Samuel Lwara Is Just A Noise Maker - Comrade D Phiri
Вставка
- Опубліковано 6 лют 2025
- On Nyasa VoiceBox, Comrade D. Phiri says that people should disregard Samuel Lwara’s comment on APM’s age because Samuel Lwara is nothing but a noise maker.
Pa Nyasa VoiceBox, Comrade D. Phiri akuti anthu anyalanyaze ndemanga ya Samuel Lwara pa zaka za APM chifukwa Samuel Lwara si kanthu koma wongopanga phokoso.
#malawi
Ndipo zowona alwala masiku ano akunyoza kwambiri inenso ndawatuluka akusokoneza kwambiri
LWARA ndi member wa UTM
Nde tizikumbukira kuti chipani cha UTM ndi Chipani cha anthu akatangale akamwa,okonda kunyozana azawo
Koma Kabambe sitsogoleri wabwino komanso sakuyenera kukhala vice president
Lwara ndimamukonda kmno adayamba mbwerera ,mwayankhula bwino comrade.
Ndipo zolankhula zake ndi za ziiiiiiiii zopanda mchere.
Lwara ndipo ndi kuti ndi chitsiru cha mzibambo chopanda nzeru ndi chadyera kodi lwara amazitenga ngati ndani chitsiru ameneyi nzeru zopusa zake asake kopangira osakhala kuno ku Malawi zikuvuta usowa kokajiya wanya
Chilungamo chimawawa. Let all parties stand paokha, peter wakalamba and thats the reality. Zodabwitsa mzakuti amene mukusapota pitala ndi achinyamata kodi ndekuti achinyamata muzingoonbera manja nkhalamba? Aaaaah hate Lwara the more you can komano zoti pita wakalamba ndizoona. Do you want to tell malawians kuti amene angalamule ndi nkhalamba basi? Ndipo Lwara wayankhula bwino kukalambatu sitchimo ndi mdalitso ochokera kwamulungu. Retirement age m'boma ndi 60 yrs and peter is heading to 90 years amalawi tikufuna chani? Utm singaberekedwe ndi mkhalamba.
Komansotu iyeyo akupita kumweko kugogoko
Kodi iwe Samuel mesa umamulangisa kabwira thawi imeneija atanyoza apm ndipo unapeleka chisanzo chomcheka bwino
I can see more from your accent but what Lwara says is right. We needed to find a younger candidate
Ife a utm tikagwirizana ndi sam lwara amene mwakwiya ndinu a dpp ndipo musova. Mkhalamba ayi period. Lwara keep the fire burning. Lwara sanatukwane wayankhula zoona zokhazokha
Ndie utm ingawine payokha?
@@LevieMwanayayapamenepo
Lwara ndi munthu wopusa kwambili ineyo ndinasiya kumvera ma audio ake
Sam anathawa ku mcp ndiye akufuna asokoneze kabambe chimene mungaziwe kabambe sangawine pa yekha
A lwara ndi munthu woti zoyankhula zake saziwika kuti Ali mbali iti ......a lwara siyani kuyankhula za dpp
Samuel Lwara ndi wanganyu wa D Kabambe ojiya anamuthamangitsa ku MCP
Lwaala akunena zoona bridge yakutha ayi ingagwetse wanthu pitala ayi akapume
Kabambe ayenela asogole ngati pangakhale mugwilizano kuti athandize malawi osati kuthqndiza zipani akunena apayu ndi mbuli yothelatu
Zikomo pomuyankhu ameneyu amaonjeza ine ndinasiya kumvera ma odiyo ake
Samuel akunena zoona osanama peter sangathandize amalawi analephela kale komaso panopa wakalambisisa bwanji ku dpp asankhe achina suleman ayendese malawi osati kuyendesa dpp.koma vuto amalawi timangosapota zilizonse vuto umbuli
He is just a noise maker and nobody
Wadya fodya wakupoto ameneyo ndiopusa
Panopa tikufuna musogoleli woti akhoza kuyendesa dziko osati chipani ndiye dpp achina chisale azatipweteka kutibelaso ndalama tatopa nawo a dpp mbava
Pita muthanyula ndiokalamba
Ndipo comrade D Phiri mwamuyankhula bwino nkulu ameneyu wayankhula mosefukira kwambiri, kutheka kuti anadya Fodya
Samuel lwara ndi kabwira amaganiza modotha
Mwinanso Lwala ndi Kàbwira amapakulana 😂😂😂