Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Mwazi wayesu uwayender kumene aliko god is power
Iyi ndiyabwino, osati zonyoza kupemphera zija. Keep itup!
Si mmangochi uyu muyao phili
Km mtola nkhan uyu ndi dolo mmmm iweyo umatha❤
😅😂😂😂 the guy is a good guy he deserves that 2,000 kwacha i hope you really sent. Hes very funny cant blame a guy for trying a man must be a man
@@HumphreysPodcast101 iwe ndi scammer uyo atha kubera agogo a khansa mmaso muli mbuu
Wayaluka satana wakuba uyu koma yuh wakhaulisa kkkkkkkkkkkkkk😂😂😂😂😂
😂😂😂😂 koma guys Malawi wa yaka Moto eiish Koma mtola nkhani weyo dolo big up
Kkkkk kutali ndi moto yesu akukhululukireni bana😂😂😂😂
😂😂😂😂😂yang'alulika nkhani ija wasataniki mpaka ndigaile 2 pini 😂😂😂Akut koma ndimaesesatu eti😂😂 Mmakwanila inuyo 💪💪💪💪
Member chabe oyimba ma phone😂😂😂simmene kuliri
Haha ati ndmagwilitsa WiFi poimbira phone call, 2 pin mpaka ndayesetsa kkkkk wasataniki uja kuno, milandu yake ya zii kkkkk
Zomba prison anakonza 😂😂
Kkkkkkkkk koma kandiwazaa eeish eeish ati uli ndende iti
Its sikuti ndanena kuti ndikupitatu for me😂😂😂😅🤣🤣
😂😂😂😂😂 Pitako kkkk
Miracle money ending up to 2pin 😂😂😂😂
Inu musakhulupilile ameneyu ndima guys osowa,zochita town mu amabela wathu pogwilisa tchito mau okut ndi asatanic
Watan
😂😂😂😂😂😂😂😂 anyway mwati alikundende pamenepo simnavetse😂😂
Koma ada awawa amatha ndipo ndi Dolo heavy 😂😂😂😂😂
Koma chintolankhani ichi ndichidolo😂😂😂😅mafusotu mwalamwala😅😅😅
😂😂 I'm surprised he wasn't talking more like mangochi guys
God is good always
😂😂😂😂😂😂 ai ndithu 🙌
CHDr saulos chilima
😂😂😂😂😂 Koma abale zovetsa chisoni bwanji kkk
Kkkk ndipo chisoni bwino ummmm
Koma amalawi mukafa ndithuuu🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
kumalawi nkobeba
AlljomoMom😊o pkhmbmMnm n
O Omooo N.mmmLook😅MoO
PoooM*😊
KoMo
I just like the way this conversation ended 😂😂
Pachibale umaziwa
kkkkk koma iyiyi ndi mbambande aise that's great
Kkkkk mbava Izi aaa tieni tilimbikila kugwila mchito
Koma we wachiyao sitizatheka kkkkkkk basi khemesi mpaka Pa home kkkkk
😂😂😂 koma munthu uyuyuu amatha mafuso awawa Mulungu amuthandize😂
😂😂😂😂koma ndaseka iiiiiiiih Mbava iyi ayifooketsa. Imagine mmene amayankhulira ine i was like izi nde zeni zeni koma kumapeteko iiih hahaha
Km abale ambuye atithandize masiku ano otsiliza😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Munthu omvetsa chisoni kwambiri akufunika deliverance
😂😂😂akaidi awa lol mbava chabe izo anangotutumuka ndmmene mutu akufunsra eh
Moti iweo Morton ku ntaja ukukuziwa? 🤣🤣🤣
Kkkkkkkkkkk koma abale zinazi ine pheeeee kumavera koma zomwe ndamva kumapetoku aaaaaaa😂😂😂😂😂
Zinayamba macheza et 😂😂😂😂😂😂 Nankha zichani zimenezo agent mpaka maluzi
Ine pheee kuvetsel km ndava kumapeto mmmmm ndafooka moti alikundende alipo aaaaa ambuye akhululuk km aaaa kkkkk zina ukava ngat uzililatu
🤣🤣🤣🤣
Koma ndaseka kumapeto kwake ndaseka wallahi😂
big up
Koma ndiyokoma ndaimaliza😂🤣😂🤣🤣😂🤣🤣🤣
ndiyinayakedi
Tapangan number yo ifeso timponyele kenakake 😂😂
Ndigayileni number yake ndimuponyele ya drink
Mbava iziii anthu osowa zochita
😂😂😂😂😂😂ati ningozikanda PAno blungete la biiii😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
That was a very honest confession.
Apapa nde atambwali ametana bas 😂😂😂
😂😂😂
Awa ndy ametana mipala yeniyenitu😂
Kkkkk atabwali mwakumana mzoonadi sametana
gyz izizi ndizabodza ndipo ndi mbava izi ndipo zabodza a satanic satumiza massage iliyose koma zimangochitika mwa automatic
😂ati koma ndinayesetsa eti kkkk ndafa ndiphwete
Inu wakumangochi sapanga za satanic koma akanakuuza zamankhwala🎉
Ati ndimagwilisa ntchito wi-fi 😂😂😂
🤣🤣🤣 milandu yake yaziii,,,kugulisa ti madrug
Miracle money went wrong 😂😂
ati 6 dabo 6
The devil will surely be exposed in these last days,let look only upon Jesus and be saved
😢
Kkkkk eeee koma ndaseeeka mpakana kumupephelela ukhale kutali ndimoto I like kuti zowona amaziziwa
😂😂😂 koma Peter Phiri wandiseketsa
😂😂😂. Koma akulu awa ali pavuto 😂😂😂😂😂
Tchimo limazunza 😢😢😢😢😢
Big mwabwera ndiyimeyi sopano
Wachiyawo wangalusa dzatheka bwanji kuluza nso?😂😂😂😂
mmmm ndiakuba chabe ameneo
Ndi Akayidi awa akubelani ndipo samalani nawoni
Kona umbuli ulibe mwini ndinthu 😅😅😅😅
Kwavuta🤣🤣🤣 next time baba😅
akayambirenso ameneyo
Kkkkkk this conversation made me to laugh
😂😂😂 ma feeling station
Iiiihii kom zinazi ukamamva😂😂😂🙌🙌🔥🔥
Wabodza uyu ndiwakuba ameneyo,,ndiaja amaba ndalama aja,,zabodza izi.
wagwa nayo iyeye
koma unakampasa 2pin imeneyo
Zachisisi zimabwela PA media?
😂😂😂😂😂😂😂 eh wapephaso 2 pin
Awa ngakuba aja awa wakumana ndi dolo mzake zoonetseratu kuti mbora
Mau a pilirani awo😂😂
mukuziwana eti?
@@mutafire I mean amafunsa mafunsoyo not mbalayo
Suja wa ku prison uja uyu amaba uja
Iyi ndi yabwino 🔥
Koma zandimvetsa chisoni kwambili Ambuye athandizeni ali ku Ndendeko.
😂😂😂😂koma abale kukuchitika zithu
Kkkkkk that was so funny 😂😂
Ku Capital Hill Konko😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂 uyu atha kupitisa business patsogolo , amatha kuyankhula. , wasatanic wa bwino
Anthu a ulesi awa... 😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅... Koma ndizonvetsa chisoni.
Morton ndy wati 😂😂😂
Koma kumapetoko ndaseka😂😂😂😂
😂😂😂😂😂 opitersen kuzombako 😂😂😂😂
🤣🤣ati ku Blantyre kuli chakuti chaine kom iwo sanachionepo
Mbava iyi ndikuidziwa
Olo ine ndikulidziwa zedi imeneyi 😂😂😂
Koma akaidiwa eeeeeeish 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Vuto akapita jon amakabela amalawi anzawo
Eeeh koma ka 2piniko katumizidwa 😂😂😂😂
Iwenso zokudya achule ndi njoka ku China wapitako zimatinyasa mesa wamba kudya galu ndi mphaka iwe
Bolan waziuluraaaaa😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Koma ndaseka 😂😂😂😂. Ish ma guys amu ndende wa😂
kkkkkk km yeah mumakwana mwamgwesa nayo
🤣🤣🤣🤣🤣 KOM YAAA
Wausilu ameneyi bwanji
Ati ukumveka kuti ukudya ndalama tu😂😂😂
ngati munthu ndalama zimachita kumveka
Ati ku Balaka sangaike filling station nka town kakang'ono
But at 1st he said alindi ma filling station each & every district here in Malawi so is Balaka not a district of Malawi?
Eish guys i like it crc
😂😂😂😂😂😂 eeee iwe umatha
Akukhululukile mulungu iwe 😂😂😂😂
Mpaka kumuseketsa wasataniki🤣🤣🤣🤣
😂😂😂😂
😂😂😂😂😂Koma Abale ndaseka
Wasatani kusekelela 😂😂😂
Amatha kukopa anthu
Mwazi wayesu uwayender kumene aliko god is power
Iyi ndiyabwino, osati zonyoza kupemphera zija. Keep itup!
Si mmangochi uyu muyao phili
Km mtola nkhan uyu ndi dolo mmmm iweyo umatha❤
😅😂😂😂 the guy is a good guy he deserves that 2,000 kwacha i hope you really sent. Hes very funny cant blame a guy for trying a man must be a man
@@HumphreysPodcast101 iwe ndi scammer uyo atha kubera agogo a khansa mmaso muli mbuu
Wayaluka satana wakuba uyu koma yuh wakhaulisa kkkkkkkkkkkkkk😂😂😂😂😂
😂😂😂😂 koma guys Malawi wa yaka Moto eiish
Koma mtola nkhani weyo dolo big up
Kkkkk kutali ndi moto yesu akukhululukireni bana😂😂😂😂
😂😂😂😂😂yang'alulika nkhani ija wasataniki mpaka ndigaile 2 pini 😂😂😂
Akut koma ndimaesesatu eti😂😂
Mmakwanila inuyo 💪💪💪💪
Member chabe oyimba ma phone😂😂😂simmene kuliri
Haha ati ndmagwilitsa WiFi poimbira phone call, 2 pin mpaka ndayesetsa kkkkk wasataniki uja kuno, milandu yake ya zii kkkkk
Zomba prison anakonza 😂😂
Kkkkkkkkk koma kandiwazaa eeish eeish ati uli ndende iti
Its sikuti ndanena kuti ndikupitatu for me😂😂😂😅🤣🤣
😂😂😂😂😂 Pitako kkkk
Miracle money ending up to 2pin 😂😂😂😂
Inu musakhulupilile ameneyu ndima guys osowa,zochita town mu amabela wathu pogwilisa tchito mau okut ndi asatanic
Watan
😂😂😂😂😂😂😂😂 anyway mwati alikundende pamenepo simnavetse😂😂
Koma ada awawa amatha ndipo ndi Dolo heavy 😂😂😂😂😂
Koma chintolankhani ichi ndichidolo😂😂😂😅mafusotu mwalamwala😅😅😅
😂😂 I'm surprised he wasn't talking more like mangochi guys
God is good always
😂😂😂😂😂😂 ai ndithu 🙌
CH
Dr saulos chilima
😂😂😂😂😂 Koma abale zovetsa chisoni bwanji kkk
Kkkk ndipo chisoni bwino ummmm
Koma amalawi mukafa ndithuuu🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
kumalawi nkobeba
Alljomo
Mom😊o pkhmbm
Mnm n
O
Omooo
N.mmm
Look
😅
Mo
O
Pooo
M*😊
Ko
Mo
I just like the way this conversation ended 😂😂
Pachibale umaziwa
kkkkk koma iyiyi ndi mbambande aise
that's great
Kkkkk mbava Izi aaa tieni tilimbikila kugwila mchito
Koma we wachiyao sitizatheka kkkkkkk basi khemesi mpaka Pa home kkkkk
😂😂😂 koma munthu uyuyuu amatha mafuso awawa Mulungu amuthandize😂
😂😂😂😂koma ndaseka iiiiiiiih
Mbava iyi ayifooketsa. Imagine mmene amayankhulira ine i was like izi nde zeni zeni koma kumapeteko iiih hahaha