Kulibeko zosakana apa, this song was composed and recorded before all these assassinations of vp happened and messages in this song are clearly without insulting anybody but facts. We are not scared even afraid of anybody. Special messages to the composer my boy Frances keep it up for your good work.
Mtima wazako ndi sidya Lina, ndiwolose kakutafune 😭😭 a Joyce Banda ndi azimzanu mwamuphesa mwana ndinu amene mumamukopa kuti achite geirizano ndi mbali ya akambukuwa. Enoch chihana ndinu amene munamupangisa chilima kupanga gwilizano ndi afisiwa Lelo mwana ali mmanda pomwe Inu muli kunjoya ndimabanja anu okay Koma mukuyenela kumenya nkhondo kuti uyu nayeso achoke pa mpando a Timothy mtambo mumve komwe muliko
Woow what a good song .. this song deserve to award
I'm telling you brother he deserved to get award for this song but you know malawi 😢
Mwalo mwa award amangidwa😭😭💔
@@tyrachiumia3681Zoopsa zedi mmm
Kulibeko zosakana apa, this song was composed and recorded before all these assassinations of vp happened and messages in this song are clearly without insulting anybody but facts. We are not scared even afraid of anybody.
Special messages to the composer my boy Frances keep it up for your good work.
He's my favourite brother ❤❤❤
Yaa that's great songs , palibe zomalozana zala apa yaaaaa❤
@@WillmotChiuimia-vr6ouNdipo koopsa zedi boss
Its all facts only koma poti boma li limadana ndi chilungamo pajatu
Very well said brotherman 😍😍
This song it's very good hope wayivela kale iyeyo
Wow! What brought me to this song? My time not wasted
chilombo pogwira ntchito ndimanganyayu
I cried listening and watching this song
😢 😭
God have mercy on our nation
Ndipo asati mitu gwaa, Atiyankhe basi. 😎😎😎😎😎😎😎😎😎👍👍👍👍👍👍👍
This song deserves award this year
I have been listening to this song for the whole day
Ndiwetu galu kwa basi chakwela udzikalamulila banja lakotu osatitu ifeyo mayazi Allah Akbar 😅
Mfana adzatisaka ambiri pachilungamo koma mmmm enafe ndinyimboyi mmm yabayiratu mawu tiribe .
Kambani inchipotiquizi ena ave
Ambuye ndinu mwini kulanga ndikuweluza. Please mumufikire chakwera aliko mumuzindikilitse mwazi wanthu 10 ataya miyoyo yawoyi mwazi wawo ukhale pa mutu pake
I love this hit guys big up bro
Nice composition well done boy
Evance and your producers u are so genius to the core,this piece drops tears from my eyes, it's tough to be a Malawian during this week in particular.
Which Evance???😢😢😢😢😢😢 This song it's for Francis Jameca bro
😭😭😭😭😭 its indeed a bitter pill bro & it has even touched us beyond the borders of Malawi. We're mourning with u
Penapake ndi bwino kukhala chete ngati sukudziwa.
Mwaza malume keep it up mmmmmmm ma gens adaa awawa ali fire chan!!!
Joyce Banda sakonda Malawi ndipo ndi munthu Oipa kwambiri, anangokhala ndi Dumbo chane😢😢
Mfiti ijaa brother
ndi momwemo ndithu esh mayi aja Dumbo basi
Km
Wayimba panthawi yake mulungu amudalise
Beautiful song ❤
Mwapita basi akulu tidzakupedzani basi koma mwatisiyira mabvuto omwe inuyo munawapanga
Brother mwanena ngati mmene ine ndanenelanso muli ndi mnzeru chongodandaulitsa ndi choti wamwalira ali muuchimo basi
@@MarthaJafalimwaweluzatu brother
God is watching
Nice song ndipo idatuluka sanamwalire
Nice song brother, nthawi zina 🌶 chimakhala ngati mwano
Wow❤❤ amazing song
I can give it 💯 🔥
Wow, this song deserves some recognition from the activists it kind of tarcoz the vital corners of our dying political landscape in the county ❤❤❤
Nice song ......... osaopa man ife tili mbali yanu palibe chitachitike
Am very impressed with this song
More fire alliance
Some times we shud think where we are coming from
And see where we are going to 😢😢😢😢😢😢😢
Nice song akumusaka Kut watani nyimbo ayamba kumvera yoyimbidwa bwino pa Moyo wawo ndiimeneyo
Ndipo mmmm
Walakwisa chani? Zonse zilimunyimbozi mesa ndizomwe zipa ground,,wayimba bwino zed
Chakwla nfit safuna kuva chilungamo
Awa sazatheka zimene amapang kumpingo kuja pokakamila pampando angakhale zimavuta zimakanika lelonso akupanga chimodzimodzi , lelo ndi awa akupwanya panganolawo ndidyela
Wow!!!! What a sweetest song❤❤❤❤❤❤❤❤ keep it up brother mbambande zedi eeeeee chinyimbotu mmmm❤❤❤
❤❤❤❤ mwana wakwathu kuntchewu uyu amayimba zenizeni ndipo ayelekeze kukamumanga akaphwanyidwako uyu nde namalila weniweni proud of fj timakukonda
Anyamata apa town kuyibongetsa
Fransis Jomeca ndioyimba owopsa waluso zedi poluka nyimbo komanso creativity ❤❤❤❤❤
My brother Francis Jomeka anyamata a mudzi mwa kwanthu ❤️🔥
Mwana owopsa zedi eeeeee❤❤❤❤ apatseni Moni boss munene Kuti Manuel Malunga atii Moni mumatha kuimba zedi❤❤❤❤❤❤❤❤
Choka iwenso mmai oipitsitsa...iwe ndi amene wakolezera malawi, kuthira parafin nkuyatsa moto...lero muli chete! Anthu akuwauka ku Chigwiri...😂😂😂😂😂
Ndaonaso legend Charles nsaku akupereka salute
Aise ulikuti ndikutumizire ya fanta..... Massively song osati ija atulusa asoja ija❤
Soja ndi chisiru
Soldier ndi achitsiru brother kuyambira kale
Ndiye mukumusaka waimba nyimboyi kuti watani ? Mukufuna mumuphenso anthu oipa
Umakwana brother ndipo mcp sidakawina ndipo live chakwera oipa moyo
Bwana wakuba Chakwera must be held accountable.
Good song keep it up Malawi now is in Bagamoyo
Kuimba kwabwino keep itup.
Ndi chilungamo wayimba mu nyimboyi ndiyebwslakwitsa pati,kumangomangana zili zonse,mwasowa zochita
Mbambande a very good song
Nice song 🔥🔥🔥
Chomusakira ndichani,akufuna amuphenso
Tinakunyadilani pa dzana paja poti munapha njobvu ndi buma. Ndipo timaona ngati ndinu munthu opemphera koma za ziiiiiiiii😢
Chakwera ndiwolotse chilima nkakutafune😢😢😢😢😢 rest in peace chilima
Kkkk nyimbo yabho kwambili no mantha ayi 💪💪💪🇲🇼
Tili mdziko la democracy. No kucheuka . Koma vuto chipan chamagazichi mmmmmmm. Koma God protect him
Ndaikonda ❤
Kumachangamuka town
This song need to be given award, song of the year award❤❤❤❤❤❤
Good song l ❤ loved it
Amakanika kusaka ndege azimusaka munthu kuti waimba nyimbo za nziii
Dyela pa chuma akuluwa ,anabwela kudzatizuza zedi.
My Banda dziko lija ndiye laphulidwa chilima alikuti amayi ?
The real definition of adani oseka
Malawi will never change
Foram Mozambike the Song is very good.
Nice song
My favourite song ever❤❤❤ eeeeee guys chilungamo ichi zedi❤❤❤❤❤
Agalatiya mwataya chipangano 😢😢
@@user-hq8nn1uq6n 😃😃😃😃Ndipo zedi brother
Very nice sony
Dziko la malawi likufunika anthu olimba mtima Ngati awaaaaa onena chilungamo ❤❤❤❤
Eeee ndiolose ndikakudyr
The real definition of chisoni chinapha nkhwali. Tatiye nkuwolotse anapereketsa moyo wake
Iwetu uhv done great session mulungu akudalitse waphaso njovu ndimwala
Keep up good work kuganiza mozama
I like this song its very nice
Sumu iwemi, mbweee ikuyowoya vinandi
Chirungamo chokha chokha mpaka afika pokupha anthu 9
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂koma ndafwaaaaaa ine koma yaaaaah 😂😂😂😂😂😂
Song of the year
Mwauze atume lamaphosa kuno azamange yine mumadana ndichilungamo bwanji zoti anthu napaka midzimu apeleka dzina loti gunda kamodzi zaziii amange bas
Pena ukamuvetsela malawi kenako kumazifutsa, tikupita kuti?
Amusaka bwanji ngati waimba zabodza?
Komatu lero wadyetsa MOYO WAKE saulosi chilima mayoooo
charles nsaku's apparentice😂😂😂😂😂
He has hurt us and brought down Malawi's money in silence
We once had Sidik Mia...we once had Chilima. May their souls continue resting in peace.
Sound yabwino. Koma vuto akhwitotowo Adana nayo nyimboi mpaka kumusaka kut aphedwe oimba nyimboi. Mmalo movomeleza kut dziko lawakanika. Awa kwao kwatha. Amene akusapota anthu awawa ndi amfiti sure
Fire Mabomba 🔥🔥
🎉🎉🎉🎉🎉 eya tinaivera kale
Keep on playing this songs facts are there u can not see pictures of the alliance day.
Man 🔥
Malawi yanukha
Eish man
Kuswa kuswa
Km Jomeca umatha kuzuzur ase kkkkk
Or kuidako nyimboyi uyambila pat...message on point, ma producers nawo anaigwira 😂😂
Iiiiiii ndiye azingosaka aliyese kkkkkk
Ilibwino ndithu
Well done boy, tell them
I like this song baibulodi ❤and muli mfundo zothyakuka
Kkkkkk eeeee waiswatu nyimboyi
Utsogoleri ukayamba kupanga zinthu zotero it means Alephera kutumikira Amalawi, Bible limati anthu Anzeru nthawi zonse akalakwisa amamva chidzudzulo
Azimayi athu ndi amene amatengeka kwambiri ndi zautsiru, mumve pansi pansipo ndemanga za azimayi , kumvomeredzana ndi mbavayi
Kkkk ndipo waiswadi nyimboyi man wa ndioganiza bho heavy😂😂😂😂
Komatu anthu muphana ku Malawi kuno 🤣funso lophweka koma lopasa chibwibwi.m’gwirizano uja uli nkhu? Ayankhetu😂😂😂😂
Umakwana malawi dyera misonko yathu ikukoma kudya
True bwana. Chinyimbo ichi mmmmmmmm! Ndaimika manja m,manja
I have enjoy so much
Mtima wazako ndi sidya Lina, ndiwolose kakutafune 😭😭 a Joyce Banda ndi azimzanu mwamuphesa mwana ndinu amene mumamukopa kuti achite geirizano ndi mbali ya akambukuwa. Enoch chihana ndinu amene munamupangisa chilima kupanga gwilizano ndi afisiwa Lelo mwana ali mmanda pomwe Inu muli kunjoya ndimabanja anu okay Koma mukuyenela kumenya nkhondo kuti uyu nayeso achoke pa mpando a Timothy mtambo mumve komwe muliko
Ndiolotse ndikakutafune indeed Rip SKC 😭😭😭