Amen Mary apume abale olo ine zinandibowa kwabasi kuwayankhula bwino akubanja Muthu akhudze imfa ya munake koma Ambuye amukhuze Mary muthawi yowawitsayi
Za candle sitisiya ndipo iweyo chikukhuza ndichani ngati Eni akewo akuti tilira mpaka kale kale nafeso ma candle tiyasa mpaka kale kale Chilima anali wandale ifeso tikulira malirowo mwa ndale ndiye zikukhuzani ndichani
Amen Mary apume abale olo ine zinandibowa kwabasi kuwayankhula bwino akubanja Muthu akhudze imfa ya munake koma Ambuye amukhuze Mary muthawi yowawitsayi
MHSRIP 🌹 may almighty God still xomfort the family to be strong ameen
Indeed we lost a strong man 🕊️😭😍
Ine usi yo akungondinyasa
Onyasa kwambiri ndiiweyo
Kulankhula motani. Nsanje basi. Whether you like it or not he's the vice president.
The Bible says respect your leasers.
ineyo zoti chilima anamwalira sindikhulupilirabe aaaaaaa😭😭😭😭
Exactly my dear
Nde pita ukamutenge komwe alikotu ngati sukukhulupulira
Ineso, kuvomeleza kuvuta 😢😢😢😢
zikomo@@user-rl2ko1zr9z
Nanga zot Yesu Khristu ndi Ambuye do you believe this??
Biyeni😭MYSRIP.
Skc 😭😭why? Only almighty God knows everything. Abieni 😭😭😭😭😭
Yamakenduloyo mukunama anthu sangasiye, Rest in peace SKC
We lost a strong man 😭😭😭
Mau abwino ndithu 🙏
I miss him already kulira kwake kaya mkumatan mmmh
Mukumva bwanji amagazi m'manja inu, simunati candlelight ija ikuotchani m'matako zenizeni, kupha anthu 9 ma million aziombela m'manja zopusazo in multiparty system of government, kale lomwelija chifukwa chipani chidali chimodzi, anthu chisoni mbiri yanu idzapindula chani padziko lapansi pano. 😢😢
Am still in denial
Amen indeed 😭 😭 😭
MWADYA BANZI INUUUU
Mtima udakawawabe ine 😢😢😢😢
😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Inu mkumayimba fon kwa Mary Chilima ndinu opusa zichepe zimenezo mkufuna mumutani zitsiru
Kunena zoona chilima anakhiyidwa , komanso munthu amene uja anatipwetekesa, koma sanachite bwino kumuchita chiwembu
Kumakana ndithu AAA osazamuyimbila phone my chilima ,musiyen alire malilo amwamuna wake
Hi
😭😭😭😭
Komano akubanja mwaiwala kutiko chilima anali ndani ... anthutu sasiya kupitako kumandako coz muthu uja anthu amamukonda
Ngopanda mantha chani, mmesa anali ndi asilikali mbweeee kuposa okafufuza ndege ya SKC and 8 others
Mukafatsakwambili chipanicha UTM chitha , akulu aja anali ofasa mozipweteka okha
Pumulani mwa Ambuye
Kwambili
Yama kandulo sikutha mpaka zaka 50 muuzane a MCP
❤
😭😭😭😭😭😭😭😭
😭😭😭😭😭🙏🙏🙏👍🕊️
Koma ngati sewero inu zoti chilima anamwalira mmmmmmmm
Muyaluka osamakayatsa pokumbukira Bingu wanuyo
Tilira mpaka kalekale
Ine siwandale koma ndimava kuwawa achakwera munaganiza Bwanji?
Uku ndiko kulankhula osati zomwe akulankhula azibusa opusa analowa ubusa chifukwa chosowantchito.
Zovu zed
Mau amphabvu kwambiri. Zikoma kwambiri
Gona bwino chimwene mabara mutima anakawawabe nzimu wako uwuse mutendere wosatha ame
DPP ili pa ganyu koma ikulenga kwambili
Manganya garu akuzatani😢mfiti
Zoonadi
Ngat bodza
But why a dpp people were there whalist they hurted this man called chilima that's funny
The people who hated chilima are the MCP people
Mwana wa nkaz wa achilima uli ndi mphuno yosefukila bwino kwambir
Awanso amakendulowa muwalese zomwe akupanga atsokoneza dziko, kulila aphatikiza ndi ndale
Aàaa makendulo alipo pakaaa
Kkkkkk wakutuma ken msonda 😂😂😂 mfiti imadana ndi mapemphero fire🔥🔥🔥
Iweyo ngati zikukunyasa zama candle usamazisate its not your business
Za candle sitisiya ndipo iweyo chikukhuza ndichani ngati Eni akewo akuti tilira mpaka kale kale nafeso ma candle tiyasa mpaka kale kale Chilima anali wandale ifeso tikulira malirowo mwa ndale ndiye zikukhuzani ndichani
Candle 🕯️🕯️🕯️ group
Muuzeni kalindo, ndi mtanyiwa apeleke ulemu ku banja misala yakeyo akapangile infa ya alomwe anzake,
Iwe Machende ako wamva
😂😂😂😂@@Tawina0101
😭😭😭