Soldier Lucius Banda the Malawi 🇲🇼 country shall shall never forget you. The history of music in Malawi can not be mentioned without Soldier Lucius Banda. MHSRIP ❤❤
I can't believe Kuti pa maliro soldier vice president Dr Saulos Chilima penalize anali ali malemu power pa 07 June anapita kukamuona Soldier kudos chipatala kudos South Africa imfa iweyo ndiwe chirsiru kobasi ndalira ine mosalekeza
This is so touching 🤦♂️
Last time to hear Jane's voice was at Check Point in Salima
Me, Jane and others we made a small circle nkumavina
Soldier Lucius Banda the Malawi 🇲🇼 country shall shall never forget you.
The history of music in Malawi can not be mentioned without Soldier Lucius Banda.
MHSRIP ❤❤
Koma mabala ndiye akupwetekadi . Mmmm that's my favourite song by Soldier "Mabala".
He was a great man, Soldier indeed he was ….bro you were a great Man
Eeeee l am out of words mmmmm this Mouth of June taziona big people just gone like that God help us May their Souls rest in peace 😂😂😂😂😂
So mwat mwakondwa
I can't believe Kuti pa maliro soldier vice president Dr Saulos Chilima penalize anali ali malemu power pa 07 June anapita kukamuona Soldier kudos chipatala kudos South Africa imfa iweyo ndiwe chirsiru kobasi ndalira ine mosalekeza
Eeeesh mwezi wa June mmm ai mavuto mmmm
I feel your pain Jane, Mulungu akutonthozeni ndithu 😢😢
Ndipo aunt Jane mhuuu💔💔💔😭😭🙌
She is being real
Mmmmmm sad, Lord have mercy
Pepani tonse tikulira, chipiliro mnunkha Cape,town.rest in peace.
Jane ulipo ? Mmmmm kusalima koma wanenepatu , sorry for the loss tikulira tonse
Ndasangalala kuku ona jane ❤ ukuoka fit pitiliza kuzisamalila sister, sorry
Ma Media Houses muziadziwa anthu anu, kumadziwa omutumiza ku function yanji...Si aliyense mungamutumize ku Function iliyonse... Zikomo.
Mmm zoliliritsa
Repose peacefully soldier.
Funso lanji limenelo? Anali ndan kwa iwe personally,usanayambe kuyimba? Ukufuna ayankhe kuti chani?
Usanayambe kuvina?
Et this is being unprofessional
May his soul rest in perfect peace doctor Banda😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Akuwoneka bwino Jane. Sorry
Koma zinani😅😅
Sorry Jane
Oh sorry MHSRIP
Wina aliyense alindinthawi yake ndithu tiyeni ziziyike mmanja mwamulungu
Pepani akumudzi.. Tikulira nanu
Imfa ndikapu yamadzi yomwe chamoyo chilichonse chidzalawa kapu imaneyi,komano kukhala ndi umunthu ndikuwawelengera anthu ena umasiya mbiri yabwino Lucias umunthu anali nawo,tengeranipo phunziro ochakwera posintha kuti anthu azasimbe zaubwino wanu sinthani
Kumakumbukila komwe wachoka
Tikulira nawe limodzi Mula
Abwino sakhalisa rip
Sorry sister be strong
Kmano kuliraku adaonjeza mpakana watsuka mamina
Zoonadi Jane wakhaladi naye
Zosaenda kwambiri 😢😢
RIP sir 😭😭
Sorry sister 😭😭
May God comfort you Jane
Pepan aunt jane😢
rest in peace 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
May his soul rest in peace
Rest well soldier
Zowawa
Rest in peace sir Lucius
S amadya momwemo
May the Saul of sir Lucius Banda rest in eternal peace
Pepani aunt Jane
RIP
𝑻𝒊𝒌𝒖𝒍𝒊𝒓𝒂 𝒏𝒂𝒘𝒐 𝒕𝒊𝒎𝒂𝒎𝒖𝒌𝒐𝒏𝒅𝒂 𝒌𝒐𝒑𝒐𝒔𝒂 𝒓𝒊𝒑
Koma zinani😅😅
Sorry jane
Rest in peace sir Banda
Rest well Lucius Banda