for a vice president.. Big whyyyyy?
Andiso ukunena zowona zokhazokha,,,,kukaronga panopa akulembetsa
Tili pambuyo panu biggy
Zoona the DC
Bushit really
Zaumbuli
The DC mwana owopsa kwambiri
Always he stand with truth and mulungu iwe azikudalisa ndinthu ,amalawi let's wake up ,nde imeneyo ya MRA ayi akuba anthuwa ,ukapusa kwambili osowa ndi transport yopitila kwanu katundu yonsenso atagawana agalu awa mamba lendee anthu kuathamanga kut adyeste ma family awo inu nkumaba, ta police tanonda akut a traffic amangokhalila kuimika anthu museu nkuwaimba timilandu topanda page, nde ineyo ndikunenesa simuzaudyatu yanga ndalama anthu aphulupulu inu
😂😂 the mwayankhula momveka
Malawi ndi dziko lanthh opusa kwambiri tichikhala ndi anthu 20% like D.C. bwezi mcp itatula pansi udindo
Bon Kalindo Mwana Wakwathu sopano mmatiimilira kwambiri ndizowonad zikoli tikunzunzika lili ziko lanthu,mulungu azikutetezani Kwa adani agalu A mcp
The DC bon kalindo 🎉🎉
😂😂timakunyadirani
Mwana ooopya kwambiri the DC
President Wanda wazigawengatu ayida mini uyu
The DC on fire
Like malema ❤❤
The DC muzimuvela analema kuchenjeza,
Long live in Jesus name 🙏🙏🙏
😊😊😊
may God protect you mr kalindo mumatiyankhulira
Nkhope chigawenga chenchen zoti ndrama imawongora nkhope ngat bodzaru
The DC mwana okwiya kwambili!!!!!!
Amalawi tinafasa mopusa
Mwatiyimilila boss ma venda tikudzudzika kwambili
Ali kumbuyoyo ndi body guard? Or Sing'anga,,, let me know plz
The DC ❤❤❤❤❤
Km apavnde tantha pasi 😢😢😢
The Dc katundu omanga ndi mawaya
Bigy Mumakwana dzoona
Number one
Mumatiyimira big man
Zimenezi ndiza serious or pa songwe boder akunyoza kwambiri anthu
Kip up bro
Aliyese akavota basi
The DC Bon kalindo president wathu 🙏🙏🙏
No 12 ndinkhumba kuzitchemerera sikwabwino
😂😂😂😂I can feel your pain bro zakupweteka kodi chilungamo chimawawadi kani ndiye uvatu nyunyunyu ase karindo ndi moto ase❤❤❤❤
@@MoosaChirwa zaziii akufuna kofera zikachitika muzinena kuti ndi Mcp zaziii atokota atopa
@@EmmanuelKatadzukacomedy Ndiye zoti mcp ndi yakupha ukuka
Ur special bon kalindo😅
Ukali kwambili booon kalindoo
Apule❤
Chakwelayu akuzuza a 13:55 malawi aaaasah
Malawi 🇲🇼 akupita kuti Please
Long live
Big up
Dc 🆚 bakili muluzi tv😅
Anthu awa mulungu wa kumwamba awaone
Big man
Kkkkkkk tikamanena kuti ma drug akukupwetekani,nanga 11 khumi ndi chiwiri (11)
Ndi zomwe watenga iwe, mutu ngati gwafa
😂😂😂Inu ngosokoneza
The Dcccc inu mmakwana
The DC
More fire we are together
Dc 🆚 bakili muluzi tv😅
Vs comrade Ntanyiwa🎉
@@TheresaKuluwembaMoto kuti buu
Dc 🆚 bakili muluzi tv😅