Zomwe Ndikambe Za Ku Chikangawa Pa Social Media Panunkha Mphira - Ben Longwe
Вставка
- Опубліковано 6 лют 2025
- On Nyasa VoiceBox, Ben Longwe offers his opinion on what may have happened to Mike Alpha Foxtrot - Tango 003, the Dornier 228 that crashed at Chikangwa, killing Vice President Saulos Chilima and 8 others.
Pa Nyasa VoiceBox, Ben Longwe akupereka maganizo ake pa zomwe mwina zinachitikira Mike Alpha Foxtrot - Tango 003, Dornier 228 yomwe inagwera ku Chikangwa, kupha Vice Presidenti Saulos Chilima ndi ena 8.
#malawi
Fact Check: Ben Longwe claims that the Malawi Defence Force (MDF) suspended the search and rescue mission. This is not true. It was the Malawi Police Service that suspended their search and rescue mission. The MDF, under orders from the MDF commander, continued the search throughout the night. This information is available on page 42 of the Commission of Inquiry report.
Onani Zowona: Ben Longwe akuti gulu lankhondo la Malawi Defence Force (MDF) lidayimitsa ntchito yosaka ndi kupulumutsa anthu. Izi sizowona. Apolisi a Malawi ndi omwe adayimitsa ntchito yawo yosaka ndi kupulumutsa anthu. A MDF, molamulidwa ndi mkulu wa MDF, adapitiriza kufufuza usiku wonse. Zambirizi zikupezeka patsamba 42 la lipoti la Commission of Inquiry.
Which commission of enquiry?
@ COMMISSION OF INQUIRY INTO THE AIRCRAFT ACCIDENT
INVOLVING A MALAWI AIR FORCE DORNIER 228 (MAF-T03) AT
NTHUNGWA, NKHATA BAY ON 10th JUNE, 2024
Nkhani ndiyoti Boma linatseka kufufuza ndege kusiya ana ayeni mtchire
Kd kuifunda mcp uku kut kumene asirikali anafufuza usiku onse chomwe tikudziwa ndichoti kufufuza kudaimikidwa that's all
Most welcome sir now u r really Malawian
A Ben longwe pitani muzikabandila chimanga uko, mukuoneka mwasowa kolowela 😂😂😂😂, ife tinakutulukani kale kale
Well come back
Wel come back
Aaah akupempherereni ndani inu anzanu tu analorera kuika mutu pa njanji achina Namiwa kuimilura mw aaah tinakutulukani
😂😂😂😂zaziiii unali kuti àaaa
Ben apapano ndiye wabwera monga mwakale muja osati zija umapangapo pakatipa
Ati kufuna kuoneka ngati munthu wa nzeru, garu wachabe chabe, pano ndalama zatha
Kodi tindalama tija anakupatsa a Mcp aja tathano eti..
Bola ukudziwa chilungamo unali kt chilima adafa sunafune kunena zinsisi kt asakwere denge munamupha apa ukufuna uzioneka ngt wabwn watumidwa nd mcp iweyo atakupasa ndlama zakuthera wasowa zochita amalawi tisankhulupilire ben longwe nd kazitape
Ukamba relo kale unalikuti ulakhula zimenezo ndalama zakuthelani
Kd mwana olowelera uja atafika kwa makolo ake anamukana kapena anamulandra??oky ngt alipo akumsaka wina achdwa nazo koz moyo wa aliyense uli manja mwa Mulungu full stop.
Nthawi yonseyi unalikuti? Tamakaotchani makala.
Katha kandalama kaja
A Ben longer ubilimankhwe ndi umene umawavuta amawanyiza ma activists anzawo ndiye pano akuonana beanji ndi anzawo??
Ben longwe wachila basi mutu wake wayamba kuganiza bho
Kodi iweyo unali kuti pa nthawi imene comission ija imaitanitsa ma umboni kuchokera kwa anthu? Iwetu ukuyenera kuti udzipemphelere wekha
Tinkava nanu kukoma inu muli ku SA munkayakhula zenizeni koma pano aaaa mbola
Mu phesa anzanu Ada
Awa ben longwe ndi ausilu
Maluzi awa pweteka awa
Benlogwe mwabwelamotu bwino coz mau anu pakatipa amalephela kutuluka bwino kapena kumveka bwino mcp imaononga sogolo lanu komaso la amalawi abiri coz mumalakhulila aphawi ndiophinjidwa zikomo
Achisilu awo kusowa zonena
Nthawi yonse adali kuti ngati akufuna ndalama zamuvuta zimenezo zilibe ntchito kuwatola a Malawi
This reference is fake just to defend the lies and don't forget that lies shall always be lies even if you can polish it up ndipo ifeo we're to tell you that maso anu sakuona patalî ndipo we want to tell you Kut go and do extra research bcoz this one is not qualifying.
Kodi mukakawafwala akhongolesi aja eti
Ben longwe dollar yata mufuna kusizimutsa Chakwera akuitaneniso kachikena 😂😂😂😂😂
Nthawi yonseyi a alikuti kwacha yawavuta awa
Wasala Dan LU
Zauuma zomwe anakuninkha zija kupusa😂
Sizikupindulilani inu that is zachamba eti kungovuna koononga kaganizidwe ka anthu basi iweyo unali kut aaa shame on you