ZOMWE ZACHITIKA VICE PRESIDENT MICHAEL USI ATANGOFIKA KU PHALOMBE LERO

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 18 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 24

  • @rexphiri7242
    @rexphiri7242 2 місяці тому

    Ena sakusangalalawo sanadye

  • @EuniseMasuku
    @EuniseMasuku 2 місяці тому +1

    Ai zikomo muzaziona

  • @JuliusChinangwa
    @JuliusChinangwa 2 місяці тому

    Mr vip phalombe is suffered district all passed government migowi to Nambazo no good road mr minganjira pass our massage to our president mr chakwera

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 2 місяці тому

    Ovina ake ndiye mwalipila ochepatu bwanji, change chinatha?

  • @CollinsMwale-l4p
    @CollinsMwale-l4p 2 місяці тому

    Mmalo movala makaka a mcp akugwiritsa ntchito za UTM zamanyazi

  • @ophlexmkondowe8107
    @ophlexmkondowe8107 2 місяці тому

    Wichita kugulidwa awa kkkkk😅😢😂

  • @CourageSydney
    @CourageSydney 2 місяці тому

    Achewa aliyese ndi yoweyooo munakhala bwanji ndi manganya wa MCP kumuvinila

  • @DeliaKaduya
    @DeliaKaduya 2 місяці тому

    Kuchititsa manyazi anthu anga, mphamvu zodukulirazo mukuzitenga kuti? Kukondwako kusonyeza kuti zinachitika ku chikangawa zija inu munaiwala? Anthu omvesa chisoni inu 😢, rest in peace SKC😭😭😭😭😭😭

  • @edsonkamba3170
    @edsonkamba3170 2 місяці тому

    Dr Michael Biziwick Usi VP has two hearts from the whole of last two weeks in Blantyre, Mulanje and. Thyolo he was preaching to the youths not to praise politicians and the youths and women should not be used as dancing objects but should be busy making money and now he who said those words is allowing the same to happen on his road side rallies.

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 2 місяці тому +1

    Manganya ukulakwitsa kugwiritsabe UTM yet unachokako, man , use MCP or odya zake alibe mulandu.

  • @MtenjeHassan
    @MtenjeHassan 2 місяці тому +1

    Azimayi mukamalza kuvinako muzikagona ndi njala,wat a shame

  • @TimothyKabumbuKendrix
    @TimothyKabumbuKendrix 2 місяці тому

    Komano ndi chifukwa chani akuyankhurira ali mu galimoto? Mantha kapena kunyada

  • @AmosScott-z9x
    @AmosScott-z9x 2 місяці тому +1

    Aphalombe amzanga mutichitisa manyazitu😊

  • @ElizabethKazambwe
    @ElizabethKazambwe 2 місяці тому +1

    Bumphawi sizinthu

  • @saidimwanyali8969
    @saidimwanyali8969 2 місяці тому

    Azionela okha

  • @lacksonsiyadi943
    @lacksonsiyadi943 2 місяці тому

    Ndale nd bzns apa manganya ali kokawoda mavote 😢😢

  • @douglastholo390
    @douglastholo390 2 місяці тому

    Mr. Ussi please stop wasting taxpayers money. It is as if you are celebrating your boss's loss of life. Time will judge you mapwiya wanga.

  • @ArnaldoMtawanga
    @ArnaldoMtawanga 2 місяці тому

    Ndichifukwa chianti vice president akuyenda yekha? Kapena alibe mkazi?

  • @kennethkaunda3636
    @kennethkaunda3636 2 місяці тому

    Kundichititsa manyadzi

  • @MisheckKamwendo-w9n
    @MisheckKamwendo-w9n 2 місяці тому

    Uphawi sizithu

  • @MachesoSamuson
    @MachesoSamuson 2 місяці тому

    Anthu aku phalombe muli ndimanyazi koma

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus 2 місяці тому

    Idyani ndalamazo ndi zathu...osakavotera MCP mwamva😅

  • @FrancoKaunga-rq2ki
    @FrancoKaunga-rq2ki 2 місяці тому

    Koma galu uyu akuti chani makamaka? Zinazi umangoti waziyambadala manganya the spirits of nine people are waiting for you and chikangawa.