KWACHEMA VICE PRESIDENT MICHAEL USI KUBWEZA MOTO | LERO WAVALA UNIFORM YA UTM |

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 18 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 24

  • @MapetoZwaneboy
    @MapetoZwaneboy 2 місяці тому

    Momwemo salute madam merry chilima🥰🥰🥰

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 2 місяці тому +1

    Nkhani ndiyoti muli ku utm kapena mcp sankhani chimodzi bwana utsi

  • @AndrewKadammanja
    @AndrewKadammanja 2 місяці тому +3

    Palibe amene abwere kuzakambilana nanu bwana pangan zanu zakubomako ife tikupanga zachpan full stop.Tanamuona ife Chilima was a vice president kwa peter Muntharika km anachokamo ndkuyambitsa izi mukudyerera inu leroz kupanda Chilima bwez muli ndan a Michael Usi,am not happy with you Michael Usi and am not differentiate you and Judas Iscariot 😭😭😭😭

    • @ShillahChisi
      @ShillahChisi 2 місяці тому

      Ndipo chilima anawaika pa boh anyway uniform ikuwakhala

    • @ShabaniKuswere
      @ShabaniKuswere 2 місяці тому

      Mukadzazindikira Kuti mukulimbana ndi munthu osalakwa komaso okonda dziko lake,zoti Kaya pachipanda Chilima bwezi alindani kumeneko ndikulakwa komaso chipongwe chachikulu chifukwa palibe anabwera pampando waukulu Ngati umeneu payenkha,olo Chirima popanda Mutharika anali palibe.tiyeni tikondaneni ndife amodzi.

    • @AndrewKadammanja
      @AndrewKadammanja 2 місяці тому

      @@ShabaniKuswere inuso kaya akutuman zanu zmenezo ine ndanenandanena bas iyeyo apange zakubomako ife tkupanga zakuchpan full stop

  • @zondanitzulumusicfly.5202
    @zondanitzulumusicfly.5202 2 місяці тому +2

    Mr mthiko, usi

  • @YamieManda
    @YamieManda 2 місяці тому

    Enanu bachedwani boma likupita citsogolo

  • @peterkakhome6976
    @peterkakhome6976 2 місяці тому

    A vice president ndi a Richard chimwendo Banda osati inu

  • @IdaMasonga
    @IdaMasonga 2 місяці тому

    Zoona bwana VP nkhondo siimanga mudzi

  • @OliverChimsewu
    @OliverChimsewu 2 місяці тому

    Amicheal usi simuli serious ndi utm ayi,inuyo ndi wamcp,musamanamize anthu.bwanji dimumapitanawo anzanu kumene akupangisa misonkhano misonkhano yachipani?

  • @HopesonLyman
    @HopesonLyman 2 місяці тому +1

    Masapota omse ali apawa sia Utm ayi angovekedwa makaka ndipo ngongole akufuna anthu atengezo akufunapo ma ID kuti akhale ngati avota kale

  • @josephkafupa
    @josephkafupa 2 місяці тому

    Makaka a chipani ukavale pano? Mesa umangoenda oosavalaza utm

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz 2 місяці тому

    Munthi olakwa amatero, guilty conscious ikumumenya mamganya anagulitsa bawana ake a Chilima maka kukakumba nsewu asanamwalire kenako ngozi yan denge.... Manga nya ndi mfitiiiiiii

    • @shadreckphiri1799
      @shadreckphiri1799 2 місяці тому

      You are right. You can easily tell that he is very guilty.

  • @MustapherLino
    @MustapherLino 2 місяці тому

    VP opanda mfundo

  • @Jasonnyatwa
    @Jasonnyatwa 2 місяці тому

    Osokoneza wakupha

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus 2 місяці тому

    A Michael Usi
    Kodi muli ndichidwi chofuna kudziwa chomwe chidapha chilima...? A MCP ndi oganizilidwa kut anakonza chiwembu...nde inu simukututumuka nazo mwangot phati konko....nde UTM yeni yeni osati inu a yudasi ikufuna kudziwa zoona zeni zeni
    Atamwalira Malamu Bingu ,Joyce Banda anali kalikiliki ngat vice wadziko .Chodidabwitsa ife a malawi ozindikira ndi chakuti inu chimwaliliren Chilima munangokhala chete monga mmene adanenera wa Bakili muluzi kut akulonjezani u vice .Nde lero mufuna muzichuluka nzeru kuonetsa ngat munthu wabwino..what a shame and selfish..Amalawi akubwera pafupi ndinu nchifukwa cha umphawi ndalama mukugawanazo km zamumtima nzawekha...They can't vote for you...

  • @Drmuhammadchiwona
    @Drmuhammadchiwona 2 місяці тому

    Kungo waveka nsalu basi zausilu wti

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 2 місяці тому

    Kodi ka kaliati kakuti chani?

  • @MustapherLino
    @MustapherLino 2 місяці тому

    Galu wachabe manganya

  • @peterkakhome6976
    @peterkakhome6976 2 місяці тому

    Bodza

  • @frankiechasokoneza5802
    @frankiechasokoneza5802 2 місяці тому

    This guy is useless
    Firstly: since the death of Saulos Klaus Chilima's death he didn't make any statement as concerned

  • @MatthewsJohn-kv8fj
    @MatthewsJohn-kv8fj 2 місяці тому

    Wakupha iwe ndi chakwera wako mulomo ngati full you're sheet