Kodi Ku DPP Vuto Lanu Ndi Chani Kukakamila Munthu Wamkulu - Samuel Lwara
Вставка
- Опубліковано 6 лют 2025
- Today on Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara is question why the Democratic Progressive Party is so adamant in keeping Professor Peter Mutharika s its candidate despite his advance age.
Lero pa Nyasa Voice Box, a Samuel Lwara akufunsa chifukwa chomwe chipani cha Democratic Progressive Party chikuwumirira kuti mtsogoleri wa Prof Peter Mutharika asamuyimire ngakhale kuti wakula.
#malawi
Apm my vote
❤
Nzeru ulibe ndipo malangizo ako kutsogoloku adzakubwerera pafupike patalike ngati wasowa zolakkula ingosiya ndipo uyambe kupemphera dziwa kuti mulungu wasunga mau ako
Kabambe sitsogoleri wabwino
Kuvotera Kabambe kuli ngati osakavota
Atupele Muluzi my Vote
APM it's my vote omuwopa mukuchuluka APM Boma 💙💙💙💙💙💙💙💙💙 ☝️☝️☝️☝️☝️☝️
Atupele Muluzi my Vote
APM my vote
Unkaoneka ngati woganiza koma ndiwe kape otheratu page yakoyi wainonga ndi audio imeneyi .koma uli agogo ako iweyo .kwanu kulibe okalamba ?iweyo ndiwe munthu omvetsa chisoni ndipo mulungu akukhululukire .sunga mau awa
Ndimakuona ngati wa nzeru poyamba koma ndiwe chitsiru cheni cheni
Ndipo iwe lwala upenga misala ife ndivoter Apm mufune musafune Apm akulowa😂😂😂😂😂munya in
Ndipo ndkukavotera APM 😅
Okanika ndi aMalawi .Koma Boma ndilomweli ..Mcp sitikusintha .wa 90 years akagwere uko .
Ndpo modzi mwao ndineyo okanika aise ndpo Peter or atakhal ndi zaka 400 koma vote yanga kwathu komse Peter tkachonga or akuyendera wheel chair or drip ii pamkono koma hahahahaha Peter basiiuiiiiiiiii or atakhala ali bokosi
Iwe lwara ndiwe opusa kwambiri, komaso iweyo siwe wa utm, ndiwe wa mcp timadziwa, umazitenga ngati ndiwe wanzeru kwambiri kuposa onse
Age is just number but we need experience how to run government so keep quite
Aaaah za ziii ukawafunse Ambwiyako fotseki tamufuna APM ndife osati iwe dont talk nonses.
Luwala panga chako chipani uwauze amalawi akakuvotere
Chifukwa nyamata ndi chitsiru nthawi zonse monga uja analonjeza koma osakwanirisa
Iyeyo ndichifukwa chani Ali ndi makolo ake akulu osawapha bwanji
Ndpo iweyo ukunama Peter or akanakhala zaka 400 komabe ndi votee yanga kwanu ngt kulibe nkhalamba zili kwanu komweko
Tikuonamu ubwino mwankhalambamo akulu musatiuze zochita ovota ndife
Are encouraging de parties not to have alliance??? den u jst pretend coz u knw our president kabambe payenkha sangawine no doubt abt dat
Nawe wasowa zochita
Wamkuluyo siMunthu??
Chitsiru chamunthu
Wamwa mtonjani iwe