Michael usi ndi kape or akubomawa akuziwa kt alibe chikoka km popeza anasankhidwa as VP that's y akuluakulu aboma akuopa kunenapo kanthu km akuziwa kt uyu watha basi
Manganya ndi mbuzi ya munthu, chimene akulimbanabe ndi utm chifukwa chani? Iyeyi ndi chikangawa sakusiyana afune, asafune wachotsedwa apite akayambitse chipani chake apo ai apite ku mcp asatinyase..Chipani cha manganya ndi mcp osati utm awasiye a utm apange zawo ngati uli ufiti adzika adzikapanga ndi zache chikangawa.
Ndikape Usi,,, akuona ngati dzikoli ndi hall yoti akupangamo sewero,,, akagwere uko sitikumufuna ku UTM mthira kuwiri uyu.
Mutu siukugwira usi.... ndipo ndi oipa ndithu
Aaaah inu manganya akukhuzidwa ndiimfa yachirima uyu
Manganyatu zip wamupani😅
He knows what he is doing.
Ayi asamagwilise makaka a UTM
Sizoona za ndalama,amutuma kusokoneza masuppporter a utm,it's a strategy yanoma imeneyo💝
Strategic plan ya chakwera,nchifukwa anusankhanso kuti apitilize u vice president manganys ndi munthu oipitsitsa.
Abwelele ku Tikufelanji basi tiyisowa😂😂😂ndale ndizazibambo osati Ausi
Apite kwa mbale wake chakwéra amupase udido wona asiye UTM wopusa alubalalitsa anthu
Usi akudziwa chomwe akuchita Ndipo amatha kuwerengera bawo uyu. Pandale osamadelerana
❤🎉
Waesangati akupanga masewelo amenei ndiwausilu
Usi akupanga ngati munthu wamisala kwambri and ufiti ulimoso akufuna kusokoneza ku UTM then chosecho iyeyo adalowa MCP bwanji uchotsilu umenewo
Madocument agwile tchito bas khani yatha
Ausi ndi opepera zed kd ngat akuzimva kt angalimbe pa ground akadangoyambisa chao chipan mamembala ndi omwe akuwatsatilao bs
Buli iyinso ndiye yati kwana bwanji kodi osamango pita ku masewero basi ku UTM kulibe chake
Utsi weed ndi syisya amakoka kwambiri,akukakamira chiyani ku UTM azingodya nawo ku MCP ,azolowera kukhsla ndi zinyama, ndiye watenga khalidwe lanyama.anampatsa unduna woyang'anira nyama anadziwa
Usi ndiukila ameneyo
Manganya is using his power of vice president for dividing UTM ,
This is happening from the sponsor of mcp.
Ausi alibe chikondi, ndipo ndiosokoneza kwambir, lye sakumvetsa pati, Kukomveshoni sadapiteko, sadalipile ndalama, lero azitenga gulu mkumalipatsa makaka a utm, Ufiti kwambir mmm, angovomeleza basi, ndikudzichepetsa ndikukonda azitsogoleriwo, Mulungu amukweza, Sure ndithu.
aliyese,amene,anapita,kumaliloko,anayendetsa,nao,mwambo,wamalilo,km,zandalama,alongosole,kupanga,nao,mwambo,sindiye,kt,,adatenga,magawo,onse,,
Usi amaona ngat Chilima akamwalira iye ndikukhala VP ndie kut akhala president wa UTM ndipo kut atenga chipanicho ndikupita nawo Ku MCP. Joker wamufera m'manja, zomwe amafuna zakanika.
UTM yikanangomusiya kape uyu nthawi yake yatha kale. Cabinet yikangothetsedwa watha uyu. Kulira uku paja njoka ikamafa Malinga awa tsopano.
Usi ndiwozunguza chonchi kumpasa u pule dziko lingayende? Ngati Ali dolo azitaye za UTM apange zake though tamva zoti akhala presdnt wa umodzi party😂
Moyo wake was usi kaufiti kalipo ndithu muzakhulupirira kuti za imfa ya chilima
Usi sakudziwa zomwe akuyakhula
Kd galu ameneyi usi akufuna chani
A Usi ndi opemphera poyamba aganizire lamulo la chikondi,
Usi akuwonetsa mtima osava ndikusamalila maganizo azawo akufunabe kuti azikhalabe ndi mcp
Kodi chipani chiliko munthu wongochoka uko ndikuzakhala musogoleli apapa autm sanaganize ngati amapanga zodana ndi usi lelo ndi izi zikuvuta aziona azawo ku dpp or mcp munthu amakhala pamamupando atakhala zaka zambili muchipanicho koma utm iiii zizikhala zikuvutabe onani akaliyati zinasokonekera ndi azawo ose no mupando ndiye chipani aziyendesa ndi achitendo okha?
Michael usi ndi kape or akubomawa akuziwa kt alibe chikoka km popeza anasankhidwa as VP that's y akuluakulu aboma akuopa kunenapo kanthu km akuziwa kt uyu watha basi
Awa ndale alinazo chilendo.atha awa basi
Mumuuze usi mboliyache machende ache asewele yake not UTM party
Munthu uyu Usi siakudziwa ndale komanso munthu oipa mtima wabalalika opemphera onama
usamakjale,ngati,ukukhoza,kulankhula,pamene,ukubisa,anzako,amene,adadya,ndalama,zo
Achoke
Manganya ndi mbuzi ya munthu, chimene akulimbanabe ndi utm chifukwa chani? Iyeyi ndi chikangawa sakusiyana afune, asafune wachotsedwa apite akayambitse chipani chake apo ai apite ku mcp asatinyase..Chipani cha manganya ndi mcp osati utm awasiye a utm apange zawo ngati uli ufiti adzika adzikapanga ndi zache chikangawa.
Ndiopepela usi angovomeleza azake apangeposo
Chilipo chikumusata satana yu chomwe ukufuna uchipeza wamva dziko lolenga Mulungu ili mr.Betrayer
Inu amanganya azanu akachosedwa amakayamba chipani chawo kd inu vuto ndichan mesa mkt muli ndi maspoter ambiri km oyamba siinu kuchosedwa aaa
Kumenyenitsa anthu otsogoleli sakuziwa
Mfiti iyi yompha chilima chifukwa cha udindo
Usi a kadi vin a ukoo asatibowe ameneyi mwamva eti
Akudalira boma kape
First comment
Kodi akusowa munthu oti atha kumukuntha manganya?chifukwa nde wafika pokwanatu
akat,mwambo,wamalilo,sizikukhudzana,nindalama,zomwe,akunena,usi,musabisale,,
kapeee
iweyo,usawayankhile,anuwakeo,alibe,pakamwa,kapena,udadyanao,,anzakoo,adadya,ndalama,zapamalilo,
Usi akazivina uko asatibowe etu
Angolongosola zandalamazo
Dolo la madolo onse ku UTM ndi usi basi
Chikangawa iwe
Yudas ndipo ndiwe satana weni weni
Mizimu ya anthu 9 ija osaipwekesa yayamba kugwira ntchito yake apenga ameneyo musiyeni
Kuri khondo kumeneko
Wachamba usi
😅
ingopelek