Chakwera watutumuka zomwe wanena wa Catholic mosaopa pa imfa ya Chilima

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 14 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 459

  • @Ybm-o5y
    @Ybm-o5y 2 місяці тому +35

    Powerful message,,,we silute you,,,, keep on doing this please

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 2 місяці тому +39

    I hope bishop mwatumidwa ndi mulungu ❤❤❤❤

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 2 місяці тому +16

    Mathembelelo akhale pamutu pa onse amene anakhudzidwa ndi imfa ya a Chilima ndi anthu 9 mwadzi wawo ukhesedwe pamitu pawo omwe anapanga izi Mudzina la Jehovah's...Amen..

  • @EdenEreneo
    @EdenEreneo 2 місяці тому +16

    Tsoka kwaiye anatengako mbali pa ifa imeneyi sazaona mdalitso Amen 🙏

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 2 місяці тому +25

    Mmmmmmm, koma a Bishop inu mwamaliza zonse, ndipo kumene aliko mutu waima Chakwera ndi boma lake la MCP. Tili pa mbuyo panu Bishop, osafowoka, osatopa .❤❤❤❤

  • @Ybm-o5y
    @Ybm-o5y 2 місяці тому +36

    I will vote next year because of chikangawa accident witnessed by my naked eyes,rest well my handsome VP SKC

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma 2 місяці тому +3

    Powerful massage father,mwatiyankhulira ndipo chakwera am sure wamva ndipo akudziwa kuti next year zake zada or atatani ndi manganya wakeyo mfiti zokupha zimenezi zikapume

  • @Geraldmkwewu
    @Geraldmkwewu 2 місяці тому +39

    Amen amen amve Mr chikangawa fiti

  • @ANYAMAINGATV
    @ANYAMAINGATV 2 місяці тому +12

    Tiyen tipitilize kuyatsa ma kandulo iziwapweteka daily mpaka kampen wao azakhare opanda mphamvu Amen🙏

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 2 місяці тому +12

    Ndipotu zoonadi ambuye kudziwike kuti kuli mulungu pa ifa ya athu amenewa ikhale panutu Pao ndipo china chake chichitike ndithu ❤❤

  • @Hellenistic109
    @Hellenistic109 2 місяці тому +6

    Thank You very much Bishop for the Wise Preaching,I Salute You..😢😢😢

  • @jjhollyland4918
    @jjhollyland4918 2 місяці тому +7

    We need this everyday. Men of God come out and preach the truth 🙏

  • @UsenLashid
    @UsenLashid 2 місяці тому +33

    Mawu amphavu kulakhula mosaopa munthu koma kowopa mulungu

  • @Creslevison-vj2sl
    @Creslevison-vj2sl 2 місяці тому +2

    Aaaa yes bishop watokota chilungamo uyu eshiii i lv the way he cud articulate the whole story fearlessly amidst mr chikangawa eshiii

  • @MaxwellChiwaya-tv7kn
    @MaxwellChiwaya-tv7kn 2 місяці тому +27

    Ine mpakana lero sindikumvetsabe kuti Biyeni anamwalira mmmmmmmmm only God knows

  • @TonychisalaPhiri
    @TonychisalaPhiri 2 місяці тому +3

    Uthenga usu ngati Chakwera sanawunve pls mutumizileni awunve.
    Tony Momadi.
    Johannesburg, RSA.

  • @NeemaMatewere
    @NeemaMatewere 2 місяці тому

    Powerful gospel,imfa yowawa ngati ya Yesu Christu,ngati yaa Martini Aku Uganda,ngati yaa Postoli
    Mtima woyera WA Yesu,mutichire chisoni,a Martini Aku Uganda mutipemphelerw Ife,woyera ose akumwamba mutipemphelere ife.
    Kuyankhula kulalika zomveka .Amen

  • @JoyceChaima
    @JoyceChaima 2 місяці тому +13

    Ambuye Mulungu odziwa kuweluza.... aweruze ndithu. MZIMU WA CHILIMA usowetse mtendere aliyense amene anatengako gawo pa infa imeneyi😢😢😢

  • @EstherChibwana-lp3gx
    @EstherChibwana-lp3gx 2 місяці тому +8

    Abig message to malawians I salute u bishop

  • @MirriamChakanza
    @MirriamChakanza 2 місяці тому +10

    Powerful message, wakuva wamva. Amen 🙏

  • @AmosKayira-y1m
    @AmosKayira-y1m 2 місяці тому

    Amen, that's why am proud of Catholic bishops! 🙏🙏 may his blood be like those of Martyr RIP SKC

  • @RuthMasamba-ms2di
    @RuthMasamba-ms2di 2 місяці тому

    Amen and amen, kma2 kudziwike ambuye kt mumatha

  • @MosesBanda-h4x
    @MosesBanda-h4x 2 місяці тому +1

    Very very powerful , may God continue giving you fearless speeches for Malawians to know the truth of God.

  • @chinomwephiri1183
    @chinomwephiri1183 2 місяці тому +5

    Amen, and powerful
    SKC, may your soul rest in peace

  • @ifristathope1131
    @ifristathope1131 2 місяці тому

    Amen bishop🙏🏿 chatsika blood on his hands. God gonna answer our tears. Osaopa osatopa n osafooka we need better Malawi for all not za sikusinjazi

  • @LuskaMoses
    @LuskaMoses 2 місяці тому +3

    Ambuye yesu akudakitseni Fathar😢😢😢choonadi chimamasura

  • @AlifeChiwanda
    @AlifeChiwanda 2 місяці тому

    Amen ndipo mulungu akudalitseni Muthu uyu chilango alandila ndithu mulungu sagona

  • @Hellenistic109
    @Hellenistic109 2 місяці тому +1

    Bravo Bishop Bravo tell them..They should know that people are watching..RIP SKC 😭😭😭💔

  • @MackdBanda
    @MackdBanda 2 місяці тому +1

    God bless you bishop the power of message

  • @JonesChilonga
    @JonesChilonga 2 місяці тому

    Very powerful message indeed Ambuye akudalitseni father

  • @HashimNyirenda
    @HashimNyirenda 2 місяці тому +43

    Uthengawu nde ndiwankaka ndi uchi

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 2 місяці тому +1

    ❤❤❤❤ bishop anga akutetezeni Yehova choona chidzatimasula ndiye ndiinuyo abusa, a bishop, onse kuunikira anthu anu amen

  • @JustinaKadammanja-u1z
    @JustinaKadammanja-u1z 2 місяці тому

    Powerful words chilungamo ichi

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr Місяць тому

    Kuiponda fadah. Kuipatsa Fire. OSAOPA, OSAFOOKA,OSATOPA.

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 2 місяці тому +2

    We love u bishop .......sitikhala chete ai paka mcp ichoke

  • @liz9425
    @liz9425 2 місяці тому

    Lord protect this pastor for us we want more of them to come out . SKC ❤

  • @stevenfrancism3638
    @stevenfrancism3638 2 місяці тому +2

    mzina la Dada nalamwana Nala mzimu utuwa . Amen.

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 2 місяці тому +7

    Amen. Pastor uthenga wamveka uyu opanda chilema

  • @lameckmbeza6532
    @lameckmbeza6532 2 місяці тому +1

    Straight to the point amen 🙏 prist

  • @Andrewmwamadi
    @Andrewmwamadi 2 місяці тому +1

    Once catholic always a catholic and our tears for our vp skc will never end until justice prevail

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 2 місяці тому +10

    chakwera wazimvera yekha ma umboni apose apo chakwera ndiwe chigawenga ndithu

  • @DoYouKnow3838
    @DoYouKnow3838 2 місяці тому +1

    What a powerful message 😢❤

  • @MaryAaron-nn8ec
    @MaryAaron-nn8ec 2 місяці тому +8

    😂😂😂😂Amen pastor and thank u for reminding us that we don't have a president 😂😂😂😂

    • @EstherDebwe
      @EstherDebwe 2 місяці тому

      Iiiih koma abale😂👐

  • @IanAllstal
    @IanAllstal 2 місяці тому +2

    Pachilungamo palibe Mantha ; osaopa .osafooka. osaopa . Koma tizafela mbendela iyiiih 👉🇲🇼🇲🇼🇲🇼

  • @JonesChilonga
    @JonesChilonga 2 місяці тому

    I love the Catholics they stand on the truth may God bless you all

  • @JeanBanda-zy6wu
    @JeanBanda-zy6wu 2 місяці тому

    Osawopa.... kuyankhula koma uku osawanyengelera awa aziuzidwa chilungamo evil people Ambuye achite nanu

  • @thomasbotha9790
    @thomasbotha9790 2 місяці тому +1

    Powerful preaching mau Amphamvu

  • @vivianmkwate8536
    @vivianmkwate8536 2 місяці тому

    Amen a Bishop tikulira ife Amalawi

  • @mussamapira801
    @mussamapira801 2 місяці тому

    Mwamvatu a chakwera ngakhale mukubisa umboni anthu akutopelani poti chilungamo nchowawa kuyamba kumanga koma mwa Allah mwini chisoni ndichifundo Ali nafe Ameen mwa Allah

  • @SangwaniNkosi
    @SangwaniNkosi 2 місяці тому +2

    Amen mtumiki wamulungu,chilungamo mwanena ndithu

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus 2 місяці тому +3

    Chakwera ndi mbuzi yachabe chabe ..ndichimunthu choipitsitsa pa zolengedwa zonse...matembelero a Mulungu,angero ,komanso onse amene amadziwa kutembelera akhale kwa chakwera oipa kwambiri😏😏😏😏😏

  • @WisdomPupweeMwalilino
    @WisdomPupweeMwalilino 2 місяці тому +4

    Our God will do it and make us move forward with grace.

  • @TonyMhone
    @TonyMhone 2 місяці тому +2

    Amen. Munthu wa Mulungu walalikira mopanda mantha.

  • @AndsonYusufChiwamba-jw3vl
    @AndsonYusufChiwamba-jw3vl 2 місяці тому +3

    Powerful message to Malawi 🇲🇼

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 2 місяці тому +8

    Achita bwino kulankhula ku tchalichi,,atidyenawo akwiya kuteleku,,koma ali mbuu,,

  • @misoMoyo
    @misoMoyo 2 місяці тому +5

    Munthu wa mlungu wayankhula mosaopa nae ndi okhumudwa ndi IFA ya bambo Biyeni

  • @Gwedeza-oz3jv
    @Gwedeza-oz3jv 2 місяці тому +1

    6:52 Kulankhula mosaopa osati enawa. Amalekeza wakuphayo chigawenga kamba Koti wapatsidwa ndalama , uwu ndiye utsogoleli osati abusa ndi asheikh ena Aja aaa anangoziwikiratu Kuti akugulitsa mawu aMulungu Kwa chikangawa (chakwera) ndi ntengo wotsika mukankhanthidwa patsiku lomaliza ndipo mukasowa kothawila ndalama mubazo sizikakuthandizani chifukwa kuzakhala kulibe,

    • @GraceMwase
      @GraceMwase 2 місяці тому

      Azibusa ena mzimu ndi mphamvu za Mulungu zinawachokela kalekale angokhala zitsiru kumakalandira ndalama kwa chakwera chigawenga chouma mtima ngati chimenechi chisatana

  • @MATTHEWSANDREWMANDUTU
    @MATTHEWSANDREWMANDUTU 2 місяці тому +4

    Mmmmmm achakwera muzivere nokha akuti tilbe tsogoleri nanga inu ndindani kodi?awa akutemberelani mufune musafune simuzalamulanso dziko lamalawi

  • @ChristopherChimbalanga-ez5he
    @ChristopherChimbalanga-ez5he 2 місяці тому +6

    Indeed chakwera next year azipita bas

  • @DENSONZULU
    @DENSONZULU 2 місяці тому

    The Catholics are very powerful 🔥🔥🔥🔥

  • @AllanChabwela
    @AllanChabwela 2 місяці тому +2

    Amen,mafunso alipo nmitima mwathu ambuye okha akudziwa

  • @KondwaniMbalu
    @KondwaniMbalu 2 місяці тому +1

    Koma ndizoona izi??

  • @martinnyirongo2892
    @martinnyirongo2892 2 місяці тому +4

    Amen and amen chauta akalange azibusa ena amene a kupanga nawo katangale muboma limeneli amen

    • @EmmanuelNgambi-y6h
      @EmmanuelNgambi-y6h 2 місяці тому +1

      Amen

    • @LukaAfromad
      @LukaAfromad 2 місяці тому +1

      Amen " Katangaleyo olo atamapanga km ine chikundipweteka imfa ya my favorite mzimu wake uwuse mumtendere mpaka kale😭😭😭😭😭💔💔

    • @GraceMwase
      @GraceMwase 2 місяці тому

      Ndipo akawafulatile asakawamverenso chisoni

  • @EllieMvoso
    @EllieMvoso 2 місяці тому +5

    Panopa zomabisa chilungamo zinatha mau awa ndawakonda kulakira kwabwino ndithu Bishop

  • @MasterBlack-r2n
    @MasterBlack-r2n 2 місяці тому

    Kulalika mosaopa. Koma chilungamo chokha chokha. 🇲🇼🇲🇼😭😭😭😭😭😭

  • @GiftMlinde
    @GiftMlinde 2 місяці тому +6

    🔥🔥🔥🔥🔥 Mr Chikangawaa uveee ndithuuu

  • @petroszgambo9949
    @petroszgambo9949 2 місяці тому +3

    Still can't believe our Biyeni is really gone forever 😢

  • @NedsonMatia
    @NedsonMatia 2 місяці тому +2

    Amen amen ntumiki anve zimenezi oyipau nfiti

  • @LukaAfromad
    @LukaAfromad 2 місяці тому +2

    Chilima Rest well 😭😭😭😭imfa yokhumudwisa kwambili

  • @fannyzimba149
    @fannyzimba149 2 місяці тому +4

    Amen indeed 😭😭😭😭😭 timenyereni nkhondo mulungu kumwambako

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 2 місяці тому

    I salute you bishop 🙏🙏🙏🙏🙏🙏

  • @lukepangani1373
    @lukepangani1373 2 місяці тому

    If there's change let's change for better Us Malawian

  • @EllinaBitto
    @EllinaBitto 2 місяці тому

    Awwwwwwu😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭Rest in peace Chilima

  • @JUBECKPHIRI
    @JUBECKPHIRI 2 місяці тому

    Mlalikiyu amatha go up mtsogoleri

  • @PidoMaganga
    @PidoMaganga 2 місяці тому

    Zandinvesa chisoni nkatolika kulilila mwana wake SKC😢😢😢😢😢😢

  • @SabeehaIbrahim-h1y
    @SabeehaIbrahim-h1y 2 місяці тому +3

    Amen Man of God

  • @MercyChiwaya-um6us
    @MercyChiwaya-um6us 2 місяці тому

    yes yes yes my vote will do

  • @HajiraMustapher
    @HajiraMustapher 2 місяці тому

    Koma ulaliki uwu 💯 perfect

  • @chipiesato-ut7hx
    @chipiesato-ut7hx 2 місяці тому +2

    Amen Amen powerful message ❤❤❤🎉

  • @edmiltontambala1393
    @edmiltontambala1393 2 місяці тому

    Uthenga wabwino n olongosoloredwa bwino ndithu.ambuye tithangatireni

  • @elsiekandiona7321
    @elsiekandiona7321 2 місяці тому

    Uthenga okhathamira bwino Amen

  • @TroubleMuthala
    @TroubleMuthala 2 місяці тому

    Ulemu wanu 🙏 bishop

  • @BlessingsCperumal
    @BlessingsCperumal 2 місяці тому

    Koma chikakagawa mene kunalili muja kuzizira mmmm kumusiya ndithu kukagona ambuye ngatidi mulipo ngatimuzabwerenso ndthu intervine your self

  • @MaryKhoropa
    @MaryKhoropa 2 місяці тому +3

    Amen, wakumva amve, osamva akhale?

  • @BwanaGD
    @BwanaGD 2 місяці тому +3

    Chibaluwa chawelengedwa kupita kwa babo chikangawa zivele mtoloooooo kuchikagawakooooo

  • @AlepharMakawa
    @AlepharMakawa 2 місяці тому

    Amen chikangawa akuva bwanji?kumene aliko munthu oyipa

  • @VanessaMilanzie-m2l
    @VanessaMilanzie-m2l 2 місяці тому

    Panyopako chakwera mr chikangawa fiti

  • @JonathanMsiska
    @JonathanMsiska 2 місяці тому +2

    Chowonadi chiwoneke abusa thank you.

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 2 місяці тому

    Chakwera ayerekeze kupha father uyuyu.chilungamo chikuyenda ngat madzi

  • @CathrineBizza
    @CathrineBizza 2 місяці тому +3

    Chikablngawa ipangitsa kuti ena aluze Zisankho ndipo zoxhitika

  • @KikaGray
    @KikaGray 2 місяці тому

    Mmmgh am intoxicated with this message

  • @NatashaBema
    @NatashaBema 2 місяці тому

    Mau mau Bishop mwalaliksa ndithu

  • @StelliaKuyokwa
    @StelliaKuyokwa 2 місяці тому +1

    Powerful massage

  • @PempheroMoleni
    @PempheroMoleni 2 місяці тому

    Uthenga wachoka kwa mulungu live anamutumizira utsiku live live fireeeee

  • @cellinakandevu
    @cellinakandevu 2 місяці тому

    I'm proud to be a catholic

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g 2 місяці тому +3

    Uthenga uwu umufikire chakwera nimumene anamuphera chirima

  • @PaulineKamwana
    @PaulineKamwana 2 місяці тому

    Popangira vn ndipati abale amzanga?Km chikangawa chakwera wazimva izi ?SKC rest in peace 💔

  • @PrinceGIdanah
    @PrinceGIdanah 2 місяці тому

    Eshiiih kuswa kuswa anthu atopa ndithu

  • @AlexNjanje
    @AlexNjanje 2 місяці тому

    That's what we call prophecy osati ndayankhula ndi Mulungu Mulungu wake utii eeeeee aaaaiiiiii Mcp 2025 boma ndiye kutii chani??? Awaa ndiye mau

  • @TeddySabawo
    @TeddySabawo 2 місяці тому +2

    Am proud to be a Catholic