Це відео не доступне.
Перепрошуємо.

MAYI UYU WAFIKA PA MAYI PATRICIA KALIYATI | INE MCHEWA WENIWENI WAKUKASUNGU NDIKUTI CHAKWERA AYI |

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 12 лип 2024

КОМЕНТАРІ • 77

  • @michaelkallyz2425
    @michaelkallyz2425 Місяць тому +1

    APM MY VOTE!!!!

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Місяць тому +5

    Yeah, zinthu zavutadi, koma pangani alliance ndi DPP, UDF ndi UTM, ndipo pasakhale mtsogoleri wa dyela, aliyense akhale ndi udindo mu bomalo.

  • @user-uf4db7im7d
    @user-uf4db7im7d 25 днів тому

    Make alliance guys the mcp has to be booted out

  • @georgengwira3152
    @georgengwira3152 Місяць тому +7

    Eeeeeeh kwachema MCP will not breath 😂

  • @KereeditseMotsetse
    @KereeditseMotsetse Місяць тому +3

    Afford simungawine olozitatani

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp Місяць тому +3

    Mcp yata munya chaka chamawa 2025 yasala pang,o achakwera you go 😂😂tatopa nanu 2025 moto 🔥🔥

  • @kingsleyhopematchaya5184
    @kingsleyhopematchaya5184 19 днів тому

    Mnchewa sanga

  • @AbrahamTembo-z5k
    @AbrahamTembo-z5k Місяць тому +1

    Izi ndi ndale zomwe a Malawi tikufuna. Osasankha munthu chifukwa choti amachokera m'chigawo cha kwathu, koma UMUNTHU. Let us practice ' DYNAMIC POLITICS.'

  • @user-ro1pl7rv7z
    @user-ro1pl7rv7z Місяць тому +4

    Respect anthu 14 Million omwe muli Pa Central Region 😅😅😅😅😅😅😊😊 😂😂😂😂Mwayankhura mosaona mtundu 😅

  • @user-xx4jb9se3z
    @user-xx4jb9se3z Місяць тому +2

    Koma kumeneko kkķkk mcp paulendo woza woza. Chikangawa yonse 2025 paulendo

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Місяць тому +1

    😂😂😂😂😂 komatu ndaseka mmmm madala awawa ndiyantunda mwambi oopsa kwambili

  • @user-lj7lm6ly7z
    @user-lj7lm6ly7z 21 день тому

    Afford ndikale inayamba kuphuphaphupha komabe kankhani basi mwina one-day is oneday

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 27 днів тому

    Indeee indeeee mu kwidzingeni momwe anakwidzingira anzake kuchita kupuntha ngati akupha njoka kupha Chilima

  • @user-iz5ui3xm4g
    @user-iz5ui3xm4g 27 днів тому

    Aaaah fundo zanji zimenezi NDE kulubwa lubwa

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Місяць тому

    Good Messnge

  • @AnnoyedBocce-ls5ob
    @AnnoyedBocce-ls5ob 29 днів тому

    Kkkkkk kumalawi madyera awa ndare simuzidziwa kkkkk

  • @MphatsoSimoko
    @MphatsoSimoko 23 дні тому

    iyi ndi nthano osati mwambih

  • @BambordKabambe
    @BambordKabambe Місяць тому +1

    😂😂😂😂😂 nyekhweeee

  • @christopherjere5001
    @christopherjere5001 Місяць тому +2

    Osaopa osafooka,imfa ya chilima imatiwawa kwambiri

  • @NaysonDayson
    @NaysonDayson Місяць тому

    🎉❤

  • @user-un8yq1gg2i
    @user-un8yq1gg2i Місяць тому +2

    Mwati bwanji pa msamphapo? Kkkkkk koma guys

  • @dawsonwaya4722
    @dawsonwaya4722 27 днів тому

    President mtumbuka,running mate mtumbuka ,hahaha zowina iwalani a aford,ngati mumazazana mma office mu mukapatsidwa mwai ,ndiye apa zizatani,woooo forget.

  • @MouriceMtubakachimay
    @MouriceMtubakachimay 28 днів тому

    Kma mzukambilanaso zowatsitsira fetelizer amalawi suger misinkho ma transport ndkubweletsa mankhwara mzipatala zose muno m Malawi ndpamene mzawone kut amalawi akukukonda mponda kukulodzan zala

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Місяць тому

    Chakwela you mast go

  • @LameckBanda-gk6ri
    @LameckBanda-gk6ri Місяць тому +1

    Boma ndi u MP chosavuta kuwona ndi U MP ngati kwanu sadakusakheni u MP nde akusakheni u president ndani ?

  • @user-jb5yb9wq3y
    @user-jb5yb9wq3y Місяць тому +1

    Tipange alliance guys

    • @HappyBirchForest-zy8nq
      @HappyBirchForest-zy8nq 27 днів тому

      Pangani afford, utm,udf,ndi dpp mose mukapasane ma udindo mumbomamo basi

  • @dinganinedsontchongwe610
    @dinganinedsontchongwe610 Місяць тому +1

    Mchewa weniweni amene ali Gausi wa aford

  • @WallyMsiska
    @WallyMsiska Місяць тому +1

    Chipani cha chilungamo

  • @SitheZulu-bi2jn
    @SitheZulu-bi2jn Місяць тому +1

    Chikuvuta Mcp kuvomeleza kuti ndiwolephela

  • @vincentkhunsanama584
    @vincentkhunsanama584 29 днів тому

    Ndale za kumalawi zikukoma kwambiri ma team apweketedwa ulendo uno😹😹😹😹😎

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw 27 днів тому

    Nthawidi yakwana yochosela chakwera

  • @user-qd7sz1pf1i
    @user-qd7sz1pf1i 26 днів тому

    Kuno ku kasungu MCP yathapo even agogo anga anazindikira pano

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Місяць тому

    2025 Boma ❤ good mayi

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg Місяць тому +1

    Koma chakwera ameneyi afa ndi bpp

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 Місяць тому

    Koma mchewa uyu .msampha utipweteka kunena chakwera koma chakwera wazionera

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 Місяць тому

    Koma adzimayi kuyankhula mosaopa

  • @chirwaellace1093
    @chirwaellace1093 29 днів тому

    MCP wazionera

  • @AronZayaweh
    @AronZayaweh Місяць тому

    Let us wait until 2025

  • @GiftJulius-ro9ev
    @GiftJulius-ro9ev Місяць тому

    Adyeleni..

  • @moseskavalo3304
    @moseskavalo3304 Місяць тому

    Mcp will go by the same way

  • @promisewataya3315
    @promisewataya3315 Місяць тому +1

    Mcp ili pa moto

  • @AginesiTheu
    @AginesiTheu Місяць тому +1

    2025 AFOD Boma

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu Місяць тому +1

    Nawoo moto

  • @mikesandali8425
    @mikesandali8425 Місяць тому

    Ku opposition nkowawa kwambili kkkkk

  • @user-lv4qd4pm1e
    @user-lv4qd4pm1e Місяць тому

    This man is mad mohi is it true kugi ku North sitimakondana mtesi uyu

  • @KereeditseMotsetse
    @KereeditseMotsetse Місяць тому +2

    Gwilizanani ndi DPP , UDF ndi enawa panokha simungawine

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h Місяць тому

    Nde ine ndmadabwa kwambir mumene zinthu zikukalira pano ena akusapotabe mcp,,,,,, ufiti chan

  • @Leonilde-wn4le
    @Leonilde-wn4le Місяць тому

    😂😂😂 koma abale😂😂

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda Місяць тому

    Chipani chakujinylthika makola,,not vyakutukna

  • @user-nf9od6ls5l
    @user-nf9od6ls5l Місяць тому

    Mwana wa Simbiyamoto moto kuti buuuu

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy Місяць тому

    Chakwera 😂😂😂

  • @ArmitageHardson
    @ArmitageHardson Місяць тому

    Kkkkkk km aford imandiseketsa

  • @user-jb5yb9wq3y
    @user-jb5yb9wq3y Місяць тому

    Katundu

  • @user-im7sc2my4w
    @user-im7sc2my4w Місяць тому

    Pitani ku alliance muchotse msampha

  • @user-im7sc2my4w
    @user-im7sc2my4w Місяць тому

    Kkk 😂😂😂 nonse andale ku satanic mumenyanako yooo

  • @user-ld8gb9xm7v
    @user-ld8gb9xm7v Місяць тому

    MCP paulendo

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of Місяць тому

    MCP sikuchoka boma enawa angobvutika

  • @mikesandali8425
    @mikesandali8425 Місяць тому +1

    Kambani mfundo idzi sidzikuthandizani

    • @user-uk3bz1hr5t
      @user-uk3bz1hr5t Місяць тому

      Ndale ndikuipisana Kaye amwene zinazo pambuyo,,aisetere kae MCP poti inaziyamba yokhaq

  • @user-wq9ex2sf3b
    @user-wq9ex2sf3b Місяць тому

    MCP yampa athu anzelu ndipo mairo achuluka mu Malawi

  • @UsenLashid
    @UsenLashid Місяць тому +1

    Ntchewa wazelu zamphavu zamphavu

  • @user-cf9yz3ei5o
    @user-cf9yz3ei5o Місяць тому +1

    Peter mutharika is. too. Old. listen malawians

    • @EmmanuelNgambi-y6h
      @EmmanuelNgambi-y6h Місяць тому

      Exactly,,,,, let's think about this

    • @spargomw
      @spargomw Місяць тому

      Tikufuna okalambayo coz Chikuni chachikulu chimasunga moto, achinyama nd awa akungopanga zoirawa.

    • @michaelkallyz2425
      @michaelkallyz2425 Місяць тому

      I think it's your kindaf thinking which is too old. APM, people's president!!!

    • @EmmanuelNgambi-y6h
      @EmmanuelNgambi-y6h Місяць тому

      APM idalephera kale